Mwaswela bwanji nonse amene mumamvela pa nkhanga zaona.ngati mulibwino dzikomo
@AliajoeAliajoe-vv1wo4 ай бұрын
Taswela bwino kainu kumeneko bas dzikomo kwambili
@amadichembe4068 Жыл бұрын
Mwaswela bwanji abale anga pa nkhanga zaona,ineyo kuno ndilibwino
@Medson-u7n3 ай бұрын
Zoona koma lipopo mbambande
@DoricaGoweka Жыл бұрын
More fire broo osaopaaaa kunena chilungamo.
@OmegaChingamuka5 ай бұрын
Limpopo FM radio ndi one 🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪
@Yoxym6 ай бұрын
Also were waiting for bakili tv thanks you guys
@AdaKalinde-c4j4 ай бұрын
Apa ndiye mwangarula zenizeni😂😂😂
@zimmekapachika67846 ай бұрын
Yomweyo galu iwe Nankhumwa😅😅😅😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅
@Rameck-z4z6 ай бұрын
Iipopo fm mukutiimilira keep it up to
@SamuelSamuelJemus Жыл бұрын
Mukutiyimirira kumred go go go km ndikufuna nyimboyi yoti chakwera watipweteka anayimba ND ndan
@AndrewMdala7 ай бұрын
Live from south Africa Muyaluka chaka chake ndi chino
@MarthaJafali6 ай бұрын
Auzeni
@PreciousLewis-su2pl7 ай бұрын
timakunyadilila big man .mtiuzilekoso wa bakili Muluzi tv tawasowa mau ake😢😢😢 guys timakunyadilan
@peterphir2250 Жыл бұрын
Atsogoleri tikuyamikireni koma nkhani zanu simukumaliza mukaziyamba ngati mukunena kuti ntchito zomwe akugwira anthuwa ndi malipiro pa zomwe achita powotcha wa police ku Nsanje kutanthauza kuti anatumidwa ndi abomawo, ndiye a bomawo akuuzani chilungamo chotani? Inu mukadaulula zifukwa zomwe adamuwotchera wa police kuti womutumawo adziwe kuti abisala mmbatata musamangochulukisa kuseka ndi kamangoyimba nyimbo ayi, ifeyo timamvetsera ndi chidwi kuti nkhanga zaonanji tidziwe koma mumango nena molumpha lumpha ngati kuti zomwe mukuwulusa ndi zongopeka so please help us we love you
@SheenahMwalabu-iz3pr Жыл бұрын
Ndipo message yomwe imasowa muno ndeiyiyi kkk kumatambasula bobo ngati muja apangila DC Kalindo, otherwise zikumavuta kuzitsatatu. Love you ❤❤
@TimothyBilly11 ай бұрын
That's true muzimalizisa nkhanizo kut tiziziwa zoona zenizeni wr real love you mr Comrade
@CatherineDesire4 ай бұрын
Sikuti nkuopa bill ya mkadzi ati nkukhwimila anamunamidza Kwa sing'anga akabiba mu toilet apenga a Vaya 😇🤣🤣🤣
@DanielMjasten5 ай бұрын
Ine ndili pheeeee vela limpopo fm
@SalimMeer-fk9do6 ай бұрын
Zana amayi asanka chifanti malunga ngati vice koma pano ndi opposite ndi zambiri zomwe amalankhula za boza
@MagretMvula Жыл бұрын
Tikuthokozeni ntciito ndi yayikulu mukugwila more fire mulungu aikepo zanja tione mphumulo mumalawi