He is talking nonsense about missing money he was the leader of the same party before he became a Vice President and was still a leader of the party until the convention so if money was missing he knows where it is because he was a leader
@HannockMesiwni2 күн бұрын
Usi ndisokoneza sozesi anatumidwa ndi MCP kuti assoneze anthu akumwera ndipo muchenjere kwambiri maboma akumwera kamba Michael usi
@jelsonmlowoka86112 күн бұрын
Nanunso Sankhani okutumani
@BORNFACESIMBOTA2 күн бұрын
Uyu ndikape
@TakalaniGlenda2 күн бұрын
Usi akulapa kuti Ananya ndalama za UTM ponena kuti iye anali leader ndiye zinapita luti? Propaganda iyi Usi
@MagieJames2 күн бұрын
Naweso mcp mmene ukumenyera anthu zigawenga zachinyengo basi
@thomasbodo40992 күн бұрын
Kodi mene ndalama zinkaberekedwa anali tsogoleli anali ndani a usi is not a leader
@petergoba42242 күн бұрын
Atibweresere anapha chilima aja then tipange za ndalamazi
@KennedyKManda2 күн бұрын
Usi ndigalu kwa basi
@BwanaliMtwiche2 күн бұрын
Usi akusitenga wundolo
@CatherineMunthali-r1f2 күн бұрын
Iyeyo ndamene anali mtsogoleri nthawi imeyo afotokoze bwino za ndalamazo ndiyeyo, kumalironso si aliyense amapita komanso amadya
@NoxiousGondwe2 күн бұрын
Kamunthu kameneka kosokonoza kwambiri kambuzi
@OscarChandema2 күн бұрын
Kuziwa kulondoloza ndalama Koma Za imfa ayi Kuba basi
@KelvenNakhalare2 күн бұрын
To be honest Usi ndi munthu osokoneza even mmasewero ake amakhala osokoneza bas
@SydneyNyasuli2 күн бұрын
Muhango yeyela kumupotoso dpp ukunama
@KennedyOManda2 күн бұрын
Manganya ali pagulu lokupha Dr chilima
@Kamwachale2 күн бұрын
Dr. Usi skungosonyeza umbuki wawo ngakhale sli Dr. Pa nthawi ya Maliro a Chilima, iwowo, a Usi anali President Cha UTM bwanji mwambo wamaliro utatha sanafunse momwe ndondomeko ya ndalama yidayendera. Izi xikusonyeza kuti a Dr. Usi sadali a UTM, nanga chawapangisa a Dr. Usi ndi chiyani kukambapo za ndalama yomwe idaperekedwa kuti iyendetse mwambo wa Maliro a chilima pa nthawi ino when he is no longer the member of UTM.
@SamuelMtambo-p1z2 күн бұрын
Kuba ndalama ndi convention ndi zosiyanatu
@TaniaMphalumo2 күн бұрын
Mwamasukatu achoti poti chilima anamalila uzaziwona panyo pako
@jelsonmlowoka86112 күн бұрын
Iwe Mzomera ulichindere wakuwa penepa apa kuti bwampini wako na dpp walikupusika bina mpoto kuti akuzenga MOMBELA UNIVERSITY 🎓 apo ukawa utesi akibanga malibwe na kugwentheska kkaguriska ku Tchayina 😢
@EvansEgra2 күн бұрын
Manganya ndi mthandizi, samangopanga ndale zopusa ai
Ati tichose boma ilii poti akuthandizeni ndi boma la DPP 😂😂😂😂 olo amalawi ali zisilu koma mpaka DPP again 😂😂😂😂 zoopya kwambiri
@MussaAli-h4i2 күн бұрын
Kkkkkk
@EvansEgra2 күн бұрын
Zisiru za Dpp angapange nchiyani? Ayiwala muja mankhwala ankasowa mu zipatala,Palibe zomwe angapange makoswe amenewo
@jaffahbattirey34232 күн бұрын
Panopa ndiye akupezeka mankhwalawo🤔
@IreenSemu2 күн бұрын
Muona chaka chamawa DPP 🎉🎉🎉🎉
@CatherineMunthali-r1f2 күн бұрын
Msewu wa chiweta nanga?
@mabvutomichaelpanagona19492 күн бұрын
Manganya ndi munthu osokoneza wa bodza ndipo ndi wa MCP
@GetrudeBanda-sd1yf2 күн бұрын
Anthu omwe akusatira usi ndi m'buli wani simalawi ndie a kutengeka malo moti asapote zika ya M'Malawi shame of yoursef
@CharlesBwino2 күн бұрын
Ulibe dzeru ukafuse lero zimenedzo
@LoyceChipwaila2 күн бұрын
Koma manganya ndi a chakwera ?🙆♂️🙆♂️
@ChibisaBanda-i1q2 күн бұрын
Ndi chitsilu
@PatrickZinenanie2 күн бұрын
Manganya machabwada ako
@emmanuelchikowi878623 сағат бұрын
Guys you are reallyserious? Unsteady kutsekulamarket ya admac at our door step then you are telling malawians that mwayamba kulima, please help us one bag of maize here in Lilongwe we are buying at 60mk per bag of 50kgs