KAMLEPO WATULUKA PA BELO | WINA WANJATIDWA |

  Рет қаралды 19,882

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 98
@MusaWilliam-t8n
@MusaWilliam-t8n 3 ай бұрын
Ikosiyo ilibe nzelu mbuzi zanthu agalu amafumu ife tili ndimayakho kale zovuta ndichani iyeyo ndi amene wachita mbolozanu pamozi ndimafumuwo
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 3 ай бұрын
Ambuye tichoseleni satana amene akuononga moyo wa anthu amalawi anthu akhazawa muwachita chani ambuye tichoseleni onse amenewo
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 3 ай бұрын
Mafumuwatu samapita kukapepesa za maliro amapita kukapempha koma njala sizinthu akulu akulu ndevu pepeya kumakagwada kwa cakwera yemwe wapha chilima amakamuudza kuti wachita bwino kupha nanga amakapepesa kuti ladzalo watani
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 3 ай бұрын
Paja anthu mtendere ndi chikondi akumachita kuwagula anthuwa kut akhale ngat akuyelesa mbiri Yao,mukudziwa inu zisankho zayandikira.kkkkk
@Kilocssreaction
@Kilocssreaction 3 ай бұрын
Nde kupha anthu mzipha koma osazuzuridwa tiyakhurabe 😂😂😂😂😂😂
@yassinn5634
@yassinn5634 3 ай бұрын
Imfatu imaoneka yophweka ikakhala kuti yagwera kubanja la ena koma ziri kwanu siungapangetu zopusazi . Ndiye anthu opeperawa azimangidwa kumene.Ngati zili ndale osamangopangitsa misonkhano muzipanga kampeni yanuyo bwanji kusiyana ndikuyalutsa maliro a munthu olemekezeka ngati malemu Chilima.
@Manyatwako-z8v
@Manyatwako-z8v 3 ай бұрын
Nkupàsa matama chakwera zopusa izi kutaya Moyo akuona ngat masewera haaaa amudziwe yesu ndi ophunzira ake
@GabiBanda-r3o
@GabiBanda-r3o 3 ай бұрын
Inuso aku MBC mulibe ndidzeru zomwe agaru inu
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 3 ай бұрын
Mukungu akupasani chilango posachedwapa muona inuyo ameen
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 ай бұрын
Zaziii osatchula zina lamulungu pa zinthu zanyasi ngati izi mukungotengelapo machimo chabe zinazi zikubwelelani nokha muzisamala mayankhulidwe osangotengela zopusazi muzazindikila 2 lent musatchule dzila la mulungu pachabe zitukwanani koma musathule dzina lamungu, mulungu samamva pemphero lanulo zikomo
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 3 ай бұрын
Anagwetsa ndenge, Osati ndenge inagwa ayi, Chakwera ndi chimwendo,Banda ndi amene adapha Chilima, apólice aku wophyseza chani?mbolo za Manu,nyini za Manu nonse apólice nonse amene muku lowerera zimenezi muku zowona ngati ndinu ndani? amene aphedwa aja muku wona ngati samafuna Moyo M uku wona ngati A Malawi saku ziwa zimene zida chitika mukhale phee, muone.Popeza okupha ndilu panga nayenso azafa ndilu panga u, will see what it gonna happen to Chakwera one day masiku amatha nkugona
@DennisDonework
@DennisDonework 3 ай бұрын
Ingotiphani tose palibe umboni olondola omwe mungatiuze zokhuza ngoni ndinthawi yanu kuweluza ndikwa YEHOVA Kwinaku tizuzayenda door to door. Kumuzi kwanduna kuotcha
@SamuelMsyali
@SamuelMsyali 3 ай бұрын
Inkosi yopusa iyi, basi kupita kukapepesa muthu okupha chakwera,
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 ай бұрын
Matondo yinu kalaya
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 3 ай бұрын
Kodi pamenepa pakati pa awa mafumuwa ndi Chakwera, ndindani yemwe amayenera kupepetsa mzake popedza ndi a Malawi omwe aludza vuto mafumu nawo kaya kuchita maintain maudindo kaya, popedza ngakhale president akhale wankhanza amangoti ife tikugwira ntchito ndiinu a president malo modzudzula
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 3 ай бұрын
Mafumu dyera inu....bwanji osakapepesa mabanja oferedwa?
