VERA KAMTUKULE NDIPATSENI 20 BILLION NDIGWIRITSE NTCHITO KUTSATSA MALAWI GOTANI NDIYIMILIRA AMAYI |

  Рет қаралды 19,309

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 89
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 2 ай бұрын
Jelas anthuwatu sakumagona ndi blue 💙💙💙💙 APM my my vote ndipo awawidwa sanate achakwera komwe aliko akungoti vwevwevweeee zipwisi kudwalika mumimba ndi sanje yopanda phindu😅😅
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 ай бұрын
Mahule akulamulira mmabwinjamu....mbuzi ndife amalawi we allow mbuzi to be leaders
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 ай бұрын
Vela kantukule panyopako wanva anthu azidya zimenezo??? Hule iweeeee
@jameskadete2196
@jameskadete2196 2 ай бұрын
Palibe chanzelu Mami 20 billion ndarama zachuluka ndalama zimezi simuzinyatha mama
@LeterbJime
@LeterbJime 2 ай бұрын
Vela kantukule adwala misala
@officemoyenda-rj2hz
@officemoyenda-rj2hz 2 ай бұрын
Jona ndi good news presenter; nice voice and audible enough
@AdamAhamad-k2i
@AdamAhamad-k2i 2 ай бұрын
20 billion yachani iwe Hule kumalawi kuli njala gulani chimanga muwapase anthu amene akufa ndinjala zakumtumbo eti
@RoydNamphandu
@RoydNamphandu 2 ай бұрын
Kmatu vera vera . Njala mmene ililimu ndalama mkuonongera zimenezo
@Kamwachale
@Kamwachale 2 ай бұрын
If Malawians were sensible enough, this parliamentary sitting coul be an interim one because the legitimate one ended in May 2024
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem 2 ай бұрын
Pamene anthu akufa ndi njala iwe uli busy zampila; we ndiye ukukhuta kodi mzelu zobela amalawizi mukumaka mpumzila Ku college ya u Ka chenjede eti! Titseka ife college imeneyo.
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 ай бұрын
Ambuye tithandizeni pamene pafika Malawi anthu amawudindo sakusamalanso za njala , mavuto komanso umphawi uli mdziko muno nanga 20 billion yongogulisa Malawi pomwe ena akugona ndi njala
@HuzaifAbdullah-m6s
@HuzaifAbdullah-m6s 2 ай бұрын
Chimanga kulibe kukagula laber Ya uniform 😂😂😂😂😂 Malawian
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 ай бұрын
Anthu azifa ndinjala
@GiftNkhoma-n2w
@GiftNkhoma-n2w 2 ай бұрын
Khope ngati malungo mai inu 😂😂😂😂🚮🚮🚮🚮 😢😢😢 Zoona anthu akufa ndi njala kuno 😅😅
@MoosaChirwa
@MoosaChirwa 2 ай бұрын
20 billion osangogulira fertilizer Kuti muthandizile anthu akumudzi osowekera basi inu busy kulongosola zampira Kodi munthu angasatile mpira Ali ndi njara m'mimba Mitu yanu sikugwila akamtukule banja simungasunge ndinu akape
@JamesMadina-uv6xe
@JamesMadina-uv6xe 2 ай бұрын
50kg thumba lqchimanga 😢😢😢😢😢😢
@innocentissah2636
@innocentissah2636 2 ай бұрын
Tatengani 20 Billion yo mugule chimanga anthu azidya.
@ArmsonMalikhwa
@ArmsonMalikhwa 2 ай бұрын
Komatu anthu akuvutika ndi njala bwanji zogula malayazo mukanazisiya kae.
@IbrahimJackson-i8h
@IbrahimJackson-i8h 2 ай бұрын
20 billion misala chani anthu chakuja alibe moti akagule chimanga apase anthu, koma akagule malaya zoona abale ai chipongwe kobasi 😢😢😢😢
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
Ndipo uchitsirutu, amalawi afika popanga sponsor ma team a kunja?, njala ili thoh, mankhwala ku chipatala kulibe. Akidi akugona ndi njala, ndende za dzadza. Angofuna pobela ndalama awa a MG2 wa basi.
