No video

LIMPOPO FM YABWELETSA MAI MARY NAVICHA A DPP LIVE NDITHU MULI NKHANI ZOCHULUKA ZAKAMBIDWA UMU

  Рет қаралды 25,065

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 75
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo Ай бұрын
APM my vote🎉
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera Ай бұрын
Peter Mthalika must come to resque Malawian from the hands of the devil, God must help APM.
@ListerBarsonBanda
@ListerBarsonBanda Ай бұрын
Zabwino zonse limpopo fm and always God protect you with more grace and favors
@user-xk9vs9qc2s
@user-xk9vs9qc2s Ай бұрын
Mai navicha mayankhulatu mkadzabwera mdziko ndizakuyenderan kuyankha molimba mtima
@user-xk9vs9qc2s
@user-xk9vs9qc2s Ай бұрын
Kodi tingathe kuvota tili kuno RSA
@EdwinMangani
@EdwinMangani Ай бұрын
It will be my first time to vote for peter mutharika and Dpp.
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Zoona mama panopa ndarama sikugwira ntchito ngakhare wutapeza ndarama yochuluka bwanji mayazi mavuto okhaokha ndipo Pano tikungokhalira kulimba moyo wukuwawa kwambiri 😭😭😭
@HenryMero-nf4vh
@HenryMero-nf4vh Ай бұрын
I love this confidence member of parliament
@user-ii6lu1wy5f
@user-ii6lu1wy5f Ай бұрын
Mai navitcha and APM my vote
@georgesmart3791
@georgesmart3791 Ай бұрын
Powerful interview mama Mary Navitcha
@ChristopherMasanza
@ChristopherMasanza Ай бұрын
Br mukafusa dikilirani kuti munthu ayankhe osamusokoneza. Kma zabwino ndithu
@JamesSaidi-rw6ek
@JamesSaidi-rw6ek Ай бұрын
Dpp is my vote, whenever it or not
@user-dd1qq5xq1k
@user-dd1qq5xq1k Ай бұрын
DPP my vote woyeere.
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
💙💙DPP boma mufune musafune
@BaulenChipala
@BaulenChipala Ай бұрын
Mukuona ngat muzapezaso chance yobela?
@AubreyWilson-j8w
@AubreyWilson-j8w Ай бұрын
Mayi wafuko ndinu dpp my vote
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj Ай бұрын
Good my chilima Analakwisa chilima kupanga tonse alliance ndi anthu akupha anyau awa akanakhala moment mu DPP
@LamekiSamson
@LamekiSamson Ай бұрын
Ndipo analakwitsad mwamva inu inenso ndimadandaula kwambili
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Ай бұрын
​@@LamekiSamsonambili timadandaula kut analakwisadi
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi Ай бұрын
Ankafuna polowera
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Ай бұрын
She is a true politician,u can tell by how she refuses some questions
@RobertChisenga-ci2mq
@RobertChisenga-ci2mq Ай бұрын
Masten amandiyakhulira bwino kwambir kaya anali loya kaya I love you masten
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Good Messnge mayi navicha
@johnmpatama1461
@johnmpatama1461 Ай бұрын
Best interview ever ❤❤
@user-tw3fl7vh7j
@user-tw3fl7vh7j Ай бұрын
Apm my vote
@augustMag
@augustMag Ай бұрын
Powerful words mum💪💪
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Ndipo mai olo mutakhala plesdent dziko likhoza kukhala losangalala mukhale ndi moyo chikhaleli mai❤️❤️
@MrsNankhumwa
@MrsNankhumwa Ай бұрын
APM my vote
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 20 күн бұрын
Tivomereze Dpp zina sizimayenda koma 85% zambiri zimatheka, Mulungu atiyendere kuti Ngati kuli kotheka Dpp ikoze utsogoleri wake ku conversation then akoze dzikoli popeza Amalawi osauka chiyembekezo chawo ndichomwechi. Let's Beg God to give us maso auzimu
@user-rb9jq2pv2t
@user-rb9jq2pv2t Ай бұрын
big up Mary Navitcha
@CharlesKachipanda-jz9jv
@CharlesKachipanda-jz9jv Ай бұрын
My Favorite radio station
@DeborahHetekere
@DeborahHetekere Ай бұрын
Mary Navitcha MP Thyolo thava constituency moto unandiiiiii
@user-bs8nk1si4e
@user-bs8nk1si4e Ай бұрын
Limpopo Radio woyeee.Mai Navicha Woyeeeeee
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm Ай бұрын
Powerful 👊
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Mau a mphanvu mai Navicha, ndipo a Malawi tili pa vuto kwambiri. Chakwera walepherela basi.
@MikeKathumba
@MikeKathumba Ай бұрын
Ngakhale chiphatso cha ubatizo chikagwira ntchito pokavota.....
@KennethMpininga-iz2ie
@KennethMpininga-iz2ie Ай бұрын
Super ❤
