pephelo bale uyu wapita kumene ndi week sinathe tionetseni apanga za school za agriculture tionetseni alimi anapita kalekalerewo kuti akukhala motani mutionetse atha miyeziyo ali kudimba tione kuti agwilako bwanji agwila nthawi yaitali bwanji komaso palizabwino pamankhala zovuta tione kuti muwafuse kuti akumana ndi mavuto aji tifuna tione komaso muyankhulane ndi anapita kalekalewo
@JasonNdaba-zs7rm3 ай бұрын
Zikomo guys ndikubwera next trip tidzakupedzan proud ov u guys
@petersekani98083 ай бұрын
Awesome guys..tasilila oneday hope will meet there
@Sunnygw2603 ай бұрын
It's 2024 let's gather here and listen to this and like this
@user-tu7sh3ss2f3 ай бұрын
Nice stay.. missing guys
@daisykay6883 ай бұрын
Can't wait for my turn,all the best koma anzathu
@preciousdiyere92843 ай бұрын
Nice one lsee
@user-xm4pz5hu5r3 ай бұрын
Powerful 🎉🎉
@mphatsochitimbe22053 ай бұрын
This is amazing,,,,May God Guide and protect you, inuyu ndima millionaire basi olo ena afune asafune inuyo mwaiphula basi
@PhilliphofenKuwanje-fs5wy3 ай бұрын
Nice ,,,,
@enockdickson41822 ай бұрын
God bless you guys, and protect as well
@faithkamlongera51283 ай бұрын
Great
@user-rg4du4vu9r3 ай бұрын
Munthu ngovuta moyo uno kumapanga chomwe wachiwona kt kwaiwe miriphindu ukayendera zot akut chani utuwa vuto ndirot enewo akungoziwa kunyoza km kuthandiza munthu sangathe god bress you guys
@GodInks2 ай бұрын
Bafrep my guy..!
@user-eg8wx8oi5z3 ай бұрын
i personally know this guy is my nebour
@user-qw4pk7wj8i3 ай бұрын
Zonamaz guys uyu asakunamize uyuuu watotumidwa zaboza ask me
@CollessTambala3 ай бұрын
No akunena zowona Israel is well advanced in everything
@atholechiwala99973 ай бұрын
Phawafu. .. work hard and represent us...
@wangachindeya85773 ай бұрын
For what? Zachisoni
@nicksonjohnjumbe83823 ай бұрын
Nafenso ku jonz tikunjoyanso tinabwelanso tokha sizotengedwa ngati ukapolo. Big thanks to you guys I wish you well
@alickkachepa38013 ай бұрын
Kuypatsa moto paja 🤣🤣
@JeremiahPaulNgalawah3 ай бұрын
Kamtima aka sakangakupindulisen
@JusticeBornNdhlamini-fp7ic2 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@user-um6dy1kr8t3 ай бұрын
What about the laptops, anawagulilaso ?
@victoriazomba16743 ай бұрын
wish u well my pipo
@EditahLaundanАй бұрын
My dream 😊
@MichaelChisambi2 ай бұрын
God first ;party less and invest more at home!we are proud of you!
@user-wp2yp3vh6b3 ай бұрын
Good news
@user-oe5kj6rb5b2 ай бұрын
Nice
@masterchitabwino898Ай бұрын
Mwayamba kunyozatu mmm khalani ndi khalidwe
@AmosMarkko-fp6pg3 ай бұрын
Chipe voice eeeee ! Loud en clear koma Boyz
@BLESSINGSPEARSON3 ай бұрын
Ok
@user-rn9cd3be6k3 ай бұрын
Nanga mowa simumwako ma weekend 😂😂😂
@PeterGabriel-uh2lh2 ай бұрын
how can be there be safety pomwe nkhope tikuiwona direct
@josephychikaonda67013 ай бұрын
Not bad...
@grantgphiri70853 ай бұрын
Ndiye kukungo woneka ngati kuyudeyatu 🤸🤸🤸
@Isaactembo11113 ай бұрын
See you there
@samiljames57193 ай бұрын
Tipatseni link yobwera kumeneko
@amabhohlela.34923 ай бұрын
5yrs..azikazanu akukudikilani
@elizabethsokoe26353 ай бұрын
Muzilyala ma bed oyaa!!! Inu ife tili ndima iconso kuno ku jozi and with remote control
@wabitha97693 ай бұрын
Auze zoonad 🎉
@user-rc2wo9bm9w3 ай бұрын
Power of chimidzi
@BlessingsGoma-zc4rl3 ай бұрын
Boys are enjoying
@KunyengaMoyo2 ай бұрын
Ndye akubitsa dzina why??? 😂😂😂
@lusungubanda82803 ай бұрын
Ati sinditchula dzina koma nkhope taiona aaaaahhh
@user-iy7oh7hf4s3 ай бұрын
tsiku lopuma limodzi pa week, mbola.
