Kodi A Nankhumwa Akulowela Kuti - Richard Mphepo

  Рет қаралды 43,578

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

3 ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Richard Mphepo discusses rumours that Hon Kondwani Nankhumwa is about to register his own political party, the People's Development Party (PDP).
Pa Nyasa VoiceBox, Richard Mphepo akukambirana za mphekesera zoti Hon Kondwani Nankhumwa atsala pang'ono kulembetsa chipani chawo cha ndale cha People's Development Party (PDP).
#malawi

Пікірлер: 112
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 2 ай бұрын
Morning Sir,May God bless you,mawu and overall bwino ndi ogwira mtima kwambiri,ndinakakonda komwe alike once azitsogoleri average zimezi,thanks Sir,this like bomb, oooh what a wisdom words.
@GeorgeClement-bg6to
@GeorgeClement-bg6to 2 ай бұрын
⁰😊
@user-lx9yn1ru9i
@user-lx9yn1ru9i 2 ай бұрын
Mr Mphepo let me thank you for the motivation talk you made.
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 2 ай бұрын
The best analyser ever since, proud of you Bwana Richard Mphepo
@user-je9sz4zg7o
@user-je9sz4zg7o 2 ай бұрын
Amen Amen for the well dignified speech God is the best fighter he can't allow His images to cry with hunger , poverty , rising of commodities, Kwacha devaluation, violence and telling lies of developments ,,, Carry your vote inside yourself
@maxwellmakocha3039
@maxwellmakocha3039 2 ай бұрын
May God bless you my brother for sharing the words of power
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x 2 ай бұрын
Zoona oopa Mulungu ngati peter my vote❤
@user-yk4by8iy8k
@user-yk4by8iy8k Ай бұрын
Apm my vote
@richardbanda9997
@richardbanda9997 2 ай бұрын
Thanks bwana Mphepo. Funso n'kumati tsopano akapha opposition dziko lidziyenda bwanji? Zirzonse yes bwana ngakhale tikupita kuphompho?
@user-nt9qh8li9w
@user-nt9qh8li9w 2 ай бұрын
Peter ndisogoleli osamagwidwa ndi mulungu kut awatumikile wathu with hole heart anaunikira patali pomwe enafe tinaweluza kuti walakwitsa God bless him
@richardnyasulu8790
@richardnyasulu8790 2 ай бұрын
Amphepo tsumukudziwa Anankhumwa apopo chomene ayambila chipanichi nachi, agwirizana anthu amenewa kunena kuti chawo Anankhumwa chizaphatikizane ndi Cha MCP ngati alliance ndekuti azapeze anthu ochuluka kumwera chifukwa Cha Anankhumwa, makamaka ku mlanje, Tholo. Nkhani ndiimeneyitu ngati sumukuziwa ine nadziona kale. Nankhumwa ndiwa MCP mu indirect, apala plans yoti angazasokonedze bwanji ku chigawo Cha kumwera. Nankhumwa amuletsera Dala a MCP ku laws panopa chifukwa Cha chimenechi.
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 2 ай бұрын
True
@user-yu9uj9rk6m
@user-yu9uj9rk6m 2 ай бұрын
Siyani kumagoganiza zinthu muzifufuza
@fanie6913
@fanie6913 2 ай бұрын
Mukukanikanso kulemba bwinobwino chichewa 🤷‍♀️🤷‍♀️🤷‍♀️🤷‍♀️
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 2 ай бұрын
@@fanie6913 Bola wamva
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Ndipo izi ndizoona zokhazokha alliance zikhala kutsogolo ko
@user-pl6it7zc7c
@user-pl6it7zc7c Ай бұрын
iwe Ndiye sudziwa kanthu PA democracy and kukhala president dziko litha basi
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 2 ай бұрын
Kkkkkkk plani idatchoka thanks brother
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 2 ай бұрын
True Malawi is on a very big problems because of Chakwera
@user-uv1vu6ub5o
@user-uv1vu6ub5o 2 ай бұрын
Bwelera
@StanziaElias
@StanziaElias Ай бұрын
Kkkkkkk anankhumwa zoti mungalamulile dzikoli muyiwale
@user-nl5nk2wx1q
@user-nl5nk2wx1q 2 ай бұрын
APM IS MY 2025 VOTE 🎉
@augustMag
@augustMag 2 ай бұрын
Mulungu si James Anankhumwa samadziwa kuti prophcer Athor Peter Muthalika si munthu wamba ndimunthu oti simungamumvese kaganizidwe Ambuye pitilizani ku muteteza Peter Muthalika ndi nzeru zomwe munawapatsa 🙏
@monicatambala5615
@monicatambala5615 2 ай бұрын
If they want to make their own party let them do so , they were chased out of the party
@sheila5812
@sheila5812 2 ай бұрын
Dzinalo ngati Dpp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 2 ай бұрын
Nankhumwa ndiosokonza ndipo kwathu stikumuvotela ndoipa
@PatrickChirwa-cv5cd
@PatrickChirwa-cv5cd 2 ай бұрын
A Richard Mphepo muzikachongetsa ma Audio anu kwa abambo anu a Francis Mphepo. Kulikonse komwe mtsogoleri wakale akufuna kubwerera pa mpando chipani chake chimasokonera. Yang'anani UDF kwathu kuno inatha ngati makani chifukwa cha 3rd term. UNIP, MMD, now PF ku Zambia zinatha chifukwa Kaunda, Rupiah Banda, ndi Edgar Lungu anafuna kubwerera pa Mpando.
