ZINA UKAMVA NKHANI YA UDF IJA YAVUTASOTU UKU CHIFUKWA CHOMWE ATULUKILA MU MGWILIZANO

  Рет қаралды 15,140

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 106
@MariamJaffali
@MariamJaffali 5 күн бұрын
Udf yatha basi ife tipita kwa adadi apm woyeeeeeeeeeee 💙💙💙💙💙
@HondaFredzoG
@HondaFredzoG 5 күн бұрын
Ubwino wake udf tinaitsika kale kale
@TimeAbilu
@TimeAbilu 5 күн бұрын
Kabwezeni ndalama a UDF mukhala nokha nokha, from Mangochi south west, Mcp tilibe nayo mawu, maso ali pa Adadi inu muzipanga za ndalamazo(Adadi ali pa 89%)
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim 5 күн бұрын
Abakili muluzi zoona chakwera alinazo ndalama zoti angaguleni anthuinuyo no ndiinu asatanadi
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 2 күн бұрын
Dyela limakomola.Ndipo Sumapindula ai.ASokoneza ma supporters
@JasonMailos
@JasonMailos 5 күн бұрын
UDF ithela limozi NDI MCP
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 5 күн бұрын
Udf inatha kale kale linakula ndi dyera, ayiwala awaphera shanil dzimbiri very shame.
@calvinjamal7117
@calvinjamal7117 4 күн бұрын
Wadya za Chikangawa za magazi Atupele
@isaaczuze
@isaaczuze 6 күн бұрын
Wadya mabazi atupele
@CatherineDesire
@CatherineDesire 5 күн бұрын
Ma yellow banzai or Dobi
@CatherineDesire
@CatherineDesire 5 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤕
@RosinaPatel
@RosinaPatel 2 күн бұрын
Nkhani ndi DPP basi siawa..ana a chakwera awa
@TimeAbilu
@TimeAbilu 5 күн бұрын
Kabwezeni ndalama a UDF mukhala nokha nokha, from Mangochi south west, Mcp tilibe nayo mawu
@CatherineDesire
@CatherineDesire 5 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@bornface4786
@bornface4786 6 күн бұрын
Andale mukutikhumudwitsa kwambiri
@McfallenKayuni
@McfallenKayuni 5 күн бұрын
Ndiufulu wa UDF
@BerthaMATUMBO
@BerthaMATUMBO 2 күн бұрын
Akupha chipani okha anthu akupita ku dpp😊
@YousufuJohn
@YousufuJohn Күн бұрын
ife tapita kale kwa peter muthalika
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 2 күн бұрын
Akudziwa aUDF adziwakuti mumapusitsa adatopa kwagwilitsa tchito
@S-rr1eu
@S-rr1eu 2 күн бұрын
Chipan chadyera cha UDF
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 2 күн бұрын
Mabodza ndithu awa
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 күн бұрын
asiyen apt kumen akufuna ndi ufulu wake
@thokozanindalama
@thokozanindalama 2 күн бұрын
😮😮😮😮😮
@MaryNgola
@MaryNgola 2 күн бұрын
Udf ndaituluka vote yanga ikupita kwadad basi
@YousufuJohn
@YousufuJohn Күн бұрын
ife tatuluka udf chipani chawusilu atupele ayiwale zawu president mpaka kale
@LafickDickson
@LafickDickson Күн бұрын
Udf yata atupele patumbopanu
@PatumaCassim
@PatumaCassim 2 күн бұрын
UDF yatha bas mutu wawo sugwira sizalamuliraso
@BashielSalade
@BashielSalade 6 күн бұрын
Udf ikhutikhumudwitsa
@rasheedjohn6956
@rasheedjohn6956 2 күн бұрын
Kumango limbana ndi udf basi
@DumisaniMhango-e4i
@DumisaniMhango-e4i 6 күн бұрын
Atha awa
@ChristmasChapeta
@ChristmasChapeta 6 күн бұрын
Udf kufuna kupusisidwa Ngati sakudziwa Kuti democrancy tinaimvera kuphweteka APA zafikapa sipakufunika dyera NDI ndalama kupanda app timalliza chipani
@Nelie-k4z
@Nelie-k4z 5 күн бұрын
LL 😊
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 6 күн бұрын
Mavuto alipo
@blessingssaiti
@blessingssaiti 5 күн бұрын
Wayamba manyiii
@TomatoKabichi-t1k
@TomatoKabichi-t1k 2 күн бұрын
Koma sangalime ngat inu kumeneko muzikhalila kulila chocho lipopo munthu mutu juuu mukhala aphawi mpaka kalekale
@isaaczuze
@isaaczuze 6 күн бұрын
Chipani cha udf chikutha chimenechi
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 4 күн бұрын
Kabwezeni ndalama 😂😂😂😂
@MlaziJames
@MlaziJames 2 күн бұрын
Atupele ifa yanu ilipafupi mcp ikuphani mwaonesa uchisilu wanu
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 5 күн бұрын
Machimo
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 2 күн бұрын
Zanyasa iweyo
@maidadyton2604
@maidadyton2604 6 күн бұрын
Wabaza iwe
@MonalisaMwale-c5k
@MonalisaMwale-c5k 5 күн бұрын
Wabodza ndani nanu munawaonako audf kumene kuja?
