Zili bwino komatu mukutisokoneza, Pati 13 inathera tonde Ali nyumba mwa anagumbo simunationesetu kuti zinatha bwanji achibiliti atamupezelela
@nkhalangomultimedia Жыл бұрын
Tathokoza bwana, apa zaonetsa kuti mukulitsatira kwambiri seweroli. Zikachitika chonchija nkhani imazapitilira either in the next episode or the other. Keep following. Thanks for the feedback and thanks for following. Kwatsala mutipange sponsor.
@AuntRuth Жыл бұрын
Kkkkk tonde emweyo😅
@malikazinajames-qq7bf Жыл бұрын
Kunoko kamunthu kamabodza ndi gaga hhhhhh
@nkhalangomultimedia Жыл бұрын
Mbiri yake yada basi, kkkkkk
@GODFREYMKWERA Жыл бұрын
Makware😂😂😂 🔥 🔥
@markchimpeni7819 Жыл бұрын
Gaga maboza akupwetekesa kkk
@kondwanimwamba6907 Жыл бұрын
After long Time
@rhodrickmpumila1820 Жыл бұрын
Atonde ndi akatundu omanga ndi mawaya
@herbartkaphamthengo9978 Жыл бұрын
Muderanji ulesi kukana ntchito kkkkkk
@bizwickmbwindinga9751 Жыл бұрын
Kom mukuchedwas kuponya
@futuremoyo5714 Жыл бұрын
Kodi atonde muna siya kutulusa ma video
@MBzoOvuta265 Жыл бұрын
Kodi zikuyenda bwanji Mesa tonde anamugwila ndi kazi wa achibiliti mu Episode 13 nde 14 ikubwelelaso ?komaso Episode 12 kumapeto ziveka analowa nyumba nde bwanj pano akuti kulibe akusauka .zikuti bwanji kodi?