WA MCP WATI DR CHILIMA NDI OMWE AKUYENERA KUDZAIMA 2025 NGATI PRESIDENTIAL CANDIDATE WA TONSE |

  Рет қаралды 18,711

DZIWE TV

DZIWE TV

2 ай бұрын

Пікірлер: 100
@FrancisDindani
@FrancisDindani 2 ай бұрын
The man is honest and bave. You can tell from his face that he is what he is saying. Big up
@user-gd2kl1fx1q
@user-gd2kl1fx1q 2 ай бұрын
This man is saying the truth
@CidrickMbengwa
@CidrickMbengwa 2 ай бұрын
Mr luwara is saying the fact
@user-tb6bp7br1m
@user-tb6bp7br1m 2 ай бұрын
That is the truth of the matter
@StevenAjusugama
@StevenAjusugama 2 ай бұрын
Zingovuta koma chilungamo
@user-vp3ph1ig9f
@user-vp3ph1ig9f 2 ай бұрын
Akunenadi zoona izi ndizosilana sizamuyaya
@EmilyBauti
@EmilyBauti 7 күн бұрын
That is true I like that man
@user-vp3ph1ig9f
@user-vp3ph1ig9f 2 ай бұрын
mumupase mpata muzanu wayimepo zosiyilana izi😊
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 2 ай бұрын
This man is patriotic. For the very first time to hear a courageous man telling the truth how Chilima has been mistreated by Chakwera. The truth shall set Malawi free.
@timenchenga1141
@timenchenga1141 2 ай бұрын
Yes chilungamo chofunika
@user-iw6cz5ft2l
@user-iw6cz5ft2l 2 ай бұрын
Lwara waing'alura uku
@user-cf9yz3ei5o
@user-cf9yz3ei5o 2 ай бұрын
A good urguement but mcp is cannot see that
@ephraimkadamika
@ephraimkadamika 2 ай бұрын
His is saying the trueth
@jamaliedwin-cu1ip
@jamaliedwin-cu1ip 2 ай бұрын
akunena zoona
@daniellomoliwa7394
@daniellomoliwa7394 2 ай бұрын
100% truth..
@user-yf3st5yb1n
@user-yf3st5yb1n Ай бұрын
Waziwa ameneyo kut saphula kanthu or atayima😂😂😂😂😂😂
@user-lb6ek3ee6d
@user-lb6ek3ee6d 2 ай бұрын
This interview is very interested,brilliant and full of truth.I like this man bcs he is saying the truth, what was happened btwn them.And now don't take Chilima as a stupid man follow up your agreement.
@AlpheousKaluwa
@AlpheousKaluwa 2 ай бұрын
Ndizowona kwambiri ndithu
@victorauwana7258
@victorauwana7258 2 ай бұрын
Kuimilatu kokha osati kuzawina
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 ай бұрын
This is a justice Man true citizen
@JamesSpondo
@JamesSpondo Ай бұрын
Mai mukhosi mwatani😮😂😂😂
@FefieTenisha-du7ge
@FefieTenisha-du7ge 2 ай бұрын
All what this man is saying is next to truth...The only thing that i can sense from his emotions is that he probably must have been frustrated with something within their party... Its a direct jab to President Chakwera...Let me also correct him; we the citizenry of Malawi regard both the president and his vice to have failed us... They are both in the presidency office
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 2 ай бұрын
Imeneija inali contract ya Chilima yowachotsa a Malawi ku DPP ndikupita nawo ku MCP ndiyeno contract ikatha contractor amakhalapo ndi gawo?? Pamenepo a Chilima angovomereza kuti anagwira ntchito mopepera
@landiraniwhite2756
@landiraniwhite2756 2 ай бұрын
Achilima ndiokoma konsekonse ndiomwe apweteketsa Malawi Anamunyoza Peter munthalika, vuto anthu timayiwala kuti takhumudsitsa ngati, ino ndi nthawi yoti akolore zomwe amachitila ena.
@user-pn7cj9hb3t
@user-pn7cj9hb3t 2 ай бұрын
Ndugwirizana nazo ase
@KennedyBanda-ci2wt
@KennedyBanda-ci2wt 2 ай бұрын
Wow
@harrykalenga915
@harrykalenga915 2 ай бұрын
Zoona
@mavutochilungamongoma6488
@mavutochilungamongoma6488 2 ай бұрын
Nice talk
@sandilezikhali9753
@sandilezikhali9753 2 ай бұрын
Wadya banz uyu kuchokera kwa chilima wakeyo
@hendschipiekhonje9877
@hendschipiekhonje9877 2 ай бұрын
Zoona zokhazokha
@jameschidafumbwa1039
@jameschidafumbwa1039 2 ай бұрын
This guy is telling truth!