@SoundmasterElectronics
@SoundmasterElectronics 5 күн бұрын
Uyu ndi galu ntchito kususa paja mumalipidwa
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 6 күн бұрын
inu musadandaule uyo kodi ngati amalepera kwawo kukhala mp. ndiye mukuganiza kuti akhale president ameneyo musiye wadya banzi uyu, musiyeni apita inu, akafike uko ku chikangawa. Ko
@ClementsKamanga
@ClementsKamanga 2 күн бұрын
Ai kma mwagulitsa ndalama zingati
@SymonMwingitsa
@SymonMwingitsa 6 күн бұрын
Musamagwirirse mau a tonse alliance kuno tonse alliance inatha mwina yatsala ndi inuku limpopo ko poti kumeneko ndi kutali
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 6 күн бұрын
Kkkķkk
@emmanuelchikowi8786
@emmanuelchikowi8786 5 күн бұрын
Kodi a chair awathila doom mkamwa ndani ,a chair atani kutulika bwino bwino ku babulo ,azembela mtundu wa Malawi kubwelela okha mozembela a Malawi kukaphatikana ndi fano,maineeeeeee kuno ,a Charles kamphulusa, samu mpasu , a makhumula , a chair kuno zawaoneni
@RelaxCool-dp9jn
@RelaxCool-dp9jn 2 күн бұрын
Boza ili Muluzi analemela kale guyz sangakabweleke ndalama ku mcp
@TomatoKabichi-t1k
@TomatoKabichi-t1k 2 күн бұрын
Kuyakhula kumeneko big
@lyiemax
@lyiemax 5 күн бұрын
UDF inatha
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 6 күн бұрын
UDF sitilola kukhala munkhwapa mwa MCP or DPP sitikuifuna tipita tokha kumasakho win or lose period
@UseniMailosi
@UseniMailosi 6 күн бұрын
Shupt
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 6 күн бұрын
Ndpo nonsense yake yoooo​@@UseniMailosi
@MzadziWanga
@MzadziWanga 6 күн бұрын
😂😂😂😂 ali mbuuu olo ku udf alibe udindo uliwose sakukudziwa mkomwe , takasamben uko msatichimwitsep apa tangothandiziran kudya ndalama zamagazizo uku mukusakaza kachipan kanuko
@EllenGomani-i4f
@EllenGomani-i4f 6 күн бұрын
Atupele wayamba uchitsiru
@SaidSamuden
@SaidSamuden 2 күн бұрын
Uyu wadya Bazi olo za ifa ya chilima munavapo atupele kapena joyis Banda akukambapo kanthu
@TomatoKabichi-t1k
@TomatoKabichi-t1k 2 күн бұрын
Anthuyo anawuzidwa kut mcp yokupha ndiye atupele azikamba chan zawusilu
@mollymasangano473
@mollymasangano473 6 күн бұрын
Kikikiikiki Koma Atupele ngwirizano ndi A MCP malo moti awauze anthu kuti tilibe ndalama ma Supporters a UDF khani ndiyimenyo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@SnodenKambakodwa
@SnodenKambakodwa 5 күн бұрын
siwe wa lipompo
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 5 күн бұрын
Ubwino wake UDF inatha kale
@THANNAMTENDERE
@THANNAMTENDERE 4 күн бұрын
Apanga bwno a udf ubale okomela mbali imodzi aliyese ayendele yake nde ufuluwo umenewo
@ronaldordinga6537
@ronaldordinga6537 6 күн бұрын
Tiziwiseni ana anu ife
@scoltenroma6240
@scoltenroma6240 5 күн бұрын
Kodi kufika tsiku lalero munthu ungamalankhule za UDF......tizipani tonse tomwe tatchulidwato tilingati village bank.
