Atha kubwelera ku DPP no problem,, Mu Ndale mulibe udani wokhazikika ndiye tingoti phee tione.
@PaulMlotaКүн бұрын
Upepera Kweni Zisiye za UTM
@AmosMumba-s7r22 сағат бұрын
Kwao ndi chipani Cha DPP akawinaso uku
@felixjoseph8161Күн бұрын
Ngati MCP inalandila Ben longwe uja ankati chakwera ndi osadula komaso Mai yolamu alibe zokoka lero akudya ndi chakwera uku akumupwala opanda zokoka Mai yolamu
@UlayaInan3 сағат бұрын
Akufuna kuthetsa UTM Awa mbuzi za anthu ndi galu kwabsi kaliati
Mai kaliati ngati akufuna kuti akhale mp pakufunika kuti alowe Dpp basi
@FracksonMadani2 күн бұрын
Apite ku dppko adzatipeza tikalowa m'boma chaka chamawa
@ElizabethMulindeКүн бұрын
Ndipo kupangila zithu mphuma sizingawapindulile Kodi amafuna anthu onse awine Kodi aaaaa asaonetseso umbuli nawo akaliati mwava kabambe anamusakha ndi anthu osati amalowa ekha ayi ngat sakufuna akhale ubwino wake mulungu akaloza waloza utm idzidzimutsa anthu next year take it or leave it
@CatherineDesireКүн бұрын
Mlimotsemo kaliati iwe umakwana ku DPP ku UTM you are welcome kupatula ku MCP kokha ayi utsaelekedze,Akweni DPP ,UTM kaya Aford ndi bho bho basi
@kechu289Күн бұрын
Oooh! Yes, she fits well in DPP. She would be getting back home. I party of angry leadership. Listen to their press conferences,always looking angry. If there is no thaw in the presentation, DPP will prequalify for for the opposition.
@DalitsoKaundaКүн бұрын
Abwelere akweni Ku DPP Ife tisangalara kwambili ❤❤
@KondwaniLimitoniКүн бұрын
Taikonda imeneyo❤❤❤❤😂
@ephraimkamwana26094 сағат бұрын
go back ku DDP mamie
@ChristopherChanza-i4y2 күн бұрын
Olo atabwelela tkhoza kumulandila ki dpp
@KennedyPhiri-h9h2 күн бұрын
Aka Akalowe ku dpp ndi akakhala mp kwawo akawina mosavuta
@alickmathias20972 күн бұрын
Appange momwemo abwere ku dpp
@Enock-gu5ffКүн бұрын
I agree with you atabwerera zicita bwino kwambiri tizinena zoona dpp imatha zipaso zace ziripo mwaaona abusa mayankhidwe ao kunyumba ya parliament kurephereka kuti angoti zoona zinthu sizilibwino komakumangoonjezera kuwawisa amarawi ntima
😂😂😂 sitimavotera munthu ife koma timavotera chipani
@kechu2892 күн бұрын
An opportunist polician.
@INNOMAXOGEZZUКүн бұрын
Tiyen ku DPP mayi anga
@WarriorKB-l3iКүн бұрын
Ndamvetsedwa kuti anthu a ku dera kwake amuza kaliyati kuti ngati akufuna kuti amuvotele pa uphungu abwelele ku dpp cifukwa dpp imapanga zimene munthu wakumuzi akufuna nde ngati akweni angabwelele ku dpp musadabwe anena ndi anthu akwawoko. Adad ndiomwe ali mmitu ya anthu
@AbdulAbelabelAbelКүн бұрын
Abwelele ku dpp
@Moyoyohane-i9hКүн бұрын
Inetu ndikugwiri zana nazo zoti apite ku D p p
@ThomasChaiwela19 сағат бұрын
Abwelele ku mudzi
@AlumakioChingalu2 күн бұрын
Abwerere ku DPP ndipo adzapambana u MP..?UTM manyaka sangawine ali mu UTM
@SirahtSafuone2 күн бұрын
Zikawoneka ndinthu
@MathewsMandutu-q9lКүн бұрын
AKWENI AKWENI bwelani malo alipo
@VeronicaSekobi-is6dk2 күн бұрын
❤🎉
@Chikumbutso-i6q2 күн бұрын
Waganizabwino
@BlessingsKamwendo-z9gКүн бұрын
Bwelani akweni takulandilani kale tilibe nanu vuto
@AxelDada2 күн бұрын
Sono za manganya zili pati???
@Edward-y3v2 күн бұрын
Azipitaso ku tikuferanji kkkkkkk
@MagretMatemba-r7xКүн бұрын
Lowani dpp mupambana kwinaku mmm
@RajabIsmailazahaya-x9t2 күн бұрын
❤❤❤
@HaroldMgomezulu-i4m2 күн бұрын
Good decision go back to dpo
@anthonysawa20392 күн бұрын
Koma adzapezeka wa mtima ofuna kutumikira a Malawi posayang'ana udindo? Mayiwa akundikumbutsa royalty yomwe anali nayo pa a chilima