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 2 ай бұрын
Anali pa mission yoopsa not knowing God is greater than their plans ✌🏾
@user-rk3gq7gd8f
@user-rk3gq7gd8f 2 ай бұрын
Well done abwana awuzeni zona
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k Ай бұрын
AMEN.
@DiscipleMleya
@DiscipleMleya 2 ай бұрын
@Richard Mphepo pitani ku times exclusive interview
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Azamuvotera amake ndi ana ake sua
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 2 ай бұрын
Amen
@user-kb7gw3tu7r
@user-kb7gw3tu7r 2 ай бұрын
NDIPO MULUNGU akumva kulira Kwa a Malawi professor Auther Peter muthalika it's my vote munthu owopa MULUNGU
@VincentNyabanga-zm8fm
@VincentNyabanga-zm8fm 2 ай бұрын
APM my vote
@StanziaElias
@StanziaElias Ай бұрын
A P M my vote ❤❤❤
@MemoryKamanga-pu1tj
@MemoryKamanga-pu1tj 2 ай бұрын
Musiyeni Nankhumwa ufulu ndi wake ndiwoloredwa kuyambitsa chiyani mukachedwe kukamba za anzanu a Dpp muphoyilaso after all 50+1 mwachepa nayo a Dpp.😂😂😂
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 ай бұрын
Ameen❤❤❤❤
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 2 ай бұрын
Ndipo kubwela kuli kwa yehova ndipo 😢😢 mulungu ave kulila kwathu mulungu akhale nanu blother
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 2 ай бұрын
Ndipo pephelo la ndikulilila Malawi kuti mulungu atipatse m,tsogoleli owopa mulungu
@user-uu7ni4ex6b
@user-uu7ni4ex6b 2 ай бұрын
Ndale nzomvetsa chisoni.Akungoganizira za ubwino wao wokha osati mtundu wonsewa a Malawi.
@estherkauyange6548
@estherkauyange6548 2 ай бұрын
APM MY VOTE
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 2 ай бұрын
Akufuna kuti azigogo azikafoyila malo mozotela dpp azikavotela pdp bwanji akanasankha dzina Lina zopusa zimenezi amalawi tisamapusisike ndi pakamwa pa munthu dpp ndi chipani chomwe chili chothekela kupulumusa ife tonse amalawi
@user-qx3dd7xt9c
@user-qx3dd7xt9c 2 ай бұрын
Machine
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 2 ай бұрын
Nankhumwa watha po basi
@user-yn9ky7gj7v
@user-yn9ky7gj7v Ай бұрын
Dpp my vote anankhumwa manyazi akugwileni mulungu akukantheni sure
@thokoJames-gp8mk
@thokoJames-gp8mk 2 ай бұрын
kondwani nankumwa zamukanina kuba chipani ndiopepera
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t 2 ай бұрын
Ambuye akudalitseni
@user-lv9vf6rf8r
@user-lv9vf6rf8r 2 ай бұрын
Ankhumwa akufuna kutisocheretsa ndipo tazindikira kuti iwowa ndiwosakhwima munzeru tiyeni tiwasiye adzayirira DPP kutsogoloku.
@user-xb5rf2vd6h
@user-xb5rf2vd6h 2 ай бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉
@user-yz5bq8rj9w
@user-yz5bq8rj9w 2 ай бұрын
Koma bvuto ndi A Namkhumwa akuwoneka kuti Ali ndi dyela. La utsogoleli chifukwa ambili tinakhumudwa 4 years ya opostion sanawonetse kutikonda amalawi
@monicatambala5615
@monicatambala5615 2 ай бұрын
Continue being disappointed , all the best in your journey of being disappointed
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Big up Mr mphepo mwayankhula Zomveka God is in control.. 🔥🔥🔥Nankhumwa zamuvuta phuma.
