BON KALINDO LERO PA 16 AUGUST 2024 | PHIRI LIKUDWALA LIGWA POSACHEDWA |

  Рет қаралды 21,381

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 79
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 2 ай бұрын
Eyadi .Akuphawa azipita akawruzidwwe ndi Ambuye Yesu mnkhristu..kuphatikizaponso.Inspector geneal of police Merylyn Yolamu agwere limodzi cos she is soo wicked.May God punish them all .refer Jeremiah 32 vs 26 amen
@abdullahmalinga1445
@abdullahmalinga1445 2 ай бұрын
Zikomo kwambiri ine ndimachinyadira chanel chanu chomwenso tsopano tinenetse kuti ndi chanel chenicheni cha amalawi. pitilizani kuchita support Bon Kalindo, president wa ine ndi anthu tonse osauka muno mu Malawi. ndipotu moti nawonso aja onse olemera aja nawonso akusilira kuti Bon Kalindo the D.C. Atakhalanso president wawo. Azingopemphera mwina n'kudzaterodi zikomo.😂😂😂😂😅😅😅
@MemoryLikaka-to7ho
@MemoryLikaka-to7ho 2 ай бұрын
DC ❤❤❤
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 2 ай бұрын
✊🏻✊🏻✊🏻✊🏻✊🏻 THE DC mumakwana
@bonfacemoyo5171
@bonfacemoyo5171 2 ай бұрын
We are with you
@AlexanderBilliat
@AlexanderBilliat 2 ай бұрын
Following the DC
@SostenPiyo
@SostenPiyo 2 ай бұрын
Uh uh Kodi Bon kalindo lero wasanduka wamisala,kt MCP ilowe mboma wamisalayu anatenga nawo mbalitu,mwayiwala? Okay ndiye kt nchifukwa chake zinthu zakezi zkyenda mwa misalamisala eti,ndimadabwatu, the DCccccccc more fire wina akomoka
@ChristopherChakometsa
@ChristopherChakometsa 2 ай бұрын
Tiuzeni zoona Mr DC
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 ай бұрын
The DC ❤❤❤❤❤❤ only you is best of malawi
@enerstmakochera3956
@enerstmakochera3956 2 ай бұрын
Kudos dziwe TV to keep us posted every day
@cacksygustarf6260
@cacksygustarf6260 2 ай бұрын
DC❤
@CharityChanzah
@CharityChanzah 2 ай бұрын
Always wishes de best for his motherland
@BlessingswazaDyress
@BlessingswazaDyress 2 ай бұрын
Auzen Mr DC
@EmmanuelMalata-r4j
@EmmanuelMalata-r4j 2 ай бұрын
Pangolin wathuwathu DC mufune musafune azaimabe pa chilungamo ❤❤❤
@Noel-y6t
@Noel-y6t 2 ай бұрын
Mr Kaindo plz push for Malawi to go into partnership with Russia.The EU and the West will never do good for. Africans.Plz my big brother push for this agenda it will help Malawi and Africa at large.