@user-ti2gf1dn1b
@user-ti2gf1dn1b 2 ай бұрын
We was very happy that time to win election together UTM and MCP but mr president chakwela is the one make big mistake and is the one disappoint the all malawi to stop Mr chilima to work with them they took all power to mr chilima that is why people disappointed they believe mr chilima that's why people vote mugwilizano and the people the don't believe mr chakwela and without chilima chakwela it can't be president thanks a lot am Emmanuel am sty jobeck south africa
@Benson-cf6qd
@Benson-cf6qd 2 ай бұрын
Kkkkkk koma utsi uli uku
@ernestobenissonizocomabebe8113
@ernestobenissonizocomabebe8113 2 ай бұрын
Zona
@user-gg6zc4hi5i
@user-gg6zc4hi5i 2 ай бұрын
True VP sakuramla nao
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 15 күн бұрын
Chilima is suitable to be president 2025
@user-mb8rk5vm3x
@user-mb8rk5vm3x 2 ай бұрын
Kodi akuti chani?
@PasquaMapemba-my9mw
@PasquaMapemba-my9mw 2 ай бұрын
President asamanàmidwe, Chilima ndi president yemwe tikufuna. Very good president. PEPANI SIMUNGATIUZE ZOPUSA IFE, TINADZUKA A MALAWI PEPANI. Chilima si president wà YES BWANA, WÀ ANDIUZA KALE NDI MUNTHU WA NDIMVE ÑDEKHA SO, NDAMENE TIKUVOTERA NOW, Kuchedwa nazo izizi takayamben mthilira bwàaa muchedwa. TINADZUKA A MALAWI GUYS
@edwinearlkachiwala3070
@edwinearlkachiwala3070 2 ай бұрын
Kuyankhula uku ndiko komwe. Kukufunika
@user-ju5eu9sq9t
@user-ju5eu9sq9t Ай бұрын
Izo ndizoona paja amati wakukeliyala saimba belu
@ArnoldMatewere
@ArnoldMatewere Ай бұрын
Onse ndi amodzi.agreement anatibibisila.akufuna kuulula nthawi ya masankho itayandikila.asatipangile zochita.chilima osamupatulamo. I
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 2 ай бұрын
All of you out 2025 chilima ndiyemwe awononga dziko la Malawi
@user-iy8vi7nn8r
@user-iy8vi7nn8r 2 ай бұрын
Enough with chakwera and Enough with chilimas as well both should leave the office these people are liars
@user-vq9if2ep5q
@user-vq9if2ep5q 2 ай бұрын
Ku Malawi.....kokoma suredi😅😅😅😅😅😅😅😅
@user-pn7cj9hb3t
@user-pn7cj9hb3t 2 ай бұрын
Malekano amafunsa mafunso opusa guys amaona ngati angafike pa Brian Banda, komaso chilima wakoyo ndi akagwere uko ndi wabodza, osocholetsa dziko.
@FosterChilumba
@FosterChilumba 2 ай бұрын
Kodi ayima bwanji SKC Hamdan wanuyo Mr Chilima has served two terms as VIP it's over for Chilima by the way Malawi is upside down now coz if these two idiots Lazaro ndi Chilima wakeyo nonsense
@FelixMaiden-cj4de
@FelixMaiden-cj4de 2 ай бұрын
Chilungamo chimawawa koma muthuyu waima pachilungamo bc
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
Kwaine wosewa zeru zawo ndizimozi sindingawa sapote wosewo awononga dziko la Malawi
@homeremedys3748
@homeremedys3748 2 ай бұрын
Akazi apamalawi u slay queen sukuthandizani kuzafa mudakapempha azimuna, Yesani kuphikaniko Mandasi Muzigulitsa Momwe ankapangila azimai anu, Ife azimunafe sitikumba pansi ndalama ayi.
