Kkkkkkkkk! Koma the DC kubweza dic kumeneku iiiii! Koma akaimva imenei samwa mazi 😂😂
@MphatsoChilewe2 ай бұрын
Kkkkkkkkk koma tiona zinthu😂😂😂😂😂 ,,The Dc tiyenazoni bwana kkkkkkk
@ShamimuBisaniАй бұрын
Ben Longwe ndye ndaninso or pajonz anali kape chsru chotheratu bolanso Amalawi ambri pajon ndi madolo kom Ben Longwe shubu weni weni kwaamene sakumudziwayo koma Ben Longwe omvesa chson
@Chipilirochinthenga2 ай бұрын
Mumatiyimilira bwana Booooon Kalindo. 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@GraceShaibu-i9dАй бұрын
🔥🔥🔥🔥
@GraceShaibu-i9dАй бұрын
Ambuye mutitsongolele pa zisakho!!!!!!
@Hannah-m2t2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 the DC motsoooooo
@JoyceBanda-k8t2 ай бұрын
Mr dc osamataya nthawi ndi chisiru ben longwe mmalawi muno tikati mphawi mwa amphawi ndi iye akati wadya wakapepha ku mcp ndiye osamalimbana ndi osowa zocita
@JacquereenPereira2 ай бұрын
Shaa mpakana horse kkkk
@JoyceBanda-k8t2 ай бұрын
First coment mumatiimilira
@MuzamiluDouglas-pf1ms2 ай бұрын
Akuti after getting drunk 😂😂😂😂
@NickUpoche2 ай бұрын
The DC timakunyadilani
@AlexNkhoma-x5q2 ай бұрын
MCP or kubela osabela km osawina chifukwa anthu ndye akuziwona mmmmmm
You was creeted to say the truth. God is still with you president.
@lizzymotika38952 ай бұрын
Koma mwanva Anamiwa
@AnnieDonda-i3s2 ай бұрын
Umatiimilila,theDC
@ElsonyamzyMajorDavid2 ай бұрын
The DC
@PrinceGodfrey-vc5vn2 ай бұрын
The D.C.
@FrankKambwani2 ай бұрын
MCP idzaberadi koma sidzawina.amalawi tilimunkwiyo oopsa kwambiri ndi nkhamza zimene akuchitadzi
@DeenesNurudMeke2 ай бұрын
Wamisala anaona nkhondo indeed
@FrankWaleke2 ай бұрын
The dcccccc😅❤❤
@KendrickLuckyc2 ай бұрын
Ulemu wanu bwana
@LotiBanda-uo5vy2 ай бұрын
Kulira kwayambira patari mpaka kuzilembera kalata kkk
@hanifahmponda87112 ай бұрын
Aaa MCP za DI ndinjila yobela ma vote koma amalawi imeneyo nde nkhondoyo chifukwa anthu ambili sasa ngalala szoti opanda ID asalembetse amalawi ndidzipani dzosutsa tikodzekela MADEMO PAKA ANTHU AMBILI ADZAMVOTE komatsotu awa a MCP kumagula anthu ku mangochi kaya amachinga zomba tingoti kumwela kotse MCP kulibe chawo ma vote anapedza chifukwa cha chilima uja
@EsetaGerate2 ай бұрын
❤❤
@JeremiahKapundu-j1p2 ай бұрын
Zoona muli pacilungamo
@Visiongaming72 ай бұрын
More fire aboniiiiiiii
@DeenesNurudMeke2 ай бұрын
Mwana oopsa kwambiri
@CeciliaMunthari2 ай бұрын
Mumatiyimira bwana ulemu wanu
@OliverPillow2 ай бұрын
Awa ndiopengadi
@MemoryLisah2 ай бұрын
Same to you thank you
@Debbie2004-x9q2 ай бұрын
Wamisala anaona nkhondo
@FanizoKawindula2 ай бұрын
Kodi anakuvotera ndi ndani kuti ukhale president wa mphawi Chisankho chake chimachitika kuti
@IbullaTaimuКүн бұрын
Ndiye ulire
@idrissaIshumail2 ай бұрын
Zoonadi
@DeborahHetekere2 ай бұрын
Koma kwachyematu
@KondwaniLungu-x5l2 ай бұрын
Kwavutilatuuu
@manaseisrael83122 ай бұрын
Mpaka kugwetsa hatchi?
@Debbie2004-x9q2 ай бұрын
@@manaseisrael8312😂😂😂eesh anthu ena ndodabwitsa 🤣🤣🙌. 🍆🐎 zoona
@YusufJames-f5f2 ай бұрын
🎉😂❤😮😅😊
@OmegaChingamuka2 ай бұрын
MCP lero anakati bambo anga ali moyo ndinakagwira dzanja kuti ankanena zoona za chapani cha MCP lero ndi izi koma pano Amalawi tachenjera sife opusa ngati manganya