@YusufMapata
@YusufMapata 5 күн бұрын
chitsilu yiwe udf ndichpani cholemela ndipo anthu wochikonda ndamene amachithandiza
@MandalaChaona
@MandalaChaona 6 күн бұрын
😂😂😂😂 Koma ziliko liko 2025. Koma Zipani zitatu ( 3 ) zapanga mgwirizanozo zili ndi kuthekera kutenga Boma DPP, AFFORD, UTM Gwiranani Manja ndikumanga Chimodzi ndipo mzotheka.
@MabushPaulo
@MabushPaulo 5 күн бұрын
Koma inuyo mumafuna udf ipange mugwirizano ndi chipani chiti?
@SandikondaIsaac
@SandikondaIsaac 5 күн бұрын
Kuononga chipani
@jaydee1236
@jaydee1236 6 күн бұрын
😂😂😂 simukudziwa inu this is politics
@RajaAlicky
@RajaAlicky 6 күн бұрын
Ife tmazwa kt atupele malingaliro ake Nd amenewo km ubwino wake ma members sakufuna kukhala pafupi Nd MCP so kumeneko aptako tuleleyo km ma members akuziwa kopta
@Sofi-p1v
@Sofi-p1v 6 күн бұрын
Kutha kwa udf uku
@DamaliceWamalanguluko
@DamaliceWamalanguluko 5 күн бұрын
Nanuso atupere mzafera ku chikangawa mzaona zizakuchitikirani khalani osamala kwambiri
@NicksonKotokwa
@NicksonKotokwa 6 күн бұрын
5 billion ikugwila ntchito ku UDF
@MahometAli-e8w
@MahometAli-e8w 5 күн бұрын
Udf yatha ine ndatuluka
@chrischelewani
@chrischelewani 5 күн бұрын
Muphunzire kulankhula zoona akulu inu mukunyozetsa anthu osalakwa Mulungu akuchitireni chisoni😢
@TomatoKabichi-t1k
@TomatoKabichi-t1k 2 күн бұрын
Sure
@JabulanMussa
@JabulanMussa 5 күн бұрын
Zaunsilu basi
@blessingssaiti
@blessingssaiti 5 күн бұрын
Musaiwale kuti UDF Bakiri amakonda kupepha nde izi sizodabwisa
@NickUpoche
@NickUpoche 6 күн бұрын
Udf/pp/ndi chinacho Kaya mukuti chipani cha nankhumwa ndi zofooka stikuopa
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 5 күн бұрын
Tilibe nawonso ntchito basi
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 5 күн бұрын
Atsogoleri. ndiomwe akufuna mgwrizano ndi MCP pomwe mamember akufuna mgwirizano ndi zipani zotsutsa ,,,eish! tiona
@SaidSamuden
@SaidSamuden 2 күн бұрын
Apitako okha
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 6 күн бұрын
Atupele ndi munthu oipa
@JamesIngeni-ku3qj
@JamesIngeni-ku3qj 5 күн бұрын
Anthu mukulimbana ndi udf chipani chot sichingawine ma elections or zitafutabwanji tafunani zina so zochita
@AcsonSaulos-d6s
@AcsonSaulos-d6s 2 күн бұрын
Zitsiru inu a Limpopo mmangofuna kuyambanitsa mukutumikira satana aziwanda inu
@RodwellChisambo
@RodwellChisambo 2 күн бұрын
Shame satanic iwe go away
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 6 күн бұрын
Inu a udf olo mutayima pa nokha olo mutagwirizana ndi mcp inuyo a udf mwatha komanso simuzalamula dziko la malawi inu atupele abakili muluzi timakupasani ulemu koma apa machende anu nonse iwe bakili muluzi uli ndi uzimu mmene akuvutikila amalawi mungapange mgwirizano ndi chipani chija cha magazi kod magazi aja atha? Iwe bakili uzafa movutika mbuzi yamunthu
@FazackKambwiri-he8xe
@FazackKambwiri-he8xe 6 күн бұрын
UDF Inatha inu kuli ma mp angati kunyumba yamalamulo kut mpaka anthu azinjenjemela
@maidadyton2604
@maidadyton2604 6 күн бұрын
Ukhalira maboza omwewo
