No video

Anatumiza njuchi pa msonkhano wa Kamuzu Banda ku Thyolo anali ndani?

  Рет қаралды 86,914

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Күн бұрын

Пікірлер: 128
@zombagrecian8543
@zombagrecian8543 Жыл бұрын
Respect to you chief 🇲🇼 ,,,Koma nkhani za nkhondo zili pati ku ,Ukraine, chief wanga please 🙏
@matembamadadada8291
@matembamadadada8291 Жыл бұрын
please captain musamachedwe kutitumizira ifetu tikangova mawu anu timawu umasangalara kwambili osati zinazi zinazi timangovera kusowa zovera ulemu wanu captain
@JailosChirwa-xq6fk
@JailosChirwa-xq6fk 10 ай бұрын
Iwe umazitenga kuti very young Ife tikava mawu timanyasidwa ukamatchula za atsogoleri akufa funa njira yina yopezera ndalama chaboza ichi
@matembamadadada8291
@matembamadadada8291 10 ай бұрын
@@JailosChirwa-xq6fk your lie kudana chilungawe iwe suziwa chilichose
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 ай бұрын
​@@JailosChirwa-xq6fk inunso nde ndinu achitsirutu, kudana ndi chilumgamo mukhala Choncho.
@kubengovender6996
@kubengovender6996 Жыл бұрын
Inu ndi number one, big up yourself man!! Koma tikudikira update yaku Ukraine please our master!!
@afreenibrahim7656
@afreenibrahim7656 Жыл бұрын
Awuzen
@JeremiahNgwira
@JeremiahNgwira 2 ай бұрын
Bakili Muluzi Channel should continue producing documentaries like this one not nkhani za politics mukutulutsa zopanda umboni.
@patrickkasamba5353
@patrickkasamba5353 Жыл бұрын
Inuyo musadzafe srs mulungu azikuonjezelani dzaka
@hamdanmasuku4800
@hamdanmasuku4800 Жыл бұрын
Mumakwana bro 💯✔🇲🇼
@user-qk1zg5ec5h
@user-qk1zg5ec5h 11 ай бұрын
Mdalitso obadwanao keep it up good work brother
@georgemsangu
@georgemsangu Жыл бұрын
Thanks bro you are a man of integrity
@ChamanChataika-jt4ik
@ChamanChataika-jt4ik 10 ай бұрын
Powerful
@andersonmaster8055
@andersonmaster8055 Жыл бұрын
Ulemu wanu big tadziwa nawo zinthu zoti zinachitika karekare
@jamestsabola1376
@jamestsabola1376 Жыл бұрын
Eya simumasazika mumangosowa basi kkkkkkkkkk
@petermitambo9257
@petermitambo9257 Жыл бұрын
BMTV iyi ndi TV yotsogola basi. Koma tikuprpha kut kutifukulile chiyambi cha wanthu obwela kujoni kukagwila magobo from malawi zidaymba bwanji. K
@ziwani3682
@ziwani3682 Жыл бұрын
BIG 👍
@imransamson5308
@imransamson5308 Жыл бұрын
Thanks 👍👍👍👍👍
@frankfriday3141
@frankfriday3141 Жыл бұрын
Ngati ine Frank ndilipano kudikilila saku Ukraine Big ine ndiwa Putin enough is enough to hear about American staff African we suffering because of them a I'm Putin too
@icelenzoaustin9513
@icelenzoaustin9513 Жыл бұрын
Ulemu wanu bro 🙏♥️🇲🇼
@YussuffPillow-el7ng
@YussuffPillow-el7ng Жыл бұрын
Respect
@hariyalymhaka7882
@hariyalymhaka7882 Жыл бұрын
Zili bho
@belnardsompho5617
@belnardsompho5617 Жыл бұрын
Yes bro Pali khani yomwe ndimafuna ndizakueuze yamwino kwambiri
@gelitofernandojose6654
@gelitofernandojose6654 Жыл бұрын
Timakunyadilani nthawi zose Big . Koma zaku Ucrânia zili pati pano? Tidziwitseni Big.
@iqrapalelo1191
@iqrapalelo1191 Жыл бұрын
Ku Ukraine zili Pati big mani
@user-mi5pe3wd6d
@user-mi5pe3wd6d 20 күн бұрын
Bakili muluzi tv 💯💯💯💯💯💯💯🤝
@VitumbikoKumwenda-sd1uo
@VitumbikoKumwenda-sd1uo 14 күн бұрын
Best Tv🎉
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 19 күн бұрын
Ulemu waanu Mr timakunyadilani kwambili.
