Mulungu salakwitsa watilanditsa ku mimbulu imenei ngat ndi zoona ai zakhala bwino akanatitha tose koma ambuye atilanditsa
@festongreston13 сағат бұрын
Let the will of God fulfill
@JuniorHala-vf9ov5 сағат бұрын
Osamasewela ndangoni amene anapanga nao program yokupha chilima paulendo bwezela agwile ntchito yake apa
@dhaoudhiabedinegomaseko236314 сағат бұрын
Ndi wamwayi amene amabwelako ndi moyo ku Galden city koma Mulungu akukhuzeni nonse omwe muli kuchipatalachi imfa siyabwino ngati kuli moyo.Moyo kunyenga nthawi yolapa inalipo koma chuma chimanyenga
@MarkManyowa14 сағат бұрын
😂😂😂😂😂
@MarkManyowa14 сағат бұрын
Imfa yanji yokondweretsa 🤣😂🤣🤣 Koma ngati sizitheka panopa His days are numbered for sure 😂
@Alice-z7t4z14 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂@@MarkManyowa
@ElizabethMulinde13 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂@@MarkManyowa
@MarkManyowa13 сағат бұрын
@@ElizabethMulinde 🤣🤣🤣🤣 Akanangopenga Misala onse omwe anatenga nawo mbali pa plan yozimitsa Chilima ndi ena onse aja