@Owen88887
@Owen88887 2 ай бұрын
Kkkkk yah the fact is now prevail
@user-ds6zj9um6g
@user-ds6zj9um6g 2 ай бұрын
Fact
@ZephaniaJoseph-zq8jj
@ZephaniaJoseph-zq8jj 2 ай бұрын
Ndizona akunena akuluwa mpatseni mpata mnyamatayu musakakamulepo chomwe munagwili.zana chigwile ntchito
@NelsonLwanda-ls9qd
@NelsonLwanda-ls9qd 2 ай бұрын
He is calling a spade by its name
@jamestimothy1537
@jamestimothy1537 2 ай бұрын
People hide the truth, kuopa kumangidwa but chomwe walankhula mkuluyi chakwera zimukhuze,ndipo Chakwera kungovomereza agreement and ndikubwera poyera kuti ino ndinthawi yoti dzanga apitilize adzalandila ulemu ooophyaa, koma ngati ayi he will be a glutton
@user-kl1vk1gx2q
@user-kl1vk1gx2q 2 ай бұрын
Akagwere uko chilima wakeyo n
@user-gv9vl7uq2e
@user-gv9vl7uq2e 2 ай бұрын
Ine mataya kuno kumbayan aliwara sakunama chakwera alibefundo ndipo chilima asamunamizile tonse kunjaku chilima ndamene anthu akumudikira pagalaundi
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 2 ай бұрын
Ndiye ngati chilima sali m,boma ndiye palibe chifukwa chokhalila ndi vice president kumangolandila ndalama za Amalawi mwaulele.Very sorry
@kamwazabonomali825
@kamwazabonomali825 2 ай бұрын
Chilima is waiting for the demise of the president 😂😂😂😂 Koma akulu awa awathamangisa muMCP.
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 2 ай бұрын
Kaya adzaimila chilima or chaKwela onse ndi Amodzi akutizu nza.Malawi mwaiononga pano tikuvutika kwabasi
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 2 ай бұрын
Aaaaa a Tupele woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 2 ай бұрын
😂😂😂😂....mxm nonsense chilima ll never be president in malawi
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 2 ай бұрын
Chilima the best
@user-nk2iu1ym6o
@user-nk2iu1ym6o 2 ай бұрын
Kma achakwela aganize mofatsa kwambili chifukwa aliyese akudziwa kt iwowo Ali pamenepo chifukwa Cha chilima zoona ndithu
@edwinearlkachiwala3070
@edwinearlkachiwala3070 2 ай бұрын
Akulu awa ndi a dyera basi
@christophergibson72
@christophergibson72 2 ай бұрын
Chilima wachan zopusa
@user-cr4kn2wm3g
@user-cr4kn2wm3g 2 ай бұрын
Mudengu kuola imodzi zonse zaola
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m 2 ай бұрын
Zoonadi zomwe akunenazi komano chilima Yu bwanji osachokamo mu MCP mu eshhhh ineyo zimandikhudza Tu Kut mmalo molandila ulemu chilima pano akutengedwa ngat galu ndi MCP
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 2 ай бұрын
Chilimatu akamasewera motere adzaona ngati kutulo ataletsedwa kuimira ndi utm yake yomweyo asamale
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg 2 ай бұрын
Koma eeeee ziliko
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 ай бұрын
Chilima waziphera sogolo waonongesa mbiri yake ndi chakwera ndizovutanso kut athu amukhulupire
@user-tk6wf2eg4z
@user-tk6wf2eg4z 2 ай бұрын
Achilima mukapangaso ubale ndi mcp mwagwa nayo ndipo pazavuta kt boma muwine ngat muli oganiza tulukanimo menemo mcp sikuyenelaso kuwina ndipo inu or mukapembe man festo Anu sitiwakhulupirila
@user-ll2fy4kd8t
@user-ll2fy4kd8t 2 ай бұрын
Achikulilewotu akunena zoona chifukwa choti anali nawo patsikolo ndiye kuti achakwela saziwawatu ndale ai ndichifukwa chake anthu agowanamiza zili zonse yiwo kumvomela komatu mawa akachoka pampando aliwoo azkukhuta mano azawoo atawasiya 😄😄😄😄
@user-ll2fy4kd8t
@user-ll2fy4kd8t 2 ай бұрын
Taonaninso zanazanali awanamiza za mapasipoti palibe chomwe achita agoti duuu ngati simzogoleli waziko eeeee abwanawa ndi wokanika basi
@robertmminamachael7140
@robertmminamachael7140 2 ай бұрын
Galuu ameneyo,wadyela
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 2 ай бұрын
Mcp sititekeseka ayi or titakhala kosusa sitipanga ngati adpp ayi zikoli ndilawina aliyense kaya wautm udf mcp dpp ngati wapeleka kuti nthawi iyi ndiyachilima kapena atupele ndinthawi yawo basi yehove akanena wanena koma kugulisa chipani ayi mcp sichipani cha munthu kapena chabanja ayi ndi chamalawi