@alimonngwinja9514
@alimonngwinja9514 Жыл бұрын
Mmawerenga plus ur talented keep it up
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera Жыл бұрын
Abwana ku Ukraine kwavutatu moti tikuyembekezera inuyo kuti mutiwuze mwasatanesatane kuti zikutinji chonde amwene tiwuzeni
@rashidchumah631
@rashidchumah631 Жыл бұрын
Timadikila inu big
@ChrifordNamphimba
@ChrifordNamphimba 20 күн бұрын
History is a best teacher
@mcdonaldajibu
@mcdonaldajibu Жыл бұрын
Yes big koma musamasowe kwambiri
@anudihlee210
@anudihlee210 Жыл бұрын
Big man inuyo palibeso, ineyo mbuyo mwanu basi even this week I have been waiting for ur updates I hope u will drop another one as soon as possible
@fanekonala
@fanekonala 7 күн бұрын
Thanks
@dysonmasiye5736
@dysonmasiye5736 20 күн бұрын
Zoonadi mukamachoka simmasadzika inu timangodabwa kanyimbo ko akukupitira kenako ziiii 😅 Komatu ulamuliro wa Kamuzu anthu ambiri anazunzika nao ndipo ambiri anaphedwa mmmm... Detention without trail eish 😢
@user-bn5ed4ky6q
@user-bn5ed4ky6q 7 ай бұрын
Best TV
@isaledambe
@isaledambe Жыл бұрын
Ko. A kuzungulirakooo... Nkhani yonse akanatha kuinena mu mphindi zitatu basi. Chonde mudziyesetsa osamabwerezabwereza.
@humairamalombe295
@humairamalombe295 Жыл бұрын
Very nice bro Yatsala mbiri ya macholowe
@wisikitiyesi1224
@wisikitiyesi1224 Жыл бұрын
Thanks brother
@Samkay66
@Samkay66 2 ай бұрын
Mr kuThyolo ufumu waNgamwani Uliko ndipo uli muKhonjeni Kuli Ngamwani 1 komaso Ngamwani 2, so tatifotokozereni bhobho
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer 23 күн бұрын
Kma Malawi sazathe ndithu coz zinthuz zidachok patal 😏😏😏😏🙆‍♀️🙆‍♀️
@alexahmedmwale-es8hk
@alexahmedmwale-es8hk Жыл бұрын
Ufumu wa ngamwani ku thyolo udakalipo, bambo anga kwao nka mfumu ngamwani yomweyo chaku khonjeni uko
@ruthtimothy9583
@ruthtimothy9583 Жыл бұрын
Thanks big brother ❤🔥🔥
@mtholabdulchafi-du7zg
@mtholabdulchafi-du7zg Жыл бұрын
Thanks bro ulemu wanu
@mussapeyala5981
@mussapeyala5981 Жыл бұрын
Timamva kukoma big,respect...
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Жыл бұрын
Kanyimboka musaleke kukayimba.
@patisonlufan2823
@patisonlufan2823 Жыл бұрын
Timakunyadilani big.muzitipatsila nkhani dairy plz
@christopherbokosi514
@christopherbokosi514 Жыл бұрын
Kodi nkhondo yaku Ukraine ikuyenda bwanji brother
@victormaulika6523
@victormaulika6523 Жыл бұрын
Ndinu dada amwene
@mustaffahhemmad
@mustaffahhemmad Жыл бұрын
U are n 1
@dytonkunchwachwa-sk8jg
@dytonkunchwachwa-sk8jg Жыл бұрын
Mumatimvesa kukoma brother keep it up 👌
@farookousmane715
@farookousmane715 Жыл бұрын
Thanks taphunzira
@fredodhawadi482
@fredodhawadi482 Жыл бұрын
Mulendo wina kamuzu
@gvtl7201
@gvtl7201 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂
@chrissygama8678
@chrissygama8678 Жыл бұрын
Tikufuna update yaku Ukraine
@sergiopauloposse7610
@sergiopauloposse7610 Жыл бұрын
Obrigado pela informação.
@ayamijackson1443
@ayamijackson1443 Жыл бұрын
Athu akaletu anali ogwilizana ndiolimbatima sati Bado wathuwuno zovetsa chisoni kwabass kumaona kut zikuchitika ndizoipa koma timangozisekelela cholinga tipezepo kenakale bass mmmmmm
@symonyohane6989
@symonyohane6989 Жыл бұрын
proud of my home Thyolo ,Tachoka kutali !!!!!
