Chakwera walephera ndithu akuvutika si DPP Okha tonse ndi omwe akuti boma ndi lomweli akapita Ku nyumba maso gwaaaaa
@HevenChiwaya6 күн бұрын
Zadala mumafuna kuwona kusintha amalawi sitimachedwa kuiwala zedi tinazolowela ukapolo kuzunzika sitimafuna kumadya bwino DPP imayesesa chakudya ma grocery anali otchipa koma kumafuna MCP kodi mudali angono nthawi ya kamuzu banda Congratulations MR Bakili muluzi zabwino munayesesa kutichosa mmavuto koma a Malawi umbuli unavuta kwambili ndiye mukhaula zedi ku Malawiko ndizanwela MCP ikazachoka
@ChanceZambika6 күн бұрын
Chilungamo❤❤❤
@friquerapper90864 күн бұрын
Zasangalatsa pakuti adzibusa mwaziona
@isaaczuze5 күн бұрын
Boma ili likuyendesedwa ndi zisilu kwambili ......
@JamesALLi-m8i6 күн бұрын
Chakwera ndi mwana uyu wa chepa kwabasi walephera kuyendedza dziko Mwanayu zamukanika bas ine kuno agogo anga akudya chiteze nthutu atha Apm is coming soon to be president of this country we love Malawi 🇲🇼 💙 adad come pls 🙏 😀
@Maulana-s2n6 күн бұрын
Uyu nde m,busadi wokhuzidwa ndi mmene ziweto zake zikuvutikila ndi luzu mukenani
@SolomonNjolomole6 күн бұрын
Kunali kulodzedwa ndithu kumene kuja mmm
@CliveMhango-e9m9 сағат бұрын
Mukuwona ngati muli za mulungu mwa a nsembewo? Zausatana zokhazokha
Aaa bishop amalawi tadzukadi ndi mcp ZAKA 4 koma yaaa nde machine obela CHITSANKHO AKHALETSO DZINA 5 IIII MULUNGU ATIYANG'ANILE NDINTHU
@AbdulazizWyson-dq3ce6 күн бұрын
Abusa mwanena zoona
@StewartGoma6 күн бұрын
Chakwela must fall CHIKANGAWA must sign
@ChristopherMtundumula-o5e6 күн бұрын
Munthu osalimba pa chikhiristu pake
@PrinceBlessings-bv5bs6 күн бұрын
Maso auzimu anthu nthaw imene ija mudalibe
@collengoma65426 күн бұрын
zoonadi amene akusangalara ndi utsogoleri ulipowu ndi afiti asatana Malawi akupita ngati Zimbabwe
@AlexKaunda-ny2eg5 күн бұрын
Muwudzeni choona chakwera akungo chinda ana chinchila chachitali shame on him
@marychavula6986 күн бұрын
Koma asamayike bishop mtumbuka
@madalitsomakawa97084 күн бұрын
Pemphero la ulendo let us allow God's perfect will to be done and not permissive will. Tisakhaliretu ndi munthu pa mtima pathu koma tilore chitsogozo cha Mulungu
@MrMagombo6 күн бұрын
TATOPA NDI CONGRESS
@JulioChiwalo-t4f5 күн бұрын
A mcp ndi Chakwera avomereze alephera kuyendetsa dziko
@jackalview74916 күн бұрын
Chakwela Siya upulezident anthu akukudandaulani ndalama Mwaba zambiri
@ChanceZambika6 күн бұрын
Abishop mwayankhula chilungamo amene akukondwera ndi fiti
@MarthaDeborahMhango-sx8dk6 күн бұрын
Mmmm sizikuyenda ndizoona tikulira mokweza
@ChrisyMbewe6 күн бұрын
Emen
@RoseThindwa6 күн бұрын
Zoona sitinasakhe moyenera results ake ndi awa Malawi's kulira mavuto ambiri chili chonse chakwera
@ChanceZambika6 күн бұрын
Kma mcp yatikwanaa
@Littlefair74 күн бұрын
Wansembe wabodza uyu, nanunso munali patsogolo kung'alura APM, lero mukunyoza Chakwera, mawa mudzanyozanso yemwe akubwerayo, ansembe mitu yanu simagwira.