@JunaKananji
@JunaKananji 2 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤Dc
@ChristinaSimwaka
@ChristinaSimwaka 2 ай бұрын
Bad to be done
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 ай бұрын
DC kuswa kuswa basi❤❤❤❤
@Elson-cf1gy
@Elson-cf1gy 2 ай бұрын
D C yakuthebay osaisiyla pangila boma ililieee nd lopanda nchison menyelani ufulu m' tunthu wanu presdent wa aliyese D C❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@HafizaMussah
@HafizaMussah 2 ай бұрын
Nkadakonda phiri limenelo litakhala uyo akuzitchura kut mtsogoleriyo. I mean chakwela
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Ukufa ndiwe kalindo koma iwe kalindo ukafa ukafikila kuti ndi maboza ako wo ndi ufiti wakowo
@IssaLazack-ij1gf
@IssaLazack-ij1gf 2 ай бұрын
Wamabosa ndiwe namapwala osadulao amako
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 2 ай бұрын
Takangazani kuno tizanvere limozi
@williamdaka79
@williamdaka79 2 ай бұрын
Chikangawa out
@UremuSimon-w3w
@UremuSimon-w3w 2 ай бұрын
Nice
@IshmaelDenzo
@IshmaelDenzo 2 ай бұрын
Oyipa awa
@BakaliYassin
@BakaliYassin 2 ай бұрын
Exactly moya
@DamaliceWamalanguluko
@DamaliceWamalanguluko 2 ай бұрын
Babiloni agwesedwe kkkkk
@DeborahHetekere
@DeborahHetekere 2 ай бұрын
Zama scale pa thyolo ndizoona ndithu ine ndi mboni
@MaryKassim-vw9kv
@MaryKassim-vw9kv 2 ай бұрын
Zoona zake
@CatimboJosé
@CatimboJosé 2 ай бұрын
Th Dc
@VosterMkandawire-u8p
@VosterMkandawire-u8p 2 ай бұрын
Good speach
@blessingchimunda5639
@blessingchimunda5639 2 ай бұрын
Dziwe tv❤❤❤❤❤
@Benjamin-h4k
@Benjamin-h4k 2 ай бұрын
Koma MCP ndi yankhaza
@MosesMkandawi-e2v
@MosesMkandawi-e2v 2 ай бұрын
Zamphamvu the DC
@HendrickBanda
@HendrickBanda 2 ай бұрын
♥️♥️♥️
@BaulenichimenyayohaneYohan-n9p
@BaulenichimenyayohaneYohan-n9p 2 ай бұрын
the dc makwana timavera inu phiri rigwe basi auzeni ine bauleni watikwa chikangawayu
@PaulMalunga-i5i
@PaulMalunga-i5i 2 ай бұрын
Bwana DC...there is sense in you..simisala iyiyi....work more
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 ай бұрын
Ndipo mr chikangawa aziwa chaka chino
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o 2 ай бұрын
Chosecho umachipangira kampen ndimwe 😂😂😂😂 wamisaladi iwe
@MikeEvason-rx4qf
@MikeEvason-rx4qf 2 ай бұрын
Guys.changu D C wafika
@InnovativeSealing
@InnovativeSealing 2 ай бұрын
@phillgatoma4857
@phillgatoma4857 2 ай бұрын
Umakwanila Moya
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 ай бұрын
The DC'S mwana woooopsa kwambiri
@KelvinSamboSambo-m1q
@KelvinSamboSambo-m1q 2 ай бұрын
Zopanda tchito
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 ай бұрын
A nalibe chakudya a police akugona ndi njala ndipo zola da ndalama zo a aphuzitsa apolice ndi Ken zikhale kubera anthu ama business
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 2 ай бұрын
The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC bon kalindo 🇲🇼 ✊️
@NancyNyelenda
@NancyNyelenda 2 ай бұрын
Osafowoka osatopa the DC
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 ай бұрын
Anthu akamanena kut bon kalindo ndi mbuli ndimayesa akungomunamizila koma ndi mbuli yeniyeni
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 2 ай бұрын
Phili lake ndilitilo please tilidziwe likufuna kugwalo
@Daniel-cf4tu
@Daniel-cf4tu 2 ай бұрын
Amzanu akuthamanga pa ground inu muli busy pa social media daily Ndinunomweso mumasogolela athu kuyenda pa mseu mkumaononga zithu
@UTHMAN-WAYA
@UTHMAN-WAYA 2 ай бұрын
Sono iweyo umabwera kuzamvera iyeyu fukwa chani? 🤣🤣🤣
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 2 ай бұрын
More 🔥 The dccccccc
@LangtonJackson
@LangtonJackson 2 ай бұрын
Phiri lake ndiliti bwana??
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un 2 ай бұрын
Anthu awà afikap dzikoli tingoyigawanapo tizilamulira muzigawo atikwana hvy kuba daily
@LangtonJackson
@LangtonJackson 2 ай бұрын
Tikumva nawo.
