No video

ABDULL..CHIPANI CHOLAMURA UK CHAULUTSA ZISANKHO

  Рет қаралды 11,060

Club Junta

Club Junta

Ай бұрын

Пікірлер: 62
@user-ui4ux5kc8d
@user-ui4ux5kc8d 29 күн бұрын
Chosadziwa anaimbira fiti mmanja ndizomwe tinachita amalawi
@user-kq6rp6hn7y
@user-kq6rp6hn7y 27 күн бұрын
Ukufuna Atupere apitirize chitukuko Cha mizikiti aaaaaa
@EllinaBitto
@EllinaBitto Ай бұрын
Atupele yemweyo❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@HallimaMakwinja
@HallimaMakwinja Ай бұрын
Zoonadi brother these is true tinapanga mistake posankha chakwera Satana koma Mulungu atinkhululukire tinalakwisa lnshallah
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 29 күн бұрын
Chakwela you mast go watikwana
@johnkanyika9465
@johnkanyika9465 21 күн бұрын
Ng'oooooooo. Ukamvotere wekha wamva
@twavysibale4751
@twavysibale4751 Ай бұрын
We need atupele right now...
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 28 күн бұрын
Chimwendo Banda mphuno Ngati tomato waku Tanzania 😂😂
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Ай бұрын
Unali uchitsilu wa a Malawi kuvotela MCP chikhalileni amadziwa nkhadza zomwe imapanga MCP nthawi ya kamudzu mavuto owaputa dala
@user-kq6rp6hn7y
@user-kq6rp6hn7y 27 күн бұрын
Atupere umuvotera wekha!!! Wachamba ife.....
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 Ай бұрын
Dr Chakwera, the State President is a charismatic leader as I had been writing them jointly with his Vice President Late Dr Chilima.Unfortunately,he is served by leaders in all walks of human life who are lucre-minded,self-centred and callous.Dr Usi,it's your turn..accost HE and redress the current national teasers.Political invective or censure will not transform our beloved nation?Let's concentrate on philanthropy and patriotism.
@CeniaMayeni
@CeniaMayeni Ай бұрын
Mbo......li
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 28 күн бұрын
Panyopako iwe galu ndi Chakwera wakoyo
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Cakwera anawaseka anthu maso kuti asaone makutu kuti asamabe komanso asamaganize ndimkona anamuvotera cakwera mbusa wasatanic uyu 2025 acoke acoke
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef Ай бұрын
Kulisotu a Enock Chihana
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Ай бұрын
Ndipo zoona zokhazokha ndithu eeish
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk Ай бұрын
2025 tikuchotsa nyansi zonse
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
UDF chipani changa ❤❤❤
@augustMag
@augustMag 27 күн бұрын
2025 APM DPP is my vote ❤
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Abdull 🙏🙏🙏🙏🙏
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Ай бұрын
Vuto loika pampando munthu osauka oti analibe kanthu panopa nchifukwa akuzilemelesa yekha ndi family yake
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 28 күн бұрын
Monica ndi chisilu chamunthu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 29 күн бұрын
Chakwera kwake kunatha kale
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Dpp my vote
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
🔥🔥🔥🔥
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl Ай бұрын
Zoonadiitu tinavotela manyi kobas satana wachabechabe
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx Ай бұрын
Angofuna kubera ma vote afuna ku tiona ngati zitsiru mulungu akuona ngati makape
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn Ай бұрын
Palibe cha nzeru chomwe mwayankhula
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 Ай бұрын
Vote for dad and dpp udf ayi nthawi ya udf tinavutika ndi umbamva .udf chopanda chitukuko
@user-yu4np2wq4s
@user-yu4np2wq4s Ай бұрын
Mwayakhula zoona inde athu atopa ndithu koma musawauze kolowela aliyense akuziwa kopita ndiufulu wankulu sauzidwa kuti khala bwino amaonela phepo kuti peeeeeee😂😂😂😂😂
@user-jc5tf8jl1m
@user-jc5tf8jl1m 28 күн бұрын
Ndizoonadi ayao ndi ochuluka zedi angakhale kuno South Africa zimaoneka kuno
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z Ай бұрын
ULEMU WANU ABDULL ZOONA KWAMBILI
@FLETCHERBANDA
@FLETCHERBANDA Ай бұрын
Zoona izo
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 28 күн бұрын