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 2 ай бұрын
Koma ku parliament kuli wosusa boma?
@Kamwachale
@Kamwachale 2 ай бұрын
This is illegal parliamentary sitting.
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 2 ай бұрын
Kaliya ukuyankhurira mcp iwe
@emmanuelhassan-v1s
@emmanuelhassan-v1s 2 ай бұрын
Useless minister, 20 billion for what?
@PayesaPatrick-px1ob
@PayesaPatrick-px1ob 2 ай бұрын
Panyopanu a MCP inu Akupha
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 ай бұрын
20 billion imeneyo kagulen chimanga athu akufa mmalawi Muno Za uhule bas
@BoosterItika
@BoosterItika 2 ай бұрын
Komatu Akatukule osayamba kunkonza Kaye mavuto tili nawo muno bwanji musaiwale bwana ananena kuti maboma 28 akhala pa njala .
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 2 ай бұрын
Zaugalu basi amuziwe malawi ndani osagula chimanga anthu akufa ndinjala kumudziku komatu afitsi inu mwafatsadi kubomako
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem 2 ай бұрын
Chakwela akamalakhula chizungu ngati ndiyemweyo koma ayiii si uyu.....
@MadalitsoIbrahim
@MadalitsoIbrahim 2 ай бұрын
Malawi pano siwobisikanso ayi, muzangogwesa ndege muja matchukisa malawi basi
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Ziko loyendesedwa ndi mbava komanso zigawenga .......agalu awa atikwana ... ...George chaponda mugwileko ntchito yabwino ku parliament
@MoosaChirwa
@MoosaChirwa 2 ай бұрын
Katunduyo wazaulimiwo unabedwa bwanji Malo Ngati amenewo palibepo azilonda mbava ndinu nomwe musamanamizile anthu ma solar panels abedwa bwanji katundu wa ndalama zambili sipangalephele kuikapo azilonda
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 2 ай бұрын
Mmmmm zimayi opusa uyu zed malaya ndye chan anthu akufa ndinjala kumizi
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 2 ай бұрын
20 billion ya chani imeneo akufuna adye chani akufuna kuba ndalamao mbamva imeneo asaipaseso ndalama kod mukufuna mumpase hule la chabe chabe anayambapo wapangapo za sports galu ameneo kungofuna kuba ndalama chani za usilu
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 2 ай бұрын
Zimenezo akunena amuna ake a Chakwera amupatsa ndipo zichitika.
@maxwellmashon4897
@maxwellmashon4897 2 ай бұрын
Uyu wamva ambuye mtengeni
@Noel-y6t
@Noel-y6t 2 ай бұрын
A Kantukule nkhani ya njalayi mwaimva koma?
@GogoChigome-us2no
@GogoChigome-us2no 2 ай бұрын
Ndalama imeneyo agulile mankhala mu sipatala chifukwa mulibe mankhala komaso kuganisa iweyo kamtukule kuganiza kumene kuti uli ndi abale anuso amadwala kuphita ku chipatala ukuyika manyado tikusauka chomchi
@clarkebrink4282
@clarkebrink4282 2 ай бұрын
Mwawonatu vuto lotsogoza azimai😂 20 billion mmmmmmm
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 2 ай бұрын
Athu ose ango oneka mdima palibe zimene mwachita jelesi basi mubwezeletse kungo sonyeza kuti chipani chakumidima chikangawa kudana ndi kuunika zalu ija imawa otcha
@Mainje-jr4pl
@Mainje-jr4pl 2 ай бұрын
Kutaya ndlama pongofuna kuonetsa kuti iwo ndi a kongels...kaboma aka nde ayi
@Mickeykasambula265
@Mickeykasambula265 2 ай бұрын
Koma amalawi ife tili pamavuto kwambili ,,,
@EDGARMPIKAMEZO
@EDGARMPIKAMEZO 2 ай бұрын
Pankhani ya ku nyumba ya Malamulo concerning za change of seat covers colours it's useless excuse. We as voters are just stupid to you heartless politicians. Remember you are not forever but malawi will remain forever...
