ASILIKALI AULULA ZA IMFA YA Dr Saulos Chilima

  Рет қаралды 290,141

Beyond Borders Odyssey-

Beyond Borders Odyssey-

Күн бұрын

Пікірлер: 457
@FrankAndisen
@FrankAndisen 2 күн бұрын
God will protect you mr❤
@MirajiYusuf-vx5ux
@MirajiYusuf-vx5ux 7 ай бұрын
Mcp ndiya kupha God bless u brother for your information
@SidnChisanga
@SidnChisanga 24 күн бұрын
Thanks bro God protect you
@VanetMusale
@VanetMusale 7 ай бұрын
Thanks for that info
@FosterBonongwe
@FosterBonongwe 7 ай бұрын
Thank U brooo
@LovenessGerald-n7f
@LovenessGerald-n7f 7 ай бұрын
Thank you bro God bless you til
@edsonKatanda-o1y
@edsonKatanda-o1y 7 ай бұрын
There's no secret under the sun . You are the most brilliant person, the truth will prevail.
@JanaJovian
@JanaJovian 7 ай бұрын
MCP milimazi
@JanetPhiri-b9x
@JanetPhiri-b9x 7 ай бұрын
Thanks for your information boos
@JosephNgona-f9v
@JosephNgona-f9v 7 ай бұрын
Mbuzi za anthuwa thanks brother may GODbless you .komanso ndamva kuti boma likukusakani be strong brother GOD is with u
@SkevaMustapher
@SkevaMustapher 7 ай бұрын
Big man osawopa mulungu akutetezen muchilichonse polimba mtima kulankhula chilungamo kut amaliwi adzidziwa chilungamo pitilizani kutidziwita ifenso ngat amalawi zikutiwawa kwambili nmitima yathu😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@BlessingsMadaSiment
@BlessingsMadaSiment 7 ай бұрын
Please look over ur self mwene we proud of you since u has done the best what you have done take care of yourself mwene❤
@MwaleNoxious
@MwaleNoxious 2 ай бұрын
Thank you so much for being so courageous. We want courageous soldiers like you_KEEP IT UP!.
@ZenzenWezere
@ZenzenWezere Ай бұрын
Thanks bro god bres you ❤❤❤❤❤
@ChiccoJeke
@ChiccoJeke 2 ай бұрын
God is with you no worry for this truth thanks
@ClaraMakowa
@ClaraMakowa 7 ай бұрын
🎉🎉osaopa brother chilungamo chiululike bas kuipadi anapangaku mmmhu
@PeterMakwiza
@PeterMakwiza 7 ай бұрын
Thanks for the information. God will protect u from evil people.
@ceeceenel4254
@ceeceenel4254 7 ай бұрын
Amen
@DerickZiba
@DerickZiba 7 ай бұрын
May God protect us Malawi please in Jesus name.
@DerickZiba
@DerickZiba 7 ай бұрын
Thanks
@TithahChauluka
@TithahChauluka 7 ай бұрын
Thank you oir brother
@kelvinskada5619
@kelvinskada5619 7 ай бұрын
Thanks bro, may heavenly god protect you
@GiftMunthali-k6e
@GiftMunthali-k6e 24 күн бұрын
Mmmm
@feliciajohn6041
@feliciajohn6041 7 ай бұрын
Ambuye akudalitsen brother osaopa
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 7 ай бұрын
Good Messnge Chakwela you mast go
@Kaliati91
@Kaliati91 7 ай бұрын
must
@FosterBonongwe
@FosterBonongwe 7 ай бұрын
​@@Kaliati91😊l
@FosterBonongwe
@FosterBonongwe 7 ай бұрын
​@@Kaliati91😊l
@dorcagmrs1776
@dorcagmrs1776 7 ай бұрын
May God protect you brother and keep you alive for your family and friends 🙏 Amen
@MugabeKenneth-kn5ug
@MugabeKenneth-kn5ug 7 ай бұрын
God will protect you sir
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj 7 ай бұрын
Much impressive solder peace of malaw👍
@hastingsganizani9698
@hastingsganizani9698 7 ай бұрын
Thank you brother for your information! 😭🙏😭
@LuciousJohn-f6r
@LuciousJohn-f6r 7 ай бұрын
May God protect you from your enemies
@ehinsupport3217
