Iwe ife tikufutika ndi njala palibe angapite ku mpira asanakhuteee wamvaa
@Dellingsmunthali2 ай бұрын
Kodi achimwendo ndio a bordgard akungot zunguli zunguli😆😆
@RoseChiphiri-ts8jx2 ай бұрын
Ndemwati ndi sonkhano wa president? 😂 Sorry mwatipeza tili ku phiri kowotcha makaka tigulise tikagule ufa 😂😂😂
@chimwemwechathapo64052 ай бұрын
stadium inayamba nthawi ya dpp iyo ndipo yamangidwa ndi dola za boma la dpp osati awa kuzipaka zinthu zokuti sizawo komanso zitukuko zawo ndi kumanga anthu basi
@RaymondKaumbaАй бұрын
From 2017 mpaka kutuluka m'boma osamaliza just maintainance 😂😂😂😂😂
@PrinceGodfrey-vc5vn2 ай бұрын
President kufika pamalo athu 100 osakwana 😢
@HarrisonKalonga-k7p2 ай бұрын
Chisiru iwe chimwendo anayamba ndi a dpp stadium imeneyo
@tasmania5272 ай бұрын
A DPP amangoyamba zinthu mowaphimba anthu mmaso koma osamaliza, ndalama zitadyedwa. Amangokhalira kuyika ma foundation stone kuti anthu aziti akupanga chitukuko. Achina Mombera university anthu kumalipiridwa ndalama ngati aphunzitsi koma university palibepo. Pali zitukuko zambiri zomwe DPP inapanga chinyengo. Kodi anthu inu a DPP chifukwa chani mumasapota munthu chifukwa cha mtundu? Lozano zomwe anapanga Pitala. At least Bingu anatenga ngongole ku China nkumanga stadium, parliament ndi university ya MUST. Segulani maso ndipo muyamike zinthu zabwino wina akachita. Musakhale anthu ongomuda munthu. Chakwera has a vision ya patsogolo, and you will prove me right soon.
@PrinceBlessings-bv5bs2 ай бұрын
Ukunama iwe
@pemphokatembe4432 ай бұрын
@@tasmania527hahahahahahahahaaa
@PrinceKachimanga2 ай бұрын
what an embarrasment ,ukuku MCP...EXPECT ZERO VOTES😂😂😂😂😂
@HopeNgalande2 ай бұрын
TIKUFUNIRANI UTSOGOLERI WA MPHAVU MULUNGU YEKHA WODZIWA KUSAMALA KUSALIRENI PAMODZI NDI A VICE PRESIDENT DR USI AMEN AMEN 🙏 AMEN
@HassanJameskananjie2 ай бұрын
Unyamuke uzipita mwatikwana iya dikila kenya ikubwela mpaka ku state house wooo
Ka deputy president kafupika sikangawone za kutsogolo
@EvalistoDarwins2 ай бұрын
Nsonkhano wa bank mukhondee chani?? 😂😂😂🤣🤣🤣😂😂
@CharityChikomo-hl1gz2 ай бұрын
Zonsezo apanga liti akuchoka awaaaaaa mark my words 2025 nkhondo ilipoo
@GoodsomSaires2 ай бұрын
😂😂 Ndiye ndikumati ukuyakhula ndi ndani
@PrinceKachimanga2 ай бұрын
this is the only president in malawi history ,that has terribly failed malawians......
@PatrickLungu-hq2tz2 ай бұрын
President uyu ndiwakutiko abre😢😢
@actuarialscience22832 ай бұрын
Stadium ya Peter ija mwati ndiyanu afiti inu. Inayambidwa kumanga 2017.
@ClementbWatches2 ай бұрын
Zomba sisunga makape. Anthu ali manyumba mwawo pheeee
@SamKaposa-i5c2 ай бұрын
😂😂😂😂
@modestamhango77372 ай бұрын
Zoona anthu akwathu sasekelera zopanda pake. 😂
@Blessings-b7h2 ай бұрын
Ku zomba ndie munaonetsa kukwiyatu kwambiri simunawapatse mpata anakhalako okhaokha Mbalame za anthu.
@doreenkaliati31662 ай бұрын
Za ugalu basi mbuzi zakupha munadya chilima inu tsiku lina mudzatsadza nyama yake ndukuudzani Continue Rest in peace My Chilima misonzi yosatha kwa ife 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@JohnstonNyirenda-zw6jd2 ай бұрын
Olo kulimba mtimako 😂😂😂😂 aaaaah 😊
@tomasmtunduwatha-bl6ix2 ай бұрын
zomba ndi mangochi kuli athu osanyengelela zopusa tazionela tokha
@DennisDonework2 ай бұрын
Meya umakwana akumbuseni kuti inayamba2017😂😂😂😂😂😂
@ChrispinNkusa2 ай бұрын
Ndipo mumuuze chakwelayo machende ake akandifuna andipeze muthu yemwe wagwetsa dziko la malawi even maiko akuja or vote imodz sangapeze
@clementeverson2 ай бұрын
Bora kwa oimba kwa jetu kumadzadza
@lindaphiri35432 ай бұрын
Kodi ndevu za white zi zili mfasho?
@ChriKezi2 ай бұрын
Kodi anthu aku Zomba muli busy osapezeka nawo kkk
@ChrispinNkusa2 ай бұрын
Musamunamize president cholinga chongofuna ndalama muuze chilungamo nd galu wa pasi pa nyanja uyuu
@MuhammadInack2 ай бұрын
Wasala ndi miyezi I ngati galu iwe😢😢😢😢
@EdnahShantell2 ай бұрын
Koma kunali chinamtindi eeeee🙆😝😝😝😝😝🤣🤣🤣🤣🤣
@fradricknyamula71012 ай бұрын
Meya wakikumbutsani kut anamanga Peter adad muwamalizile
@pemphokatembe4432 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂kwathu komwe ukoooooo ku Zomba.,,koma nde kunali unyinji wa anthutu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣hahahahaha uziona
@andykelvin-x9j2 ай бұрын
Anthu ake omwewo Zomba yense uja....
@dingiswayojere53202 ай бұрын
Kodi anali kunali msonkhano wa mp 😂😂😂😂😂
@christjahseenmusic23622 ай бұрын
Kķkkk stadium imeneyi or ground? Kķkkk
@fundoniccoo-fk4ld2 ай бұрын
Ndi nsokhano wa khasala or president zoona zomba yense anthu okhawo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@henrymbalame2222 ай бұрын
Kumwalira kwa Chimwendo Banda uku!,,, Wafa basi!,, After kunva voice yako!,, Zikomo kwambiri!,,
@masterchitabwino8982 ай бұрын
Panalibe anthu eti angoonesa oyankhulayo kkkkkkk mumati Chimwendo eish anthu anachangamuka pa Nyasaland
@ShaffinhoKazembe2 ай бұрын
A bambo asikono mpaka anayang'ana stadium yakeyo after chimwendo kuyankhula😂😂😂