No video

A Chakwera Ndi A Mutharika Onse Ndi Olephela - Samuel Lwara

  Рет қаралды 9,808

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara says neither His Excellency Dr Lazarus McCarthy Chakwera nor former president Prof Peter Mutharika are fit to rule this country. They are both failures.
Pa Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara wati Olemekezeka Dr Lazarus McCarthy Chakwera kapena pulezidenti wakale Prof Peter Mutharika sayenera kulamulira dziko lino. Onsewo ndi olephera.
#Malawi

Пікірлер: 208
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 Ай бұрын
Samuel you are right ✅ 👌....Chakwera ndi Muntharika...tiwaona zintchito zawo....Onsewa olephwera we.Need New Blood....Mkulu uyu akalankhula chilangamo....zoona zokhazokha......More Fire 🔥 Samuel...👍👍👍👏👏👏👏👏👏
@Mahmoodwargison-op2gm
@Mahmoodwargison-op2gm Ай бұрын
Vuto munthuu akalakhula ngamo mumamuda kma chilungamo chimawawa keep it up nr Rwala
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
Ukhale president iweyo
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Zoona ndithu zimene a kunena Rwara
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt Ай бұрын
Ofcz munthalika failed somehow but these one eeeh aonjezaa
@OMEXTWAIBU
@OMEXTWAIBU Ай бұрын
I'm really agree with you Samuel , keep it up and don't fear. True true big.
@GiftPhiri-tt7nn
@GiftPhiri-tt7nn Ай бұрын
Chipani cha dpp bingu anapanga chitukuko kwambiri and ndimachikonda koma president amayenera kukhala wina ku dpp ko , sankhani president wachinyamata ife tikamuvotela , dpp bola singafanane ndichakwera koma ma president tiyese atsopano
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Mwayankhula bwino kwambiri, anthu amadana ndi chilungamo
@haneefmuyaya7472
@haneefmuyaya7472 Ай бұрын
I prefer, Muthalika ataimanso ndi Atupele, Zikhiza kukhala bwino, akazatopa, mwana azapitirize, Koma zomatenga anthu isaziwika bwinozi, 5yrs it's not a joke guys
@anniedennis7127
@anniedennis7127 Ай бұрын
That's very true , only a patriotic Malawian cannot vote for failed leaders Chakwela and muthalika.
@GRACIOUSKENAN
@GRACIOUSKENAN Ай бұрын
Ndiyambe chochi,Neleson mandela uja sanalamulire dziko ali otha msinkhu?? chikhala kuti peter anthu akumuda bwezi kumaliro kuja anthu akumulira kut ayimile?? so iwe ukamat peter ayi what do you mean so tayimilatu iweo tione ndi mkamwa modambanamo aaarrriii. iwe do you compare chakwela nd peter,chambaaa chani,ngat sukufuna khala usavote uzidya soya peices bass kumpotoko ndi atumbuka azakowo bwanji? pita ukooooo
@Littlefair7
@Littlefair7 Ай бұрын
Akunena zoona, koma mbuli ngati inuyo simungaone.
@user-es4jt6ds8m
@user-es4jt6ds8m Ай бұрын
Ayi osanena Kuti stumbuka pliz zichepezo tseka Chikamwa icho
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki Ай бұрын
Mr lwara you are number one! Apm and chakwera same what's up group both are fools. Malawi is a cursed country leader ship is worse.
@MasterMwandira-q8v
@MasterMwandira-q8v Ай бұрын
Ndizoonadi. APM, CHAKWELA, awa ndi anthu olephela, bwanji tiyeseko afford nawoso tione kulephela kwao
@Littlefair7
@Littlefair7 Ай бұрын
Chilungamo chosatenga mbalin keep up the good job, zitseguleni mitu mbuli zimene zimavotera atsogoleri olephera, 80% ya anthu ovota ndi mabulutu, akufuna Chakwera olephera kubweretsa Mutharika olepheranso.
