No video

Dalitso Kabambe watuluka monyanyala ku DPP ndipo statement yasonyeza kale ku Chipani chomwe akupita

  Рет қаралды 13,300

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 68
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w Ай бұрын
Akuzakhala running met wa APM MUZANDISIMIKIZA IYI N MISSION mark my wards
@PharrohmagawaZimba230
@PharrohmagawaZimba230 Ай бұрын
100%
@PharrohmagawaZimba230
@PharrohmagawaZimba230 Ай бұрын
100%
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Ай бұрын
Nde runningmate azayimira chipani chanji poti ku UTM azayimira Mary Chilima
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
He is our president at UTM. Wachoka kuchipinda kupita pa seating room. UTM and DPP we are one.
@hamischikalimba6626
@hamischikalimba6626 Ай бұрын
Welcome to our beloved party UTM osaopa, osafooka osatopa SKC ndi ineyo ndi iweyo ndi ifeyo
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Akabambe amafuna uprezdent ndiye mmene inangocitika ngodzi ya kuchikagawa achilima mkutisiya mumtima mwawo.amakondwa kuti atenga uprezdent ku utm akuluwa musavutike nawo asiyeni akaimire ku utm
@thokojames5231
@thokojames5231 Ай бұрын
Musaiwale naenso anali gulu lofuna kuba chipani la kondwani nankumwa ,komanso after kuionera patali kuti sangamake pa adad basino kuthawira ku UTM KUMENEKO MPATA AKAUUPEZA ayende bwino usazabwerenso ku dpp
@jeremiahmalikebu2393
@jeremiahmalikebu2393 Ай бұрын
Dalitso was a favourite wa adad, he is the only one amene adad amamukhulupilira kuti atha kumupanga endorse. Believe me, iyiyi ndi movie ma guys wa(adad ndi Kabambe) akudziwana.
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c Ай бұрын
Mwana amalira ninkodzo wake asiyeni ayende bwino both him and others are not settled kutha kwamunthu kumeneko
@thokojames5231
@thokojames5231 Ай бұрын
Komano movie imenei zitengera kuti akupitako akakhaladi president
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Ngati watuluka muchipani cha dpp pali ndjira ziwiri zokha zimene ndingamuwuze 1 kuyambisa chipani chake. 2 asalowe chipani chilichose mumalawi. Chifukwa pali njira imozi imene ndawona kuti kumalawi kuli vuto loti anthu wosiya zipani zao ndikumalowa kwina amakhala osokoneza kwambiri komaso amakala anthu okula mutima palipose safuna kukhala opanda udindo
@SueWahna
@SueWahna Ай бұрын
Akuwoneka upule akufuna ndithu maganizo anga nduwona ngat Dpp itat yapanga alliance uyuyu afuna cholinga azakhale running mate
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Kumalawi kuyenelaso kukhala lamulo loti ngati munthu ali muchipani asatuluke ndikulowa chipani China ngati watuluka basi a siye ndale. 2025 tikupempha ku parliament kuti akachose lamulo loti 50+1 aliyese apite ndichipani chake 2025. No alliance ( mugwirizano ) Zikupangisa phokoso ziko silikuyenda bwino
@chisomokawotcha1766
@chisomokawotcha1766 Ай бұрын
Ndi running mate wa peter uyu from aliance ya utm ndi dpp kuti anthu aku dpp asadzayankhure zambiri iyi ndi plan
@bysongeorge3243
@bysongeorge3243 Ай бұрын
Ikhoza kukhala good move , tiona zambiri sitinati. Ku DPP kuli vuto komabe izi sizintha chikoka chomwe chilipo pakati pa anthu ngati tisaonenso ena akuchoka..