@MzadziWanga
@MzadziWanga 6 күн бұрын
Iweso ukhalira yojiya yomwei kt akupase ya bundle 😅
@MalidadJaffalie
@MalidadJaffalie 6 күн бұрын
Km ngakhale zitakhala zipani 4 km ngat amalawi fe tikunva kuwawatu stinhavotele chipani chifukwa choti ilipo 4 mayazi
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 күн бұрын
Point boss
@Freedomchennl47
@Freedomchennl47 6 күн бұрын
amakili nd atupele akupanga za mabanja awo kma ngat ine sapota amene ndimachikonda chipanich kma pano bas znandipweteka pano or kumamuona atupele zot ndikonda ndkurumbila or pang'ono ndipo aziwe kut ine ndekha alipo ambri amene awtuluka a udf kwasiya agalu ameneo
@JamesAdmin-hx4ks
@JamesAdmin-hx4ks 4 күн бұрын
Atupele auze bambo wako kuti akalamba akusiye iweyo kuti uyendese ndale pa wekha ndi anthu ochikonda chipani cha UDF. Koma zokhazi mwapangazi zogwirizana ndi MCP mwalemba mmadzi vote ya masapota a UDF simuzaiona tinaziwa ife speech yomwe analankhura Bakili muluzi ku convention kuja
@SaidiEnock-z5b
@SaidiEnock-z5b 6 күн бұрын
Ife tikukoza chipani chathu tisiyeni pangani zanu inu
@TomatoKabichi-t1k
@TomatoKabichi-t1k 2 күн бұрын
Ndichocho
@joelsanthekachikuni718
@joelsanthekachikuni718 5 күн бұрын
Omwe aja ankati Chakwera wamwalira aja. Abodza awa
@MonalisaMwale-c5k
@MonalisaMwale-c5k 5 күн бұрын
Abodza kutiko?nanga unawaonapo A UDF uku
@SoundmasterElectronics
@SoundmasterElectronics 5 күн бұрын
Eya omwewa koma nanga udf inapitako?
@SaidiEnock-z5b
@SaidiEnock-z5b 6 күн бұрын
Udf sikutha ai musaipangile chochita
@TomatoKabichi-t1k
@TomatoKabichi-t1k 2 күн бұрын
Kumeneko ndiye kuyakhula mulungu akudalisen big
@YOUNGKIDS-k5d
@YOUNGKIDS-k5d 5 күн бұрын
Uyu akunama musavele wa dpp chisilu ichi UDF iima yokha zot apita ku sonkhanowo boza lokhalokha kalata inabwela kumamawa pomwe anthu kumneko amapita 01:00 to 02:00pm chitsilu iwe
@nicksonjohnjumbe8382
@nicksonjohnjumbe8382 5 күн бұрын
Naiwe wa limpopo kudziwa kunama kkkkkkk, muzinamizana konko ndambuli anzanuoo
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 5 күн бұрын
Tamatiuzani nkhani zoona wosati zamaboza apa timaona ngati mumanena zoona koma eshii lachuluka ndi bodza
@StevenMagalasi-y6i
@StevenMagalasi-y6i 6 күн бұрын
Bakili muluzi dyela
@YousufuJohn
@YousufuJohn Күн бұрын
ife tapita kale kwa peter muthalika
ZAULULIKA MCP YAPHA MUNTHU WAKE YEMWE - UYU NDIYEMWE WAULURA ZONSE
5:04
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 27 М.
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 262 #shorts
00:20
SISTER EXPOSED MY MAGIC @Whoispelagheya
00:45
MasomkaMagic
Рет қаралды 13 МЛН
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 34 МЛН
Não sabe esconder Comida
00:20
DUDU e CAROL
Рет қаралды 37 МЛН
Times Exclusive featuring Enock Kamzingeni Chihana - 19 October 2024
1:03:59
SKEFFA CHIMOTO WAIMBA NYIMBO IYI KU CONVENTION YA MCP LERO
9:33
UMBONI WA PASTOR CHIWANDA - ANANDIUZA KUTI NDINAFA KALEKALE
34:49
Charles Shonga
Рет қаралды 7 М.
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 262 #shorts
00:20