We choose dull people to be leading us...,.tose tiliziko muno can we fail to develop likoma
@fridaygonelaАй бұрын
Ngati dziko kumayambitsa nkhondo nkhani yake ndi iyi,kumozambique ku cabo de ligado mpaka pano anthu akuphana nkhaniyake ndi meneyi prezidente opuma anagulitsa dela lose la cabo de ligado ogula akufuna malo awo beni dziko akukana kusamuka mpaka pano anthu akukaniza ife tikakhala kuti ndiye kulikomako chonde musalole kodi kamtukule kwawo ndikuti mumuze akagulitse boma lakwawo likoma ili ndi eni ake kale amend anazolowera kukhala kumeneko ndizochita zao
@idilissmuyer2914Ай бұрын
Mmmm chaka chobwezera ndi cha 100 ameneyu ndi galu bwanji
@FrancisNyayiАй бұрын
😂😂😂 koma kumagulisa malo anzao alibe awo mangermans ofufuza ndege ma gemaz ahhh
@ChikwawaАй бұрын
Zovuta. Mzika za ku Likoma zikuyenera kuteteza malowa.
@FrankMkwalaАй бұрын
Koma Boma Eli eeee ndilopanda sogolo
@DONNEXKhama-bk1gyАй бұрын
This is too much mpakana kugulisa likoma mm why chakwera
@FrankKambwaniАй бұрын
Dzikungowonetseratu kuti Chakwera kwawo adamaliza kugulitsa minda ya abale ake.Idzidzi sidzingatheke kwa a Malawi alerofe ndiwosiyana ndi akale aja
Ndichifukwa chake tikuti nkhaniyo ndiyabodza palibe kugulisa Likoma ngakhaleso opposition sadaikambe nkhani imeneyo ndizabodza koma pali Malo a church ndiamene adakayenderako not ku gulisa
@MalawianCameraАй бұрын
@@SaidiMbawa-st6bjmmmmmmh amwene do your homework a church anakana boma ndilomwe likugulitsa
Zaka zimenezo matsiku anowa munthu akumabadwa atakalamba kale kumafa mu zaka 30- 75 angadzakhalepo ndani? Utsogoleli wa anthu a dziwanda
@SadamBitoАй бұрын
Osat likhoma lokha koma dziko lonse lamalawi anthu awa akamachoka boma akhala chilichonse agulitsa ngakhale nyanjaa
@TryMoo-c1eАй бұрын
Ndeno Ana akubadwawa azadziwa kuti Likoma ndi lawo osati la anthu aku 🇩🇪😂 Germany??Best idea I think angogulitsa Malawi 🇲🇼 yonse ku German it will be better than Kugulitsa Likoma island 🏝 and tisalore 😂
Not kugulisa Likoma zimenezo ndi zabodza nkhaniyo simunaifufuze bwino anthu akulikoma sakuchoka koma Pali malo a church ndiamene akufuna kuno amangidwe ndicholinga cha business
@ChimwemweSaukaАй бұрын
Azabwedza akachoka pampando
@RajabShahidaАй бұрын
Stupidity chakwera ndi mcp izizi zisachitike ndipo
@NovemberMmangathayoАй бұрын
Chakwela ndichitsilu kwambili
@lastonmasoatenganji-bs5gfАй бұрын
Tsoka lalikulu ku dziko la Malawi. Kodi cholowa chomwe Yehova anapatsa ana ake, mumachipereka motero kwa alendo? Mlandu uwu aulembe Chauta kuti ulowe nkaundula wa milandu yonse. Ndikhulupirira adzapukuta misonzi yathu yonse patsikulo.
@somzyg-wb1ezАй бұрын
Koma ameneyi tiona kt akagulilana kt
@YOMALO.Ай бұрын
😢Mmmh
@NdemboBrothersAdamАй бұрын
Zimenezo analephera maiko andalama mpaka pano anasintha maina ndipo mpaka pano akulephera kubwezeretsa mmanja mwawo ndiye Inu muzayambira. Pati?
@JohnWame-u3lАй бұрын
Wamaliza kugulitsa Anthu, tsopano waolokera Ku nthaka,shame😢😢
Ndi boma lachakwela kodi mphamvu zogulitsa ndikusagulitsa zilindinandani
@HanifiYaumuАй бұрын
Mabattery ambuyake ndithu ameneyu
@gmxplayboy6559Ай бұрын
Kodi boma ilili kweni kweni mchiyani? They always think about themselves. Iwo diso lawo liri pa ndalama zoti zizilowa mmatumba mwawo basi. Kenako tinva zoti dziko la Malawi lagulitsidwa sure. My question is, kodi pa kugulitsa Likoma Island ndi phindu lanji lomwe aliwone m'Malawi osauka?
@moseskavalo3304Ай бұрын
People of Likoma and general public must not allow this
@SadamBitoАй бұрын
Akagulitse kukasiya
@ManganiStanleyАй бұрын
cakwera Boma 2070 wooo anthu opusa ife
@VitumbikoMagwiraАй бұрын
Uchiailu wake wafka pa 99
@FrancisDay-br7xbАй бұрын
Peter mtalika anati sankhani mwanzelu , chifukwa tsiku Lina Malawi will be lead by evil, sananame, kuende konse achakwera kuja ndikuka gulitsa Malawi
@NovemberMmangathayoАй бұрын
Akufuna adzichotsa mafuta
@JuliusMphamba-lz5yuАй бұрын
Ďo not sell likoma Island please 🎉
@jonathanmbewe4246Ай бұрын
Yoh too bad
@PrinceThom-pe6ieАй бұрын
Blame opposition party
@LawrenceSparta-wb9qvАй бұрын
Ndchfkw galu ameneyo anapta ku German et
@JessicaManda-zm1ugАй бұрын
Musalore alikoma eeee akayika kut anthu wosewo
@victormsibandemenyu665Ай бұрын
where on earth to sell part of country thats crazy u can't do that mr president and ur cabinet stop that Man is it because Malawi is poor