VICTOR MUSOWA WAMANGIDWA KU BLANTYRE KAMBA KOLANKULA MAU OYAMBITSA ZIWAWA KU NDIRANDE DPP RALLY

  Рет қаралды 9,780

AM TV MALAWI

AM TV MALAWI

Күн бұрын

Пікірлер
@MussahMussah-p9n
@MussahMussah-p9n 18 күн бұрын
Kd azikwanje ajanso awamanga??
@MathewsMakina-z6n
@MathewsMakina-z6n 19 күн бұрын
Apolice a Mcp tiwonana 2025 mudzaithawa Ntchito mukuifuna
@BysonTuwanje-d8d
@BysonTuwanje-d8d 19 күн бұрын
Thawi mkachitsilu izizi mudziwe kukanika kumanga azikwanje mukamanga musowa manyazi mulibe
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 19 күн бұрын
Milungu akuziwa zose
@LysonMkomadzinja
@LysonMkomadzinja 19 күн бұрын
Apa nde DPP ipeza mavote anyoooo iiiiii
@fatsanibanda5733
@fatsanibanda5733 19 күн бұрын
Good news
@symoldicky
@symoldicky 19 күн бұрын
Pali good news apa? Kod adzikwanje aja alikut sakumangidwa. Nanga chimwendo naye amayankhula koma samangidwab. Y ? Kod lamulolo lidzigwila mbali imodzi?
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 19 күн бұрын
Anthu opusa inu.
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 19 күн бұрын
Ndigwilizane ndi azanganu kuti amumanga cifukwa ndi wa oposition, akanamumanga cifukwa cofuna kuyambitsa cisokonezo akanayamba kumanga adzikwanje aja, koma cifukwa dzifwamba zija ndiza manyaka congres party (mcp) ndicifukwa sidzidamangidwe. Ndicifukwa timati police ndi ya mcp osati a malawi simwaona.
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 19 күн бұрын
Mulingo onyenga unyansa Yehova.
@KasembeJames-h5e
@KasembeJames-h5e 19 күн бұрын
Kod zimayi ameneyi ana ngomphuzila zomanga a Dpp ndizipan Zina zosusa
@GraceMvula-x3n
@GraceMvula-x3n 19 күн бұрын
Osamangako aja ankachita kunena kuti Peter asowe kapena asasowe aja bwanji ankatanthauza chani
@MagieJames
@MagieJames 19 күн бұрын
Osamanga anthu azikwanje aja bwanji anapita ku parilament kuja bwanji
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 19 күн бұрын
Panya panu apolice nonse amen mukulora kumatumidwa ndi andale
@WilsonMbendela
@WilsonMbendela 19 күн бұрын
Makape osamanga azikwanje aja bwanji
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 19 күн бұрын
Kkkkk kusowa zowauza wanthu a dpp. Zamanyazi ndithu
@DesireLuka-nf5is
@DesireLuka-nf5is 19 күн бұрын
💪💪💪💪💪💪💪💪💪
@IvyChithyoka
@IvyChithyoka 19 күн бұрын
Akamangeso a zikwanje kkkkkk
@GuejendraMk
@GuejendraMk 19 күн бұрын
wapasidwa belo masana ano
@IvyChithyoka
@IvyChithyoka 19 күн бұрын
Koma azikwanje bwanji?
@MikeJuma-q1j
@MikeJuma-q1j 19 күн бұрын
Kod azanu akangopangisa nsokhano bas kuwamanga zisilu za mcp
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 19 күн бұрын
Eish dziko losakoma ili
@DaimanAbwanja-h8h
@DaimanAbwanja-h8h 19 күн бұрын
MUSACHEDWE NDIKUMANGANA ULENDOU NDIWAWUTALI INGOSUNGANI UMUNA WANU.PANDALE SITIMAMANGANA NDIYE UKAPE UNENEDWAO UMENEWO.AVICTOR ATULUSENI
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 19 күн бұрын
Zisru za police malo mopita kolimbana ndi Mai Suluhu ku Tanzania muli busy zaziiiii mupheni musangalare akanayankhula wa MCP ndye kokhalirako mbeeeee police my foot
@AlicksonMakata
@AlicksonMakata 19 күн бұрын
Ayenera kumangidwa chifukwa akuipitsa dzina la ndilande .
@BysonTuwanje-d8d
@BysonTuwanje-d8d 19 күн бұрын
@@AlicksonMakata anathamangitsa kumkuyu Anja nga ku chirobwe?
@JackMvura
@JackMvura 19 күн бұрын
Achikhaulitse chimenechi chopusa maningi DPP zamanyi angolipira ndalama zochuluka ameneyu chinkhumba kusasamba kuli tho ndakulira ku ndix ine makape samasamba ngati iyeyo
@ElsaMalunga
@ElsaMalunga 19 күн бұрын
Kd azikwanje aja arikuti kd mukufuna anthu aziopa km ifenso tiri ndi maso timaona ok mwamanga cz kungoyakhura ochita zithu ndi opanga oyenera kumangidwa zopusa ayi kunari azanu mwatsara madzi angati muona
@OscarKathumba
@OscarKathumba 19 күн бұрын
Choncho muziti tizakuvotereni
@FellenMwale
@FellenMwale 19 күн бұрын
Good news uyu amangidwe bas cz tonse ndife amalawi