@isaaczuze
@isaaczuze 3 ай бұрын
Boma la anthu oyipa kwambili koma amalawi tiyeni tigwilizane ...izi zisapitilile .chakwera walephela kutumikira amalawi ...chakwera ndi munthu wokuba koopsa
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 3 ай бұрын
Iweso mumberwa ise kuno ku mupoto tiku nkhumba tiji usenge tenkha kuno ku mupoto Andi ufumu wakwa jereman mahowe tiku nkhumba ukhale munyumba yeneko uyo wakwendeska ufumu wakwa jereman mahowe ngwake yai wenecho walipo ,l Mwenecho ni Onenti mahowe tiku nkhumba mutivwile watole ufumu wakr
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 3 ай бұрын
MCP adapha chilima 😢😢😢
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 3 ай бұрын
Ziko likauamba kumanga mubusa muziwe kuti muzikomo mazuzo akhala ambiri. Ndipo amalawi tikhala pamavuto ngati zochita zathu sitiganiza. Zimene zikubwera kumalawi ndi zakale ziko sopano likusintha zimezi tiziziwa. Mutsogoleri wabwino samanga anthu akuopa chani kuti azimanga anthu. Zikuonesa kuopseza anthu mwina chilipo chimene akufuna kuti chiziwike. Ngati palibe chimene adachita amasule anthu tisavutane ndife amalawi tose.
@Blessingsseleman-d4x
@Blessingsseleman-d4x 3 ай бұрын
kod mukuti zaboza inuyo zenzen mukuziziwa ?
@DouglasDazuKamwendo
@DouglasDazuKamwendo 3 ай бұрын
Dziwe TV usamabweretse nkhani zapa MBC ife sitizifuna kapena ukuona ngati tilibe ma tv?
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 3 ай бұрын
A Mberwa mwaganiza bwanji?
@LiamChitsulo
@LiamChitsulo 3 ай бұрын
Km abale akumangani kkkk
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k 3 ай бұрын
Mafumu adyela
@rabsonswathera738
@rabsonswathera738 3 ай бұрын
Chakwela wapha 10 people including lasambara
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 3 ай бұрын
Mumanga anthu angati agwape inu😂😂😂
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 ай бұрын
Ifetu sitikumufuna mwina mafumu omwewo zaziiii,
@ChristopherKawilam
@ChristopherKawilam 3 ай бұрын
Nde mumanga anthu angati???
@LamieTiger
@LamieTiger 3 ай бұрын
Tsogoleri ndekut Chan mudzingot mfit chakwera
@samsonyuda674
@samsonyuda674 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂 Koma kulowa anthu ambili nditu
@JosephNgona-f9v
@JosephNgona-f9v 3 ай бұрын
Zikundithera data yanga zaziii
@HaroonMaundala-lg5lg
@HaroonMaundala-lg5lg 3 ай бұрын
Komatu nde mutimanga athu ambilitu. Kodi mukufuna tisamalankhule tikamawona zompusa zikuchitika? Sono ufulu omwe mukumawuntchulawu nde ndiwutiwo? Aaaaaaa ifetu zompusa zanuzo tatopa nazo. Pa mtumbo panu achakwela mwava.
@DennisDonework
@DennisDonework 3 ай бұрын
Chipepesocho munakwpita kwa mawanja omwe anataya achibale awo not ku BOMA MWAMVA AGALU INU MAFUMU OPEPELA MUMAKAPEMPHA INU
@Gift-kc6fd
@Gift-kc6fd 3 ай бұрын
Magazi anu fultseck mitumbo yanu
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 3 ай бұрын
Inu ifeyo mumatitenga ngati ma blind?
@MussahIman-cw1cu
@MussahIman-cw1cu 3 ай бұрын
Na pokhapo poti tivomeleze zosatira zakafukufuku ameneyi zikabwera zaoneseratu kuti yakho walidziwa iweyo wa mcp ndipo losiysna ndizoona za ngoziija
@ClementSakala-s2k
@ClementSakala-s2k 3 ай бұрын
MCP kumanga anthu nde mumathatu koma kuyendetsa bwino boma ng'oooo mudziona ndipo tsimukwanitsa kumanga anthu zikupwetekanidi anthu ayankhula
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l 3 ай бұрын
Mafumu adyera apatsidwa ndalama kuti azipusitsa anthu chakwera anapha mafumu wopusa agulitsa anthu awo anthu aku German abwerao azikasaka kunyumba Kwa chakwera ife zoona tikuzidziwa tonse mu dziko la malawi
@BwanaGD
@BwanaGD 3 ай бұрын
Osamanga bwanji mafumuwo kuti mukudzapepesa zichani
@HarryChindiwo
@HarryChindiwo 3 ай бұрын
Mfumu zopusa
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 3 ай бұрын
Ngati uli umphawi pezani zochita plz musapezele pa ifa yachilima plz
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw 3 ай бұрын
Ndeno kalindo bwanji simunapite nayo ku court?
