Hon. Ntanyiwa Comrade, we are praying for our nation, God is doing his deep part on every thing. Amen
@DavidJackson-ox4xm3 ай бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you all the time
@mishecksipolo71533 ай бұрын
Ndege ya military imakhala full equiped komaso oyendetsa uja anali msilikali yemwe amadziwa kudumpha ndi paratute,how came onse anafamo
@joshuaagabu30323 ай бұрын
Kudumpha ndi parachute is not as easy as you think. Only trained professionals can jump out of an airplane under certain conditions. Pilot ntchito yake 1. Aviate (fly the plane)., 2. Navigate (Know where you are, and are going), 3.Communicate. In an emergency the last thing you want your pilot to do is abandon the aircraft and passengers. Inu ndi ine kutikweza ndege, kutipatsa parachute duphani opanda training, titha kuvulala modetsa nkhawa kapena kumwalila kumene chifukwa sitidziwa kagwilitsidwe ntchito ka parahute. The VP or any of the passengers onboard were civilians not trained paratroopers or skydivers. letting them jump with parachutes would have done little to save them.
@AARONCHISUKAMZION-we3vp3 ай бұрын
Zomvetsa chisoni dziko la Malawi. Mzimu wa chilima ndi anthu ena onse ena onse ukause mumtendere. Ndani wamuyaya olo titatsogoza anzathu. Long live Mkango kamuzu Banda anapita. Ndiye Long live wina ndani Padziko lapansi palibe wamuyaya. Kubisala pa chande Malawi ndiwochepa kwambili😢😢😢
@DoreenMaida2 күн бұрын
Nice one comrade Ntanylwa keep it up please
@collinssululu-o4c3 күн бұрын
Comrade , we appreciate you so much indeed ,May the good Lord be with you brother , we are always with you .........
@doreenkaliati31663 ай бұрын
Aaaaaaaa iwe Mtanyiwa no one 2 kuopa kupindika Ambuye Mulungu kumwamba akufungatire akudze malire a moyo wako ndithu ndilipano kumvetsera❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndilibe chonena apa mulungu ndi amene akamulanga chikakhawa 😢😢😢
@YvonneZekka2 күн бұрын
Comrade your not alone were together 🎉
@jowiemhango50583 ай бұрын
Mmmmhu koma Lord have mercy
@FilbertKomba-fi2nl3 ай бұрын
Antanyiwa ngati ngati ndi zowona mukunenazi chonde liport iyo tiikieni pa Air pamene mwawenge kuti Malawi ikulupilile
@NizigiyimanaChantal-c2p3 ай бұрын
Aaaaa km Inu
@mikebernabechimundi34723 ай бұрын
Pa air paponse apa? Pa air pake Pati ukupafuna iwe? Ngati president Chakwera akunvela nawo nkhanga zaona pa air paponse apa
@joshuaagabu30323 ай бұрын
@@mikebernabechimundi3472 tione lipoti limene wawerenga. We should cross check what he is saying and what is in the report. Tidzimva uku tikuwerenga. Ku church timapita ndi bible aliyense kuti abusa akamawerenga verse aliyense tikhale page imodzi wina asatibwatike ndi bodza pa chifukwa zodziwa yekha.
@BeckhamDavid-v6c3 ай бұрын
Koma kuipa moyo kwabwanji kuphana chifukwa cha mpando otsala nayeso chakwera adzafa pangatalike pangatani naye tsiku lake lilikudza palibe wamuyaya tsogoleli wachinyengo musayembekezere dziko kuchita bwino ai koma imfa ndy zikuchulukila ambuye atithandize mulamulilo umenewo aliyese waphuzilapo kanthu
Mr NTANYIWA usiku wabwino yehova mulungu akutetezeleni Kwa adani
@GeoffreyMaulana-rh5rx3 ай бұрын
Comrade Ntanyiwa Allah azikutetezani ndikukupasanimoyowanthanzi nthawizonse
@williamchinunda3 ай бұрын
Report yoona
@punchufred51183 ай бұрын
Koma anafa imfa yowawa 😢😢
@davidwakhokamoto11243 ай бұрын
Welcome big man ndakhala ndikudikira report
@elishamael-shadai3 ай бұрын
Nthanyiwa amapasidwa info basi,so guys who are close to the source amugaolako info😊
@lolinichitute2 күн бұрын
APM my vote
@doreenkaliati31663 ай бұрын
Ulemu Wanu a Mtanyiwa 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@Rose-wu5ef3 ай бұрын
Mr ntanyiwa mulungu akupatse moyo ochuluka
@EVANCEKAGONEGONE3 ай бұрын
Antanyiwa inudi ndiwakwao kwa joni chilembwedi
@MCDAISONNKHWAZI2 ай бұрын
Cool
@nasserbandeКүн бұрын
Koma mizimu 9 iyiyi ikadzangotopa kumandako! Wena ad zafa ndi mantha zitawakhikha pakhosi P
@robertkabade50113 ай бұрын
Timadikila ife report ndimakunyadilan Mr NTANYIWA
@chigalusilvester11143 ай бұрын
That's exactly what's in the report
@Chimwemwekaunda-r9l3 ай бұрын
Ambuyeakhala nafe mu nyengo zathu
@FrankChakanga-v4t21 күн бұрын
🎉Musautse mikwiyp ya anthu tiyeni tmusatchuke pazithu zotimulibe umboni weniweni zose mwanena apa palibe chazeru ku anthu oganiza
@FatimaNakoma15 күн бұрын
Nawenso uti chani
@MariaMlendo3 күн бұрын
Mlungu yekha azikubisani Kwa Adani omwe amukusakaniwa.ngati akusaka Kalulu Ali nditsoka lalikulu inuyo Amtanyiwa.muzafa ifa yochokera Kwa Mlungu basi osati Agalu amenewa.we.pray for u all de tym me konda u
@mcsellahntv68963 ай бұрын
Mr Nkhanga inuyo muzangosowa basi osatinso zafufa. Ife mumatinvetsa kukoma.