@PharrohmagawaZimba230
@PharrohmagawaZimba230 Ай бұрын
Guys apa pagona ndale zazikulu iye uja akatenga president ku utm azapanga alliance ndi dpp
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e Ай бұрын
Ayende bwino bola ngati machoka mwamtendele
@user-ln7ff4su2r
@user-ln7ff4su2r Ай бұрын
It is mission not kunyanyala mungopusapo
@TimothyPalira
@TimothyPalira Ай бұрын
Zitseko ndi zotseku ku utm
@lyiemax
@lyiemax Ай бұрын
We love DPP and we love UTM as well, the decision is very good and powerful than joining MCP ❤❤❤
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Bola ngati abwelera utsogoleri weniweni osati kupusisa anthu patsogolo kutembenuka hmmm
@jomochirwa
@jomochirwa Ай бұрын
Musapusitsike inu izi ndiye amati ndale zenizeni akungofuna kutipusitsa awa ,iyi ndi plan yoti dpp yonse idakhalilana pansi kuti ipangidwe ndicholinga choti utm ija ijoyiniletu ku dpp ndiye kabambe watumidwa ngati nthumwi kuchokela ku dpp kulowa utm.woooo!
@yassinn5634
@yassinn5634 Ай бұрын
Pitani ku UTM.We want energetic leaders in UTM
@leonardmalirana7423
@leonardmalirana7423 Ай бұрын
Pamene zafikapa sip
@user-nu1dj3jh7b
@user-nu1dj3jh7b Ай бұрын
Njomba zimenezo kufuna kupusitsa a Malawi 😂, adakali ku dpp komweko koma akufuna apusise wanthu apite ku utm akatero akasankhidwa kukhala president wa utm kenako azapange n'gwirizano ndi DPP ndiye ku dppko azakhala VP wa peter akatero peter azachita resign ndiyekuti kabambe azasala nkukhala president wa DPP. Izi nzomwe amadananazo achina Nankhwa aja , peter waku Thyolo, kabambe waku thyolonso.akufuna azasiilane mpando anthuwa akuziwa chomwe akuchita
@user-gp10.10
@user-gp10.10 Ай бұрын
Apa mwaganizo mozama bro,zitha kukhaladi chomcho
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Aaaa palibe ubwino wake mnzeru za alliance ife a UTM tadzidziwa ndipo tikudzidziwa takula nazo mpaka taluza president wathu palibe angavotere izi mukunena iwalani
@JamaniNyirongo
@JamaniNyirongo Ай бұрын
Pitani mmtendere anthu adyera inu. Kususukira upresident nkana mwatuluka mtawona kuti ku utm sck wamwalira
@user-pu1fy9rs3h
@user-pu1fy9rs3h Ай бұрын
Samapita ku UTM SKC alimoyo🤣
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Kkkkkk
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y Ай бұрын
Let's meet on our alliance
@Aminayaumi.in8tn
@Aminayaumi.in8tn Ай бұрын
Apa nde akufunadi kuimaliza UTm cholinga akasakhidwe kudzakhala Vice president kuti UTM itheretu iyi ndi plan
@FarookStambuli
@FarookStambuli Ай бұрын
Welcome Mr kabambe to utm
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Ай бұрын
Welcome to UTM monga ngati member chabe osati President
@paularason
@paularason Ай бұрын
Welcome to UTM Mr
@ChifundoChiwanda-ru3pg
@ChifundoChiwanda-ru3pg Ай бұрын
Ngati akufuna kupita ku UTM apite koma tione kaye performance yake Ali ku reserve bank and also ku DPP. sometimes timakhala ndi anthu oti atha kugwila ntchito bwino dziko ndikutukuka koma amalephera chifukwa sapatsidwa mpaka bwinobwino or kuwagwiritsa ntchito mosiyana ndi mbali yomwe iwowo amayiziwa and atha kupanga deliver mosavutikira if they given the necessary resources. So I believe ngati anagwirako ntchito ngati nkulu wa reserve bank nzeru zilimo, he can be useful ku dziko lathu
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Wayiwonera patali sangamake pa Apm
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Ай бұрын
Osapusisika inu uyu ndi Cousin wa APM pachi bale chawo
@PatrickMtira
@PatrickMtira Ай бұрын
Mwapusa mr mukanangokhara komweko bwezi trem inayo akanakupatsani kuti mudzaimire km apa palibe mwachita
@robertkalima874
@robertkalima874 Ай бұрын
wachita bwino kusiya chipani cha kubanja
@JasonMailos
@JasonMailos Ай бұрын
Muuzeni akalowe Ku MCP asati nyatsa
@AbdulrahimoMassamba
@AbdulrahimoMassamba Ай бұрын
A UTM musanyadire,woteroyo ngwa dyera
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d Ай бұрын
Wachita bwino akalowe UTM . Vote yanga azaipeza
@user-ru1mm7bf4p
@user-ru1mm7bf4p Ай бұрын
Wadabwitsa ndani munthu olo chipani alibe
@BrianJoe-z7u
@BrianJoe-z7u Ай бұрын
Aaaaakabambe kabambe
@user-jj1zv2rs7f
@user-jj1zv2rs7f Ай бұрын
Munalibe impact iliyonse mwainu yen Danish bwino
@user-kq6rp6hn7y
@user-kq6rp6hn7y Ай бұрын
Welcome to UTM
@user-jj1zv2rs7f
@user-jj1zv2rs7f Ай бұрын
Go well
@AndreaSignala-hk2yg
@AndreaSignala-hk2yg Ай бұрын
DPP 2025 boma muzakumbuka
@yassinn5634
@yassinn5634 Ай бұрын
Kabambe akuthawa chani ku DPP? Kapena Biden wa Malawi?