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 3 ай бұрын
Mmmmmm
@mrsmoseskita9180
@mrsmoseskita9180 3 ай бұрын
Nyau mbc kuyankhula za kutumbo kwa boma
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 3 ай бұрын
Koma ndiponso abale inu, m'malo mokapepesa kwa akubanja la Chilima mukukapepesa boma palibe chanzeru tu apa
@EllenPhiri-xt8pt
@EllenPhiri-xt8pt 3 ай бұрын
Manyi Ake chakwela anampha anthu osalakwa basi azitipusisa ife amalawi fumu inabwelayo anayipasa ndalama kuti izayakhule manyio
@LinahNgulube
@LinahNgulube 3 ай бұрын
Kwa chakwela mkataniko,kupusa kokha basi
@LukaMutikitha
@LukaMutikitha 3 ай бұрын
Lazarus Chakwera ndi nduna zake mwatiphera Saulos Chilima ndi anthu ena 8 Osatiwopseza inu a Satan
@babranzima8120
@babranzima8120 3 ай бұрын
Mafumu kumzimba ndizisiru zimakonda ndalama
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 3 ай бұрын
Mmalo mokapepesa kwa family ya chilima inu busy mukukapepesa kwina
@GeofflyDyton
@GeofflyDyton 3 ай бұрын
MBC 😂😂😂😂 sewelo
@JosephNgona-f9v
@JosephNgona-f9v 3 ай бұрын
Zaziii zopusa basi akadauloakeanthu a mcp wa ife tidzaonana mu 2025
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 3 ай бұрын
Misala mafumu , agalu pamodzi ndi chakwera
@DumisaniMhango-e4i
@DumisaniMhango-e4i 3 ай бұрын
Aaah
@MarvGerald
@MarvGerald 3 ай бұрын
Ife mbc tinaitaya kalekale tilibe nayo chikhulupiliro. Izi muzimvera gulu la Azikhale ng'oma uku mutamenyeka majeket aana
@LamieTiger
@LamieTiger 3 ай бұрын
Chakwera unapha chilima ukane usakane ndanena ndanena
@MahallaMinistries-fv1hw
@MahallaMinistries-fv1hw 3 ай бұрын
Oorumiwa, anerollumiwa.
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 3 ай бұрын
Mafumu opusa amenewo abulutu😡
@FosterChakanga
@FosterChakanga 3 ай бұрын
Police ya Malawi kuchita kunyadila kumanga munthu😂😂😂😂
@HarryChindiwo
@HarryChindiwo 3 ай бұрын
Anamachendewa
@MsondaBanda
@MsondaBanda 3 ай бұрын
Kutuka vilekeke ,
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 3 ай бұрын
Aaaa KOMA MCP MUKAFIKA NADZO KUTI KUMANGA ANTHU NGATI TILI MUULAMULILO WACHIPA iiiii koma muchoja 2025 chifukwa anthu amawona ngati mwatsintha ena mawona ngati zabodza police yatsanduka chida cha MCP tabwelelatso kuchipani chimodzi iiiii MULUNGU ALOWRLELEPO IFE TACHEPA NADZO
@BrightZionga
@BrightZionga 3 ай бұрын
Foseki chakwera waluzapo chani useless
@TalazanGamah
@TalazanGamah 3 ай бұрын
Chakwera u also stulpd
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 ай бұрын
Ose ofalisa nkhani za boza social media amangidwe akutiwonongela dziko pamalilo sipotengelapo mwayi wa ma vote ayi
@GilbertKuchipinda
@GilbertKuchipinda 3 ай бұрын
😢
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 3 ай бұрын
Iwe tachoka apa kod inuyo mulungu ndemene angakulengeni ndithudi mulungu akukantheni nonsenu ndipo khwiyo wa mulungu upite kwa inuyo ndiposo akutembeleleni nonsenu mwamva
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 ай бұрын
@@AndersonBishop-i2t ine sindiweluza munthu chifukwa ineso ndizaweluzidwa sindikuziwa kanthu ngati mulindi umboni bwanji osapita live ngati mukuziwa kanthu zotukwana zikupibdulilani chani mumangidwe basi mukapelekele umboni uko mesa mumaziva kudoda or mwina munapha ndinu ndiye mukuthamangila kutukwana kutiseka kumaso kuti tisaziwe mukhaula tuuu inu mavoti simungawapeze pa socal media or mutatukwana motani mulalo mogwilana manja tizilila pamozi mwalusatu kuposaso enuwake amalilo koma inu nde yaa muzitolele
@Peterchirwa-tf1ox
@Peterchirwa-tf1ox 3 ай бұрын
Ikosi ndiwe mbudzi yamutha,
@MoosaDawood-l5c
@MoosaDawood-l5c 3 ай бұрын
Mcp Athenian anthu aku mpoto chifukwa chodana ndi udf.Anthu akumpoto ndiako uku amafuna kukhala anzeru
@IdrissahChuma
@IdrissahChuma 3 ай бұрын
Dzaziiiii zomwe akupanga ma gyz awawa akuona ngati li mu one party system koma mukunama gyz