Koma ndi anthu ambiri akukudandaulani inu a chakwera..tsokatu ili
@DavidPhiri-o6w5 күн бұрын
Soon a bishop muzakhala pakati pa opposition alliance kodi tizakukhulupirireni kuti mukukoza or kuwononga? Chifukwa few years munali nawo pa mugwirizano wa tonse koma chinamubale is happening you don't come to rebuild. I am losing hope in you father bishop
@isaaczuze5 күн бұрын
Anthu nthawi ija samaziwa kuti chakwera ndi mbuzi Taonani kukwera Kwa zinthu .....kusowa Kwa mafuta agalimoto ....njala ndiye ndi iyi chakwera ndi munthu woyipa kwambili ndipo munthu wokuba .....Ife sitimaziwa kuti zinthu zingafike apa
@CatherineMunthali-r1f6 күн бұрын
Tikavota mwakathithi
@AchimMdala6 күн бұрын
Ndikukhulypilira zinachita bwino kuti kusogoloku tizaziwe ubwino ndi kuipa kwa anthu ena
Arugula yanuyo pitani nao uko zoonad zinthu zikudula paliponse koma komwe kukudul zinthuko ulamuliro wawo wabwino osati zaugaru zasatan zili ku Malawi osauka athawira kutiko ulamuliro opepera ndpo suunati satana nae sapwekesatu ationesa znthu sanatic leadership
@CatherineMunthali-r1f6 күн бұрын
Boma ndilomweli lolephela
@EDSONNAKULENGA5 күн бұрын
Kkkkkkkk komadiyetu mwazidikilatu zilibwino mbomaili dilaziwada pakana so antuopepela kumanamizilakufa pa 10 paji kumwabakutivuta
@isaaczuze5 күн бұрын
Chifukwa choti iwe ndi mbuli ndi chifukwa ukuti zili bwino .....chakwera waononga ziko ili ....mbuzi ya munthu imene ija
@IshmaelMakamba-gb8pu6 күн бұрын
❤❤😅
@PolinaChilasaКүн бұрын
Kwayine musanamize akhristu kuti bola adadi monga mukunenera apa ayi. Kodi titero kuti kuphedwa kwa malubino zinalibwino kwainu? Kuphedwa kwa amasambuka zidalibwino zoona? Mmmm mafutawa sadasowepo munthawi ya dpp? Nanga kuba samaba amenewo? Ndivomerezane Nanu kulimavutodi koma tisanamize anthu kuti solution ndi adad..
@WisikiBlack-gj4guКүн бұрын
Iweyo ukukumba izi mcp zomwe yachita ungaifananize ndi dpp
@ShamimuBisani6 күн бұрын
Lero misazo zili kutiko makolona amene munamchosera Peter anataika kapena mademowo alikutiko sopano mukapanda kupanga kuthekera komchosa satana wanu munamuikayu Mulungu akukanthani nonse take it or leave it
@MarkGonda-qr4vm6 күн бұрын
Mmmmmm kupanga kothekera kwawina aliyense mavutowa afikira wina aliyense let's come together and sot out issues
@ShamimuBisani6 күн бұрын
@MarkGonda-qr4vm broh anali ma flont line anthu amenewa ndizoonad tonse tikukuman ndizopsinja abweres ayambe tasatira
@MarkGonda-qr4vm6 күн бұрын
@@ShamimuBisani yaaaa it was mistake and now they are regretting and what is needed is to come together and sot out these problems
@ShamimuBisani6 күн бұрын
@MarkGonda-qr4vm wow this is hard to undestand may God help us the suffering is too much
@MarkGonda-qr4vm5 күн бұрын
@@ShamimuBisani zoonadi braz
@Ramosfresh6 күн бұрын
Sizaubusa izi... izingodyani tsembe musaphatikize ndi za dziko lapansi
@ShillaShamil-v2y6 күн бұрын
Akuyenera kuyankhula akuyeneranso kuphatikiza
@Malawian-q5f6 күн бұрын
Nawonso ndi anthu , ali ndi achibale ndipo akumva kuwawa
@RemitterFlik11306 күн бұрын
aaaa iwe yo ndiwe oweluza? Ndipo panzonse zomwe akuyankhula apazi chomwe akunama ndichani musakhale anthu odana ndi choonadi
@MCHopeson6 күн бұрын
Koma azipita ku state house azilandila ma brown envelopes ngati azibusa enawa???
