Limpopo kupha Chilima zinachoka kutali tamvani bwino bwino Ntanyiwa wabweletsa

  Рет қаралды 38,929

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

24 күн бұрын

Пікірлер: 95
@tanishadias
@tanishadias 23 күн бұрын
Ineyo a Limpompo fm ndili pa mbuyo pano ❤❤❤❤❤ mumatiuza zoona ndithu
@FazilCastin
@FazilCastin 23 күн бұрын
Ine Langa ndi Funso Kwa inu Mr ntanyiwa Kodi Radio yanuyi imafikira anthu akumudzi. Chifukwa enafe tili ndi mwayi womvera komanso tili moyenda Monga out off country. Chifukwa akumudzi ndi amene akufunika Kuti adzidzitsata komanso ndi amene Anga Vote
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 23 күн бұрын
Zoonadi akumudzi akufunika azizidziwa chilungamo cheni-cheni. Ndi amene amathamanga kukavota.
@Vwalavwata
@Vwalavwata 21 күн бұрын
Ndipo ndimaisata kwambiri radio imeneyi from Malawi mzimba
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 23 күн бұрын
Koma a chakwela mukuwoneka mulibe mtendere ndipo simunati mzimu wa munthu ndiwoopsa soseji mukuimva kunyung''unyatu ngati madimu musova😂😂
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 23 күн бұрын
A UTM mukalola manyiwo musalamo nokha mu mgwilizano wanuwo ife zikwangwani talodza kale ku DPP mutsalanaye RUTO wanuyo
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 23 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂chi RUTO bwino
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 23 күн бұрын
Kkkkkkk koma apatu misala yayambika😂muziwona munakhetsa mwazi wa anthu osalakwa
@Stewartchikoja
@Stewartchikoja 23 күн бұрын
Respect sibonda
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o 23 күн бұрын
Ine sindipitako
@BlessingKimu-yk8uj
@BlessingKimu-yk8uj 23 күн бұрын
Moto wachilungamo tilinanu limodzi ifemso before amthu tikudziwa amthu okudana ndi chilungamo.
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi 23 күн бұрын
Jumah Mubarak. Our beloved Ntanyiwa ❤ freedom fighter 💪
@benbanda19
@benbanda19 19 күн бұрын
Respect you Ntanyiwa Kumulakwira Chilima ndiena onse anafela mundege😢😢😢
@user-ny3it3jp9l
@user-ny3it3jp9l 23 күн бұрын
Lipopo❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ fire 🔥
@georgesmart3791
@georgesmart3791 22 күн бұрын
Kutha kwa Shasha... Apm 2025❤❤❤❤
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i 20 күн бұрын
Zinakanika kukambilana naye chilima chifukwa amaziwakuti chilima ndimuthu wachilungamo koma ngakhale mwamumpha zimu wa chilima ulamula ziko lamalawi ngakhale anachoka pakatipathu koma muchisomo chamulungu tilamulidwa ndi chilima S K C still I remember you 💔💔😭😭😭
@MandalaChaona
@MandalaChaona 23 күн бұрын
Koma Malawi Chikangawa Party ikusavuka sinati . Mimbulu yoyipa iyi, Mwazi wa anthu osalakwa ukupengesani. Tiye nawo Mchimwene NTANYIWA kuwayika pambalambanda basi.
@Vwalavwata
@Vwalavwata 21 күн бұрын
A khristu a CCAP ena ndi opusa amangosapota zilizonse even akuiziwa kuti akuzipereka yekha kwazigawenga kuti zimuphe
@EllinaBitto
@EllinaBitto 22 күн бұрын
Limpopoooooooooo❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 23 күн бұрын
Mtanyiwwa ulemu wanuw bassi mulungu ationesa nkena kalikose iyyemwini ankubissa bwanj mulungu atiphasa nkuwona shoonad 🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲🤲
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 23 күн бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa ndi dolo kwambiri uyu akhalise Malawi.