@jameschipula4475
@jameschipula4475 Жыл бұрын
Make more videos please
@princempalira2748
@princempalira2748 Жыл бұрын
nice one boss, but ufumu wa Ngamwani ukadalipo sudathe ulipo, ineo I am from that village
@charlesmasauko4651
@charlesmasauko4651 22 күн бұрын
Im on top
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 Жыл бұрын
Respect wankulu umantha
@christophermmakiwa7829
@christophermmakiwa7829 Жыл бұрын
Ufumu wa ngamwani ulipo mpaka pano,ine ndi wakuthyolo komweko
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 17 күн бұрын
Koma history yovetsa chisoni it's same ndi masiku ano chakwera adzipita wakupha
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Жыл бұрын
Aaaaa kodi mademowa sanayambire lero eti
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 2 ай бұрын
Kodi mukufuna kufotoza zotani fokozani mutu wa nkhani bwino bwino
@abdllahalie2633
@abdllahalie2633 Жыл бұрын
Ulemu wanu big koma tipaseni mene zikuyendela za nkhondo ya ku Russia ndi Ukraine
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 23 күн бұрын
Inuyo mumatha bro mulungu adzikupatsani moyo wautali
@JosephGkalumako
@JosephGkalumako 7 ай бұрын
Intergrity man timasangala nfi history yanu boss
@samiracharlief-su2bx
@samiracharlief-su2bx Жыл бұрын
Respect ✊🏻 igweeeeeeeeee
@moniqb7373
@moniqb7373 23 күн бұрын
Please keep reposting and making this type of content. AMalawi ambiri history yathu sitiidziwa. Ngakhale achikulire amene.
@musicoftheviolinstudios.1109
@musicoftheviolinstudios.1109 Жыл бұрын
ulemu wanu bwana.ine ndiwa kuthyolo ku khonjeni zimene mukunenazi makolo amandiuzaso ai ndithu mumakamba zoona.
@daviemafunga
@daviemafunga Жыл бұрын
Timakhara tikudikira Dairy pano brother chonde ziyesesani kutiponyera pafupipafupi
@madaritsoreis-ip3qr
@madaritsoreis-ip3qr Жыл бұрын
Zilibwino big koma za Russia zili pat
@abumussah9766
@abumussah9766 Жыл бұрын
Was big problem
@ibrahimalie8549
@ibrahimalie8549 Жыл бұрын
ndiye mwati mwasazika pamenepa big kkkkkk
@RatifMakiyi
@RatifMakiyi Күн бұрын
Tikudalira inu kt tiziwe zambiri
@BizweckMasamba-pe5bu
@BizweckMasamba-pe5bu Жыл бұрын
Mulandile ulemu mtsogoleri 👏👏
@dannkhoma8189
@dannkhoma8189 Жыл бұрын
Ufumu wa Ngamwani ubwerere nsanga
@JeremiahNgwira
@JeremiahNgwira 2 ай бұрын
Ngati m'mene mkunamila ngozi ya ndege ya Chilima'.
