Nkasa akuyenera kulemba buku ana aziliphunzira coz uyuyu ndi legend owopsa pa music, kulemba amatha kulemba koopsa amaluka nyimbo moopsa komanso upeza nyimbo yonse kungotha ndi miyambi izizi ndizofunika zed ndie sukuluyo.
@RiteRoderick5 ай бұрын
Eeeeeeee Koma Nkasa guys eeeeee kunena chilungamo Ku Malawi kukinekoyi size yake Komanso pama Tribute onse palibeyi angafike apapa❤❤❤ kuswa kuswa umatha zedi big up❤❤❤❤❤❤
@ChristopherLaundani5 күн бұрын
Inuyo nyimbo zanu zimandilimbikitsa since I was young.ndinu mkango pa mayimbidwe & our late Thomas Chibade may his soul continue resting in eternal peace.
@MarieKadyar5 ай бұрын
Tizawakumbukilabe pakutengela❤❤❤ chomwe analinacho anthuwa km eeeh Nkasa ndikatundu🎉🎉🎉
@wilsonsawasawa37945 ай бұрын
Good composer Nkasa, best tribute to Shanil Dzimbiri
@ridsonmoffat62725 ай бұрын
A Nkasa mumatiliza 😢😢😢 with your touching songs. You're One of Our remaining legend
@stanleymollen72735 ай бұрын
Joseph Nkasa delivers
@yusufmtuwa90445 ай бұрын
Big timakunyadirani ndi luso lanu. lomwe simupikisana ndi wina aliyense, lanu lochoka kumwamba ndipo ndi lam'daliso. kip it up. May almighty keep glorifying ur way to good music.(Ameen)
@vosterchipofya3 ай бұрын
You are Powerful, ❤ Phungu Josephy Nkasa the great conquerer
@ishmaelmakwinja69125 ай бұрын
Wonderful tribute to this non vocal woman . I am sure God is happy with the soul of this mother, by staying alert of her day of death it shows she was in touch with God always. Congrants Phungu J. Nkasa.
@khadijailiyasa53155 ай бұрын
🔥 🔥 🔥 🚒 🔥 Joseph mkasa ndakatundu ❤❤❤
@Sunnygw2605 ай бұрын
It's 2024 June unforgettable month for our mother Malawi
@HamzahMiles5 ай бұрын
Legend amene tili naye pano ndinu Nkasa, Allah bless you
Thank Mr Joseph Nkasa mwabwelera mwakale kuyimba nyimbo zogwira mtima zachilimbikitso komanso zotonthoza
@MiddayDeleza5 ай бұрын
Koma yeah big man nkasa mwaliratu apa tikukupatsani ulemu imfa yosayiwalika imene ija kuphedwa ngat nkhuku zachisoni ndithu mizimu ya anthu wonse anaphedwa kuchikangawa ikuyenda be pa dziko pano Mulungu akudalitseni big man nkasa❤❤❤
@AbrahamNseula5 ай бұрын
Big up Nkasa, inuyo mumatha wakulu, mzimu wawo upitilile kuusa mu mtendere.🙏
@leffatmumba33214 ай бұрын
The ashes of your fire will rise against you... Am very confident that Lucius created more soldiers who will continue to fight for him
@daviendeleman48475 ай бұрын
Yomweyo Nkasa chikangawa yomweyo
@OlariaBanda5 ай бұрын
Big up Joseph Nkasa, poganizira zoimba tribute ya mayi athuwa, mzimu wao uziutsa mumtendere 💔💔
@DalitsoAlufeyo5 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥 more fire
@luciuszuze81975 ай бұрын
Wow, what a composition. big up Nkasa, aNadzimbiri pumani bwino.
@FysonM-hz2vx5 ай бұрын
The genius at it again 💪
@rashiddhu5 ай бұрын
What a nice tribute song, Nkasa does better always. RIP Hon Shanil Dzimbiri
@HappyNawanga5 ай бұрын
U r the machine nkasa real voice of Malawi
@ndalamaandrew5 ай бұрын
Atleast we count on you Nkasa, Lucius Banda is gone.
@SolomonMbewe5 ай бұрын
Nkasa you are just a genius... Munthuyu amatha kuimba.
@MussaZimba5 ай бұрын
Woyimba wa ineyo kumalawi ndameneyu bc ❤❤❤❤❤
@AuspiciousKalambula-hp7gj5 ай бұрын
What a best tune👏🥳
@JuniorchokaniKhanene5 ай бұрын
Uyu ndi katundu
@marynsasa17895 ай бұрын
Nkasa you are a treasure👍👍👍am a big fan
@DonTechCompanions5 ай бұрын
Legend Nkasa. Receive your flowers chief while u can smell them🎉
@PaulChaleka-lb4vx5 ай бұрын
Imfa ya Ndege ija eeeee idandiliza koopsa yationongera mtsogolo la ndale
@MakamuPhilip-vb9km5 ай бұрын
What a tribute!!! Sleep well mum always in our hearts together with 8 other💔💔💔😭😭😭
@jamespatsommboma43285 ай бұрын
My favourite artist Mphungu is always on time much respect best tribute song
@John-to8gl5 ай бұрын
Nice one Adala Nkasa 👍👍
@anthonymarcelchirwa14875 ай бұрын
No one is better at playing with words ngat Nkasa mmmh mmatha
@jjhollyland49185 ай бұрын
Thanks Joseph for this mama
@BonneynjanSosola5 ай бұрын
Nkasa umatha iweyo🎉🎉
@matchonaeddie14465 ай бұрын
this guy he doesnt play with his mind on usless thinngs ,,,,when it comes about music...... big up chief