Am not a fan of chakwera bt let me correct u Mr abbudul josephy was made a governor in a foreign land without experience so leadership is nt all about where your coming from or your background bt it's just a matter of heart
@MajidKasim-pn8kt
@MajidKasim-pn8kt Ай бұрын
Zoona nkulugwangu
@henryhenry6632
@henryhenry6632 Ай бұрын
Achawa mbuzi za anthu
@emilynthite6545
@emilynthite6545 Ай бұрын
Chimwendo banda ndigalu kwabasi
@JowasiMasina-fy8ji
@JowasiMasina-fy8ji 22 күн бұрын
Satanic amenewo ndimene akuyidziwa
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 28 күн бұрын
Chakwera Aku dalira asilikali ndi apolice dzisilu dza anthu
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg Ай бұрын
Chakwela watop kkkk
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 Ай бұрын
Iwe ukunama chipani cha udf chabodza cholephala
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Aaa MCP 2025 achoka awa
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 28 күн бұрын
The wife to the president what role does she play very bad koma don't worry darkness is coming to an end very soon
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Ай бұрын
Achimwene or chakwera mutamutukwana bwanji sangaluze ndipo mufune musafune chakwera sakuchoka
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 28 күн бұрын
Pamtumbo pako iwe ndichakwera wakoyo Chakwera anawina chifukwa cha mgeilizano wamva nde zowinazo muzitenga kuti, inu musangalala azipha chonchi
@kayceesamuels
@kayceesamuels 27 күн бұрын
Iweyo wakutumayo akupwetekesa ulibe chisoni iwe eti kod chakwera anavoteredwa kapena anabwera iwe galu ndi amako pamodzi ndi agogo ako kagwere mbuzi ya Mano kunsi iwe
@BambordKabambe
@BambordKabambe Ай бұрын
😂😂😂😂 kodi mukuganiza kuti DPP angakhonze zinthu
@kayceesamuels
@kayceesamuels 27 күн бұрын
Yap kusinabe mpano
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Ай бұрын
Ine vote yanga ndi Apm not mcp
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Ай бұрын
Palibe chachilendo ngakhaleso Dpp idali yolamula koma idaluza ndiye musatinyasepo
@kayceesamuels
@kayceesamuels 27 күн бұрын
Akulu kumva mkupenya mkosiyana kod adavoteredwa kapena kubera
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 27 күн бұрын
@@kayceesamuels kubera adabera ndi a dpp ndichifukwa adaruza
@JacksonMoyo-tm8dv
@JacksonMoyo-tm8dv Ай бұрын
Chakwera sazawina
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa Ай бұрын
Udf payokha singawine man ofunika gwirizano coalition professor Peter munthalika ukumunyozayo ndiamene akufunika apange gwirizano ndi atupele wakoyo think b4 u talk don't just come here and talk nonsense
@PatrickMulangala-os4by
@PatrickMulangala-os4by Ай бұрын
Komaso musaiwale kuti UDF kunali ufwamba anthu amamphedwa masana
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 Ай бұрын
Khaniyi ndi yoona ndithu Mtumiki wa Mulungu kutenga okolopa Ku toilet kumuika MPA Mpando wa President Ambuye akudalitseni
@user-xx4mt8ox8e
@user-xx4mt8ox8e Ай бұрын
Zoona timva ma billion
@lestermwalwenje7470
@lestermwalwenje7470 Ай бұрын
Poor reasoning
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Ай бұрын
Kkkkkkk ai mmalawi muno achewa ndiambili kwabasi achimwendowo samanama
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l Ай бұрын
Poyelekeza ndi mitundu yose kumalawi?
@user-tm3zh5zk4t
@user-tm3zh5zk4t 28 күн бұрын
Yiweyo ni udf yakoyo patumbo pako ukumbukila 2001 panyini pamako
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 28 күн бұрын
Chakwera useless man
Limpopo gets first female premier
4:19
SABC News
Рет қаралды 7 М.
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 24 М.
A little girl was shy at her first ballet lesson #shorts
00:35
Fabiosa Animated
Рет қаралды 17 МЛН
TIMES SPECIAL - ENG. VITUMBIKO MUMBA  |  6 AUGUST 2024
58:46
Club Junta
Рет қаралды 841
Kuyakhula mosaopa Chakwera wamupha Chilima. Chifukwa cha udindo
14:39
NKHANGA ZAONA
21:49
TIDZIWE TV
Рет қаралды 66 М.
KAMLEPO KALUA KUYANKHULA MOSANYENGELERA
29:23
HOT 265
Рет қаралды 42 М.
A little girl was shy at her first ballet lesson #shorts
00:35
Fabiosa Animated
Рет қаралды 17 МЛН