KODI KAMUZU WAWUKA? UYU AKUFANA NAYE NDIYETU WAZA NDI MFUNDO ZOWINILA 2025 ~ NDE MPAKA KUNYOZA DPP?

  Рет қаралды 7,929

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 101
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 3 сағат бұрын
Tobiasi from Mozambique,tidzalamulidwa,ndi wobwela.malawi,ndi ziko lobvetsa chisoni kwabasi.lotoledwa
@RodneyKapere
@RodneyKapere 27 минут бұрын
Olongololanso ngati skc anthu otelewa aMalawi tawaona takumana nawo kale and aMalawi tkudziwa mwabwino ndi moyipa mwawo
@JohnKalembo
@JohnKalembo 2 сағат бұрын
Kodi ndiwakuti ameneyu eeish sindingamuvotere munthu osamudziwa ine Dpp my vote❤
@ChrispineMuzungu-l8h
@ChrispineMuzungu-l8h 3 сағат бұрын
The man has good manifestal and good plans 🎉🎉 l like him
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa 7 минут бұрын
Good Dreams go ahead brother bravo❤ GOD BLESS YOU and guide you
@ElizabethMwale-z3s
@ElizabethMwale-z3s Сағат бұрын
Mmm nanu ndiye mwapupuluma mmene mukuonekeramo mukuoneka kuti mukuchoka pa dzuwa, sindiye akubanu inu, sitikukudziwani. Anthu osawadziwa ndiye akutipwetekawa. Bola tibwereze APM yemweyo ntchito zake tinazionapo nza bwino.
@MarthaGama-q1o
@MarthaGama-q1o 51 минут бұрын
Kuyipa kwake mumabwela ngati agelo pamene mukufuna kuti mudzidzatibela misonkho yathu aniyake tikuwona
@AffectionateGarden-uq4ii
@AffectionateGarden-uq4ii Сағат бұрын
Mumabwela ngati olungama komamulimbava Bola adadi
@georgeaiwa8661
@georgeaiwa8661 Сағат бұрын
Am impressed. Iwe ndiwe Vote yanga. You deserve presidency
@phillipphiri2119
@phillipphiri2119 38 минут бұрын
You would be surprised that Chakwera doesn't have all those details. The dude is lost ,crueless
@DaudRajab-o2t
@DaudRajab-o2t 3 сағат бұрын
Ndi wakuti ameneyi ine ndiye ndi votela.
@FanuelManesi
@FanuelManesi 2 сағат бұрын
Umu muli dzeru ....my vote
@Jeffrey-um
@Jeffrey-um 4 минут бұрын
Kulota ndi ulele madala keep up
@KendrickLuckyc
@KendrickLuckyc 3 сағат бұрын
Ukuyankhula Chilungamo ukhonza kutenga vote yanga, koma vuto mumakhala ndimfundo mukakhala kuti simuli m'boma
@BashilMuhamad-zx3mc
@BashilMuhamad-zx3mc Сағат бұрын
Waganyu wa chakwera uyu😂😂😂 mofunika kusamala Amalawi😂😂
@mussakapalamula1990
@mussakapalamula1990 3 сағат бұрын
Wauka kwa akufa Kamuzuyu
@RoseThindwa
@RoseThindwa Сағат бұрын
Manifest abwino koma tatopa Malawi's sweet talk pano dziko lili ndi mavuto utsogoleri power hungry
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 41 минут бұрын
We are tired with unexisting things.
@MarthaGama-q1o
@MarthaGama-q1o 48 минут бұрын
Ndinu wochepa nthupi koma tikakusankhani ndikuyamba kudya misonkho yathu nkunenepa mukatelo wosavanso madandaulo a Malawi , lero ndi izi tikuziwonazi kuva zamunthu anasiya .