@UsenLashid
@UsenLashid 23 күн бұрын
Inu mahule chokani sindinu mulungu muziona 2025 komaso iwe chakwela usamati uzafela mbendela ya Malawi Ayi iwe uzafela tambala wakuda osati frug ya malawi Ayi
@user-yh3ys3qn6p
@user-yh3ys3qn6p 23 күн бұрын
Km atanyiwa ndi kachilombo paka fukufuku kkkkkkk
@tanishadias
@tanishadias 23 күн бұрын
Adamphadi Muthu uja basi palibeso kukanika konse 😭😭mcp chipani chakupha
@AsiyatuPoya
@AsiyatuPoya 23 күн бұрын
Limpopo oyeee
@4ourcusworldwide426
@4ourcusworldwide426 20 күн бұрын
Ndipo azibusa ambiri atayadi chilungamo..kukhala osauka mpimgo siukuwerengera. Mpake alibusy kusaka chikwamq.. rip chilima
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 23 күн бұрын
Limpopo fm listening from Botswana comred number one
@JeremiahKainga-rm2np
@JeremiahKainga-rm2np 22 күн бұрын
😅😅😅 2:14 2:16 2:17 😅😅 2:23 2:25 2:29 2:36 has been 2:41 2:42 2:43 2:44 2:44 2:46 2:48 2:49 😅 3:04 3:07 3:07 3:09 3:09 2 3:10 3:11 3:11 3:13 your 3:16 3:17 😊 3:19 3:20 9 3:23 3:2 6:31 6:40 6:51 7:02 7:02 7:10 7:12 7:17 7:18 7:18 7:19 8 5:45 😅 5:55 5:57 6:01 6:02 ,, 6:06 , 6:13 6:13 6:28 6:30 3:32 3:34 99😅 5:25 5:25 😅 5:44 3:50 3:51 3:54 3:56 😅 4:59 :38 2:39 2:41
@JeremiahKainga-rm2np
@JeremiahKainga-rm2np 22 күн бұрын
7:37 7:37
@JeremiahKainga-rm2np
@JeremiahKainga-rm2np 22 күн бұрын
African 9
@JeremiahKainga-rm2np
@JeremiahKainga-rm2np 22 күн бұрын
What 😮
@JeremiahKainga-rm2np
@JeremiahKainga-rm2np 22 күн бұрын
😊😊😊😊and
@MahallaMinistries-fv1hw
@MahallaMinistries-fv1hw 23 күн бұрын
Sadly, we've moved from having men of God to men of gold.😮😮
@AlexGomani-ss5nj
@AlexGomani-ss5nj 23 күн бұрын
Apa yalimba nkandilo basi, ma plan onse kumangopanga ngati openga Mulungu atachotsa nzeru.
@CathrineRamseyJafaal
@CathrineRamseyJafaal 23 күн бұрын
Ndiye mwati chikangawa ikupita kukalapa ndiye anthu asatenge ma phone mm anagula ndiyeyo kkkk koma misala yayambika basi 😂😂😂
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 23 күн бұрын
Mai gotani Hala amachindana ndi mkulu wanga
@JosephMaduka-i9s
@JosephMaduka-i9s 23 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@sammynkata5461
@sammynkata5461 21 күн бұрын
Ing'alule basi ķkkk
@Hellenistic109
@Hellenistic109 20 күн бұрын
Kkkkkkkkkiest
@user-hx6jl2jq9j
@user-hx6jl2jq9j 23 күн бұрын
Akuyopa chani galu ameneyu pothimitsa malamya
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 23 күн бұрын
Mulungu ndimboni pagwilizano wa tose Koma ngati chinali chiwembu ine ndikunena kuti mulungu abwezela chiwembu mboni dzilipo ndipo zinalakhula ndale amapanga usiku onsakhala masana mpepa azisogoleli tiyeni tiziopa mulungu amaona dzose
@NONELWANAMANYI
@NONELWANAMANYI 23 күн бұрын
💪 tiyeni timenyele ufulu ziko lathu Mr mtanyiwa
@louismagongwa
@louismagongwa 23 күн бұрын
😂😂😂😂 kma ku malawi kwafikapo
@BwanaGD
@BwanaGD 23 күн бұрын
Kwawilira mafon timayankha uku tikuva mawu amulungu nde buzi yachabechabe akati Fon izime whay kapena akupita ndi poyison mwina akufuna akatinthemo anthuwo mkachisimo iiiii mayooo munthuyutu watsala pang'ono kufa kapena zimu wa chilima ukumutsata ndiye akuwonagati kutseka zitseko zimuwo sumupeza iiiii kkkk atate mwayambatu kuvetsa chisoni iiiii kkkk
@AlexMakweza
@AlexMakweza 23 күн бұрын
Respect you
@UsenLashid
@UsenLashid 23 күн бұрын
Ma mfumu akuntcheu chilima sanayikidwe Ku start house Ayi ngati akufuna akupezeni Ku ntcheu komweko osati inu mupiteko Ayi akoza poison wa kumpha ziwaro musapiteko Ayi