@patricgama4788
@patricgama4788 2 ай бұрын
apange dzina lina osati pdp akufuna ku putsitsa athu aziti dpp chifukwa dzikufana
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 2 ай бұрын
Munthu ali ndi ufulu kuyambisa chipani chake inu vuto lanu ndi chiyani mnachosa mchipani ndiye lelo chavuta ndichiyani
@chifundonkhoma-uv4bw
@chifundonkhoma-uv4bw 2 ай бұрын
DPP because of it's greedness,has dumped Nankhumwa who will divide the votes giving rise to further downfall of DPP.....zofuna,dyera andale opusa kwambiri,tikhala tikuzuzika ndi MCP......
@wysonkomela8223
@wysonkomela8223 2 ай бұрын
Mwayakhula dzokhuza kwambili moyo uli mavuto ife mulungu akudalisen bg
@user-cl4lh5zx9f
@user-cl4lh5zx9f 2 ай бұрын
Machine opangila anzake
@user-yn9ky7gj7v
@user-yn9ky7gj7v Ай бұрын
Ankhonthi nawo akungovomereza tizipani tochokera ntoilet bwanji
@user-us5hw4uy3t
@user-us5hw4uy3t 2 ай бұрын
Vote ndi plus one aise not subtract
@PeterNagoli
@PeterNagoli 2 ай бұрын
Papita Njere Mpeni Upita pomwepo Bingu Analamulira Atachoka Mu UDF Joyce Banda Analamulira Atachachoka Mu DPP Why Nankhumwa Kukhala leader Of opposition Atachotsedwa Mu DPP Sikuti Nankhumwayo Ndiwabwino Koma Kukumbutsana Mmenetayendera
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 2 ай бұрын
😂😂😂😂kutha kwa Nankhumwa ,mufunseni BJ zomwe anaziona
@user-dn6eg1xk7f
@user-dn6eg1xk7f 2 ай бұрын
zoona mani
@PatrickKazilala-cb4cl
@PatrickKazilala-cb4cl 2 ай бұрын
Komwe akulowerako
@josephmanyenje7107
@josephmanyenje7107 2 ай бұрын
Mmmmm wachinyamata aliyense osokoneza sazapambana
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Ай бұрын
Zimene mwakonza zichiteni koma mwachangu kuyankhula Kwa zitsilu
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp 2 ай бұрын
aaaa apa tasemphana maganizo pakufunika ifenso tidzibweza osaopa tisapuse
@user-sw8bb3iz7x
@user-sw8bb3iz7x 2 ай бұрын
Mumakwana inuyo.
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 2 ай бұрын
Man mlunje,thyolo, kuti kume nakhumwa adzapedze mavote,Anthony amaboma amenewa siziitsilu aai.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
APM for President basi ,
@PatriciaChikusa
@PatriciaChikusa 2 ай бұрын
😂😂wasowa zochita
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c 2 ай бұрын
APM my zoona zache iyeyo nawa mcp ati kalero aziti pdp apanga gwirizano nankhumwa George malemia ni chakwera wache
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 ай бұрын
Powerful enough ❤❤
@thokoJames-gp8mk
@thokoJames-gp8mk 2 ай бұрын
13:04
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 2 ай бұрын
Koma Pena zikumadabwetsa ndizoti omenyela ufulu ose kungokhala alomwe okha okha zosaendatu
@rashyklaas3930
@rashyklaas3930 2 ай бұрын
atayeeni awa akuyendetsa galimoto yopanda nyali dp achotse ayike logo yawo by
@user-px6kt8rx2p
@user-px6kt8rx2p 2 ай бұрын
Mwalira mokwana koma mtunda udakali mudathetsa banja ndi anthu mofulumira kozi boma lili ngati mamuna pamene anthu ali ngati mkazi bawasiyani amuna azanu nawo abelekemo, koseko kodi ndikupsa mtima ndi mimba ya azanu? K kkkkkk bapumani tinveko azanu
@user-yn9ky7gj7v
@user-yn9ky7gj7v Ай бұрын
Mulungu ayima ndi dpp
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 2 ай бұрын
Onse omwe akuti Adad sadzawina, ng'o munya. Inu ndi mulungu? Mukakolopa mu Nyanja muona, asatana inu.