@JonaKanyangalamakondetsa3 күн бұрын
Nkhani iyi yalowelera mundale,wena apezelapo mwai wochitirapo kampeni
@JohminMatick-q5k3 ай бұрын
We also like you bro Srub Junta
@elishamael-shadai3 ай бұрын
M fucken CP will never change. I saw it comng but Chirima was not a toddler not to know what the killing machine M fucken CP was capable of. They killed Muwalo who was the second powerful man during the reign of fucken Kamuzu banda
@PhiripChinkango-k5p2 ай бұрын
Nkhanga zaona comrade waing'amba apa chilungamo tachimvera tokha rero
@FrancisChip3 ай бұрын
Eee wina athawa ndithu
@EmilyKanyika3 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@crosbeygondwe54033 ай бұрын
Ndakhala ndikudikila report from mamawa
@festerstanford31213 ай бұрын
Report la straight forward koma anthu ndiwoyipa
@bysongeorge32433 ай бұрын
Ndipo zoona zake , straight forward! Ena anavulidwa zovala bwanji?
@Kelvin-hj5qv3 ай бұрын
NDIZOMWE TIMADIKILA APAPA🎉
@DanielJuwawo3 ай бұрын
RIP saulos chilima
@JonathanKadyenji-p7b3 күн бұрын
President anali atalidziwa kale ndi chifukwa amanena kuti muyambe ndinu a Malawi kulandira report akudziwa kuti iyeyo sakutchulidwa kuti anatengapo mbali. Zosakhala bwino Koma chuma chikuonengeka Koma.
@LuckiaMatembaАй бұрын
Mmmmm mmm a mbuye 😊
@MaggieKazombo3 ай бұрын
Mzimu wa chilima ndi anthu Ena 8 awunse mumtendere
@GoldenChandiyangana-y7u2 күн бұрын
Nyanyiwa lero wanna zoona zokhazokha. Zoti anthuwa anaomberedwa ndi zoona. M'modzi mwa ofunsidwa ku Chikangawa wati anamva ngatii anthu akuomberana. Komanso ngati akuswa miyala. Malawi anthu anachita kuphedwa awa.
@WestonRoben2 күн бұрын
Chomwe tingadziwe ndichakuti or report ndilowoona kapena labooza nkhani ndiku voter mwadzelu. Apo biii adakatipha amanawa
@SaffronJeka2 ай бұрын
Mmmmmmmm Mzimu yawo yiuse mtendere
@EmmanuelNgambi-y6h3 ай бұрын
30days yachuluka comrade ikanakhala 4days ,,,,,chakwera achoke basi
@HarryNamulewa2 күн бұрын
1:47
@GuejendraMk29 күн бұрын
Chepesan ma datewo. Mabishop ndikupempheni akakuitani musapiteko akakubwatikani zinthu za bodza.mikhale mukupemphera nonse muchipinda chimodz. Kumbukira 1993. Mabishop amkafuna kuphedwa koma onse anali pa C l ndi arch bishop the late Chiona kupemphera.
@LasieMolebatsi3 ай бұрын
Zosakhala bwino zimenezi
@KodwaniMereka3 ай бұрын
Maticheti abwere amalawi first
@doreenkaliati31663 ай бұрын
Eishiiiiiiii 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭koma Chakwera munthu oipa zedi anatilakwira kwambiri ife ndithu koma zoona chakwera kuiwala zoona kuti pa mpando wakhalapo mesa ndi chimima anapangitsa kuti ukhale pamenepo Ambuye akukhululukire ndithu Mulungu akuoneni anthu nonse amene munatenga mbali pompha chilima😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@JonaKanyangalamakondetsa2 күн бұрын
@@doreenkaliati3166 okondedwa a Doreen Kaliat,sindifuna kuti ndinyoze maganizo anu pankhani ya imfa yawachiri kwa mtsogoleri wadziko,koma mundilole kuti ndikonzeko apa, Utsogoleri uliwonse ukaperekedwa mdziko amapereka ndi Yehova ,osati munthu ai.Ndikupatsani mau mwerenge Bible pa Yohane 19:8-11.Zindikilani kuyambila lero kuti mpando wa Chakwera sunapatsidwe ndi Chilima koma Mulungu.Ife timangothandizila chomwe iye wachikomza kale.
@davidwakhokamoto11243 ай бұрын
Akuona ngat Iwo sazafa osamakhala oipa mitima za ndale zomwezi kumachosana moyo osatenga chisazo pa south Africa pompa athu amagwira tchito limodz pano dziko likuyenda bwino kma malawi
@rhajabBinIman3 ай бұрын
Share screen shot
@VINCENTCHIKUSE-b7j3 ай бұрын
wabisala mumbatata nsana ukuoneka
@AlfredHarawa2 ай бұрын
Thus very sad indeed God will answer all of you you take part of this accident