BISHOP MSUSA WAKANA REPORT LA CHILIMA KUTI SIZINAYENDEPO BWINO NDIPO CHILUNGAMO SICHINATULUKEPO

  Рет қаралды 10,570

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 62
@PatriciaChivuwa
@PatriciaChivuwa 3 күн бұрын
Amen bishop.mulungu azikudalitsani nthawi zonse🎉
@LydiaLuhanga
@LydiaLuhanga 3 күн бұрын
Amen bishop msunsa ndipo inu mumaima pachilungamo nthawi zonse....ambuye akudalitseni ndipo ambuye ationesere chowonadi
@PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
@PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 3 күн бұрын
Ndiye mbuzi Zina zizinena kuti tisiye kukamba za ngozi ya imfa ya Chilima? Iwe umve amene ukunena kuti tisiye kunena za Chilima ndiwe chitsiru Chenicheni simbale wako ayi ndiwe mbuzi yeniyeni ...tizalira imfa ya Chilima mpaka kale... nthawi ya imfa ya a Gadama chiwanga Sangala ndi a Matenje munawaopsezanso anthu kuti asalankhule.za imfa yawo .. history is the best teacher...lero pano ndikupusa kwanuko mwayesa a Malawi ndife zitsiru zanu kuti tizikokumverani.... Zikomo Bishop Msusa chifukwa cha mau anu...No secret under the....omwe adapha a Chilima ndi anthu omwe akutilesa kulankhula za imfayi.. mwanya muona 2025 mukalowa ku Chichi ri...pachedwe pasachedwe zoonadi zenizeni zimenezi ndi 2025 basi
@JusticeChitsulo
@JusticeChitsulo 3 күн бұрын
Amen archbishop, chilungamo pa report limeneli palibedi ndipo choonadi chidziwika.
@MarthaNalivata
@MarthaNalivata 3 күн бұрын
Amen archbishop pitiluzani kutiunikira chilungamo
@HarrietMtenje
@HarrietMtenje 3 күн бұрын
Congrats Bishop
@ShuritaJansen
@ShuritaJansen 3 күн бұрын
Amen Amen 😭
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 3 күн бұрын
Amen bishop inu mumayimadi pachilungamo koma tsiku lina tizaona chilungamo pangatalike pangafupike choona chizaoneka
@wendaemily3179
@wendaemily3179 3 күн бұрын
Amen Bishop Luke
@BillyLanjabu
@BillyLanjabu 3 күн бұрын
Amen Bishop chilungamo
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 3 күн бұрын
Bravo archbishop Luke Msusa
@JustinKondowe
@JustinKondowe 3 күн бұрын
Ameni and Ameni powerful message man of God.
@BlessingsNyalugwe
@BlessingsNyalugwe 3 күн бұрын
Our bishop of moment
@MariaMlendo
@MariaMlendo 3 күн бұрын
Amen.Abishop umboniwu.ngwabodza Mlungu awakanthe
@yasiniKalonga
@yasiniKalonga 3 күн бұрын
Mdima ungakule bwanji kunja kumacha,may almighty bless you ❤❤
@BandahLemos
@BandahLemos 3 күн бұрын
Aaa mwina tizaona chilungamo tikasintha president 😭
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 3 күн бұрын
Thank u to stand for justice
@GeoffreyShariff
@GeoffreyShariff 3 күн бұрын
Amen Muthu wamulungu
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 3 күн бұрын
palibe,chingachititse,chakwela,kuchoka,paudindo
@ChikkaLemani-qw6fn
@ChikkaLemani-qw6fn 3 күн бұрын
Amen . 🙏 Mulungu wathu sadzagona tulo.
@EmmanuelDanitsa
@EmmanuelDanitsa 3 күн бұрын
History is the best Teacher
@andiwochishadreck3753
@andiwochishadreck3753 3 күн бұрын
Congratulations 🎊
@GetrudeJack
@GetrudeJack 3 күн бұрын
Amen zooona koma mulungu akuona iwe Gali chakwera
@LeganNyirenda
@LeganNyirenda 3 күн бұрын
Amen Bishop
@UncleShopRite
@UncleShopRite 3 күн бұрын
Malawi trends chonde pitiliza kuwaimilila amalawi ndipo Boma likubwelali axakukumbukile or Ka unduna sazalakwisa
@vickawelama
@vickawelama 3 күн бұрын
It will be over until is over...
@Dickies-mk8cd
@Dickies-mk8cd 3 күн бұрын
Manyazi apite kwa Chakwela wamagazi mmanjayo,big up bishop Msusa for standing strong with Malawian s.