@BrightPhiri-bt6ev
@BrightPhiri-bt6ev Ай бұрын
Apa mwalankhulapo za nzelu lero.peter is not a solution to our problems tinamuyesa kale
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Ай бұрын
Mr. Lwara is a chaotic person, he wants people to applaud whatever he says, Mr. Lwara learn to be quiet sometimes, you are missing the point
@MacphersonJuma
@MacphersonJuma Ай бұрын
opepela uyu mbuzi ya munthu
@DIRECTORJARVMACK
@DIRECTORJARVMACK Ай бұрын
Ndizoona onse ndi olephela koma devaluation mmmmmmmm ndiyopweteka kwa achinyamata ogwila maganyu ife APM my vote
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Ай бұрын
Unaonako dpp ikugula fertilizer ku butchery,kwatsala iweyo akumange mpamene utadziweno kuti pakati pa awiriwa Pali kusiyana.
@MenciaMadex
@MenciaMadex Ай бұрын
Apm my vote 2025
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Ай бұрын
Pena pake nanuso Mr Lwara mumaganiza moperewera kwambiri,inuyo mungafanizire Peter ndi chakwera? Like seriously?
@TheresaKuluwemba
@TheresaKuluwemba Ай бұрын
Kkkk mwina akufuna aime iyeyo kukhala president kkk
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Pa Peter pokhapo ndie wapenga Peter sungamufanizilire ndi chakwera APM akufunika than any one
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Kodi a lwara muli mbali iti President wanu pano ndi mdani ....jnutu mwasowa kolowera .. .mmene chakwera waonongela zikoli mungayerekeze ndi apm....inuyo mukukhala ngati mbuli bwanji Mmene peter amasiya upresident katundu anali pati.....iweyo lwara wangosowa kolowera .....osachita support Enock chihana bwanji monga wakwanu.....usiletu kuyankhula za peter......amalawi chiyembekezo chimene tasala nawo ndi peter
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o Ай бұрын
Lwala Mutu wako sakugwila waoneka kale omwe amasankha ndi anthu iweyo sungafanizile Mutharika ndi chakwera , Mutharika anthu amasangalala kwambili kuposa pano ndi chifukwa anakuthamangitsa mnyumba ya Malawi housing, iweyo ziyankukula zako zopusazo amalawi Peter Mutharika wooyee
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Ай бұрын
Lwala wayamba kukhumudwitsa wanthu chakwera ungafanizire ndi Apm?
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c Ай бұрын
Lawala is looking for chihana but AFORD alone can't win how old was mandera both are candidates let them exercise their freedom
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e Ай бұрын
Apm amalize term yake munamulandila nsanje upresident l support Dpp 100%
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h Ай бұрын
Ndinu achitsilu alwara sungafanizile MCP ndi DPP aaaaa anyamata alipo muboma akupanga chani
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d Ай бұрын
Iwe mutharika ungafanize mbudzi ngati chakwela? Iwenso ndi kape kwambiri
@MosesTangwe
@MosesTangwe Ай бұрын
Naweso larwa izi ife ai. chifukwa a Peter mutharika sungafanizire chakwera never. Pali zambiri zomwe simungafananitse
@YNOTGEORGE8
@YNOTGEORGE8 Ай бұрын
Yes Mr Lwarwa thus fact APM thus not a solution
@spargomw
@spargomw Ай бұрын
Akulu ngat Mfundo zakutheran ndibwino kukhala osayankhula kalikonse, inuyo pangan Alliance nd Lyton Mangochi muyambitse chipani chanu coz apapa mwaonetsaso uchitsiru ofanana nd Lyton Mangochi.
@TypexTikita
@TypexTikita Ай бұрын
Lwara zopela zomwe walankhula za APM chifukwa munthu wanzeru sangayerekeze mavuto tilinawowa ndi APM
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 Ай бұрын
Koma pa ma President onse mu Malawi yemwe aliko bwino kuposa onse ndi Mutalika.
@RitaDickson-ls7ol
@RitaDickson-ls7ol Ай бұрын
Palibe zabola apa change position peter and chakwela out 2025
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Bola APM kusiyana ndi chakwera, nthawi ya APM zinthu zinaliko bwino kusiyana ndi chakwera.
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Peter mutalika ndi simungayerekeze ndi Chakwera. Vuto amalawi timaziwa kuyankhula koma mopanda zeru. Mcp udf ppp dpp mukhale pasi muone kuti kodi ndichipani chiti chimwe chapangapo zabwino muona kuti dpp inayesesa. Chinthu chimozi poti mutalika wakalamba koma still ali ndi zeru . Chilima sanawinise dpp. Dpp nditimene anayitana chilima. Chilima anawinisa mcp ndiyime isamanyade .
