Yes ndizotheka kubowoleza Mr Tipa koma vuto lomwe liri mu muzik industry yathuyu kunachuluka Timilungu tofuna kutilambira kuti zako ziyere nde Muthu ukasakha kulambira timilungu timeneto umatchukadi koma kwathawi yochepa kenako fwakalara Koma best musician ndiyemwe amasakha komaso kulora kuti maimbidwe ake afikire ka guru ka anthu ochepawo amene akukwanisa kuwafikira posalambira wina wake
@MahamudJustine-u5eАй бұрын
Uyuu wabooleza kale Siwe wekha is hit song now is on repeat
@laurencepetani8602 ай бұрын
I like this guy for his music, it touches me so hard, I was wondering where about of him but now am happy to hear that he is still doing music big up tipa boy!!!!.
@JamesALLi-m8i2 ай бұрын
Yes ndizitheka ndi big man ameneyu timakonda kwabasi
@MadaloChimaliro29 күн бұрын
Od mkaveleso nyimbo yake apa tamulandla kale uyu😊
@GiftYunusu25 күн бұрын
Baba,god is great it will be happening
@KaykMw-ql6mxАй бұрын
Nice koma wapanga chigabizo chabho moti ineso ndikubwelele kunyumba
@RiteRoderick2 ай бұрын
Kelly Kay you can't compare with Taimon Tipa, Tipa ndi machine owopsa zedi komanso got uncountable fans❤❤❤❤
@KhumboKondwaniАй бұрын
May the good Lord almighty be with you @Taimon Tipa🙏🙏❤❤ you may live long and in good health 🙏
@JaydeeAchalume2 ай бұрын
Aliyese amakhala ndichisankho inde iyeyo Ali okhozeka ndithudi chifukwa ndimaloto Ake angathe kukwanilisa inde kmso atafuna kubwelela Ku south kuthekela alinakoso nde let's go sapot fanayu apitilize missions
@annetmwechumu6687Ай бұрын
Ndizotheka I love the guy he has a talent
@ManueldevisoniDevisoni-j4kАй бұрын
Good luck to you
@MikeMbewe-c4l25 күн бұрын
Watengako gawo lake ameneyu ❤❤❤❤
@LivinessbandaАй бұрын
Ndpo ku ma show Nd gokonko waiphula amneu good musician taimon
@LovemoreLiwonde-kp4qc7 күн бұрын
Yes he will most famous in Malawi
@RiteRoderick2 ай бұрын
This guy is talented ndipo ndi makina owopsa zedi❤❤❤❤
@AngelinaJikaАй бұрын
You are the best ❤
@GraceLimani-zw7dx2 ай бұрын
Ilike this guy ayiphula ndithu ku malawi
@JosephFrank-m5fАй бұрын
Abooleza ndithu welcome again taimon tipa to Malawi musicians be free
@KondwaniMarkoBilliat2 ай бұрын
Welcome back madhala. Uyu amaika music ndipo agwesatu azibambo enawa
@LinlyMathewe14 күн бұрын
Chilichonse ndi chotheka kwa iye ndi mmene akuyimbira abooleza ndithu
@AnnieDyson-df9zeАй бұрын
Ok kodi nyamatayu anali kuno ku south Africa? Zabwino zonse nyamata oyimba modekha usasunthike koma pita chitsogolo ili ndi luso lochokera kwa yehova
@WithekReuben-u2s2 ай бұрын
Eya ndizotheka chifukwa athu akumukonda kale
@trymoo84792 ай бұрын
Don't hate him....uyu amayimba bwino 🎉🎉
@ChancyDzinkambani2 ай бұрын
Abooleza ameneyu muli mfundo za bho mu nyimbo zake ziti wina aliyese angathe kuzikonda and nabora atsogoze mulungu
@DavieOsman-tv7npАй бұрын
Taimoni amaimba bwino and I love him as an artist
@EmmanuelNtago2 ай бұрын
Taimon will make it and mpata anaupeza kale,,,space mu music industry yake ilipo kale
@JankaJafali-s9i2 ай бұрын
Aboledza ❤🎉 ndikatundu mwanayo
@NessieBandahАй бұрын
Ndipo ndizotheka akumaimba nyimbo zolimbikisa kwambili
According to my suggestion he is very important man in music than others
@LinnyMkomwa2 ай бұрын
Uyuyu ndi Dolo❤
@PrinceBlessings-bv5bs2 ай бұрын
Kukaika ndi chimo. Zitheka bora faith
@NevaMawandine26 күн бұрын
Mulungu wamwitana ndi cholinga
@HunswellJailos2 ай бұрын
Waganiza bwino. Coz nalo dziko la south Africa likadayambaso kumusaka kuti lizipindula mwa iyeyu. Zosatila zake zikadakhala ngati za Bushiri. Kuthawa mkusiya chuma dziko laweni. Tipa fire.
@HappyJohn-vw3ul2 ай бұрын
Ku Malawi ufiti basi😢😢
@patriciajangaza6752 ай бұрын
Bola asalowere Ku mipingo ya chionongekoyi ili dziko munoyi
@AngellaNtambalikaАй бұрын
Uyu ndi dolo,,tili pambuyo pake
@RAPHAELMASAMBA-nd9qk2 ай бұрын
eeeee man mwana uyu amatha ifeyo tili kulikonse komwe angapite eeeee waivera suli wekha ija waswatu
@LeonardoTitosQuiniosse2 ай бұрын
Ine ku moçambique 🇲🇿 taimon tipa amatha apeza malo chifukwa amatha kuimba za tathauzo
Mulungu sasankha ponchukila, polemelela etc ngati wachoka dziko la south africa kuti akukapanga za music basi kumalawi sanapange chiganizo chabwino akhale kuti wachokela zina osati zimenezo inde ku south ndikodula kupanga nyimbo kusiyana ndi kumalawi koma bwenzi akumangopanga record ndikutumiza basi ndi mfana wabho kwambili tipa.
@SurpriseNgobeni-k6z2 ай бұрын
Zitheka palibe so ataaa
@MosesDicostar2 ай бұрын
Walakwisa kwambiri
@fikrumokoro-u2l2 ай бұрын
Yah he can also make it,because talent is an unique
@BishopMaxwell2 ай бұрын
Uyu wabooleza kare amwene
@VincentMaluwankhata2 ай бұрын
mkulu uyu moopa kumwamba sanje siya bwino uyu amaimba sati sewelo ndipo abooleza mosakaika
@PreciousNgalande-b3d2 ай бұрын
Ali kale mu line ndi katundu taimon
@MadulaGift2 ай бұрын
Asakaike nyimbo zake zimaveka bwino kwambiri anthu amukonda
@EsetaGerate2 ай бұрын
Aboworeza lnde
@BrianAmbeswa2 ай бұрын
Ndizotheka abowoleza basi
@VictorUsen-f7d2 ай бұрын
Ndidolo uyuyu zitheka kwambirinso mosakaikila
@SamlexChimodziАй бұрын
It wos so sad kunva kut home afairs yamutenga .timakhala mu sem surbub kuno ku SA
@GeorgeJali-hs8of2 ай бұрын
He's going to make it
@RaffiqMahmoud2 ай бұрын
Aliyense amakhala ndi omusatila ake ,ndipo aliyense ndi dolo pa luso lake