@KingslyNamwiri-km9jl
@KingslyNamwiri-km9jl 3 күн бұрын
Mumatiyimirira a bishop ,chilungamo chiwoneke
@MarkElia-i7q
@MarkElia-i7q 3 күн бұрын
Ambuye Thomas Ambuye akudalitsen poima pa nji pa chilungamo
@PromiseKhenzo
@PromiseKhenzo 3 күн бұрын
MCP MUKAPUMA KU JAHENA😅😊
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 8 сағат бұрын
M'malo mofalitsa za uthenga wamulungu muri busy ndi kutsutsana ndi mulungu kkkkkkkk akatolika zamanyazi
@noelcheonga8247
@noelcheonga8247 3 күн бұрын
Ndipo inenso sindikukhutira nazo za report imene ija
@NoxiousGondwe
@NoxiousGondwe 3 күн бұрын
Congratulations
@ElatonGwaza-k4h
@ElatonGwaza-k4h 3 күн бұрын
Inesotu siwonkhutira ayi
@MerryWayson
@MerryWayson 3 күн бұрын
Ndamukonda Bishorp uyu tchidziwe chilungamo bas Za Imfa Za anthu amene Aja end anthu enaso akuphedwa mwachinsinsi kumangidwa aaaa Ai ndithu
@BensonGama
@BensonGama 3 күн бұрын
Koma chakwela waumva utuengau chimwendo umuuze chakwerayo
@EsetaGerate
@EsetaGerate 3 күн бұрын
❤❤❤ Amen 🙏
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 3 күн бұрын
mukufuna,chakwela,achoke,paudindo,kapema,mukufuna,lipoti,,zochoka,paudindo,muyiwale,muzinena,zalipotilokhalo
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 3 күн бұрын
Àngakhale mbuzi za MCPigs sizikukhulupirira za commission of enquiry report. Ndiye ine ndikakhulupirire?
@AchinaKellz
@AchinaKellz 3 күн бұрын
Dzawo wa biyeni uja amkamkonda uja wazelezeka angovina misokhano olo kufusa zaifa ya bwana wake apa, akuveka zovala anthu zakhope ya abwana ake mumasophenya onyasa, sikusinja akulu adalinga ataona, munthu dzako ndinjoka ndazindikira chifukwa cha mkhwari
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 3 күн бұрын
Amen amen
@AnusaNkhoma
@AnusaNkhoma 3 күн бұрын
Ndipo kuwala kunjaku zikhala poyela idziiii
@YaxedyAlast
@YaxedyAlast 3 күн бұрын
😮..
@George-zd5le
@George-zd5le 3 күн бұрын
Kunena zoona ine sindine wa utmost koma mmalawi chilima anamupha A chakwera ndi anzake
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 күн бұрын
Ndili nae limodzi Bishop yu
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 3 күн бұрын
Ndipo kwabasi
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 3 күн бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima ameni
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 3 күн бұрын
Nafe tachita kut amen
@LameckNgwangwa-g3p
@LameckNgwangwa-g3p 3 күн бұрын
Zoona ndithu bishop msusa
@WellsKasuka
@WellsKasuka 3 күн бұрын
Ndipo ufiti ulipod
@MaggieCement
@MaggieCement 3 күн бұрын
Muluzi komatu ankanena kuti kongelesi ili magazi manja misazavotere anthu kusamva bola ine thawi imene ija sinavote nawo koma lero vote yanga ikakhasulana ndiyalazalo enanu anuwo azikabwela mbuyomwanga. Akatolila finyani kolona basi chauta ayankha mapephero choonadi tichidziwa aiwala kuti alipo lero chifukwa cha chilima emweyo end asaone ngati anamaliza adzukanso ena ofanana maganizo chilimayo ndipo azagonjesa .
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 3 күн бұрын
Anthu sanabvotere Congress Koma Tonse alliance. Mfitizi zinangopezerapo mwai olowa m'boma .
@MakupeWekha
@MakupeWekha 3 күн бұрын
Zoonadi
@ReginaMzunga
@ReginaMzunga 3 күн бұрын
Ame
@robsonmapeto1911
@robsonmapeto1911 3 күн бұрын
Ngakhale agulukunyindi aja akumati boma ndilomweli aja anena Amen nawo
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂ndiponso inu
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga 3 күн бұрын
akhare muwuzeni apage wake kafukufuku
@JacobChisoni
@JacobChisoni 3 күн бұрын
Apange lake ndi akazake.
@ChikupizgaKajawaMkandawire
@ChikupizgaKajawaMkandawire 3 күн бұрын
Inu amene simukukhutila nfi za report kapangeni lanu anthu opusa inu
1% vs 100% #beatbox #tiktok
01:10
BeatboxJCOP
Рет қаралды 67 МЛН
To Brawl AND BEYOND!
00:51
Brawl Stars
Рет қаралды 17 МЛН
人是不能做到吗?#火影忍者 #家人  #佐助
00:20
火影忍者一家
Рет қаралды 20 МЛН
ARCHBISHOP'S CHRISTMAS MESSAGE (2024)
6:54
Archdiocese of Lilongwe
Рет қаралды 1,3 М.
1% vs 100% #beatbox #tiktok
01:10
BeatboxJCOP
Рет қаралды 67 МЛН