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 2 ай бұрын
Nde ku malawi kumeneko
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 2 ай бұрын
Osewo ndi mbava kuwavotera
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 2 ай бұрын
😂😂😂❤❤❤😅😅 yomweyo galu iweeeee
@JamesSpondo
@JamesSpondo Ай бұрын
😂😂😂😂😂
@user-vp3ph1ig9f
@user-vp3ph1ig9f 2 ай бұрын
anamutaya muzawo amsp
@user-ot6lt8iy8f
@user-ot6lt8iy8f 2 ай бұрын
Kuli nkhondo ya ikulu ku tonse tziona chaka chake ndichino
@PeterThomas-lw3io
@PeterThomas-lw3io 2 ай бұрын
Mukuziwana
@johnmpatama1461
@johnmpatama1461 2 ай бұрын
Sangawine olo atayima
@violetmahachi7673
@violetmahachi7673 2 ай бұрын
Achilima izii ndi zofuna moti iyeyo mcp sakaiziwa momwe akulila iwo anja
@JamesSpondo
@JamesSpondo Ай бұрын
😂
@user-kd5mp6wh6o
@user-kd5mp6wh6o 2 ай бұрын
Akunena amkuluwa zoonadi ndipo ngati athu a mcp amaopa Mulungu akuyenera kulolela kuti zomwe anagwilizana zichitike for the benefit of malawians
@mathewsbanda6053
@mathewsbanda6053 2 ай бұрын
Mazoba
@robsontyg3928
@robsontyg3928 2 ай бұрын
Nonsense
@thomasyohane987
@thomasyohane987 2 ай бұрын
😂😂😂😂 I feel your pain
@jomochirwa
@jomochirwa 2 ай бұрын
Dr chakwela akuti ndi abusa mwina iwowo akudziwa koma sakufuna kuwawuza azawo a mcp.m'busa amafunika chilungamo zimene adagwilizana ndi azawo.mpofunikadi kuti dr chakwela panopa apatse mzawo chilima 5 yrs ikubwelayi .
@AnthonyKaira-jm5ig
@AnthonyKaira-jm5ig 2 ай бұрын
Kulikonse angapite chilima ndzamvotera
@PeterThomas-lw3io
@PeterThomas-lw3io 2 ай бұрын
Meter sumayiwonela patali Ku DPP kuja ukanadekha bwino bwino ukanayima utsogoleri
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 2 ай бұрын
Vuto ndi loti amcp sangagulise chipani ngati balkili ayi achilima anakakhala kuti ndi mcp bwta koma chilima ali ndi chipani chake chipani chamcp ndichaphavu ndiye akhala bwanji upule ali ndi chipani china
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 2 ай бұрын
The only weapon to destroy DPP is to put Dr. Saulos Chilima to head Tonse alliance. A'm one of MCP big supporter, but I want Chilima to be the next president of the Alliance.
@edwinearlkachiwala3070
@edwinearlkachiwala3070 2 ай бұрын
Aaaa sizitheka ulendo uno saw ayi sangawine
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 2 ай бұрын
Atumbuka ndi chocho alibe mbali yeni yeni kaya tinakhala bwanji
@user-pw2dq1yw4b
@user-pw2dq1yw4b 2 ай бұрын
Ukamati atumbuka ukutanthawuza chani za ndale osalowetsapo zazigawo the guy is talking is not talking on behalf of a trible no he is talking for him self so leave tumbuka thing a side
@victorauwana7258
@victorauwana7258 2 ай бұрын
Atumidwa
@YohaneLino
@YohaneLino 2 ай бұрын
Wabodza ameneyu si WA mcp ndi WA utm nde fund zakezo ndi za bodza zokhazokha
ELE QUEBROU A TAÇA DE FUTEBOL
00:45
Matheus Kriwat
Рет қаралды 18 МЛН
ПЕЙ МОЛОКО КАК ФОКУСНИК
00:37
Masomka
Рет қаралды 10 МЛН
Sigma Girl Education #sigma #viral #comedy
00:16
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 70 МЛН
СҰЛТАН СҮЛЕЙМАНДАР | bayGUYS
24:46
bayGUYS
Рет қаралды 734 М.
Rechtbank: Oud-president Trump schuldig aan liegen over geld
2:07
NOS Jeugdjournaal
Рет қаралды 26 М.
Dit regelt het Europees Parlement voor je
3:41
RTL Nieuws
Рет қаралды 1,9 М.
Izindaba zesiZulu @13H00 | 31 May 2024
23:27
SABC Izindaba
Рет қаралды 46 М.
Bom gevonden in de straat van Brent, 1100 mensen moeten hun huis uit
3:16
Acties Israël in Rafah verhogen druk op Joe Biden
6:41
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
ODUU Afaan Oromo Hatattaaman Amma Nu Gahe Jun 1, 2024
19:23
Tumsa Media
Рет қаралды 306
ELE QUEBROU A TAÇA DE FUTEBOL
00:45
Matheus Kriwat
Рет қаралды 18 МЛН