MICHAEL USI WAYANKHA ZOMWE ANANENA A FELIX NJAWALA KU MZUZU.

  Рет қаралды 23,396

Nkhalango Multimedia

Nkhalango Multimedia

Күн бұрын

MICHAEL USI WAYANKHA ZOMWE ANANENA A FELIX NJAWALA KU MZUZU.

Пікірлер: 83
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Ай бұрын
Alibilethu nzeru,,zidya chabe ndalama,,monse muja umatani kupanga zimenezo
@stevezulu2108
@stevezulu2108 Ай бұрын
Awa wanthu si a UTM. Ndi a Wadya Zake alibe Mlandu. Usi angowaveka makaka a UTM. UTM ndi imodzi ya Akaliyati basi.
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Mwanena zoonadi
@user-vw7tj2ss3l
@user-vw7tj2ss3l Ай бұрын
Palibe chazelu apa palibe
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Ай бұрын
Usi is best leader of Malawi, chilima anasankha usi wanawonapo China chake Cha nzeru... I love you usi with my all heart God bless you
@ThokoFiliyamu
@ThokoFiliyamu Ай бұрын
Kabambe wapangitsa wina kuvala makaka a utm
@MiracleMalichi
@MiracleMalichi Ай бұрын
Ndale zotukwanizana zinatha nkhani ndiyoti mukambirane Ku UTM Kuti zinthu ziyende bwino
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 Ай бұрын
and those people are not UTM atengedwa kundilande bangwe and other areas. apasidwa ma 200 hands every one of them
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq Ай бұрын
Kodi inu chikuvuta ndichiyani kunena kuti ndi mcp or utmost palibe amene angakuvutitseni,athu akufuna kungodzowa bwana.
@Littlefair7
@Littlefair7 Ай бұрын
Dr. Usi, in Democracy the rule is simple, majority rules, UTM yatuluka ku alliance inuyo mwatsala nokha simuzikwanitsa, chokani ku Tonse, yendani pamudzi ndi anzanu.
@DysonUmali
@DysonUmali Ай бұрын
If I were Usi I would chosen one lose the vice president post or lead UTM . USI can has no power to lead UTM as a party unless he resigns as vice president and not work with MCP government. If Usi was intelligent politically he wouldn't have accepted the vice president post that MCP new would weaken him politicallly .
@CyrusBanda-l5y
@CyrusBanda-l5y Ай бұрын
Powerful speech
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 Ай бұрын
Dr Usi you are a democratic leader
@user-sh6gi5uq3l
@user-sh6gi5uq3l Ай бұрын
Mumafuna umboni? Zodana pa ndale ndizomwe zikuononga Malawi wanthu Political hatrage will not take us nowhere usi is the unifying factor
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Ай бұрын
Upange zomwe chilima amafuna kupanga ukudziwa kale kuti he was about to declare the separation for tonse alliance ndiye osatipusisa apa nthira kuwiri iweyo.
@billymhoni9527
@billymhoni9527 Ай бұрын
Ali yekha kumenekoko ..
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 Ай бұрын
Iwe dyera bambo sikono chifukwa chani iwe ukulabadira za imfa ya chilima
@user-es4jt6ds8m
@user-es4jt6ds8m Ай бұрын
Ma sapota osewa ndi a MCP akowapatsa malaya awo🎉
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
Kodi a usi mukuvalabwinotu kodi ndi malaya achilima
@fulabanda2115
@fulabanda2115 Ай бұрын
Ndalama zoopsa kwambiri
@KinziWindasoni-h4b
@KinziWindasoni-h4b 7 күн бұрын
Ulibe nthawi yobwezela pamenepo ukutani
@GiftKumbambe
@GiftKumbambe Ай бұрын
Kkk kodi magalasiwo amakhala akuyabwa
@dysonfysonchifundo2284
@dysonfysonchifundo2284 Ай бұрын
zoti UTM ili magulu angapo kod ndi zoonadi eti? 😂