@user-sw8bb3iz7x
@user-sw8bb3iz7x 2 ай бұрын
A kondwani zawavuta basi, anzawo awathawa
@user-nc4vi1jt5g
@user-nc4vi1jt5g 2 ай бұрын
Pantumbopako mphepo uonangati ulindizelu mboloyako udziuza amako
@MemoryKamanga-pu1tj
@MemoryKamanga-pu1tj 2 ай бұрын
Koma nkhonya yobwezela imawawadi alira mokweza a Dpp
@KhobasMaseko-yl2nw
@KhobasMaseko-yl2nw 2 ай бұрын
dpp mka sintha madala awo mzawina koma adadi anuwo sangawine boma chipani sichikhala cha nyumba
@user-or8cc5nu4c
@user-or8cc5nu4c 2 ай бұрын
Mwalankhula bwino kwambiri
@user-pl6it7zc7c
@user-pl6it7zc7c Ай бұрын
Dpp ikadapanga conversion bwezi itawina now I'm challenge you Dpp I kuonongeka coz amachitenga ngat family party. ask udf right now zidatha bwanji wait Dpp continue to finish
@chisomochavula
@chisomochavula 2 ай бұрын
Apm my vote DPP 🔥🔥🔥
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 2 ай бұрын
Mfundo zoveka ulemu wanu
@LingtonChimutu
@LingtonChimutu 2 ай бұрын
Chipanichi mukupha mwadara zawonetsa apap
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 2 ай бұрын
Malawi kuli ndale zausiro
@petermsamariamapira8933
@petermsamariamapira8933 2 ай бұрын
Kulankhula komveka bwino ,ulemu wanu
@user-bq5ev7de1l
@user-bq5ev7de1l 2 ай бұрын
Apm my vote ✊
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 2 ай бұрын
timaona ngati mwalondola a munolo
@mchipengule
@mchipengule 2 ай бұрын
A Dpp Kuba bwanji? Mukufuna muzikamubelanso Petër Muthalika? Sipaja mumamubela macard kumagula cement? Peter ndiokalamba musiyeni ause mu mtendere ku Mangochi ameneyu. Mbava inu a Dpp. Munawononga dziko inu agalu Inu!!!
@MasegoModukanele-xg2hj
@MasegoModukanele-xg2hj 2 ай бұрын
Ndingo chitilako ndamanga pa kumenyana zimenezo ndizoona sizabwino mayiko khondo zimayambika zifukwa zake zomwezo ndipo khondo imazuzitsa athu odzikhalola dziko lathu ndila mtendele ngakhale titamenyana palibe tingapindule andalewa tiueni tiwasiye amamwela tiyi lodzi
@stevienmlambala9875
@stevienmlambala9875 2 ай бұрын
anankhumwa amafunadi kugulisa chipan zoona anamtulukira mwachangu DPP ikubwelrra m'boma 2025 mulungu kunali kutiphusitsa amalawi kut tizindikile kut adale achulukawa nd business osati kuzathandiza amalawi ayi
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 2 ай бұрын
Nankhumwa my vote from mulanje,nankhumwa woyeeeee 2025 boma😅😅😅😅😅😅😅
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 2 ай бұрын
Manyaka amunthu ,pamenepo watha bas
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga 2 ай бұрын
galu lwe usatinyasepo ndi DPP yakoyo nyasi lfe ayi
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 2 ай бұрын
Zotukwana ayi
@user-cd6db5qb4l
@user-cd6db5qb4l 2 ай бұрын
Nanunso ndachisilu mudzi ya munthu pusi
@user-uu9pv6jd4v
@user-uu9pv6jd4v 2 ай бұрын
Waste of time bro anthu amavotera tambala note chakwera ku dedza bwaaaa
@FatsaSalimwaka
@FatsaSalimwaka 2 ай бұрын
Nsonda galu wamunthu
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 2 ай бұрын
Ndipo adzaona nyekhwe
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 2 ай бұрын
Iwe ndiwe galu kwabasi
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 2 ай бұрын
Inuyo ndinu ndnu woipa ngati maliro tsiku ndi ttsiku kunyoza adzanu mnakhala bwanji
@user-ez1kc7zp9m
@user-ez1kc7zp9m 2 ай бұрын
Apm my vote
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 2 ай бұрын
APM my vote
@richadaxmed6307
@richadaxmed6307 2 ай бұрын
Mtokoto kumeneko ndiye kuyakula
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 2 ай бұрын
Apm my vote
@user-yn4ee1qn2j
@user-yn4ee1qn2j 2 ай бұрын
Apm my vote
@josephmanyenje7107
@josephmanyenje7107 2 ай бұрын
Apm my vote
Chilima Simtsogoleri Wabwino - Bon Kalindo
17:28
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 11 М.
Ine Ndilibe Msika Ogula Ndi Kugulitsa Ma Activist - Lyton Mangochi
6:50
Super sport🤯
00:15
Lexa_Merin
Рет қаралды 20 МЛН
Кәріс өшін алды...| Synyptas 3 | 10 серия
24:51
APM Sanaluze Zisankho Mu 2019 Ndi Mu 2020 - Innocent Mutholo
22:47
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 10 М.
Misomali Ya Six Inches Yothana Ndi Zipani Zotsutsa - Bon Kalindo
17:18
Confessions of Charles Ben Longwe (Part 3)
32:42
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 771
Zomwe zinachitika 2hrs Asanamwalire
4:36
Sam Malvitha
Рет қаралды 86 М.