@godfreylungu3 ай бұрын
Ndikuona kuchedwa ambuye nditsogoleleni visa yanga ituluke
@estoniamoffat86333 ай бұрын
Zitheka osadandaula..we all want to go koma ndikuona kuti government likuchedwesa ngini
@NoelKaferawanthu3 ай бұрын
Uku nane ndipiteko ndithu
@chiccochimwaza47913 ай бұрын
Thanks for the video, I think anthu okamba mbwelera awonere this video , anthu amayankhulisa zosakhala bwino
@JeremiahPaulNgalawah3 ай бұрын
Sangayankhule or kupanga forward kut tionere ambiri amazilowesa ndale
@zabulirani3 ай бұрын
This is fake and akufuna kupusitsa anthu Let me tell you anthuwa akukhala bwino but kuli mavuto Let me send you text ya one of my friend mpaka pano foni yake sipezekaso
@Fortu_neDrSabba3 ай бұрын
Kodi a Manzy muliso ku Israel?
@josephchitsulo58823 ай бұрын
Akapolo inu, munagwidwa ukapolo ku Malawi kuja kunkananu kumeneko, malipilo anu simukuwaziwa, izingolilani ndi mtima
@macdonaldchimodzi27913 ай бұрын
Ukapolo wawo nde ma million nde akulowatu inu muli busy kuwanena apa🤣🤣
@josephchitsulo58823 ай бұрын
@@macdonaldchimodzi2791 life is very tough kumeneko Sir about expenses, kwa anthu osaziwa amangoti nza boh boh, i've been in Dubai very rich country but eee! Bolanso konkuno ku zinafibia kuno
@user-om4jo7cx8c3 ай бұрын
😢
@johnsonminandi14103 ай бұрын
Ena zachilendo mix furij kuziwira ku izilayero zodabwino kwa inu
@DungaNya3 ай бұрын
Makape inu ntchito yosafuna kujombayo
@nego50053 ай бұрын
Si onse akukhala kumalo abho
@zabulirani3 ай бұрын
This is fake
@mphatsochitimbe22053 ай бұрын
Mukunama ankolo you don't know israel
@LesterChiwayula3 ай бұрын
Achina Bally aku 24 muli yudeya kodi
@user-nu1dj3jh7b3 ай бұрын
Inu muli ku paladaizo sizakuno ku south africa aaa nkhanza zokhazokha
@simphiwechakana63372 ай бұрын
Mwatilimbikitsa
@HopesonJailosi-vd6ou3 ай бұрын
Nkhani ndi ndalama akumalandira anthuwo asiya mabanja Kuno mabanjawo akuthandizidwa?
@JaneMoyo-ws2di3 ай бұрын
Akupanga za chani actually?
@KhadidyaRichard-jq5td3 ай бұрын
Hybo
@rashidadan25333 ай бұрын
Madolowo alibo
@user-cb2cv9fz7m3 ай бұрын
3'2 million Koma rent ,kudya zaziii,mukumakhala ndi ka change , things there very expensive there mabobo abwino guys
@PempheroTomasi2 ай бұрын
Zonsangatsakwambiro
@user-kw7wr4kq9w2 ай бұрын
Stop undermining Malawi my buitiful land ❤
@ChamalizikaJoseph-ph1sr3 ай бұрын
aliyese akujoya sayiz yake ndi Malo ake
@user-mv8mc6tz1s3 ай бұрын
Muauzeso kt katundu amupezayo amusamale kt azawoso azagwiritseko ntchito vuto la Malawi uve,kuononga careless, chonde let's take care tisamachite kudzionetsera kt tazionera kukulu 🤩
@Tabie80212 ай бұрын
Koma Ka clean kakufunika pang' Ono coz eeeh.i can see the house is beautiful but kaumve kalipo ndithu.