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 2 ай бұрын
Kufuna kwanu kuchitidwe Rip saulos chilima
@BillyChunga
@BillyChunga 2 ай бұрын
Mipando siikuoneka bwino ai bwezeletsani blue
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Mipando ya blue ija imawala mwachotseranji? Iyi mukuooneka mdima mu parliament bwanji koma inu chikangawa?????
@babranzima8120
@babranzima8120 2 ай бұрын
Zoona mlindizeru zinenezo mene njala ili mziko Muno inuyo ukudya bwino
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 2 ай бұрын
Mipandoyo sikkongola bola Blue emwe uja simu kuwala mungo oneka dima
@EfeloYovita
@EfeloYovita 2 ай бұрын
akantukule simungapakambe za njala yomwe yafika posauzana koma anthunenawa
@CkayBBanda
@CkayBBanda 2 ай бұрын
Malaya achan?anthu akuzunzika 😢kusowa chigoba chenichen mmaso mwanu 😅
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 2 ай бұрын
Pangani zanu inu a MCP osalimbana ndi azanu
@henryphiri6100
@henryphiri6100 2 ай бұрын
Amalawi anachenjera akudziwa zomwe akufuna.nkhani yamipando singasinthe chilichonse.adzaona mzimu wa Chilima udzagwira ntchito
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk 2 ай бұрын
20b yachani.....mmmmmm azitsogoleri taganizilani moyo WA anthu akumudzi chonde.....tapelekani ku ma company ndalamayo kut katundu atsikeko chonde
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 2 ай бұрын
Section 65, sigwira ntchito ku Malawi kuno
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 2 ай бұрын
Malawi azikonze yekha Kaye.Miseu ndi zigwembe zokhazokha olo tourist wake azichokera kuti.
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 ай бұрын
angonena kut nsalu anakutila mipandoyo sakuyifuna chigukwa ndisalu ya DPP sifetu ana mwamva
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Ndipo ndi Zoonadi anthu awa ndi woyipa mwamva, nde omwe ayika o chidima mu parliament blue uja amadwala 🙌🙌
@benjaminjobo3525
@benjaminjobo3525 2 ай бұрын
Mbuzi yaminister 20billion anthu akufa ndinjala
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo 2 ай бұрын
Kkkkkk koma iwe koma m,mutu mwako muli bwino koma 20billion mukufuna muigawane ilowe m,matumba mwanu ngati momwe munaziika gawanila ndalama ya ulimi kkkk mwalo mogulila makwala mzipatala
@CardoJustin
@CardoJustin 2 ай бұрын
Zabodza nsalu mpaka yachipani MCP
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 2 ай бұрын
Iwe vera ndiwe opusa kwambiri anthu akufa ndi njala kuno agalu inu mwatasa ku bomako eti
@rashidadan2533
@rashidadan2533 2 ай бұрын
Chitukuko chomwe wabweletsa chakwela , ndikusintha msalu yamipando ku parliament zandalama yokwana 98 billion malawi kwacha , After atakwela njinga ku German
@MercyChimaliro-fi6mv
@MercyChimaliro-fi6mv 2 ай бұрын
Kkkkkkkkkk😂😂😂😂😂😂
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga 2 ай бұрын
Kkkkk
@AubreyWilson-j8w
@AubreyWilson-j8w 2 ай бұрын
Kamture wafuna kuba
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 ай бұрын
Mmalo mokonz dziko ziii
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 ай бұрын
Why not put tarmac roads going to national parks and game reserves etc nstead of football
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 2 ай бұрын
No pasiain
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 ай бұрын