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i Ай бұрын
Inu ndiye mu kuwona owina ndi ndani, plz musapange zoti wina mungomuioitsa mbiri koma mudzilankhula kuti zinthu zisinthe. Pano tikufuna kuti tisinthe dziko ndiye osinthayo ndi APM zisiyeni zikhale chonho
@user-iu6mr5xu6r
@user-iu6mr5xu6r Ай бұрын
Kodi bambo Lwara, amene afuna nzake pakati pa Peter ndi Saulosi ndani? Khalani ndi cipani canuco. Kuposa kunena zopusa ngati cidakwa. Kodi wanzeru? Nanga ulikuti ndipo ukutani?
@QueneteCatundulo
@QueneteCatundulo Ай бұрын
Asowa choyankhula awa
@PeterPhiri-di1ux
@PeterPhiri-di1ux Ай бұрын
ndimakupanga follow koma lero wangomunyoza muthalika panya pako ndipo ndakutuluka
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 Ай бұрын
Atumidwa awa, akuona ngat titha kusankha iwowa
@FionaKhoma
@FionaKhoma Ай бұрын
Ulibe mfundo nzimayi pachinyero chako dppp ikulowabe m,boma panyero pako
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di Ай бұрын
Lwara ndi wa ganyu sasamala za amalawi akungifuna kuti amupatse ndalama koma APM sangamupatse ndalama n'gooooo ozavotela APM ndife amalawi akumudzi amene tikudziwa ubwino wa APM tikufuna feteleza ontchipa ife
@VuyolwethuMbabani
@VuyolwethuMbabani Ай бұрын
Iwe uzilimbana ndi chakwela otsati Peter ngati wapasidwa ndalama ukazibwedze uyaluka komanso uchita manyanzi 2025
@JumaKachala
@JumaKachala Ай бұрын
Koma.lero ndee mwayankhula zopepelatu Peter angafanane ndi chakwera
@user-iu6mr5xu6r
@user-iu6mr5xu6r Ай бұрын
Inu ndi munthu amene amanena zinthu zimene sadzidziwa. Munapha zipani 9 kukhala ndi kusunga MCP. Lero mulalata?
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s Ай бұрын
Alwala mwayamwa tikutulukani mwayambaz,inu nthawi ya DPP mungayerekezere ndinthawi inu. Inu nthawi ya DPP anthu amamangidwa chonchi or kukwera kwazinthu zinafika apa? Njara,kusowa kwamankhwala mzipatala,kukwera kwa zinthu mungayelekeze ndinthawi ya DPP
@MarriamBakalie
@MarriamBakalie Ай бұрын
Wayambatu ku khota tidana nawetu uziyankhula za chakwela nt APM wamva machende ako galu
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya Ай бұрын
😂😂😂😂 yomweyo galu iweee
@user-nd9cm3yl7e
@user-nd9cm3yl7e Ай бұрын
Muthalika satukwana muthu olomodzi ndiwante ndele zd
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di Ай бұрын
Mulilanaye APM chomwe timadziwa APM sanaluzepo ndewu akamamenyana 1 to 1 kukanikana ndiye mubweletse 1 to 5 ndiye 5 a wine muziti m'modziyo walephela? Anthu adyela Inu tandiyankheni alwara komanso kamenyedye ka m'modzi uyo sikanasithe 40 pelesenti ndiyomweyo anapezanso pa 1 to 1 mulila ndi APM 2025 APM boma
@Emmanuelmw603
@Emmanuelmw603 Ай бұрын
mutharika akuwinaso mufune musafune.....APM my vote ✊
@AlfredSteven-v9m
@AlfredSteven-v9m Ай бұрын
Yes ur right koma mukananena oyenera muzipanimo
@OweniMalokooweni-es9qx
@OweniMalokooweni-es9qx Ай бұрын
Ndipo kwambii timufuna atupele mulunzi😊
@BertharrySecurity
@BertharrySecurity Ай бұрын
Mnthalika inde analephela Koma anayesesa, kusiyana ndiwomwe alipowa
@jonas-xh4hz
@jonas-xh4hz Ай бұрын
a rwara zikambani zanzeru musiye kuyankhula zopusa zanuzo
@StevenDastan
@StevenDastan Ай бұрын
Apm ndimunthu wankulu kwambili kuliphika dziko lino
@marcuswalker2613
@marcuswalker2613 Ай бұрын
Mbuli iwe Mtumbuka opanda mfundo atakulanda nyumba ndiye wowowoooo. Ndale zako zilibe tsogolo "mark my word"
@Samu-q3z
@Samu-q3z Ай бұрын
Apm ❤❤❤❤
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Ай бұрын
Apm my vote
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w Ай бұрын
As itikut peter alibwino koma tikut apm alikobwino kusiyana ndi chakwera basi
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu Ай бұрын
Iweyo suzakalamba omwe anakubala nd sikana wina nyamata sibwino kwanu kulibe agogo
@user-zx3pz2wy1j
@user-zx3pz2wy1j Ай бұрын
Kodi osalephela ndi ndani ngati ukutiso peter ndiwolephela iweyo wachitapo chiyani ?
