anthu a kumulanje amenya anthu otchera Bomba

  Рет қаралды 1,942

Sam Malvitha

Sam Malvitha

Күн бұрын

Пікірлер: 16
@KayceeHQuavo
@KayceeHQuavo 8 сағат бұрын
Kusadziwa ndikufa komwe😂😂😂 athu akumulanje ndi mbuli😂😂😂😂😂
@FrankSolobala
@FrankSolobala Сағат бұрын
Ndopepera Sam MAVITHAI sanave bwino ameneyi
@VernonMsowoya
@VernonMsowoya 49 минут бұрын
Education is a key, cyclone chido akuononga ku Mozambique nanga ku Mozambique ko ndikumulanje
@PriscaMussah
@PriscaMussah 56 минут бұрын
Dziko linaipa ili,anthu tungokhala amqntha ,nde eeesh zagwa zatha
@FrankSolobala
@FrankSolobala Сағат бұрын
Mmmmmmm ndy kucheza amacheza usiku osafufuza bwino bwanji zopusisana timadana nawo ife sopusa akumulanje
@AnnieJumaNaitanda-qj1iz
@AnnieJumaNaitanda-qj1iz 36 минут бұрын
Mukananena kuti anthu akumimosa osati akumulanje ayi
@MadalitsoMarcos
@MadalitsoMarcos 7 сағат бұрын
Kkkk kma abale inu polani moto❤😂😂
@MolesBrown
@MolesBrown 7 сағат бұрын
Kumulanje anthu ake ee amakhala ngati akubulundi chifukwa anthu ambili amakhulupilila minda yatiyi ndiye ena ndiwosaphunzila koma ndi amakani kwambili mungowakhulukila
@MikeLupiya-l8j
@MikeLupiya-l8j 3 сағат бұрын
Kodi Ndi mulanje yense wamenya anthuwa?
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 6 сағат бұрын
Chalakwe chikangawa delivers
@osaukaonjoya
@osaukaonjoya 8 сағат бұрын
Dziko la Malawi silili bwino ndithu
@mariawachesterweluzan
@mariawachesterweluzan 8 сағат бұрын
Athu amenewa,kwakura m'nkusazindikira umburi mungowa nkhurukirira🤦zopatsa manyazi🙏
@Justin_Nano
@Justin_Nano 8 сағат бұрын
🎉🎉🎉
@janschutte7515
@janschutte7515 8 сағат бұрын
Anawachita bwino olo akanaphedwa. Iwenso wa Sam maviltha take care pa zimenezi. usawatenge anthu aku MULANJE ngati ankapanga zopepera but they are protec their children from devil. Satana ali ndi ma agent oyenda ndi miyendo ku dziko not za mbola zomwe ukuganiza apazi God is watching you take care
@CalebStevens-qm3sw
@CalebStevens-qm3sw 8 сағат бұрын
nde ma agent a satanikiwo akanayambira ku madagascar osati ku mulanje mpwanga panyapako zaka 40
@Ggg-q5h2e
@Ggg-q5h2e 43 минут бұрын
😂😂😂 ma agent asatana et?? Iweso ndmbuzi😂😂😂
Chiganizo Cha Kaliyati Pa Ndale
4:13
Sam Malvitha
Рет қаралды 4,4 М.
Mom Hack for Cooking Solo with a Little One! 🍳👶
00:15
5-Minute Crafts HOUSE
Рет қаралды 23 МЛН
Enceinte et en Bazard: Les Chroniques du Nettoyage ! 🚽✨
00:21
Two More French
Рет қаралды 42 МЛН
Malodza Akuchikangawa A Poem by Sir Michael Benjala
5:00
Clement Thanda
Рет қаралды 12 М.
DR LAZARUS CHAKWERA ANSWERING QUESTIONS  AT THE PARLIAMENT
1:21:21
Umatha Daily
Рет қаралды 2,7 М.
KALINDO KUWATEMBENUKIRA OTSUTSA.. IYIYINSO NDE WAITENGA KUTI?
13:55
Malawi Lero🇲🇼
Рет қаралды 290