@user-zw8ns7bk7s
@user-zw8ns7bk7s Ай бұрын
Ndipo musakaike😂😂
@dysonfysonchifundo2284
@dysonfysonchifundo2284 Ай бұрын
@@user-zw8ns7bk7s kkkkkk zovuta kwabas
@user-ol6uc7bj2w
@user-ol6uc7bj2w Ай бұрын
Kkk usi ase ❤
@ChikondiAmosi-ue3jk
@ChikondiAmosi-ue3jk Ай бұрын
Koma kunena Zona umu muli mzeru kungot anthu timafuna kunyonzana koma ussi muli usogoleli
@DysonUmali
@DysonUmali Ай бұрын
Usi believes money buys favour in politics but he doesn't know what the voters who are true UTM wants and the pain they are have gone through in this bloody alliance . Undiwolose ndi kakutafune)
@HaliJana
@HaliJana Ай бұрын
KOMA AMALAWI NDINUDI OVUTIKA KOBASI KUMASEKELELA ZIMENEZI ZOONA
@lazaruschitsamba8394
@lazaruschitsamba8394 Ай бұрын
inu gulu lachina kaliyati akuononga chipani muona division
@user-yk9ow5vv9j
@user-yk9ow5vv9j Ай бұрын
Very good very good Boss
@NoelKambwese-fj9io
@NoelKambwese-fj9io Ай бұрын
Nthawi yoseyija simunkalamvala jeaz ya Utm mukamvala chilima atamwalira aaaaa zochititsa manyazi
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Ndipo inu akufuna kunamiza ndani?
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 Ай бұрын
ever since he has never been in that a tire, why now ?
@JustinWBanda
@JustinWBanda Ай бұрын
Inuyo ndiwa kulu
@FredKanjere
@FredKanjere Ай бұрын
A usi mudzichita manyazi mukafuna kulankhula,ifetu zoti inu sa UTM ife timadziwa komaso inuyo nokha pansi pa mtima wanuwo mumadziwa kt sinu a UTM,,dziwani kt mwabisara mm'batata nsana ukuonekera,,,, silent big killer
@michealchaomba9761
@michealchaomba9761 Ай бұрын
Anthu opusa owombera m'manja
@davidlinerevelation3427
@davidlinerevelation3427 Ай бұрын
But the late Chilima spoke himself of leaving tonse alliance audibly
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Ай бұрын
Ndipo apa mr chikangawa ndinu azodiyaki ngat ndabale and achakwera ndikoko chaka chamawa uku akuchoka
@ModesterMbendera
@ModesterMbendera Ай бұрын
Kd uli mbali iti usi?
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Ай бұрын
Awapasa zingati
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Ай бұрын
Wabodza sitikufuna ife tili ndi Kabambe,,osatiphstikiza ndi MCP
@LysonChimutu
@LysonChimutu Ай бұрын
That's great
@YamikanChirwa
@YamikanChirwa Ай бұрын
Km inu zelu mulibe
@lucksongondwe8266
@lucksongondwe8266 Ай бұрын
Lero Limenero, Mwayamba kuvala makaka a UTM. Zopusa
@JuuuKomba
@JuuuKomba Ай бұрын
Tipaseni ngongole zo timwele mowa kape iwe
@pearsonjnrsoko
@pearsonjnrsoko Ай бұрын
Thawi zina chete ndibwino Kumanani ndi team yanu muvane
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 Ай бұрын
Tabweretsan tonse wadula apa,mukuponya za Usi yekha bwanji
@QochiweNkhoma
@QochiweNkhoma Ай бұрын
Amanganya nanunso lero mpakana mwavala UTM 😂😂😂😂😂
@BlessingsMaheya
@BlessingsMaheya Ай бұрын
Abale ako asati athu
@JohnFrank-cg1yh
@JohnFrank-cg1yh Ай бұрын
Mr utsi chisogolo chikhala chotani chifukwa utm iyima payokha ndipo ichitisa convention mukapikisana nawo,
@DysonUmali
@DysonUmali Ай бұрын
We are following with a laughing gesture factless
@user-xq1wd6wq5h
@user-xq1wd6wq5h Ай бұрын
Iwe ndiwe wacp
@FredKanjere
@FredKanjere Ай бұрын
Yes
@FarookIbrahim-c2e
@FarookIbrahim-c2e Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@jamesstevenzondannkhana1805