@ibrahimbamusi109
@ibrahimbamusi109 Ай бұрын
Lwara tikutulukatu ali ndi chibwana
@user-or7ng3fj8f
@user-or7ng3fj8f Ай бұрын
Ndiwe kapolo wamundu Peter again in 2025 🔥
@HendresonLubano
@HendresonLubano Ай бұрын
Kuyambila pano usazanyozeso muthalika ndimunthu watendele
@FionaKhoma
@FionaKhoma Ай бұрын
Galu nzimayiiwe athu anzeru avotera dppp pitamuthalika amayesetsa kuti athu tizidya chakwera anabwera kudzaba njara yavuta km muthalika zakudya zimatsika ntengo
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Ай бұрын
2020 mumanenaso Chocho kut alowe anyamata lelo bwanji
@RitaDickson-ls7ol
@RitaDickson-ls7ol Ай бұрын
That is true Peter ngati anachoka pampando analephela tiwoneko zna asatinamize agogo l love your point keep it up mr🙏🙏🙏
@SofiyanoMayuni
@SofiyanoMayuni Ай бұрын
Peter ndiwabwino
@EmmanuelMaxon
@EmmanuelMaxon Ай бұрын
Iwe aliyese akavota yekha usati nyase usamat amalawi sakufuna dpp uziti iweyo sukufuna koma ine ndikufuna zako zimenezo mesa chilima anadziwa ndale chifukwa cha apm
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 Ай бұрын
Auzeni koma awa. Khala ngati ntawi yaPita analikuLwanda
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Abambo inuyo timakukondani panopa tisiya kuvela ma odio anu inu satana ameneu chakwela mungamufanize ndi peter muthalika muthu salephela kukhala ndi zofooka koma peter muthalika anali muthu oyesesa ndipo akatengaso boma adzalamulila bwino kwambili chifukwa wadziwa zomwe amalawawi amafuna Moyo wautali adad ❤❤
@MaxwellSakwata-wb8ep
@MaxwellSakwata-wb8ep Ай бұрын
We never voted out APM may be you did.....
@thondoyaenterprise3795
@thondoyaenterprise3795 Ай бұрын
Dpp cheated
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 Ай бұрын
No, DPP was cheated by judges
@MastonWatson-g7g
@MastonWatson-g7g Ай бұрын
Iwenso mmutu mwako nzeru mulibe nzeru chakwera ungamufanizile ndi mutharika? kape iwe wosowa chonena.
@DesmondKanguwe
@DesmondKanguwe Ай бұрын
Reality yowawa...odana ndzomwe ukunenazi sadziwa zomwe akufuna
@retirementtoafrica
@retirementtoafrica Ай бұрын
Nkhani yodya mabanzi ndiyovuta, chilungamo chimasowa ndikumagoyankhula mozungulira opanda solution.