@amonfrancisautotune2073
@amonfrancisautotune2073 Ай бұрын
Kkkkkkkl😂😂
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Akuthawa chipani cha family watopa nacho
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel Ай бұрын
Zakhara bwino chipan cha banja ichi
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve Ай бұрын
Pitani ku aford basi
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Ай бұрын
Ku Dpp usogoleri kulibeko koma dyela kukakamila udindo gogo imeneija osapasako mpata achinyamata
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope Ай бұрын
Achinyamata ngati inu alepheratu
@MzadziWanga
@MzadziWanga Ай бұрын
Chakwera wapasa ndani mpata?? Mesa nae wakakamira 😅
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope Ай бұрын
@@MzadziWangaakufuna amalizitse kudya misokho ya malawi
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Ай бұрын
@@DalitsoMatope zikugwilizana bwanji usogoleri ukufunika kwa Ana chakwela so ndi wachikulire bola awa not gogo ngati Peter kabambe kuti achoke kuli vuto kumeneko uzavomereza mochedwa
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana Ай бұрын
Ali ndi tsoka ameneyo
@hamischikalimba6626
@hamischikalimba6626 Ай бұрын
Peter Mutharika sangasiye mpando once voted into power unless death takes him. So l salute that decision Kabambe has made
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Ndipo zoona Peter Munthalika sangasiye mpando wa chipani cha achimwene ake zoona
@user-nw6ie3xx8b
@user-nw6ie3xx8b Ай бұрын
Prophet liyabunya analankhula za utm Zana kuti ayigula, liyabunya is not just a prophet like others no he is Elijah of our generation, love u prophet, bless me my name is Paul kheche mvuma
@WilisonWada
@WilisonWada Ай бұрын
😂😂😂😂
@LaitoneJefitala
@LaitoneJefitala Ай бұрын
Wachita bwino alowe chipani chapamaloponse ngati catolica
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Ай бұрын
Catholic zoonadi ndi church ya pamalo pose koma mulibemo choonadi, like praying for the dead, Christmas, forgiving sins like God himself,kubatiza ana,ubatizonso wabodza,kuletsa kukwatila,kumafuna kupanga control boma pomwe church and state siziyenera kuphatikizana, kusintha sabata from surtuday to sunday,tsiku kumayamba usiku kuthanso usiku mmalo moti tsiku liziyamba kulowa kwa dzuwa kuthanso kulowa kwadzuwa ndi zina zambili bible likuti turukanimo mmenemo anthu anga babulo wagwa wagwa amayi wa a chigololo wa zonyasitsa za dziko ndipo mpingo umenewu uli ndi ana ake omwe amaitsatira zochita zakezo monga sunday keeping and all things that are out side the bible these practices are from pagan the chief of all paganism is the enemy of God called satan thanks for understanding ❤❤❤❤
黑天使遇到什么了?#short #angel #clown
00:34
Super Beauty team
Рет қаралды 42 МЛН
Кадр сыртындағы қызықтар | Келінжан
00:16
TIMES EXCLUSIVE - 22 SEPTEMBER 2018 - DR KEN ZIKHALE NG'OMA
49:07
Times 360 Malawi
Рет қаралды 21 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 232 М.