Wina Ndinamuthyola Khosi - Samuel Lwara

  Рет қаралды 42,119

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

28 күн бұрын

On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara tells his side of the story about how he found himself evicted from a Malawi Housing Corporation house for what he believes to be political reasons.
Ku Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara akufotokoza mbali yake momwe adapezekera kuti akuthamangitsidwa kunyumba ya Malawi Housing Corporation pazifukwa zomwe akuganiza kuti ndi zandale.

Пікірлер: 58
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 27 күн бұрын
Aaaa Mr Rwara akudwala misala ayi ndi munthu wabwinobwino komanso zoganiza wachita bwino kupha chigawenga awona polekera osafooka Mr SKC my vote ❤❤❤❤
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 26 күн бұрын
Ndipo ndikudabwa anthu kungozolowera kutukwana ali zotukwanirana apa usavechi basi osangoyankha popanda kutukwana mutemeka?? Mumatibowa ife ndi khalidwe lanu lonunkhalo phunzirani kulemeza amnzanu big up Mr Rwara SKC my vote ❤❤❤
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 27 күн бұрын
🎉That's chimwendo and mkakas gungsters
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 25 күн бұрын
Lwara plz Chilima akutayitsa nthawi...sangamake pa APM
@rexnyalugwe4910
@rexnyalugwe4910 26 күн бұрын
Im confused: in one of his interviews he mentioned kuti anasiya ntchito ku state house as a gardener because samafuna kumalandila ndalama za ulele( he was just appointment but he never reported for work) but now in recent interviews akhalangati he is bitter kuti wachotsedwa ntchito. Timve ziti?
@user-fb6kh2dk1y
@user-fb6kh2dk1y 27 күн бұрын
die hard man eeee
@user-pp4kp8ib7k
@user-pp4kp8ib7k 14 күн бұрын
Why can't you report ku police bwanji kape iwe wayamba misara etii. That's the power of Nyaope
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 7 күн бұрын
Inu mukuti chakwera ananena kuti akhesa mwazi wapha chirima kalwara nkachani mukukondwa ndi zochita chakwerayo ? Sinthawi yomuopa chakwera anthu akufuna avuuke mumavuto amene chakwera wabweresa mdziko ndiye apha anthu angati iyeyo musamupase matama galuwanuyo chakwera
@MacnealNsunza-tf6cg
@MacnealNsunza-tf6cg 26 күн бұрын
Mukanatenga makiyi
@Alomwe
@Alomwe 25 күн бұрын
MCP is MCP sinasinthe still evil
@paulbanda9638
@paulbanda9638 19 күн бұрын
Lwara akuoneka ngati ndiwausilu, ngakhale ngati pali school aaaaa ndikukaika,
@jamesgama5489
@jamesgama5489 26 күн бұрын
Mcp akupha lwara nthawi ya zisankho chakwera ankanena kuti akhesa mwazi ngati zisankho siziyenda bwino nde iwe lwara nkachani.
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 26 күн бұрын
Tamba nawo koma popedza inu ndiwa MCP nde mukuyidzawa kele kuti ndimagadzi kuyambile kele kale paka pano tsinasinthe pofunika mutsamale dzedi wa dada
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 18 күн бұрын
Munachita bwino bwana kunthyola anatumidwa amenewo MCP chipani chakumpha lelo siizi
@Littlefair7
@Littlefair7 26 күн бұрын
😂😂😂, Lwara ndi deal, muzingoona ma comment a MCP, koma chonde fellow viewers tiyeni tizingosutsana popanda kutukwana.
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 27 күн бұрын
Kkkkkk
@ZaithwaBanda
@ZaithwaBanda 26 күн бұрын
Misala iyiiii sizikuveka
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 26 күн бұрын
I laugh so hard kkkkkkk ati ndamuthyola khosi munachita bwino
@Jasper-xk9iv
@Jasper-xk9iv 8 күн бұрын
Mukhare osamala plz
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 15 күн бұрын
Koma ukhale mosamala abwelaso😢😢
@mafukenimasangwi5487
@mafukenimasangwi5487 23 күн бұрын
Vuto lake kukonda ndalama mulibe mphamvu muzingo wauza otumawo kut azipitako okha amawopa ko chiyan muzingo phedwa kusiya ana a kuvutka iwo anawawo nkuma sangala
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 15 күн бұрын
😂😂😂 more fire anafela dzaeni
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 26 күн бұрын
Pena sikumveka ngati zoona komaso ngati kabodza choncho
@jameschidafumbwa1039
@jameschidafumbwa1039 24 күн бұрын
Ndi a MCP amenewo atumidwa ndi nduna
@JefreyMtambo