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Ndiwe galu Kwa basi mbuzi DPP fertilize wunaliko mapassport analiko makhwara amapezeka muzipatara ndiye zingananane Ndi MCP kagwere wuko
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 Ай бұрын
Nyamata wa chilima wasowa kolowera kkkkk
@OsmanPatrick
@OsmanPatrick Ай бұрын
Machende ako iwe abambo akowo
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr Ай бұрын
Ndipo a samuel lwara mumandiwaza nsaname kkk everytime ndikamamvera ma audio anu ndimamva sugar 😂 ndimafuna ndikumvelani daily cz mumabudula mpunga wanyama, kamba simugawa. Izizi akunena apazi akutsutsa amadya thewera lamwana 😅😅😅
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Zoona ine munthu uyu ndimafuna kumamumvera daily fact ndiyomwe akunenayi😂😂😂😂
@user-nd9cm3yl7e
@user-nd9cm3yl7e Ай бұрын
Wanamaiwe sudziwa ndale
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 Ай бұрын
Mwayambatu uchitsiru madala. Muthalika ndi Chakwera you cant put then together. Ya Chilima ija timakupangani support koma mwayamazi ayi
@kondwanbanda2671
@kondwanbanda2671 Ай бұрын
Alekeni anthu akasakhe okha
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc Ай бұрын
100% light show ndi olephela.tiyetsele,utm UDF or afford.amagona,ali pa mpando.ziko,amayemdetsa,ndi chisale.ndi,amayi akunyumba kwao.just, remember akazi awo,amachita kupita ku reserve bank kumangotenga, ndalama kumeneko,atiudza za change for what corrupt our nation? that's sheet 'we can no sitting here watching this happen.amalawi,kodi,timadziwa akamati democracy?tili kutali,ndi chitukuko mu ziko lathu.
@FionaKhoma
@FionaKhoma Ай бұрын
Pitamuthalika ndimuthu ofunika kwambili sungamufanizire ndichakwera ndiathu osiyana pita timuvotera nyiniyako nzimayi phawiiwe potauko ndiuphawi wakowo nzimayi opanda nzeru iwe mbuli setezako
@spargomw
@spargomw Ай бұрын
😂😂😂😂
@MasterMwandira-q8v
@MasterMwandira-q8v Ай бұрын
Amtharika omwe aja mnawachosa 2020
@RitaDickson-ls7ol
@RitaDickson-ls7ol Ай бұрын
Nanga anagwwelanji ose ndwolephela
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 Ай бұрын
Ndichifukwa achichotsa ntchito ndiwamisala wakutumayo akupusitsa koopsa 😂😂😂
@VuyolwethuMbabani
@VuyolwethuMbabani Ай бұрын
Udani wako ndi a Peter usasokonedze nao anthu omukonda Peter Ife Peter ndi chiyembekezo chathu usiye kuyankhula manyi
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Iwe ndi mbuzi leave Apm alone you can't compare ndi chakwera kupusa....
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 Ай бұрын
Iwe luwala iwe APM siwungamufanizile ndi chakwela ayi iwe watanikodi
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 Ай бұрын
P M munthu odziwa kulamulila munthu wanzeru akuziwa ,Larwa udakiwe
@Mahamudu-q6b
@Mahamudu-q6b Ай бұрын
❤❤ zowona
@samchibenene4458
@samchibenene4458 Ай бұрын
DPP MCP wose alephera vuto anthu akumwera ndi apakati mukulimbirana Kuti leader azichokera kwanu foseki all of these president are failed
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Zoona koma anthu amadana ndi chilungamo
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w Ай бұрын
Chi luwara ndichimbuzi APM will win you can't compare with chakwera suka ng'undu
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy Ай бұрын
Lwala nde tivotere ndanino kulephera kulitu ma stage stage enawo nde ndi zero
@blessingmanda
@blessingmanda Ай бұрын
change the system, anyone who has been who is who will be the president of malawi nothing has change and will change eccept if the system is changed. scrap the constition book
@user-qg4it7my9n
@user-qg4it7my9n Ай бұрын
Akulu fodya tamazimisiraniko a peter simungafanizire ndi mbuzi ya mu2 ngat chakwera
@KennyPhiri-zg1kr
@KennyPhiri-zg1kr Ай бұрын
Peter anayendesapo analephera chakwera walephera you are true pezani wina
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu Ай бұрын
Iweyo olo ungafanane nd APM ,,,,, ku pepera bas cisiru lwara
@VincentNgabuhvincent
@VincentNgabuhvincent Ай бұрын
Ada awawo Samuel Lwara mumuuze ma chende ake palibe chomwe wakamba chamzeru wamva ukalimbana ndi DPP poliyako wamva iwe ndy ndindani. kd nanunso Amalawi munthu kungoti wangobwera ndi ka audio kake bs mungoti that's true km akukamba zopanda munthu Amalawi mulibe mzeru kwa amene mungoyamikira zopanda pake zausichilu bs. MCP ukafanizire ndi DPP mutu wako ukugwira iweyo kd nthawi imene APM anali pa mpando kd ena inu timakuziwani kd chifkwa nthawi zina APM munangokhala chete chifkwa zinthu zikayenda bwino ngakhale zimavuta km sangafike pa mbudzi iyi chakwera . Samuel lwara machende ako mpaka uzafe ndiza DPP kuipa kwake ok.
