ndipo mulungu adzidalisa zimu wa chilima every time ⏲️ ♥️
@PhilomenaChikabadwa-dt6vy3 күн бұрын
Mulungu ndi mmodzi president amakhala wamipingo yonse.
@Alexchinangwa-k2q3 күн бұрын
komaso zimu wa kabambe ❤❤
@MaulanaIriyasa3 күн бұрын
Kodi paja akhilisi tunu paja WA catholic. Seventh day. Aroma Anglican. Living waters. Mboni paja simungakhale Malo a modzi 🤣🤣🤣🤣. Am proud to be Muslim palibe zikiti ndngaolesedwe ku pemphelo I chichi ndiye chipembedzo ndithu
@VeronicaTime-jn7fp3 күн бұрын
Ndi m,busa wabwino uyu atiphule pamoto tilinawowa
@Alexchinangwa-k2q3 күн бұрын
ineyo kabambe ndili pa mboyo pako chifukwa choti zimu wa chilima umadandaula pa dzomwe chakwela anamupanga dzona ungaphe chilima for the why