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 23 күн бұрын
Iweee ndiwabodza umakonda kunaniza amarawi
@John-to8gl
@John-to8gl 23 күн бұрын
😂
@julietbanda5203
@julietbanda5203 23 күн бұрын
Limpopo ❤❤❤❤❤❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@Mrssamalanngwira
@Mrssamalanngwira 23 күн бұрын
Limpopo f m my feveret
@AnnaElisha-b4h
@AnnaElisha-b4h 23 күн бұрын
More fire mtanyiwa
@PeterMillimbo
@PeterMillimbo 23 күн бұрын
Kodi nchifukwa chiyani a silikali amakhala mbali ya olamulila kusiya kuteteza mzika za Malawi
@benjaminjobo3525
@benjaminjobo3525 23 күн бұрын
Bwana Ntanyiwa nyimboyi tikuifuna ngati pali link tipatseni ndaikonda 🔥🔥🔥🔥
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 23 күн бұрын
Ife tikufuna tiwadziwe amene anapita kuchikangawa kukamalizitsa anthu 9 mwachinsisi ,aaa ife sitikumvesa anta ndipo sitikugona 😭😭😭
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x 23 күн бұрын
Buddy Ntanyiwa ♥️🔥
@RodgersPhiri-ju1eo
@RodgersPhiri-ju1eo 19 күн бұрын
Ubwino wake mgwilizano anthu anavota zaka 5 nde zaka 5 zikatha anthu akavotanso sikuti avotelanso alliance ayi akavotela kumene akufuna kaya avotela DPP kaya avotela AFORD kaya MCP kaya UTM sikuti akavotela alliance
@user-pp6kf6vu2y
@user-pp6kf6vu2y 22 күн бұрын
Nyimbo yu tigairen inu❤❤
@mathewsmbaluko8522
@mathewsmbaluko8522 23 күн бұрын
Zikachitika timvela kwainu ❤❤
@cacksygustarf6260
@cacksygustarf6260 23 күн бұрын
Ntanyiwa❤
@Mrssamalanngwira
@Mrssamalanngwira 23 күн бұрын
Limpopo ❤❤❤❤ 🔥
@user-vw7tj2ss3l
@user-vw7tj2ss3l 23 күн бұрын
Mbiri yoipa mpaka kale kale
@FocusGeorge-qz4sh
@FocusGeorge-qz4sh 23 күн бұрын
Yomweyo chikangawa
@InnocentNitamanMilanzi
@InnocentNitamanMilanzi 4 күн бұрын
Ngati zinali zonama kuti anapha chilima nchifukwa chani akumamanga anthu kodi nkhani yokunamizira umalimbana nayo?ndikunama ndi iwe sataniki chilima anthu azifa ndi nhlaka chifukwa cha iwe
@GeraldChisokeza-er5cf
@GeraldChisokeza-er5cf 23 күн бұрын
Zilungamo zokhazokha
@UsenLashid
@UsenLashid 23 күн бұрын
What is that Kuti anthu akasiye matelefone uyaluka galu iwe Sunati mulungu wathu wanthu ndi wa Moyo amene anafafaniza aiguputo ndipo Lero mulungu wemweyo akufuna kufafaniza chakwela ndi chipani chake zichitike mulungu wanthu wa Moyo timakudalilani sitimadalila chakwela Ayi zichitike mudzina la yesu khristu nanuso azibusa muzayankha mulandu Kwa mulungu
@Jamesmwale-iz4ri
@Jamesmwale-iz4ri 23 күн бұрын
Koma muti nichani
@giftwankhama9914
@giftwankhama9914 23 күн бұрын
Comrade mumatha.
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 23 күн бұрын
Koma chakwela sutizamuiwala ndithu muchita kusowa chiyakhula mmm ndipo watikwana
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 19 күн бұрын
KUYALUKA BOMA LA MCP KUSAFUNA KUVOMEREZA KUTI ZAWAVUTA
@Fatima-f5c
@Fatima-f5c 23 күн бұрын
Chakwela akusekesa athuu bwanji 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🎉
@DanNzima
@DanNzima 22 күн бұрын
Crocodile party ,
@jamessheki4293
@jamessheki4293 23 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 kubwera olonjezedwa
@samuelazumah1050
@samuelazumah1050 23 күн бұрын
Limpopo inu ndinu katundu waboma
@user-iu6mr5xu6r
@user-iu6mr5xu6r 23 күн бұрын
Kwakula kudzidzimbaitsa kwa ciombankhanga kufuna kuoneka ngati njiwa. Ciwanda ngati m'ngelo wakuunika. Zavuta basi.