@OMEXTWAIBU
@OMEXTWAIBU Ай бұрын
APM wakalamba akapume, akakhala akungozikodzela ndiye angalamule ndani? Kwake kunatha petulo tiwone zina, munthu osadziwa kulankhula kkkkkk akagwele ndi family party yakeyo, Tiyeni amalawi tiyese Atupele ❤
@user-xe9hp2tc4t
@user-xe9hp2tc4t Ай бұрын
IWE NDIWE GALU ASEEE NDIPO PAMSANA PAMBWIYAKOO UKHAULA IKAWINA KAPEE IWEE
@user-jj3oo6jh1l
@user-jj3oo6jh1l Ай бұрын
Mr samuel.pachimanga choola timasankhako.kt ichi ngankhale chili choola km.ndinkhonza kukazinga nde anthu tikuona kt bola peter
@AlfredSteven-v9m
@AlfredSteven-v9m Ай бұрын
Mwangolongolora 18 min osanenapo oyenera anthu tigwire ziti ndiye
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Lwara ndichisilu alibe mfundo zomveka bwino kaya akufuna chiyani kaya ..amati ndiwa mcp....chisilu cha munthu
@PetrusTlhokwane
@PetrusTlhokwane Ай бұрын
Ndipo ndizoona tinapanga mademo 2020 chifukwa cha APM analephera nde tiyeni ngati pali wina ku DPP angazawine not APM chonde tiyeni Anthu awiriwo apume km 😂😂😂😂
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov Ай бұрын
Akulu mwayowoya makola chomene ineso palije uyo angasanga vote yane anthuwa palibedi munthu ofunikila Peter anapangitsa kut kuyambe ma dembo tisaiwale ulamuliro wao
@user-fq4kv8dj4t
@user-fq4kv8dj4t Ай бұрын
Koma peter ungamufanize ndi lazalo ukunama zikatere nde kt basi kulibe wabwino
Atsogoleri Satopa  Atsogoleri Sagona  - Samuel Lwara
11:31
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 6 М.
لااا! هذه البرتقالة مزعجة جدًا #قصير
00:15
One More Arabic
Рет қаралды 51 МЛН
Идеально повторил? Хотите вторую часть?
00:13
⚡️КАН АНДРЕЙ⚡️
Рет қаралды 17 МЛН
小丑和奶奶被吓到了#小丑#家庭#搞笑
00:15
家庭搞笑日记
Рет қаралды 9 МЛН
Кадр сыртындағы қызықтар | Келінжан
00:16
HOT CURRENT YA LERO 🔥🔥🔥🔥🔥
59:36
HOT 265
Рет қаралды 2,9 М.
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 24 М.
Wina Ndinamuthyola Khosi - Samuel Lwara
14:15
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 42 М.
BRIAN BANDA KUPANIKIZA ANTHU NDIMAFUNSO
20:15
HOT 265
Рет қаралды 10 М.
MPHEPO ZINAYI: CHAKWERA AYIMANSO
48:18
Zodiak Malawi
Рет қаралды 45 М.
BON KALINDO  LERO PA 17 JULY 2024 |
18:32
DZIWE TV
Рет қаралды 26 М.
KAFUKUFUKU PA IMFA YA ACHILIMA
30:18
Jimmy
Рет қаралды 146 М.
DZIKO LA MALUZI PANKHANI YA MALUSO
10:02
Caswel Mkanda
Рет қаралды 1,2 М.
لااا! هذه البرتقالة مزعجة جدًا #قصير
00:15
One More Arabic
Рет қаралды 51 МЛН