@JefreyMtambo 2 күн бұрын
Ur time is coming coming
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 26 күн бұрын
Ipatse moto mr lwara?
@macleanmachamo
@macleanmachamo 27 күн бұрын
Ndinu mbuzi inu
@user-xf6hp3ik8r
@user-xf6hp3ik8r 14 күн бұрын
Kodi chete wakhala mkuluyu,sanadye chibanzi?
@nkhwaziaeros1845
@nkhwaziaeros1845 24 күн бұрын
Koma nkhani zake🤣🤣🤣🤣🤣 good story telling baba. Munangogwira ndikukufinya khosi🤣🤣🤣 paja its so easy to cheat malawians . Lol tiyeni nazoni
@danielmwatchipitsa7442
@danielmwatchipitsa7442 19 күн бұрын
Ndiwe mfiti ase
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 26 күн бұрын
Ur campaign is on the right the only unfortunate thing is the one ur campaigning for made a mistake for making an alliance with bad guys hence the bad reputation. But I HV that feeling also that he might be the right guy
@FatimaLuwembe
@FatimaLuwembe 5 күн бұрын
😊😊❤😂😊❤😊😂😅😊😊
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 27 күн бұрын
Mr Lwara must be sick mentally. His story is not adding up.
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 27 күн бұрын
Wachita bwino kupha zigawenga
@chizzzandazzzi6693
@chizzzandazzzi6693 26 күн бұрын
Waboza mmm😂
@marryphili5419
@marryphili5419 27 күн бұрын
Zofuna zimenezi iwe wungamasapote mbamva for what
@ZaithwaBanda
@ZaithwaBanda 26 күн бұрын
Khaaaaa lwara akunama iyeyo sanakuwe ,ok nanga khosi anathyolalo maliro ake alikuti, amalita ameneyo
@VincentAndrew-jz2gf
@VincentAndrew-jz2gf 10 күн бұрын
Chitsilu galu Wachabe chabe fokofo
@IssacMateyo
@IssacMateyo 26 күн бұрын
Kkkkkkk koma akulu awa kampeni imeneyo kufuna kuti ena akhale ngati akuwasaka kkkkkkk zazi
@francismagombabaisi5606
@francismagombabaisi5606 26 күн бұрын
Kkkkkkkk anamuthyola khosi 😂😂😂😂😂😂
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n 26 күн бұрын
zikundimvekera off key😏
@EllenNamulu
@EllenNamulu 15 күн бұрын
😅😅😅😅😅kumatchola kumene
@antonychika15
@antonychika15 26 күн бұрын
Nde munthu ungadutse mbava zikulowa mnyumba mwako muli ana ndi mkazi wako cholinga ukafuse driver kuti mukudzatani kkkkkkk MISALAA CHANI?
@RaphickBanda-hz4gx
@RaphickBanda-hz4gx 27 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 Malawi Ngokomaa
@chipanganofackison5185
@chipanganofackison5185 14 күн бұрын
Ndiwe mbuzi kwabasi 😂 Nonsense
@mellipherjohn7158
@mellipherjohn7158 10 күн бұрын
kkkkkk
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 26 күн бұрын
Kukula konseko osamanga nyumba yako chitsiru iwe
@mailos.laisoni7001
@mailos.laisoni7001 25 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkk inu
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no 16 күн бұрын
Zikugwirizana chian, bola iweyo poti sudzakula , user
@danielsulani8689
@danielsulani8689 27 күн бұрын
😂😂😂
@ZaithwaBanda
@ZaithwaBanda 26 күн бұрын
Kkkkkk 😅😅a 😅😅😅😅lot 😅to
@brimngosi1533
@brimngosi1533 13 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@robsontyg3928
@robsontyg3928 26 күн бұрын
Nonsense
@robsontyg3928
@robsontyg3928 26 күн бұрын
Wamisa uyu mbuzi ya munthu, anthu akumpoto ndi anthu ozindikila asapepele chifukwa cha galu iwe
@JamilahMaluwa
@JamilahMaluwa 22 күн бұрын
Zachamba
@IssacMateyo
@IssacMateyo 26 күн бұрын
Kkkkkkk koma akulu awa kampeni imeneyo kufuna kuti ena akhale ngati akuwasaka kkkkkkk zazi
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 26 күн бұрын
Kkkkk
孩子多的烦恼?#火影忍者 #家庭 #佐助
00:31
火影忍者一家
Рет қаралды 21 МЛН
Wait for the last one! 👀
00:28
Josh Horton
Рет қаралды 120 МЛН
Haha😂 Power💪 #trending #funny #viral #shorts
00:18
Reaction Station TV
Рет қаралды 15 МЛН
EFF NATIONAL CHAIRPERSON | VERONICA MENTE | ON RUSSIA TODAY (NEWS) |
18:49
Economic Freedom Fighters
Рет қаралды 4,9 М.
Chisankho Sichibeledwa Tsiku Lovota Imakhala Process - Bon Kalindo
15:53
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 74 М.
BON KALINDO 28 JUNE 2024
15:06
Deorccovert
Рет қаралды 1,2 М.
Nancy vs Che Nkope - Impi Biyeni Ause Muntendere
26:03
CHE NKOPE
Рет қаралды 12 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
Mbiri ya Joyce Banda
16:55
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 54 М.
孩子多的烦恼?#火影忍者 #家庭 #佐助
00:31
火影忍者一家
Рет қаралды 21 МЛН