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 23 күн бұрын
Askhristu nonse akuligadzi muphedwa mwanvatu kuti zitseko zikatsekedwa zonse tchalitchi amatseka 😂😂😂😂😂 ma foni off ,ayi zikomo achakwela kupengatu uku kodi proglam yomphq chilima mumapanga monkha ndanga enawo mwayamba kupenga nonkha tu anakupakani manyi azinkhale akukunkhuyu achimwendo ,,
@AndrewSimakweli
@AndrewSimakweli 23 күн бұрын
Mulingo umene umayeza nawo mzako ndi omwenso umakuyezela
@EsnartMalewa
@EsnartMalewa 23 күн бұрын
Koma ziliko 😂😂😂😂😂
@AdamMwanza-rf6pd
@AdamMwanza-rf6pd 23 күн бұрын
Nde utsi wafukila kut pamenepo UTM or akokoloka ndi mphepo ya pakati
@RodgersPhiri-ju1eo
@RodgersPhiri-ju1eo 19 күн бұрын
Kodi Mtanyiwaso ndiokwiya tangobwela kuno kumalawi kuti uzawonese nkwiyowo ife zachilima woti anafakale sizitikhuza ndiposo sitikukwiya nazo okwiya ndiweyo bwela uzawonese nkwiyowakowo vutolake iweso ntanyiwa ndimbuzi chifukwa chilungamo ukuchiziwa koma ungokhala momyata ngati bwampini mmalo mobwela poyela kuti uwathandize anzakowa naweso ndi galu wachabechabe tikuwuzeni nose opandanzelunu pamozi ndi chilimayo timakuwuzani kuti tafasani koma kusanva amanamizidwanso ndi kaliyati kuti ayambise kachipani kawo agwese DPP aphwanga DPP siyolimbana nayo mwatitukwana yee a UTM pano mwasowa kolowela ife a DPP tiliphee ndipo a UTM kunoko ku DPP sitikukufunani nose ndinu agalu ndi chilima wanuyo mesa munkafuna adadi atafa lelo inu mulikuti muwona DPP 2025 boma
@CatherineKumwex
@CatherineKumwex 23 күн бұрын
Uuuuu Shane
@user-gq9jg4vm2f
@user-gq9jg4vm2f 23 күн бұрын
Azapanga ta15 minits thawi ikumachuluka tipepherekon
@user-gp2zp2dj1w
@user-gp2zp2dj1w 23 күн бұрын
To honest this government it's full or shit n evil....munthu ukamayandikil kumwalira sunvaa kapena ndinene kut mbuzi ikakondwa amalonda Ali pafupi.....tionana nthawi yovotaa
@JackNagoli
@JackNagoli 23 күн бұрын
Km guys mukutinyamula 🎉
@user-sm8gx4vf1v
@user-sm8gx4vf1v 23 күн бұрын
Mafumu ena alibe fone aku ntcheu adziwa bwanji nanga
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 23 күн бұрын
Kurikwabwino akhirisithu apite koma ma phone awo aka wayike since azika record zose chifukwa ngati sapita sitiziwakuti akufuna kurapachani
@mellipherjohn7158
@mellipherjohn7158 23 күн бұрын
Limpopo moto kut buuuuuu🎉🎉
@MosesKalenge
@MosesKalenge 23 күн бұрын
📺📡❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤👑
@vincentbarnes5872
@vincentbarnes5872 22 күн бұрын
Sitikufuna DPP, MCP, UDF kapena PP ayi. Tikufuna kupitiliza vision ndi passion ya Dr Saulos Klaus Chilima with UTM basi. The grace of God is upon UTM party
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo 23 күн бұрын
Mantha kwambir
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 23 күн бұрын
Ali ndi tsoka chikangawa ndi banja lake mpaka kufikila m'bado wake wa chi 4 otembeleledwa ulibe mwai
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 23 күн бұрын
Koma ameneyu GALU kwambiri wamiyitana ndani NYANI ameneyo apite akapemphere ku Assembles kwake komweko GALUUUU!
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 23 күн бұрын
Mukukwana antanyiwa 😂😂😂
Useful gadget for styling hair 🤩💖 #gadgets #hairstyle
00:20
FLIP FLOP Hacks
Рет қаралды 10 МЛН
Викторина от МАМЫ 🆘 | WICSUR #shorts
00:58
Бискас
Рет қаралды 4,8 МЛН
НРАВИТСЯ ЭТОТ ФОРМАТ??
00:37
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 8 МЛН
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 24 М.
ANTHU AYANKHULA ZOSAOPA AWA 🙌🙌🙌
27:38
HOT 265
Рет қаралды 103 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 211 М.
ABUSA AYALUTSA KUNKUYU MOSAPYATILA KALI KONSE KULI KUYALUKA CHAKA CHINO
8:10
NKHANGA ZAONA
21:49
TIDZIWE TV
Рет қаралды 66 М.
KEN MSONDA UJA AMUKHAPA PA YAO FM ATAYANKHULA ZAKE ZIJA
17:25
Malawi Trends TV
Рет қаралды 808
Useful gadget for styling hair 🤩💖 #gadgets #hairstyle
00:20
FLIP FLOP Hacks
Рет қаралды 10 МЛН