Opposition yogona kuli makape okhaokha yaluzaso
@EvelineGalion-vw9bc
@EvelineGalion-vw9bc 2 ай бұрын
Waludza ndwe kape
@DesmondChavula
@DesmondChavula 2 ай бұрын
Fundoless
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 2 ай бұрын
indedi angonena kuti amaziwa kuti salui ndi mtundu wa dpp
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 ай бұрын
Koma mayi iwe
@SueWahna
@SueWahna 2 ай бұрын
Asanene kut asitha idali itatha akanagulaso yangat achosayo asatipusise
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 2 ай бұрын
Mcp ma devils okha okha
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 ай бұрын
Yaluzaso dpp
@MakabaBauleni-c2i
@MakabaBauleni-c2i 2 ай бұрын
Kma kabwila ukulimbana ndi Dpp bwanji osamangopanga zako bwnji iwe cisilu eeti
@EdwardChapola
@EdwardChapola 2 ай бұрын
Ndizoona
@VirginiaPaulino-xc8ph
@VirginiaPaulino-xc8ph 2 ай бұрын
Atenge ndalama Yanyumba mwake Fotsek
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 2 ай бұрын
Chitukuko chake chikhala choyitana ma player a man u?
@hardworkkayuza6353
@hardworkkayuza6353 2 ай бұрын
Za chamba 20 billion utenge yako upangre zakozo
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 2 ай бұрын
achedwa nazo
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 2 ай бұрын
Tilibe utsogoleli koma mbuzi mbuzi zokhazokha anthu akusowa mankhwala ndi kumaniti chani?useless lerders
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 ай бұрын
Mmmm
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 ай бұрын
Ambuye tithandizeni pamene pafika Malawi anthu amawudindo sakusamalanso za njala , mavuto komanso umphawi uli mdziko muno nanga 20 billion yongogulisa Malawi pomwe ena akugona ndi njala
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 ай бұрын
Ambuye tithandizeni pamene pafika Malawi anthu amawudindo sakusamalanso za njala , mavuto komanso umphawi uli mdziko muno nanga 20 billion yongogulisa Malawi pomwe ena akugona ndi njala
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 ай бұрын
Ambuye tithandizeni pamene pafika Malawi anthu amawudindo sakusamalanso za njala , mavuto komanso umphawi uli mdziko muno nanga 20 billion yongogulisa Malawi pomwe ena akugona ndi njala
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 ай бұрын
Ambuye tithandizeni pamene pafika Malawi anthu amawudindo sakusamalanso za njala , mavuto komanso umphawi uli mdziko muno nanga 20 billion yongogulisa Malawi pomwe ena akugona ndi njala
General Election 2024: What's in store for education?
1:00:06
The Sutton Trust
Рет қаралды 2,1 М.
Malawi appoints Dr Michael Biswick Usi as Vice President
6:54
SISTER EXPOSED MY MAGIC @Whoispelagheya
00:45
MasomkaMagic
Рет қаралды 19 МЛН
ПРЯМОЙ ЭФИР. Золотой мяч France Football 2024
4:41:06
World’s strongest WOMAN vs regular GIRLS
00:56
A4
Рет қаралды 5 МЛН
Это было очень близко...
00:10
Аришнев
Рет қаралды 6 МЛН
President van Georgië vindt dat verkiezingen oneerlijk zijn verlopen
2:54
Hulp Gaza wordt nog moeilijker, Israël verbiedt hulporganisatie
2:59
NOS Jeugdjournaal
Рет қаралды 22 М.
The REAL Story of Kamala Harris
26:04
Johnny Harris
Рет қаралды 1,4 МЛН
School Days Movie( Official 4Kaya Filmz)
1:14:14
4kaya Filmz inc
Рет қаралды 1,3 МЛН
SISTER EXPOSED MY MAGIC @Whoispelagheya
00:45
MasomkaMagic
Рет қаралды 19 МЛН