@ehinsupport3217 19 күн бұрын
Wabodza uyu ,adali kuti nthawi yonseyi? That is just a move brother, musatinamidzepo apa
@AlexKaunda-w7l
@AlexKaunda-w7l 2 күн бұрын
😢😢😢😢😢 koma chakwera uli ndi zambi nyini yamako
@IsmaelSaide-qg4xe
@IsmaelSaide-qg4xe 7 ай бұрын
Msilikari sakhara ndi mantha bro No retreat no surrender tigwiritsa ntchito lamulo la kamuzu loti OPHA NZAKE nayenso APHEDWE
@CremeciaMdifu
@CremeciaMdifu 7 ай бұрын
Pibenso njira ina, nayenso abale ake ayidziwe imfa kt ndiyopweteka bwanji
@ChipantaGlory
@ChipantaGlory 7 ай бұрын
God will protect you for saying the truth
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 7 ай бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@TelezinaKapichila
@TelezinaKapichila 7 ай бұрын
Shaaaa
@MosesSalle
@MosesSalle 7 ай бұрын
Alhamdulillah Allah akudalitse m'bale wanga
@VeraChalire-t6e
@VeraChalire-t6e 7 ай бұрын
Bwana musaope, Iman pa chilungamo, ambuye aika chonchinga ku mbali yanu, imfa ya wanthu osalakwA, mulungu sakhara chete
@AufiThera
@AufiThera 7 ай бұрын
We can't live you alone 😭 I know you know km bro mr wasili chilungamo mwanena ndipo chakaela ndimu oipitsita
@johnmiselo2230
@johnmiselo2230 7 ай бұрын
These are the people we want otherwise we are following you from Zambia
@Justman34_dislike
@Justman34_dislike 7 ай бұрын
Brave soldier. Bravo. Thanks. We are all affected
@LayssancautressCautress
@LayssancautressCautress 7 ай бұрын
Pipa chakwela
@LayssancautressCautress
@LayssancautressCautress 7 ай бұрын
😢
@mphatsonandolo4294
@mphatsonandolo4294 7 ай бұрын
😭😭😭😭 rest well bwana Chilima
@aggiemlotha1208
@aggiemlotha1208 7 ай бұрын
Congratulations to Manganya the VP🎉
@JoyceMvula-mz2do
@JoyceMvula-mz2do 7 ай бұрын
Koma ndi zoonadi izi? 3:01
@CeciliaMphili
@CeciliaMphili 7 ай бұрын
Mutulutse ndithu maumboni ambili iululike khaniyo 🙏🙏🙏
@Costance-nf7ue
@Costance-nf7ue 7 ай бұрын
God bless you brother where there is justice. There is no fear ,and fear not God is in control
@BlessingsmadalitsoShumba
@BlessingsmadalitsoShumba 7 ай бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉 ntchito zonyasa siziyenera kukhala mziko mwathu mulungu akudaliseni brother ♥️ love you
@HassanSinoya-wl3vl
@HassanSinoya-wl3vl 7 ай бұрын
Zikomo kwambili bg man mundu wakhulu takuvani ndithu 😢😢😢
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 7 ай бұрын
❤❤❤❤❤
@MarthaChawantha
@MarthaChawantha 7 ай бұрын
I pray for your security big ur very important to us
@WorryMwafulirwa
@WorryMwafulirwa 13 күн бұрын
Zachitsoni kwambiri pa imfa ya Dr Chilima
@Brigahchagwetsa
@Brigahchagwetsa 7 ай бұрын
Ziko la malawi 🇲🇼 ziko langa ine 😢😢😢😢😢
@ChikondiNtolo-re3ut
@ChikondiNtolo-re3ut Ай бұрын
Good soldier
@MilacleSankhani
@MilacleSankhani 7 ай бұрын
Fire
@ThammyMoyo-p6s
@ThammyMoyo-p6s Ай бұрын
😭 Mwana wa zawo,
@RoseBwanali
@RoseBwanali 7 ай бұрын
Mulungu azikutetezani brother 💕💕
@OmexMasikoya-q2h
@OmexMasikoya-q2h 4 ай бұрын
Mwazi wamuthu ndiwovuta
@blessingkamanga1781
@blessingkamanga1781 7 ай бұрын
This one is a total liar. Where is the video. Anthu 4, anyapala abundance, asilikali aku Israel ndiye tigwire ziti? Tiyeni tilire maliro mwamtendere
@KondwaniMunyimbili
@KondwaniMunyimbili 7 ай бұрын