@user-kn1hq2lp8h
@user-kn1hq2lp8h 10 ай бұрын
Kwangamwani ufumu uliko untill now
@paulthulama
@paulthulama Жыл бұрын
big ulemu wanu koma munakhalisatu koma ulemu wanu
@chitimbethegreat-pc1bp
@chitimbethegreat-pc1bp Жыл бұрын
Munayambs bwino koma mwasokoneza poti ufumu wa ngamwane unatha ili ndi bodza lakulu because my village is next to Ngamwane village and kuli Ngamwane 1ndi Ngamwane 2 ufumu ulipo kafufuzeninso kawiri
@bakilimuluzitv3371
@bakilimuluzitv3371 Жыл бұрын
Ngamwane anali Sub T/A not nyakwawa. Ufumu weniweni wa Ngamwane unathetsedwa ndipo umene ulipo uja anaukhazikitsa ndi Bakili Muluzi pa zifukwa za ndale. Go and check there and you will find out that Ngamwane is just nyakwawa not even Sub T/A
@chitimbethegreat-pc1bp
@chitimbethegreat-pc1bp Жыл бұрын
@@bakilimuluzitv3371 okay apo ndiye ndakumvani ndi nyakwawadi
@suleimanrabson4367
@suleimanrabson4367 Жыл бұрын
Respect bro
@PatisiMayilosi-h3w
@PatisiMayilosi-h3w 20 күн бұрын
Continue
@user-vl9zt9mf9t
@user-vl9zt9mf9t 4 ай бұрын
A presenter a pologalamu iyi mumabwerezebwereza mukamatipatsa nkhani maka mukamapereka zitsanzo motero mumatopetsa okutsatilani. Too much kuzungulira musanafike pa nkhani yomwe mwatibweretsera. Musinthe
@jezalakaphuka7325
@jezalakaphuka7325 Жыл бұрын
Nganwane. . Koma Thyolo nkona kunatuuka ma Prezdent
@chrischisuse-rq1lp
@chrischisuse-rq1lp Жыл бұрын
Inuyo ndi amfumu
@malolajunior5898
@malolajunior5898 Жыл бұрын
Inuyo big mumatimvesa ku koma zambili taziziwa chifukwa chainu
@georgekalichero7829
@georgekalichero7829 Жыл бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣zoonad bro simusazika
@user-bn5ed4ky6q
@user-bn5ed4ky6q 7 ай бұрын
Mumatha boss
@JailosFirston
@JailosFirston 8 ай бұрын
Kkkk mademo anayambila Kare yet
@fannyzimba149
@fannyzimba149 2 ай бұрын
Kodi ma demo adayamba ndikale?eish anthu akukwiyatu
@josephmanda2082
@josephmanda2082 Жыл бұрын
Boza a Malawi ndichifukwa chake tikuvutika relo
@AlexKaunda-ir6rz
@AlexKaunda-ir6rz Жыл бұрын
Kamuzu chinali chisilu
@JailosFirston
@JailosFirston 8 ай бұрын
Komano mmakwana
@ThokoMaggie
@ThokoMaggie 3 ай бұрын
Bg up
@user-bn5ed4ky6q
@user-bn5ed4ky6q 7 ай бұрын
Following boss
@Gudchipwaila-by9ni
@Gudchipwaila-by9ni 7 күн бұрын
Zikumvekatu kt mwasowetsedwa
@rickiez
@rickiez Жыл бұрын
Zoonadi kwa msundwe palibe mzimayi amene anagwiliridwa
@Justman34_dislike
@Justman34_dislike Жыл бұрын
History ya bhoo
@rickiez
@rickiez Жыл бұрын
🔥🔥🔥
@JosophineSolobala-hp5ds
@JosophineSolobala-hp5ds 16 күн бұрын
Summary bwana😢
@mclorydamiano
@mclorydamiano Жыл бұрын
So bad🤔
@blessingsmaulid8776
@blessingsmaulid8776 Жыл бұрын
Zikomo kwambiri big
@mussaabass925
@mussaabass925 Жыл бұрын
Inuyo mumakwana big ulemu wanu
❌Разве такое возможно? #story
01:00
Кэри Найс
Рет қаралды 6 МЛН
Magic or …? 😱 reveal video on profile 🫢
00:14
Andrey Grechka
Рет қаралды 52 МЛН
Чёрная ДЫРА 🕳️ | WICSUR #shorts
00:49
Бискас
Рет қаралды 7 МЛН
GTA 5 vs GTA San Andreas Doctors🥼🚑
00:57
Xzit Thamer
Рет қаралды 25 МЛН
Kamuzu Academy - Malawi - "The Eton of Africa" (1987)
49:37
kasiyamaliro
Рет қаралды 47 М.
HON.DAUSI kufotokoza bwino mbiri ya KAMUZU BANDA pa @MibawaStudios
29:12
LIKI-LIKI Ladies
Рет қаралды 18 М.
Kamuzu Banda House|Ngulu ya Nawambe
2:36
My Malawian Life Experiences
Рет қаралды 82 М.
GWEDEGWEDE LERO PA 5 SEPTEMBER  2024 |
30:28
DZIWE TV
Рет қаралды 10 М.
Was Kamuzu Banda a Colonial Imposter?
18:29
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 34 М.
TAMVANI NKHANI ZA MMAWA || 05 SEPTEMBER 2024
18:54
Blenac Malawi
Рет қаралды 3,2 М.
A MOSES KUNKUYU KU PROGRAM YA KULINJI
39:13
HOT 265
Рет қаралды 17 М.
❌Разве такое возможно? #story
01:00
Кэри Найс
Рет қаралды 6 МЛН