It is very very difficult for the UTM to make an alliance again with the MCP and the reason it's not only that they've killed Saulosi Chilima but even before Chilima died the alliance was already broken and Chakwera openly said that he'll stand for the MCP as a presidential candidate in 2025
@KlokkieFielies2 ай бұрын
UDF AND DPP THAT'S WOLL WILL BE BETTER WE DON'T WANT MCP ANYMORE IN MALAWI .
@user-fh4pq9lu9d5 ай бұрын
Yes in politics there is no permanent enemy,UDF ,DPP, UTM can upset the tables.
@gasperJEllias5 ай бұрын
Dpp woyeeeeeeeeee with UDF. + UTM. 2025 mcp inya manyi.
@user-pv9uk6sc3w5 ай бұрын
MCP ndi chakwera akuchoka kale, palibeso kuwina apa, a Malawi akuzunzika kunjaku.
UDF,DPP, limoz yose boh bas,we coming back home yatopesa joz mavuto okhaokha kuno,uthenga kwa ma bg boss munthalika, boss young muluz timakunyadilan zoona ndizakut aMalawi akudila inu ma bg,enawa ayime kaye we go see them in future maybe, for know ndiinuyo ma bg pasogolo peter mbuyo atupele,mukumva kukoma mipanje,
@JimmyMoyo-b5i25 күн бұрын
U D F,DPP,UTM,nde bomalo ngat mukufunana Malawi ikhale ndi juice
@user-ln5hw7dn9g5 ай бұрын
Mukuti Chilima ndi mistake munampatsako mpata kuti alamule kapena ndi zomwe mumalota
I'll never trust any alliance , onsewa ndimbava zeni zeni ndipo alibeso phindu
@SmilingFishingRod-zc4wx5 ай бұрын
Chilima ndi chipani chale musyireni akhale nacho payekha Chilima ndiokanika ndipo ndiopsya mmaganizo Atha kupanga ubale koma DPP ikazalowa mmboma mumuona azagalukilanso mmutu mwa Chilima simumayenda bwino
@user-jf3kv3jl2h5 ай бұрын
Ndip kwambiri ayiwala kale kt chilima ndioyipa mtima
@user-zf4ij4vs3d5 ай бұрын
Dpp ukulowa m,boma awa alephela basi ayenela kuvomeleza
@Kasawalah5 ай бұрын
Yes ndizoona zizacitikadi mukunenazi
@user-sf9vn7ml7s5 ай бұрын
1:32 Mcp ndi UTM akuyenela Kuykendala be limozi asaiyane
@IssahAluba2 ай бұрын
MCP sitikuifuna lokoitatheratu
@PaulChaleka-lb4vx3 ай бұрын
50+1adzapangitsa kt alliance ichitike chifukwa Pali be adzapeze 50+1% koma chakwera ndi khuluku
@user-qv4ko6ps4j5 ай бұрын
Mgwilizano wa DPP, UDF and UTM ukadzangiwina mu 2025 mkuyamba kulamulila mmmmmmmmmmmm Chakwela ndi nduna zake tidzambwandila ngati nkhuku wa ku prison because aononga misonkho ya a Malawi ndie tidzafinya banja lonse la Chakwela,,,,,,adzabweze zathu
@NgomaRaheem5 ай бұрын
Awona nyenkhwe sanati akang'wing'wiwo
@user-jn9tz3li3v5 ай бұрын
Chilima ndiwozikonda kwambiri koma is half ground ndi MCP
Ndipake DPP ndi UDF kupanga ngwirizano zikhonza kuthandiza ziko lamalawi akazalowa m boma koma azaonese chisanzo cha bwino
@abdulrafiquekalembo4695 ай бұрын
UTM ikhale komko kwa a Satana aliko.Ife DPP+UDF+Aford we can agree. UTM not good guys
@HarrisonMwanga-xy4sc5 ай бұрын
Atsitse katundu ngati satelo achoka ndipo Malawi tikati no is no.
@user-fm8ed7eo3i5 ай бұрын
Zoona UDF ndi DPP, or Aford ndi zotheka kale koma a UTM muganidze did bwino muchoke ku meneko pangani igwiridzano kuti MCP ifeletu, sitikufuna anthu ozingonda
@user-ky4ce9gb6j5 ай бұрын
Ndipo kwambiri
@user-pj3rf4rn9w5 ай бұрын
Koma zoona chilima mukumufunaso ine ayi
@SelisonChamba5 ай бұрын
Zosezi ndi udyera mwala oyendayenda suyanga ndere
@AhmadumkomaTambala-lr9gp5 ай бұрын
Tinene zoona DPP ndiyodekha Komanso gwilizano wa UDF ndi DPP bwanj akumvana mpaka lelo stinanvepo kut eeeeee❤❤❤❤
@RaphealKwelani3 ай бұрын
Wapenga matumbiyu akufunako ndalam😅😅😅
@RaymondKaumbaАй бұрын
80yrs wakalamba mdalayu
@KassimmwSteven-og8ny5 ай бұрын
Apa zikuyendera KUt chilima abwerere zachitika manyazi kuziko izi