@MpasulavisaSonjo
@MpasulavisaSonjo 2 сағат бұрын
Good analysis, but easier said than done. One maybe fitting Presidency but bitting corrupt systems and egocentrism remains a challenge Winning presidency as an independent, a hustle
@JaniNjolomole-z4m
@JaniNjolomole-z4m 45 минут бұрын
Ndale sakuziziwa uyu azikalima uko even speech presentation kumuvta
@ChibabaOficial
@ChibabaOficial 4 минут бұрын
Chakwer amater ine nde sindi kupanga nao pepani kwambilì
@GladwellZimba-jn4yv
@GladwellZimba-jn4yv 46 минут бұрын
President ndiyemweyu ali ndi mfundo zabwino kwambili
@KasimIbbu
@KasimIbbu 4 сағат бұрын
Mwasowachochitasopano kod akugayilani ndan makobiliwo
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i Сағат бұрын
Aaaah za ziii mfolena iwe akuvotela amako APM voti yathu
@StevenDastan-f5y
@StevenDastan-f5y 48 минут бұрын
Ma sweet talk ife ayi
@BandaLega
@BandaLega Сағат бұрын
Iwe ukufunika kukayima ndi DK srs
@AllahAlafred
@AllahAlafred 57 минут бұрын
Inu nde mwabwela bas km choyamba tikudziwen zikuonetsa kt muli ndi fundo zabwino kwambili bola musakhale mwatumidwa ndi udza wa mcp
@MxolisiFlow
@MxolisiFlow 8 минут бұрын
Iweso ndye mbava yotheratu atizakuvotere ndi ambuyako ndithu
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 сағат бұрын
ETI KULOWA MU OFESI CHIFUKWA CHA MADEMO.OTSOGOZEDWA NDI ACHINA TIMOTHY NTAMBO OLO NDI MAFEMÒ A BAKILI MULUZI NDI CHIHANA SENIOR 1994.ZATIZUNZA..KULOWA PAMPANDO WAUPULEZIDENT CHIFUKWA CHA MA HANDOUTS..NDI UTSOGOLERI.CHIFUKWA CHA MA ALLIANNCE IZI NZOIPA KAA!! *** KUULOWA PAUTSOGOLERI POPANDA MA HANDOUTS NDI MTSOGOLERI WOPIMAYO .KWACHAKA CHANTHUNTHU AKUPANGANA MA OFFESI HAND OUTS MWAMTENDERE..ZIKOMO.
@RodneyKapere
@RodneyKapere 21 минут бұрын
Olongolola tili nawo ambiri koma ogwira kulibe
@ChriChimbiya
@ChriChimbiya Сағат бұрын
Iwe ofunika kwangokudyela wakubaiwe
@RabbeccaChitimbe
@RabbeccaChitimbe Сағат бұрын
Mwachoka kt man simukuziwikatu
@chimwemwechimwanza
@chimwemwechimwanza 3 сағат бұрын
kkkkkkkk sitingamukhulupilire ameneyu nayenso akufuna kuti bera DPP boma basi
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe Сағат бұрын
You better be activists wava
@yakinidagalasi
@yakinidagalasi Сағат бұрын
mbavaizi dpp my vote
@DanChirwa
@DanChirwa 2 сағат бұрын
Munthu wakumozambique musamuvotere ameneyi aononga kuposa a mcp
@SandraBanda-hd1li
@SandraBanda-hd1li Сағат бұрын
Tobias... akakuvotela..... kwanu ..... ku... macambique...... palibe. Angakuvotele...... ubetsa... Chitsilu
@ronexmcdonald8742
@ronexmcdonald8742 Сағат бұрын
Iwe kape iweso ndi mmozi mwa iwo umuyang'ana okuvotela sitingakukhulupilile
@RashidKusum
@RashidKusum 2 сағат бұрын
Iye arinaxo ndarama zomayendesera ziko la Malawi panyapako
@AckimKasiya-u7q
@AckimKasiya-u7q Сағат бұрын
Mtayeni man
@ChrissieNyasulu
@ChrissieNyasulu 2 сағат бұрын
Nenani mfundo za mmutu mwanu osati za pa likasazo.
@cmsanyama200
@cmsanyama200 47 минут бұрын
Komabe umayenera kuyamba kupezeka 2 yrs ago
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 сағат бұрын
KUMWRA KWAMBIRI. IMF NDI WORLD BANK KUTI MALAWI ADZNGOKHALIRA MA DEVUATION ZINTHU NKUMANGODULA .AMALAWI NKUMANGOFA NDI NJALA NDI NTHENDA.