@TamandaniMaseya
@TamandaniMaseya 2 ай бұрын
They DC
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 ай бұрын
Mandemo basi apa dziko lonse Mandemo
@joaquegerman2250
@joaquegerman2250 2 ай бұрын
Umakwana bwana dcccccc
@NeoSoko-mo2gw
@NeoSoko-mo2gw 2 ай бұрын
But why my 🇲🇼
@OjessTetezan
@OjessTetezan 2 ай бұрын
Tiimilireni bas mmakwana inuyo
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 ай бұрын
Inuyo amene musali mbuli inu ndiye mukupanga chani??fooolish!!!!
@KalongaHappyalex
@KalongaHappyalex 2 ай бұрын
¹
@FosterChakanga
@FosterChakanga 2 ай бұрын
Ine ndingoti,,,ng'oma ndatitu ng'oma osati zikhale ng'oma😂😂😂 yoliritsa siichedwa kusweka.Okumva wamva
@EphraimMajiya
@EphraimMajiya 2 ай бұрын
Kkkkk phili lomwe likugwa ndilimenelo hetiii kkkkkkk
@FosterChakanga
@FosterChakanga 2 ай бұрын
@@EphraimMajiya inu mmati?🤣🤣🤣🤣
@dysontasowana7429
@dysontasowana7429 2 ай бұрын
Hahahaha. Chamba sizinthu....
@MartinShoza-sx7lc
@MartinShoza-sx7lc 2 ай бұрын
The DC Fire mabomba 🔥🔥🔥🔥🔥
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 2 ай бұрын
Tsopano ku dpp ko kulibe anthu a ku southern region ? Tidaiwala paja Arhur Peter wamutharika ankachita tsankho.loopsya kusiyana ndi mkulu wake uja Bingu wamtharika.Him..must also quit let God in Jesus name reign us / rule Malawi nation .one who is not tribalistic and regionalisation get off peter mutharika
@PatrickMangochi
@PatrickMangochi 2 ай бұрын
Meaningless
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 2 ай бұрын
Emen my broo akumudzi kwathu
@HaroonMKWANDA-r4x
@HaroonMKWANDA-r4x 2 ай бұрын
Tangokerulani phiri lo tilidziwe
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Zaziii boza basi bola iweyo kalindo kufa tilibe nawe ntchito kambwe iwe
@GreysonLimula
@GreysonLimula 2 ай бұрын
Kape iwe osayankha sizikukukhuza
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 ай бұрын
Nkhani ukubwelezabweleza fundo ulibe bon kalindo
@MoosaSame
@MoosaSame 2 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤
@ericmuleso5570
@ericmuleso5570 2 ай бұрын
Zoona zake
KABAKO ABIKOZE KUMUKOLO GWA SWABRAH NE BOBI GIANT
8:01
BCM UGANDA
Рет қаралды 225
Он улетел, но обещал вернуться...
00:30
ПРЕМИЯ ДАРВИНА
Рет қаралды 4,8 МЛН
Mom had to stand up for the whole family!❤️😍😁
00:39
Smart Sigma Kid #funny #sigma
00:14
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 78 МЛН
Tikuferanji 17 February 2024
14:13
Edson Gunsalu
Рет қаралды 117 М.
NZE SIFERA NGAKO HAJJI MUTEBI NJAGALA KIMU JUSTICE KU MWANA WANGE
52:58
ZURAH- AYOGEDDE LWAKI BULI MUSAJJA GWAYAGALA ASIRAANA | Unveild Experience
53:47
Grezedar Jeffrey wagulidwa close to Half Billion Kwacha ndi MCP
5:58
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 63 М.
Rag'n'Bone Man - Human (Official Video)
3:18
Rag'n'Bone Man
Рет қаралды 1
MICHAEL USI WAYANKHA ZOMWE ANANENA A FELIX NJAWALA KU MZUZU.
8:04
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 27 М.
Он улетел, но обещал вернуться...
00:30
ПРЕМИЯ ДАРВИНА
Рет қаралды 4,8 МЛН