@ABWINOALIKUTI5 күн бұрын
Zoonadi abusa chifukwat eeeee zavutu
@DavidPhiri-o6w5 күн бұрын
I am losing hope namu pano can you. Bishop don't just blaming please also nthandizani even zipani like DPP especially Peter muthalika he is doing nonsense but you don't talk before. Please avoid waiting things to be messed up. Now don't just criticism ruling government look also to the party. Always Malawi making big mistake you wake up when things are going wrong ket try to fix as early as possible
@isaaczuze5 күн бұрын
Nawenso ufuna uyankhule kuti chiyani apa ....chakwera ndi mbuzi ya munthu ndipo waononga ziko ili .....taona kusowa Kwa mafuta.....njala ndiye ndi iyi nanga kukwera Kwa zinthu .....aneneli amulungu akunena zoona ......chakwera wakoyo ndi chisilu cha munthu
@isaaczuze5 күн бұрын
Osalemba chichewa bwanji ....ukulemba broken English apa ..umbuli basi
@mutumwathongethonge78926 күн бұрын
Kwa inu mzimu wachidziwitso mulibe. Mwadziwa liti kuti mademo amene aja anali a Satana? Muchotse zimene munaikazi, because you supported this.
@MarkGonda-qr4vm6 күн бұрын
Mmmmmm oyenera kuchotsa ndi ifeyo kukavotatu basi musakhale ngati mbala pamtanda kuti unapulumutsa ena zipulumutse wekha aliyense amalakwitsa
@HappyAbyssinianCat-xt2bm5 күн бұрын
Km chakwera iwe ana amulungu azikudandaura chonchi umunthu ulibe wazunza amalawi mokwanira km mulungu apeleka njira zokuchotsera iweyo
@Yobe-on7ml4 күн бұрын
Akatolika mwalowa muzimu oipa
@WatsonMsukwa-y5i6 күн бұрын
B😂😂😂😂
@DavidPhiri-o6w5 күн бұрын
Unalephera kumanga mugeirizano nthawi ya Chilima ali moyo. Koma panthawi ta tonse munalipo bwanji wosayankhula zanzeru that time. Some time pano titaya nanu chikhulupiriro. UTM yalowa mumavuto a bishop mukuwona bwanji wosawKhazikitsa ngati muphatikira pakati wa dziko
@anoldkapolo44935 күн бұрын
Siyani unsembe dzayambeni ndale kuti mudzadziwe mmene dziko limayendera. Inu kuguwa mungobisalirako koma tikudziwa ndinu chidzukulu cha APM. Ngakhale ku church komweko mukumalanda zinthu zochuluka kuamphawi pano mukupanga kampeni. Km sindingasite chikatolika chifukwa choti mwalowa ndale . Chakwera more fire ndipo alamulabe. Ife timalima ndipo tikupeza phindu pa zolima azathu. Atiberakochiuluka atsogoeri apitawa. Ansembe Inu mukupanga ndale ,bwera oaground kt zainu anthu akulankhuleni mosakunyengererani chifukwa ifeyo mukayima kuguwa mkumakamba zonamiza anthu ku sapota xipani zotsutsa tikulepheta kukuyankhani. Bwerani poyera siyani zausembe. Ifeso ndi akatolika koma osatisokoneza nthawi yoti tipembedze mulungu
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq5 күн бұрын
Kuva ndikuvesesa ndizithu ziwiri zosiyanadi,,mavuto onse akunena apawa alipo kapena kulibeko akungopeka?Mukupinduladi ndiulimi kodi ndiangati akupindula ndikukwera kwafertilizer?mukudya koma neba wanu sakudya mumava bwanji and nanga wakutali emwe simukumuona,,,Vomelani and chosani maganizo oti aliyese angazuzule kulephera kwaboma ili ndekuti wa ford,utm,udf or dpp,,Uchitsilu wanu musauonesele pagulu,akondeni ena osasapota manyi akununkha kamba koti wanyera manyio ndichakwera
@HappyAbyssinianCat-xt2bm5 күн бұрын
Kod iweyo dziko lonse limadya pakhomo pako, ana amulungu alephere kulankhura chifukwa cha inuyo iweyo chichristu chako chili pati m'mene anthu ena akuvutikira kumalawi uko mwana wanjoka iwe
@isaaczuze5 күн бұрын
Nanunso achisilu inu .....chakwera wakoyo kuti akhale pamene alipo ma bishop anatenga mbali ...mukufuna chakwera apitilize kuononga ziko ili .....sizithekatu
@deusdeditpatrick33434 күн бұрын
I dont condon this-preach the Word. As a pastor you do not show sides. Its people like you who divide God's people. Watch what your mouth can do. Never use the pulpit to gain your side. I am like you but l will not speak like you. Know that you represent everyone in that congregation. I am sorry for you. Time is still there though to change the way of preaching. Be inspired and speak what the Lord says not what you want to say. The church is neutral and lets be that way. The assembly that you lead has many political colours. Do not choose those who wear with you the same-there are many in those places. You can better my brother priest than this. Lets preach the Word not people.