Zikuoneka zopweteka poti zili kwa zanu bro osapepusa zinthu
@CleopatraDaka
@CleopatraDaka 7 ай бұрын
To God no secret when you hide God brings you on open and God will strike back just continue praising God
@JessicaKatugwe
@JessicaKatugwe 7 ай бұрын
mulungu akukute bro and tikukuika mmanja mwamulungu wamoyo akutetezeni
@LynessBuwa
@LynessBuwa 7 ай бұрын
Iziii ndiye zoyambanisa mudziko iziii
@AndersonAnusah
@AndersonAnusah 7 ай бұрын
Come on men
@ChipiliroKafodya
@ChipiliroKafodya 7 ай бұрын
Ulura Malawi tiziwe zoona
@ProspaMitumba
@ProspaMitumba 7 ай бұрын
mulungu akhara nanu soldier msilikari weni weni aziima pacilungamo
@victormulolo8126
@victormulolo8126 7 ай бұрын
Ambuye akudalitsen supermarket mbalewanga chauta ndiwaphavu
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 7 ай бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@ShakiraKairosaidi
@ShakiraKairosaidi 7 ай бұрын
They've crossed the line koma 😢😢😢😢
@BostonMalack
@BostonMalack 7 ай бұрын
Takumvani amene Koma inuyo nanga mumkalorera bwanji kuti zosezi zidzichitika osapangapo kanthu muli msitikali braz mmadikira mpaka move yawoyi itheke nde muzikamba chomchi mwatiliza zedi mukadapewetsa mkadakhala abwino mwene taluza abale anthu inuyo move yose zisanachitike muidziwa eish
@jameschisinga7676
@jameschisinga7676 Ай бұрын
Okay
@OmexMasikoya-q2h
@OmexMasikoya-q2h 4 ай бұрын
E chakwera adapara pa mission imeneyi
@ChikuCharlie-w5f
@ChikuCharlie-w5f 3 ай бұрын
Broken heart beyond repair 😭😭
@agreementphiri5416
@agreementphiri5416 7 ай бұрын
Truth will set you free soldier
@linleychimenya7554
@linleychimenya7554 7 ай бұрын
Very Sad May His Soul Rest In Peace the Bible said Truth will Set You Free God knows what happened my condolences to Vice President Family and all the families of those who died along with His May their Souls Rest In Peace God Protect You the spirit of the dead will fight back
@JoyceKasongo-s8k
@JoyceKasongo-s8k 7 ай бұрын
God bless u
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 9 күн бұрын
Mwalowesa ndale galu uyu wa DPP iwe😂😂😂😂😂😂😂
@MathewsSande
@MathewsSande 7 ай бұрын
Ameneyo akunama si nsilikali ayi ndi kadeti wa dpp amutuma , angotaya nthawi yake yemwe ataweruze nkhaniyi ndi MULUNGU basi osati munthu ochimwa ngati ameneyo , komanso umboni owona kwa munthu wanzeru oganiza bwino mwa umunthu akudikiranso kwa MULUNGU yemwe osati wakuba onama ngati uyu akulankhula apayu asakunamizeni ameneyo
@ncubeadja
@ncubeadja 7 ай бұрын
Vuto inuyo Mbali yomwe muli simungawone vuto payimfa imeneyi zifusen nokha kut chomwe anayimisila oparetion yosaka chinali can kmaso chomwe anachedwela kuyamba kusaka chinali can chosecho office tandege imakhal ikuwona zose zikuchitika ndamene amawawuza mayendedwe kut sika kapen ay Malawi tiyen tivomekeze kut waphedwa
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 7 ай бұрын
Ziwani kuti akanakhala m bale wanu simukanayakhula chochi musamadane ndi athu osalakwa a DPP mulungu akulangeni nose
@ChikondiNyirenda-ei3vu
@ChikondiNyirenda-ei3vu 7 ай бұрын
Macadet mmatha kuononga mbiri ii
@amosphakira7936
@amosphakira7936 7 ай бұрын
Nanga umboni wako iweo ndiwotani, kusonyexa kti Anthuwa Sanaphedwe?