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 19 күн бұрын
Anthu ena anazolowela khondo basi mutsogeleri kuyakhula zimene zingapangitse kuti anthu azidana
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 19 күн бұрын
Mukanangomupha koz atulukako zakumtumbo basi pakhol pako pamakoso garu iwe umafuka udzidzitenga ngt ndani panyero pako chsru chamunthu ungokhala ngt sunatulukite kuthako kwamzimayi bwanji pamtumbo ponyasapo
@symoldicky
@symoldicky 19 күн бұрын
Kkkkkk bola munakati malawi ngwa a mcp okha cuz adzikwanje kawili kose osamangidwa chimwendo nayeso amalankhula zonga zomwezo koma samangidwa nde tizit malawi ngwatose chosecho ena ali ndi ufulu ochita nkulankhula osamangidwa
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 19 күн бұрын
Eee bola azikwanje anu aja hetii
@BeautyBlack-ls5pg
@BeautyBlack-ls5pg 18 күн бұрын
Good news yambwiyako hule iwe paliwepo njala ili thoo nyumba mwako galu iwe mukhaula tionana kovota agalu inu
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS 19 күн бұрын
Kodi adxikwanje aja mwawamanga komaso chakwera okuphayu osamumanga bwanji Nthu inu mmm ayi zkm mulungu akudxiwa zose
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem 19 күн бұрын
ameneyi ndi kape kwambiri!!!! kwacha tipanga palipose wina afune asafune !!!!!!! ife sitikusintha
@symoldicky
@symoldicky 19 күн бұрын
Inuso nde akpetu kod ufulu olankhula ndikuchita zinthu uli ku mcp kokha? Adzikwanje kuli ziii palibe wamangidwa kawili konse chimwendo naye amayankhulaso y apolisiwo samamumanga?
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 19 күн бұрын
Kwanu konko
@YamikaniMsosa
@YamikaniMsosa 19 күн бұрын
Muzit ine osati Ife mwagwirizana ndani 😂😂😂 mdichosa boma la umve ngat ili
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem 19 күн бұрын
@YamikaniMsosa iiiii tilipo gulu man tikudziwana kupatulapo iweyo ndi dpp yonse mix afford 🤣
@YamikaniMsosa
@YamikaniMsosa 19 күн бұрын
@PatrickFicklem let's wait and see ndipo ubwino wake munalowera ma demo muzachosedwaso ma demo momwemo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 19 күн бұрын
MCP police my foot abwerekotu wamoyo kumeneko tiyeni tikalandise nyanja uko sizaziiiiiii zmwe mukupangazo nonsense police
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 19 күн бұрын
This is typically nonsense
@Mutisunge-p7o
@Mutisunge-p7o 19 күн бұрын
such evil campaining words then you say it is good well done our police musungeni uyo basi
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 19 күн бұрын
​@@Mutisunge-p7omwauze amuphe musangalare
@symoldicky
@symoldicky 19 күн бұрын
​. Kkkkk welldone mcp police cuz such words when spoken by chimwendo its ok apolice alibe naye vuto adzikwanje nawo apolice kwa iwo sivuto but once is done by opposition mpomwe apoli akumadziwa kut sizabwino . koma tikuyenera kudziwa ngat izizi zipitilile one day sikudzzakhala kukonza ayi koma kuononga cuz anthu akuwona zomwe zuchitika lamulo likugwila mbali imodzi akadzatopa ndi zija mmanva kut anthu awukilana zapachiweniweni zikwanje zayambika kutemana cuz aliyese azafuna kusonyeza kut malawi ndiwake ndipo ali ndi ufulu lamulo lisakhale logwila mbali imodzi
GWEDE GWEDE | 9 JANUARY 2025
31:40
Malawi News Update
Рет қаралды 32 М.
BAYGUYSTAN | 1 СЕРИЯ | bayGUYS
36:55
bayGUYS
Рет қаралды 1,9 МЛН
The evil clown plays a prank on the angel
00:39
超人夫妇
Рет қаралды 53 МЛН
黑天使被操控了#short #angel #clown
00:40
Super Beauty team
Рет қаралды 61 МЛН
She made herself an ear of corn from his marmalade candies🌽🌽🌽
00:38
Valja & Maxim Family
Рет қаралды 18 МЛН
EXCLUSIVE WITH PATRICIA KALIATI | 04 JANUARY 2025
1:13:01
Malawi News Update
Рет қаралды 89 М.
A NAMIWA KUYANKHA MAFUSO ATOLANKHANI 🙌😱
21:23
HOT 265
Рет қаралды 25 М.
KU HOT CURRENT LERO__29 December 2024
1:21:23
HOT 265
Рет қаралды 41 М.
ACHAKWERA SINDINGAOPE KUYANKHULA KWA SULEMAN
24:40
HOT 265
Рет қаралды 20 М.
BAYGUYSTAN | 1 СЕРИЯ | bayGUYS
36:55
bayGUYS
Рет қаралды 1,9 МЛН