@jamesstevenzondannkhana1805 Ай бұрын
Convention ya utm ndi imene ikathetse kugawanikana kpmwe kulipo muchipani cha utm
@kunjemangandale1118
@kunjemangandale1118 Ай бұрын
Mukamalizile kuchitipa
@user-ck7eb7tb7v
@user-ck7eb7tb7v Ай бұрын
UTM yachina Kaliati ndi one
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x Ай бұрын
Uyu ndi Satana uyu unamusogoza iwe Galu
@IshmaelNesta-rb8dx
@IshmaelNesta-rb8dx Ай бұрын
Ka utm kabodza😂😂😂
@user-gp2zp2dj1w
@user-gp2zp2dj1w Ай бұрын
Mboli yako iweee
@ShariffAlli
@ShariffAlli Ай бұрын
Kodi abwanawa magalasiwa amakulira amawangwira ngwiratu
@AkimAmadi
@AkimAmadi Ай бұрын
Akucheza amanganyawa
@CrytonMalunga
@CrytonMalunga Ай бұрын
koma akulu mulibe manyazi bwanji
@trintasngoliwa4144
@trintasngoliwa4144 Ай бұрын
Koma amalawi dyera kumaombera mmanja zimenezi
@IshmaelNesta-rb8dx
@IshmaelNesta-rb8dx Ай бұрын
Kausiru aka ....kangonama ngongole ngongole koma sizikuoneka....wa MCP uyu
@Dentera215Music
@Dentera215Music Ай бұрын
Mzeru palibepo apa manganya uku4ira hvy
@user-rb7fs5up6k
@user-rb7fs5up6k Ай бұрын
Azimai adyela awa iiiiiiii
@trickermussa472
@trickermussa472 Ай бұрын
Mumkaoneka azeru ku tikufelanji kunjatu
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu Ай бұрын
Wabisala mbatata msana wawonekela mwazikakamiza lero kuvala makaka a utm? Chinyengo cheni cheni ndipo sindinamvele mkomwe speech yanuyu a manyanya ndangobwela kuzaponya comment yangayi 😂😂😂😂😂😂😂
@luckymalata3387
@luckymalata3387 Ай бұрын
Ngongole zake mukupereka oziwana nokhanokhazi?
@ErnestChansa
@ErnestChansa Ай бұрын
Manganya ndi ponyelela pa munthu munthu woyipa kwambili.,...amalawi ndi anthu apusa opanda zeru
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Ndipo inu osamufunsa kuti chichitikireni ngozi ija anapangapo chani monga iye wokhala wa chiwiri wake? Anali duuuuuuuu nthawi yonse ya maliro ija.
@fletcherkayira4089
@fletcherkayira4089 Ай бұрын
idyani ndalamazo
@madalitsomorris6566
@madalitsomorris6566 Ай бұрын
Nthawi yamarilo, munali zii, no Word, Why now talking after Chilima's death??
@mdyombamw7659
@mdyombamw7659 Ай бұрын
China ndi china... Panali madolo ambili koma malemu adasakha awa. Pali chifukwa, dolo amaziwa dolo
@user-hx6jl2jq9j
@user-hx6jl2jq9j Ай бұрын
Osapusisa anthu mambala iwe
@khwimamtonga954
@khwimamtonga954 Ай бұрын
VP muli zeru
@Peterchavula-e2o
@Peterchavula-e2o Ай бұрын
Gona nkuphe iweso
@MunyetaMhone
@MunyetaMhone Ай бұрын
Kachisilu aka
@peeboiofisho5254
@peeboiofisho5254 Ай бұрын
udzamva nkhwangwa ili mmutu
TONDE WADULA EPISODE 113
27:54
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 23 М.
АЗАРТНИК 4 |СЕЗОН 1 Серия
40:47
Inter Production
Рет қаралды 1,3 МЛН
English or Spanish 🤣
00:16
GL Show
Рет қаралды 17 МЛН
مسبح السرير #قصير
00:19
سكتشات وحركات
Рет қаралды 11 МЛН
ДОКАЗАЛ ЧТО НЕ КАБЛУК #shorts
00:30
Паша Осадчий
Рет қаралды 1,3 МЛН
BLANTYRE NDILANDE A DR MICHAEL USI ATOKOTA🙌🙌🙌
15:46
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 254 М.
Record Label Ya Ku Malawi, ipindula?
13:59
Sam Malvitha
Рет қаралды 11 М.
TIMES TV KUING'ALULA MBC TV - APWETEKANA AWA🙌🙌
30:44
HOT 265
Рет қаралды 19 М.
Nicholas Dausi at MCP, facing President Lazarus Chakwera
21:04
Malawi Page
Рет қаралды 141 М.
АЗАРТНИК 4 |СЕЗОН 1 Серия
40:47
Inter Production
Рет қаралды 1,3 МЛН