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 3 ай бұрын
Maimkosiwo amakapempha osati kukapepesa njalayitu siilibwino
@isaaczuze
@isaaczuze 3 ай бұрын
Koma abale zikoli likolowela kuti ...koma chakwera analidi mmbusa kapena anangobilasalako ku ubusa. ...Achakwera ndi munthu womvesa chisoni kwambili....... Kuba ndalama za misonkho ya anthu ... Kumanga anthu popanda zifukwa zenizeni komanso corruption
@StiveKantiki
@StiveKantiki 3 ай бұрын
Mungosegula ma post offices tibwelele mwa kale 😂😂😂😂
@funnynyirendafunny7888
@funnynyirendafunny7888 3 ай бұрын
Mkadaziwa kuti mulungu salanga nthawi yomweyo bwezi zinazi mtangizisiya . Mzayaluka nazo mafumu opepera Inu . Koma ziwani kuti, ngati mnagworapo bible mmanja mwanu dikirani chiweluzo choophya kwainu agalu opanda nzelu . Kufa nzanu kwakupangisani kuti mtumbwe nkhalani pompo mulungu si galuwanu amene mmayenda nayoyo ai
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 3 ай бұрын
Iweso mumberwa ise kuno ku mupoto tiku nkhumba tiji usenge tenkha kuno ku mupoto Andi ufumu wakwa jereman mahowe tiku nkhumba ukhale munyumba yeneko uyo wakwendeska ufumu wakwa jereman mahowe ngwake yai wenecho walipo ,l Mwenecho ni Onenti mahowe tiku nkhumba mutivwile watole ufumu wakr
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k 3 ай бұрын
Mafumu athu alelowa chinyengo amakonda za chinyengo zisilu
@KassimIssa-bn3od
@KassimIssa-bn3od 3 ай бұрын
Kd lediyo imenei ikugwilisidwa njito ndi chakwela eti zachamba bac
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 ай бұрын
Chakwela you mast go Galu
@YotamKamanga-p8x
@YotamKamanga-p8x 3 ай бұрын
Rekan kukaka wanthu wambula kwananga ndalama izo wanthu wakuzirekatu 😅😅😅😅
@HassanSinoya-wl3vl
@HassanSinoya-wl3vl 3 ай бұрын
Ikhodzi alibe zelu mbuzi zokhazokha
@GraciousGIbbu
@GraciousGIbbu 3 ай бұрын
Mwadya ndalama zingati mafumu???
@UmaliIshmael
@UmaliIshmael 3 ай бұрын
Mwayamba kudya ndalama zakuba
@SamuelMsyali
@SamuelMsyali 3 ай бұрын
Stupid radio
@HarrisonKalonga-k7p
@HarrisonKalonga-k7p 3 ай бұрын
Paja mafumu akumalawi ndimakape amalamba president olo azipanga zopoila
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 3 ай бұрын
Mbudzi inkosi
@BrightZionga
@BrightZionga 3 ай бұрын
Ingomangani onse amene ali otsutsa mutsale a MCP nokha foseki zanu
@CatherineKumwex
@CatherineKumwex 3 ай бұрын
Thank you our inkosi m'mberwa for respect god bless you
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu 3 ай бұрын
Osamangomanga anthu zachamba et anthu ot munapha ndinu agalu lni
@victorauwana7258
@victorauwana7258 3 ай бұрын
Mumanga anthu angat?
@GodwinJafali
@GodwinJafali 3 ай бұрын
Worthless leaders
@BIZIWECKTIMOTHY
@BIZIWECKTIMOTHY 3 ай бұрын
dziwerv
@AllenBanda
@AllenBanda 3 ай бұрын
Only God nows
@TalazanGamah
@TalazanGamah 3 ай бұрын
We follow
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 3 ай бұрын
Mashende inu
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 3 ай бұрын
Mavuto alipo ku Nyasaland
Channels Television - Live Stream
Channels Television
Рет қаралды 658
LIVE NEWS: LiveNOW FOX 24/7 LIVE STREAM
LiveNOW from FOX
Рет қаралды 940
An Unknown Ending💪
00:49
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 55 МЛН
Шок. Никокадо Авокадо похудел на 110 кг
00:44
Cute
00:16
Oyuncak Avı
Рет қаралды 12 МЛН
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 39 М.
Oyimba Akugulidwa Ndi MCP
6:22
Sam Malvitha
Рет қаралды 29 М.
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Senior Prophet Rodrick Mtupa SC
Рет қаралды 43 М.
Times Exclusive featuring Thomson Mpinganjira - 3 February 2024
1:07:40
Times 360 Malawi
Рет қаралды 154 М.
Amalawi tidzameta maliro a Chilima 2025
7:57
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 54 М.
ANTHU AYANKHULA ZOSAOPA AWA 🙌🙌🙌
27:38
HOT 265
Рет қаралды 104 М.