@amosphakira7936
@amosphakira7936 7 ай бұрын
Munthu ameneu ndi Wachiyani chokupha MCP ,nchifukwa akuyankhula manyi . Wasala ndi masiku ochepa tikudxiwa bwno lmwe kmaso pamene umakhala tikudxiwapo ,udxafotokodxa bwbwno .
@HalsonFalesse
@HalsonFalesse 7 ай бұрын
More fire
@SiboPaul
@SiboPaul 7 ай бұрын
Fight for justice
@khasimMusa-d3w
@khasimMusa-d3w Ай бұрын
Zosayenda ndthu km ubwino ukamasewela mu Damu Lang,Ona olo Ng,ona itagona km uziziwa Kut sikulina muzakumana ndpo izakuluma Chfukwa achlima anali mathu wakulu km sikut MCP samaziwa ayi 😭 vuti anafulumila kumedza adatafune lelo Makan awo Malawi tikuvutika 😢😢😢😢😢😢
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula 7 ай бұрын
Ukhare ndi wina mzako wachinsisi uzimupatsa mavideo ena asadziwe
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 7 ай бұрын
Eya chifukwa akhoza kumusowesatu mmm
@MarkChigwe
@MarkChigwe Ай бұрын
Sindiwe silikali ife timamudziwa silikali
@RosinaPatel
@RosinaPatel 3 ай бұрын
Mulungu ndi amene amalanga..soon tiziona
@StonardJacobPhiri-cs7zd
@StonardJacobPhiri-cs7zd 7 ай бұрын
😢
@GiftMusorola-l2o
@GiftMusorola-l2o Ай бұрын
Nkhani maliro yatopesano sitingathandize anthu akuvutilka Ndi njala ngati mumakonda aMalawi
@AngellaNazombe
@AngellaNazombe 7 ай бұрын
Keep it up Mr ❤
@DafatzMw-265
@DafatzMw-265 7 ай бұрын
We stand as a nation 🇲🇼
@Hellenistic109
@Hellenistic109 5 ай бұрын
Chilungamo ciyende ngati Madzi..Tell Us and Tulusani tione please!
@GiftMwaungulu
@GiftMwaungulu 7 ай бұрын
Mulungu odziwa zobisika atiululira zonse pangatalike bwanj chilungamo chizadziwika.
@GraceSayenda-dq5tn
@GraceSayenda-dq5tn 7 ай бұрын
Palibe chinsinsi Pasi pathambo!!Mulungu akhathe aliyense watengapo gawo pangozi imeneyo💔😭
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 7 ай бұрын
Muziti pa kupha kumeneko
@WadsonMlongoti
@WadsonMlongoti 7 ай бұрын
Abare mpaka apa zikomo powulura izi Allah mwini moyo akusungeni ndipo ululani ziko liziwe 😂😂
@OmexMasikoya-q2h
@OmexMasikoya-q2h 4 ай бұрын
Layivi
@AdmoreSingini
@AdmoreSingini 7 ай бұрын
Big up soldier....