@godfrey533
@godfrey533 2 сағат бұрын
Uyu Nde wabodza timukhulupirira bwanji poi nayenso Alindinjar ya ndarama Nde asaziyeretse apa Ayi
@ChrispineMuzungu-l8h
@ChrispineMuzungu-l8h 3 сағат бұрын
Koma wachokera kt
@AgnesAllan-g3u
@AgnesAllan-g3u 52 минут бұрын
Athu akuba awa chenjeran
@BreciousMbalureMangeni
@BreciousMbalureMangeni 2 сағат бұрын
🎉 Fundo zabwino
@FatsaniAlick-m7r
@FatsaniAlick-m7r 3 сағат бұрын
tapitani muzikangolima
@AustenKhaphwi
@AustenKhaphwi 2 сағат бұрын
Mwamodzi opangasapoti mulifundo zontchwapuka
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 2 сағат бұрын
Muli Mfundo zabwino 2025 boma
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 сағат бұрын
KUMVERA KWAMBIRI IMF NDI WORLD BANK.NOT KUMWERA KWSMBIRI
@FredMaidah
@FredMaidah 51 минут бұрын
Aaaaaaaaaa ichi ndye chitsiru cha muthu wakhuta chani ameneyu
@ThomasmosesMoses
@ThomasmosesMoses 57 минут бұрын
Azanuso anayakhula bwino kuposa zanuzo km tinagojezela mavuto ositha dziko NDI adadi bas amalawi tiyen tisakhe dpp pofuna kutukula dziko osat kutukula mu2
@BenzoJota
@BenzoJota Сағат бұрын
Kungochokera ku kolima basi wati bola uyimile
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 сағат бұрын
Zonama ife tatopa nazo Apm basi
@JaffalieNdembo
@JaffalieNdembo 2 сағат бұрын
Ali ndi mfundo zabwino koma vuto nayenso ndi mlenje
@AckimKasiya-u7q
@AckimKasiya-u7q Сағат бұрын
Mwafulumila yimilan u mp bwa
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 3 сағат бұрын
Kuyakhula mkusavuta Koma kuchita .Musamukhulupirire .Muli fundo Za bwino Koma mwina zophera awemba
@PatsonmahoweNyirongo
@PatsonmahoweNyirongo 3 сағат бұрын
Unali kuti iwe kuti lero uzinyoza dpp
@KalongaWhy
@KalongaWhy Сағат бұрын
Nanuso mukufuna munenepe muli m.boma munenepere Zina amalawi salola anenepesa kare a MCP bas kwakwana awature tikuziwa Ife amalawi angakhare mopanda ophuzira ayi
@MosesDicostar
@MosesDicostar 3 сағат бұрын
Koma kumalawi tizakhala dziko losauka paka kale kadziko kakang'ono koma dzipani zambiri aliyese kuziyeresa kumati ndwabwno bwanji ubwino wanuwo osauika pamodzi ndkukoza dzikoli???
@apatsaphanga9252
@apatsaphanga9252 3 сағат бұрын
Ndawakulu a Millward zao ndi bushiri
@CharlesMukona
@CharlesMukona 3 сағат бұрын
Tangokhala umphawi wakukwana ni mutibeleso tizingolima ganyu
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 3 сағат бұрын
Tatopa ndi boza kwambiri Pano kwasala ndikungoliwetsa chipani chimene akuchidziwa anthu Chili ndi mbiri kale kuti chinapanga bwino Osati manyaka amenewa anyowaniwa ayi mwatopetsa
@KalongaWhy
@KalongaWhy Сағат бұрын
Akolo mafundo anu ndiokhaokha ndi achakwera pamene amalowa m.boma Ife amalawi tatopa ndi azisogoleli ophuzira Ngati mpira bwererani muzikapanga zimene zimakupezesan ndalama ziko ndiubusa zindu ziwili zosiyana pepani musaononge ndalamazanu popanda pake is not available you to be president that's true
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick Сағат бұрын
tose,tizavotela,mcp,uyu,sitikumudziwa
@JaneMoyo-b7i
@JaneMoyo-b7i 3 сағат бұрын
Ife tikuduna mfundo isati zonyoza zipani zina ayi. Mutiuze za zipani zina ife tinali kunja? Mesa tinali mommu o tuziziwa bwino kupisa inu. Tipaseni mfundo zanu osati zomanyoza zipani zina ayi. Ife tizavotera mfundozo
@johnsoldier
@johnsoldier Сағат бұрын
Ndiwaku ntcheu ameneyu
@yusufuadamu5476
@yusufuadamu5476 2 сағат бұрын
Fundo Zanu zili bwino kwambiri komano I think Mukanadekha kaye Mwapupuluma kungofikila pa upresident with new political party, Ndizovuta kuti Miyoyo ya Amalawife tikukhulupilireni, pamenepa tayamba kale kuganiza kuti Mwatumimwa ndi chikangawa kkkkkkk
@MosesDicostar
@MosesDicostar 3 сағат бұрын
Muthu akuchita kukanika kuwelenga zithu zoti wazilemba ekha 😂😂😂😂😂😂😂
@ThandiweAssah-w4x
@ThandiweAssah-w4x 3 сағат бұрын
Wa chepa uyu pandale akafuna aphatikizane ndi zipani zina
@IsabelLuka-i8f
@IsabelLuka-i8f 3 сағат бұрын
Aaaaaaa nanunso inu iyaaaaaaaa 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@AckimKasiya-u7q
@AckimKasiya-u7q Сағат бұрын
Ali buuu
@ThoccoChimbali-h6g
@ThoccoChimbali-h6g 2 сағат бұрын
Iwe ndiye uti?
