ZOMWE AZIONA DR MICHAEL USI |

  Рет қаралды 6,196

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 43
@jozyomar5361
@jozyomar5361 Күн бұрын
Mr usi ulemu wanu ine mumandivetsa kukoma mumayakhulidwe anu komaso I'm so proud of you kuti maloto anu anakwanilitsudwa and i hop more still on the way
@HopeLuwangakaunda
@HopeLuwangakaunda 23 сағат бұрын
Uku ndye kulankhula , osangoyamikira chilichose ❤❤❤
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p Күн бұрын
Iwetso garu akupha nawe
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 23 сағат бұрын
I will meet HE to send those joining politics,first to go to MSG for training.We are misguided in Malawi by kleptocratic leaders instead of philanthropic and patriotic democrats.
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Күн бұрын
zoona zake
@MauriceMukona
@MauriceMukona Күн бұрын
A Usi ndiye SKC uyu mwamutsogoza kumanda anamaliza ntchito yake?faque Mr VP 🤏🤦🐊🐊you used this 👉🛬🔨 at chikangawa shame on you sir
@PociahMack
@PociahMack 17 сағат бұрын
Good job Mr VP
@HaliJana
@HaliJana Күн бұрын
Koma sewelo ku malawi silizatha ausi ali pa tikufelanji😂 inu kumachinga Kodi sikumalawi pomwe awa angoti ngongole kumachingako kunalakwanji
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Күн бұрын
A Malawi ena ndi onvesa chisoni kumangokopeka ndi mawu basi zopusa anthu onvesa chisoni kwambiri.
@ElizabethAlick-e6b
@ElizabethAlick-e6b 22 сағат бұрын
Iwe unathandizira kupha chilima
@Maweya-e5e
@Maweya-e5e 15 сағат бұрын
wakumoto Uli kale paulendo
@JosephFulayi
@JosephFulayi Күн бұрын
Mbalame ya munthu
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er Күн бұрын
Nfundo alibe awa guys
@MerryWayson
@MerryWayson 19 сағат бұрын
Pakunya pake wamasewero iwe kufa ndekut chan kuzolowera kupha anthu ko
@Chirwa-v5p
@Chirwa-v5p Күн бұрын
abwana tikumbukuleni ana anu pambayani
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er Күн бұрын
Wachiwiri kwa ndani?paja kumalawinso kuli atsogoleri eeeeti.kuyimba kumva😅😅😅😅
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Күн бұрын
Wamisala ameneyu!!!
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS Күн бұрын
Kodi agenda Aja Ali Kuti osachigenda bwanji tseki makutu ngt chikondamoyo
@Brihippo
@Brihippo 15 сағат бұрын
Yambani kutipatsa ndalama izo
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 23 сағат бұрын
Mxeiiiiii
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 18 сағат бұрын
Palibe utiunze iwe nawetso ngwakupha wachiwiri Kwa chikangawa Galu kwabasi
@PayesaPatrick-px1ob
@PayesaPatrick-px1ob Күн бұрын
Panyopako
@anicakandiado
@anicakandiado 21 сағат бұрын
Tapangani za anthu akuvutika ndi njalawa za ngongole sizikumveka ndi nialayi
@Maweya-e5e
@Maweya-e5e 15 сағат бұрын
akulepela kuvala Za mcp bwanji akudiwa Kuti UTM ili ndi chikoka budzi iyiyi
@JovitastoloBridane
@JovitastoloBridane 18 сағат бұрын
Akupanga kutimukhale opusitsa amalawi kuti mukhalengati achifundo nda malawi kuti anthu asakuzindikileni kutimunapha chilima dikilani chiweruzo
@KENETHMAJASA-ud5ee
@KENETHMAJASA-ud5ee 20 сағат бұрын
Sweet talks koma pa ground 0/10.
@Jaccob-t3t
@Jaccob-t3t 17 сағат бұрын
Ndimavi go ukamba
@Maweya-e5e
@Maweya-e5e 15 сағат бұрын
uyu anaphadi chilima anamugulisa kuufuna mupando ndithu
@UrdPahuwa-vf8ce
@UrdPahuwa-vf8ce Күн бұрын
Kodi inu ndi nduna yoona za ngongole za need,cuz chiyambireni mukati mwapanga nsonkhano umakhala okamba za neef
@ceciliasokoh3779
@ceciliasokoh3779 Күн бұрын
Osangomuponda bwanji
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS Күн бұрын
Ufadi ndi nzakoyo kuyimbira mfiti mmanja
@Margaret-t7m
@Margaret-t7m Күн бұрын
Takapatseni chakudya anthu akudya chiteze hiyaaaaa
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Күн бұрын
Iwenso ndi mbusi ya munthu
@BlestoneJonas
@BlestoneJonas 17 сағат бұрын
Iwe manganya chitsiru cha munthu akuuzani kuti anthu akufa ndi njala ku machinga mwapangapo chiani munthu mungamupatse ngongole mnyumba mwake muli njala mitu yanu ikugwira koma
@UssenNjirinah
@UssenNjirinah Күн бұрын
Kodi awawa adasankhidwa kuti azigwa ngongole basi palibe mfundo zinazomwe alinazo???
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 23 сағат бұрын
Koma awa ka mwambi kawo ka mwana osalilaka amakakonda bwaanji
@wypatrickdakankhoma9655
@wypatrickdakankhoma9655 Күн бұрын
mbuzi yamunthu iwe
@HaleemaAllie
@HaleemaAllie Күн бұрын
Nayeso ogenda bwanji ameyo
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev Күн бұрын
Aaaaaaaa kma mbuz iy
@enocklimani1750
@enocklimani1750 16 сағат бұрын
Mfundo less
@PreciousHenderson-qc1hq
@PreciousHenderson-qc1hq 5 сағат бұрын
0%
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Күн бұрын
Inu tamugendeni kapeyo
@RajabShahida
@RajabShahida Күн бұрын
Zovala za utm tinaletsa kumisonkhano yanu ya boma koma zikuvuta pati kumva iwe chimanganya
哈莉奎因怎么变骷髅了#小丑 #shorts
00:19
好人小丑
Рет қаралды 46 МЛН
Новый уровень твоей сосиски
00:33
Кушать Хочу
Рет қаралды 4 МЛН
Шок. Никокадо Авокадо похудел на 110 кг
00:44
MCP IKANANGOPEPESA APA  ZAWATHINA
16:23
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 4,8 М.
Chomwe Chachitika Ndi Bakili Muluzi TV .   Facebook Page
3:46
Sam Malvitha
Рет қаралды 27 М.
KUSEMPHANITSA KWA ZIZIMBA, ZOMWE ZINAPHETSA SAULOS CHILIMA 🤯😭
35:46
MICHAEL USI AT COMESA HALL
54:00
Edson Gunsalu
Рет қаралды 63 М.
DAN LU KU MCP 🙌🙌🙌-19 September 2024
8:15
HOT 265
Рет қаралды 3,4 М.
哈莉奎因怎么变骷髅了#小丑 #shorts
00:19
好人小丑
Рет қаралды 46 МЛН