@JustinShumba
@JustinShumba 7 ай бұрын
We want justice for SKC &8 others.. 😢😢😢
@DouglasLapozo
@DouglasLapozo 7 ай бұрын
😭😭😭😭 exactly bgy
@ZaithwaBanda
@ZaithwaBanda 7 ай бұрын
Amene akulankhulayo akunena kuti iyeyo adawava anthu akulira mu ndege,iyeyo adalekeranji kuthamangirako kukawaombotsa being a soldier
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula 7 ай бұрын
Ixivetsetsatu iwe
@SamuelKachepa
@SamuelKachepa 7 ай бұрын
God will protect you 🙏
@FranceQongwane-ro5yr
@FranceQongwane-ro5yr 7 ай бұрын
Ndiye ndege zonsezi zimagwa pa dziko lapansi ndi chakwera
@OmexMasikoya-q2h
@OmexMasikoya-q2h 4 ай бұрын
Manyi ako ndifuso lopoyiralo
@DavidMonjeza-mh8yp
@DavidMonjeza-mh8yp 7 ай бұрын
Mwenewa atibalalitsa Sured Mulungu ndamene akudziwa choonadi
@MaryMary-m6b
@MaryMary-m6b 7 ай бұрын
Dis s true
@AsanGeorge-yx1ht
@AsanGeorge-yx1ht 7 ай бұрын
Aziwika, aoneka, kno secret under the sun....rest in peace our hero skc
@YusufuMdala-e1c
@YusufuMdala-e1c 20 күн бұрын
Wina aliyense amene akhudzidya ndi nkhani iyi ngati sakulankhula pagulu pazomwe akuzidziwa zadzaupaza mtendere mpaka yesu adzabwera don't take this for granted simulipezatulo mpaka mulavue basi.
@FionaKhoma
@FionaKhoma 7 ай бұрын
Osaopa chilungamo chaoneka kare kmaso kulibe angakuphen gwiran tchito yanu osaopa muthu
@OmexMasikoya-q2h
@OmexMasikoya-q2h 4 ай бұрын
Ameneyi ngt mkutipha atiphadi
@ClementMwahimba-u2n
@ClementMwahimba-u2n 2 ай бұрын
If there's people who wants to revenge imfa ya skc inenso ndili ready to revenge. Skc anaphedwa mwachipongwe kwambri
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 7 ай бұрын
Talumikizanani olimba mtima inu asilikali mutatenga bomali muyese kulamulira kwa 2yrs yokha,anzanu a 1992 anali olimba mtima anapanga operation bwenzani,mzanu Ibrahim Traore 34yrs old analimba mtima pano zikuyenda ku Burkina Faso,mukawalekelera atitafuna tonse amoyo
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 7 ай бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@EstherBeza-hd3kw
@EstherBeza-hd3kw 7 ай бұрын
Abare ululani zonse athu agwidwe😭😭😭
@JonahTBrighton
@JonahTBrighton 7 ай бұрын
God is watching
@apatsachintengo
@apatsachintengo 7 ай бұрын
Zoti ndi msilikali I doubt but the info might be right
@AllanNkolimbo
@AllanNkolimbo 4 ай бұрын
I want to know more
@MayesoChingoma-zq8fg
@MayesoChingoma-zq8fg 7 ай бұрын
Bg mn Mulungu akudaliseni ndipo akutetexereni
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 7 ай бұрын
😢😢we need you
BON KALINDO LERO PA 23 JANUARY WAULURA IZI
15:38
Makosana
Рет қаралды 10 М.
Как Ходили родители в ШКОЛУ!
0:49
Family Box
Рет қаралды 2,3 МЛН
КОНЦЕРТЫ:  2 сезон | 1 выпуск | Камызяки
46:36
ТНТ Смотри еще!
Рет қаралды 3,7 МЛН
JISOO - ‘꽃(FLOWER)’ M/V
3:05
BLACKPINK
Рет қаралды 137 МЛН
🎈🎈🎈😲 #tiktok #shorts
0:28
Byungari 병아리언니
Рет қаралды 4,5 МЛН
KUSEMPHANITSA KWA ZIZIMBA, ZOMWE ZINAPHETSA SAULOS CHILIMA 🤯😭
35:46
Padziko LAPANSI PALIBE CHISISI. ZAWULULIKA ZA NGOZI. NTANYIWA
31:26
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 55 М.
Как Ходили родители в ШКОЛУ!
0:49
Family Box
Рет қаралды 2,3 МЛН