@edfrenkampala73422 ай бұрын
100%true take care and be smart
@ConfusedAtv-bs4gc3 ай бұрын
Ndimufunseko ameneyu ndinzanga Koma Moyo wake Mene amakhalila ndimene amazifilila zoti angakagwile ntchito kumunda munthu sungamvese kwanu Kuno iwe umati sungakalime chifukwa kwanu kuli antchito lelo ukuti ukunyoya nditchito yomwe umati kwanukuno sungagwile waliwona dZiko line limakhalila
@Fortu_neDrSabba3 ай бұрын
We hustle were there is Money bro. Fvxk
@RabsonPhiri-og5je3 ай бұрын
. Zabwino kwambiri ambuye Jesus alemekezeke
@user-nb8wg3fh4u3 ай бұрын
Munagwidwa ukapolo ndi chakwela pa jozi anthu akuwufila
@user-lr5bz7qk2d3 ай бұрын
Kapolo Inu
@JustinLPhiri3 ай бұрын
Nafeso tikunjoya kuno Ku joz ndalama zilikuno ndikulandila R10,000 per month
@mussabizymaunde19953 ай бұрын
Osatchula dzina for his own safety koma munthu nkhope ikuoneka??? What kind of drama is that
@garrynsikula45723 ай бұрын
Show us kumunda
@Adzukulu3 ай бұрын
Wul arrange
@mcfersonmasingi14183 ай бұрын
Zabodza
@connexchifundo80263 ай бұрын
Midzingolankhula chichewa
@grantgphiri70853 ай бұрын
If possible tango ndi jambulirako nyumba ya uja adakwatila akazi 700 and 300 hundred girlfriend 😅
@victorbanda90393 ай бұрын
Chakwera mpaka 2030
@patrickkphiri42373 ай бұрын
Zamphamvu
@grantgphiri70853 ай бұрын
Ku Israel ndi mpesa okha okha Kulibe okudya nkhumba uko 🤣🤣
@user-mq1mb4lk3m3 ай бұрын
Zamphavu
@user-bi8vn7lb4b3 ай бұрын
Zaboza basi azanu akutika zoona
@danielproro27793 ай бұрын
Fred barley
@collennyadile81793 ай бұрын
zoziwonela ku ukulu zovuta
@user-xy4hq6sx7v3 ай бұрын
Vuto lomwe ndinalipeza kwa ifeyo a malawi timangotchulako zabwino zokha zokha mwachitsanzo kunokonso ku joni kuli zokhoma komanso kuli zabwino kuli ena akuvutika ukuku moti awawa angowatukwanapo
@user-sp8ql2st5u3 ай бұрын
Kunotso ku joni tikunjoya dzimangotingela ndi kt ndiwe otan
@petermagwira55833 ай бұрын
Am single 🥴
@user-jw9np3kt9b3 ай бұрын
😂
@user-ty1vq9lq6w3 ай бұрын
Tionetseni komwe kukukhala alimi
@user-gk5ok6xp7w2 ай бұрын
KOD mwana wa aballe
@amabhohlela.34923 ай бұрын
ALIMI,,osamatiputsisapo apa!!kuti musangalara hahahahahahaha!!!munama inu..timadobadoba mufuna kuti mtima udzitiwawa!!!akulandani ma Passport inu,,,show us ur Passport.
Chokani machende anu mwalembedwa ntchito ndi a mcp mwapwala anu
@user-dn5sf3md5t2 ай бұрын
This is politics, awa achita kutumidwa palibe akunjoyako uku guys ineyo mzanga akukhalira kidandaula komweko kuti ndikanaziwa sindikanabwerayi , bodza ili awa atumidwa
@linneausmsiska11842 ай бұрын
You find maybe the signed NDA not to say what really happens
@mafukenimasangwi54873 ай бұрын
Azisilila amene sanayende osati ine nafenso tikunjoya pa RSA pompano
@mphatsochitimbe22053 ай бұрын
Sizampikisano ankolo tonse ndizongosaka ndalama basi
@mafukenimasangwi54873 ай бұрын
@@mphatsochitimbe2205 kumva ndi kumvetsesa ndi zosiyana
@amabhohlela.34923 ай бұрын
Is not citizen..is a foreigner National
@user-tb6yh1kx3o3 ай бұрын
In S A Malawians are living good life more than that😂😂😂😂
@mphatsochitimbe22053 ай бұрын
Bro israel osamaiphweketsa
@JafaliAjusa-zg2xi3 ай бұрын
Iweyo ukujambulawe umakhala kut, mwangolopana uko . Anthu akuvutikako kumeneko man ine truck driver ku UK
@user-nb8wg3fh4u3 ай бұрын
Go tu interview those they are working in the farm not this fake information
@user-cr3yw3pe1e3 ай бұрын
Zabwino zonse maguyeee. The only thing malawias are full of jealous & envy . Tizifunirana zabwino osati kunyozana
@user-vd6gu7tv5u3 ай бұрын
Ma dobadoba
@preciousnombo68753 ай бұрын
Ana school awa
@user-oq5rg5mz7q3 ай бұрын
Simunangonemo metse mwambamo mubwele ku south Africa muza Simba zambili I'm from Cape Town
@angelamkandawire76123 ай бұрын
Zagwilizanaso bwanji South Africa abale ,asiyeni azanu
@atholechiwala99973 ай бұрын
Olo bakha atavina i cant go to KHUVUKILAND 😂😂😂😂 ... South Africa = the slaughter house of Africa
@emmanuelchapwetekabanda15083 ай бұрын
Sitikupikisana nanu boss. We are all looking for greener pastures. Let's let love to lead!!!
@mphatsochitimbe22053 ай бұрын
The goal is financial freedom not competition,,,,,
@DanielJuly-dj2ji3 ай бұрын
Mindset yomagomera azungu sitingatukuke aMalawi. How special is azungu. Dangote akulemba ntchito azungu 🚮
@mphatsochitimbe22053 ай бұрын
Nsanje yake iyiyi dziko lathu lija kuti litukuke zitivutilapo kwambili
@user-ij9jg7cm7x3 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂God have mercy on you guys where is the ather people who went there for the first time and why you don't even show us where they are working why this is absolutely wrong and abomination