@KalongaWhy
@KalongaWhy Сағат бұрын
❤❤❤
@PetroLosan
@PetroLosan 4 сағат бұрын
Akusowa chochita akufuna mgaiwa uyu😂
@Thanthwe2020
@Thanthwe2020 2 сағат бұрын
Kakmeni inu iyaaaa zaziii
@SandraBanda-hd1li
@SandraBanda-hd1li Сағат бұрын
Komanso.... President.... a ngakhale.. Tobias... aaaaaaa..... ukamufune.... Omubelayo.... khope... yake... imeneyo?... Jekete... ya pakaunjika... akakuvotela... abale... akowo. iyaaaaa
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 2 сағат бұрын
mmaso mwako chamba etiunalikuti nthawi yoseyi
@HaziwellKambelembele
@HaziwellKambelembele 3 сағат бұрын
Koma vuto wayambira pakolasi ukadayambira kuti athu akudziwen big fundozo ndizabwino
@HaziwellKambelembele
@HaziwellKambelembele 3 сағат бұрын
Musaope big
@bs-malawi
@bs-malawi 3 сағат бұрын
Eeeeh wabwela ndi mavuvu mkulu yu mmmmh
@MbaleMan-o3r
@MbaleMan-o3r 2 сағат бұрын
Adakhakhala kut ndiwonenepa bdikananvotera coz nkanaziwakut alindi kakhobili koma mmmmm ndimmenebdikuoneramo ngogulisamangotu uyu
@MorrisChikoti
@MorrisChikoti Сағат бұрын
Chitsilu chamuthu iwe
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 3 сағат бұрын
Akugona ngati angalimbane ndi dpp iyeyu kkkkk uzitenge bwino sitikuufuna azibusanso ife zina ndi zimenezi tikuvutikanazozi
@AustenKhaphwi
@AustenKhaphwi 2 сағат бұрын
Koma ndi was mboma lanji
@vicshyma5644
@vicshyma5644 19 минут бұрын
Kilimane moshco
@ThoccoCharles
@ThoccoCharles 53 минут бұрын
😂😂😂😂 Wakuba uyu asatitopese awa
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 сағат бұрын
Pwala lako ukufuna wabele amalawi kagwele uko
@Zebron-kg2qz
@Zebron-kg2qz 25 минут бұрын
Chamba chamupweteka
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick Сағат бұрын
bola,chakwela,
@RaphaelLikhomo
@RaphaelLikhomo 3 сағат бұрын
iwe wangosuta suta inumungapa ngenji mulibezochita
@abubakar-n2e1b
@abubakar-n2e1b 3 сағат бұрын
Kuzamalila kundedeso Chobe
@cmsanyama200
@cmsanyama200 Сағат бұрын
Mundale mulibe oyera
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 3 сағат бұрын
Anthu akumozambiki awa
@SedoMissi-m3c
@SedoMissi-m3c 4 сағат бұрын
Iweo ukhoza kukhala wabhobh km apambuyo akowo
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 2 сағат бұрын
kkkkk awa ndiye atiso eee komatu manifest ake akunvekatu bwino kkk kom ine ayi ndamukana
@DanielMsokwa-k3p
@DanielMsokwa-k3p 2 сағат бұрын
Ok
@LawrenceBelson
@LawrenceBelson 3 сағат бұрын
Wachokera kuti kwawo ndikuti
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН
BAYGUYSTAN | 1 СЕРИЯ | bayGUYS
36:55
bayGUYS
Рет қаралды 1,9 МЛН
Арыстанның айқасы, Тәуіржанның шайқасы!
25:51
QosLike / ҚосЛайк / Косылайық
Рет қаралды 700 М.
Russia Declared War / Putin Calls for Retaliation
13:44
NEXTA Live
Рет қаралды 412 М.
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН