Archbishop Msusa is really a true man of God, who firmly stands on nothing, but justice. Such men of God are very rare in this peace loving mother Malawi. God will protect him against all types of plots leveled against him.
@BrightZionga13 сағат бұрын
Mau
@GoodwellWaluza-m3t14 сағат бұрын
Bishop' Nsusa anayankhula Ku church kwake inuyo kayankheni Ku church kwanu.Ngati inuyo mudavomereza report Sikuti aliyense avomereze,
@PeaceNkhoma13 сағат бұрын
Zoona...
@AgnessMarshal12 сағат бұрын
Mposo osapita ku mpingo kwao bwanji
@lifredsabiana865914 сағат бұрын
Akudyesan chithumba eti aaaaa zachamba Long live Bishop Nsussa
Long live our beloved bishop. You are truly the voice of the voiceless.
@kingsleykamwendo283314 сағат бұрын
Awa siasogoleri ampingo awa ndi aja azikwanje aja lero angovula masks ndikuvala masuti, in short azigogo ojiya pachakuti
@SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON15 сағат бұрын
Don't think kuti disputing his preaching will shut up this tragedy,mwadya zambiri kobasi..koma God I know will judge you all..don't think that you are too clever on the eyes of the Lord.
@JafaliTime13 сағат бұрын
Ndipo live
@BreezeBarry14 сағат бұрын
Akuyankha mowonetselatu kuti ndi satan
@MatiasChimsakasa13 сағат бұрын
Ndiye mwati simutchula zipembedzo mwachokera koma ndinu mudatengapo mbali pamwambo wamaliro amodzi apangozi aja tikukhulupilireni bwanji kuti ndinu mbusa kapena wazaumoyo otumidwa ndi boma
@SteveKanongwa14 сағат бұрын
Hahahaha anthu anji osafotokoza komwe achoka
@AbsalomKambova13 сағат бұрын
Eti agalu amenewa
@EugeneMatope14 сағат бұрын
The church has really spoken thus why dziko lagwededzeka!!!!!!
@henryphiri610014 сағат бұрын
Ojiya azikwanje awa. Zitsiru za anthu. Mbava kudya misonkho yathu opanda ntchito yomwe akugwira. Pitani mukalandire ndalama kwa Zikhale, ntchito mwagwira. Bwanji sanadzudzule 1992 kuti ma Bishop analowerera ndale. Mwaima lero pamenepo chifukwa cha ma bishop 1992 mbuyanu Kamuzu atafuna kuwapha. Dikirani 16th Sept 2025
@kaberaericdeo11814 сағат бұрын
The Monsignor Patrick Thawale was there at COI in his capacity as PAC Chairman not Catholic Church representative in the same time he can't speak against Archbishop Thomas Msusa of Blantyre or his own Archbishop George Desmond Tambala of Lilongwe in this death issue of late Vice President of Malawi Dr Saulos Kraus Chilima.
@JohnJacko-j4l14 сағат бұрын
Komatu Mulungu osamamusakaniza ndi bodza
@SpanciaLeo14 сағат бұрын
S bishop amalankhula kwa a khirisitu awo vuto lanu ndichiyani komatu mwachepa ndipo mukunama chifuwa mukanthidwa ndi Mulungu a bishop sanatchule dzina lamunthu why kututumuka
A very good questions from zodiac and times journalist we appreciate for your questions.
@JOYCEHMATTO12 сағат бұрын
Amene mukuloza chala abishop milandire themberero
@mussakapalamula199015 сағат бұрын
Musakane inu ndi atsogoleri Ojiya mbava. Dziwani kuti kunama kwanuko ziwalo zanuzo zizakhala mboni zanu pa tsiku lozakumana ndi Mulungu namalenga. Imfa ya chilima azibusa ndi ma Sheikh mwasanduka anthu Ojiya chifuwa cha ndalama ayi zikomo Mulungu akuyendeleni mwa pa dera.
@GonaMkuphe14 сағат бұрын
Kodi mukuyankhula, kapena kuyankha mafunso?
@JulietLizziePhiri13 сағат бұрын
Nde zikugwilizana bwanji ndikukaona maliro a Clinician?
@RuthKakathera14 сағат бұрын
Abusa abodza inu Mulungu akukantheni NDI banz mwaika kukamwalo
Sheikh mwanyali Allah akungatheni ndithu pazimenezo
@wizmalota243814 сағат бұрын
Kuyankha zosemphana mbuzi..
@AbsalomKambova13 сағат бұрын
Ndipo tionanatu
@LameckThomPhiri-r9k14 сағат бұрын
Bishop mwatidziwitsa mbuzi, Imani PA choonadi and lero atolakhani you have made mbuzi zo kuchita chibwibwi ndi ojiya amebewo bravo times, zodiac you are all becoming Brain Banda
@VincentwhiteKapeta-q4e14 сағат бұрын
This gyz ndalama zadibwa basi or kuyakhula zikuvuta kkk😅😅😅😅😂 Allah wamanga pakamwa dollar adyazo
@BrightZionga13 сағат бұрын
Bishop msusa number 1 zinazi ndi mbava agalu mukubisa bwanji mipingo yanu ndipo ndinu ojiya anyapapi
Ndipo ndizooona aaaa zopusa Basi ndichifukwa chani amakana kutchula maina ndi komwe achokela zachamba
@BlessingsMbewe-s8w13 сағат бұрын
Aaaaa ndinu agaru kobasi. Mwadya zambiri kobasi
@LuluKansonde-e6c14 сағат бұрын
Mwadya ndilama agalu inuu
@FisherAction14 сағат бұрын
Mwachoka mpingo uti nanga black box ili kut pogwa ndege munalipo munayamba kugwira ntchito after ngozi msosa sakulakwa sindinu amipingo yolondola mukufuna ndalama inu
@innocentchingoma120614 сағат бұрын
Ndinu anthu omvetsa Chisoni kwambiri, and truly a corrupted conscious is so destructive than anything else.
@GeorgePatels-go7wj13 сағат бұрын
More fire bishop Msusa
@MarthaGama-q1o14 сағат бұрын
Yankhani funso please azikulu akulu inu😢😢
@danielzitande523114 сағат бұрын
Aise iwe wa Zodiack wakhwana kwambiri iwo mu nthawi yomwe adzikwanje ku lilongwe sanakadzikinse bata ndi mtendele ndipo awa ndi ali ngati ojiya oyitanila
@RejoiceKaliya-i9t15 сағат бұрын
Aaaaaaa! Tchulani mipingo guys. That's very important. Bishop ndi aKatolika. Inu mwachokera mipingo iti? Okhulupilira??? 😮
Mayankho akukuvutani palibe chomwemukuchita chanzelu let's just take off president msusa he is man of God and he want the truth to be clear
@davidkajura312914 сағат бұрын
Nanga black box,nanga zankhalango yokwitima ? Kyala akaya mundu inyiputo shabandu Kyala ikwamula wait for it.
@FrezaMkwanda15 сағат бұрын
mudziwe kuti mulungu akukanthani asatana inu pothamangila chuma one day is one day
@InnocentKapesi-gx7yf14 сағат бұрын
Mukamabwera pa msokhano mudzikhala okodzeka, masanje enieni😂😂😂😂😂
@hourlyview422612 сағат бұрын
I support the position of Nsusa. A Shaikh wo adya bazi inenso ndi nsilamu
@DaudBonomali14 сағат бұрын
Mwapatsidwa ndalama ndindani sakudziwa
@patrickmacheso506214 сағат бұрын
Koma Chakwera wafikapo, Zoona kugula azibusa kuti ayambe kumasemphana mayankhulidwe, koma uchokabe Pa mpando 2025.
@ThomasChiwaya-qx9mf14 сағат бұрын
Kaya mvura siibwera kamba kazibusa onyengawa
@FumbwaLyson-371014 сағат бұрын
Akamati nkhani si ya zikwanje akutathawuzanji chifukwa mu kulakhura kwawo akuti akufuna mtendere mdziko so zikwanje zo ndiye mtendere wo zopusa zenizeni izii mbamva msusa walakhura za chilungamo osati za dyerazi 😂😂😂😂😂😂😂😂
@EstherBauleni-g8p13 сағат бұрын
A Bishop aponda mwala. Muyaluka nazotu izi.
@MaryPhoya15 сағат бұрын
😂😂😂😂zaziii...chimodzimodzi ndi onjiya
@RexMysonChinaghana15 сағат бұрын
Zonadi munapanga mwambo uja chifukwa munali mutapanga zoipazo don't lie to the nation you will meet justice
@Dellingsmunthali15 сағат бұрын
Akupasani ndarama Inu boma la corruption mwadya nawo ndarama zamisonkho Loko mtasiya akatolika ndife ambiri Loko mtakhara ndi mcp"
@AllanSili-q8y12 сағат бұрын
mafusotu kkkkkkkk
@MarthaGama-q1o14 сағат бұрын
Koma Mulungu alowelelepo ndithu, zikiwoneka kuti ndalama zikubisa chilungamo😢😢
@innocentjackson200312 сағат бұрын
If this was the movie Malawi would be the best seller of all years coz the one who scripted this series had everything needed to protect the mafia
@CyprilSiphiwe15 сағат бұрын
Mr friend have you understood a question ❓ bcz Ur answer is very different with a question ❓ 1 which church u from
@FelanjiTigu14 сағат бұрын
Iwowo azibusawo ndi azibusa onama okonda ndalama chomwe anga ziwe ife akristu awo sitinawatume ai amenewo sitigawamvere zizaoneka mu 2025
@marymalasha177214 сағат бұрын
Inu osalowa mu church bwa? Pot bishop anali mu church
@LuluKansonde-e6c14 сағат бұрын
Mashelkh opusa akumalawi
@FlemingsMwamlima12 сағат бұрын
Izii ndi zisiru zenizeni murungu wanji amene mumamupemphera inuyo, mwina wa Chakwera mukungoonekeratu kuti mwalandira chibazii paribe ndizaubusa apa mukuona ngati mungawapusise a Malawi muribe chisoni
@BrightZionga13 сағат бұрын
Very good questions from atola nkhani bravo
@HawaLongwe15 сағат бұрын
Tidzingova send off send off yakhurani fundo
@esnatseleman213214 сағат бұрын
INU TABWERESANI BLACK BOX NGATI MULI ABUSA ACHOONADI MABALA APOLA BLACK BOX MUKAITENGE.