@AmosBandula-up4yb
@AmosBandula-up4yb Ай бұрын
Okay
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f Ай бұрын
I salute you Maa
@BaulenChipala
@BaulenChipala Ай бұрын
CHOTI nikuuzeni Inu abale akummwera ndichakut kut mumuve bwino chakwera , muyenera kugwira ntchito, kazilimani kut kukwera kwachimanga kusakuwaweni bcoz kwa amene timalima timasangalara chimanga chikamadula even kugula fertilizer it's easy just sale 2 bags it's enough to buy 1 bags of fertilizer pamene kwa amene Salima namene amakhara patsogolo kudandaula, ife ogwira ntchitozakudula kwazinthu sitikukudziwa bweran central regional man mukamaziva kuchoka ku John ko muchedwa
@user-gu3sp8ci6v
@user-gu3sp8ci6v Ай бұрын
Pali zina zoti muuzane kumbali musanayambe program , mumatichedwetsa
@MustapherLino
@MustapherLino Ай бұрын
Mau amenewo amai mary Navicha
@user-gl1ev1dw6w
@user-gl1ev1dw6w Ай бұрын
Koma mayiwa amatha kulankhula
@GiftMathewe-fr3kn
@GiftMathewe-fr3kn Ай бұрын
Ndimakunyadilan mama
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki Ай бұрын
A Malawi ndiwokonzeka Kuka vota,koma Pali kuthekela Kot MCP ikumana anthu cha unzika, ndiye inuyo a opposition mulimbane nayo nkhani imeneyi
@user-nl5rq9to2s
@user-nl5rq9to2s Ай бұрын
Congress party inapanga zitheka kuvuta malawi yonse inuyo adpp chimene chikuwavuta ndi chiyani why dont dpp do the same
@Maliko-bp1xn
@Maliko-bp1xn Ай бұрын
Mai inuyo ndi loya panokha mukutimvetsa kukoma
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
💙💙💙💙💙💙
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x Ай бұрын
Mavenda ife ndye tikuliradi mmm zinthu zavuta bola adada aja ndinthu
@user-nl5rq9to2s
@user-nl5rq9to2s Ай бұрын
mchifukwa chake mcp ikutanga advantage mkumatiopsesa malawi yonse dpp ndi mboni kapena chifukwa choti iwowa akudya bwino
@user-nl5rq9to2s
@user-nl5rq9to2s Ай бұрын
ineyo mmaonekedwa anga ndikuona ngati dpp ndi chipani choonelela zinthu kwambili
@user-nl5rq9to2s
@user-nl5rq9to2s Ай бұрын
anthu akati apange mademo dpp siimatuluka pamene mcp inkajoina mademo why not dpp doing the same
@user-pw1kl3vo5d
@user-pw1kl3vo5d Ай бұрын
Chifukwa DPP simafuna Kona magazi korma MCP simaopa chifukwa NDI satana
@user-nl5rq9to2s
@user-nl5rq9to2s Ай бұрын
they are sleeping too much
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd Ай бұрын
kod achewa onse ndi a mcp
@user-nl5rq9to2s
@user-nl5rq9to2s Ай бұрын
anthu adpp ngati akufuna kuyenda ndi anthu osauka bwanji osajiina mademo
@user-tk6wf2eg4z
@user-tk6wf2eg4z Ай бұрын
Chifukwa chakut ma vote ali posachedwapa
@user-cp4qt9hs8w
@user-cp4qt9hs8w Ай бұрын
Komaso mabailodi paper mukajambulise ena ngat adachonga kl akagwe nayo
@mtenderemitembe3433
@mtenderemitembe3433 Ай бұрын
A ndale mumafuna anthu nthawi yovota yokha.
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Ай бұрын
Achitetezo ose pano ndi aboma koma kumwamba kulibe chinyengo tionana 2025
@user-nl5rq9to2s
@user-nl5rq9to2s Ай бұрын
mpakana anthupe tikonza kufa chifukwa chogona kwambili
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Bon kalindo mwana oopsa kwambiri wakuuzilani mayesotu mwachangamukanotu
@KondwaniGronyonyo
@KondwaniGronyonyo Ай бұрын
Thumba lachimanga linali pa 7000 mai osati 12,000 ayi mwaiwala mai tikukumbusen
@MzadziWanga
@MzadziWanga Ай бұрын
Mulimosemo but the truth is that as of now the price is much higher than before 😅
@MarthaBango
@MarthaBango Ай бұрын
7000 mwati
@JefulyPesulo
@JefulyPesulo Ай бұрын
Mbambande madamu
@julietmussa5103
@julietmussa5103 Ай бұрын
Muzipatuka muzimwako thobwa,muzimwako madzi amakhala ndi madzi abwinotu😝😝😝😝😝
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Ndipo zithu sizikuyenda amalawawi tili pa mavuto mulungu ave kulila kwathu ambuye atichitile chifundo dziko la Malawi atikhulukile mulungu ndipo achite chatsopano pa Malawi
@BaulenChipala
@BaulenChipala Ай бұрын
Wapanira manja mphechepeche uli mulungu akuchitire chifundo mmalo mogwira ntchito? Uyembekeza adad anuwu azakupatse chakudya , Pali chani unapangapo munthawi ya dpp?
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
@@BaulenChipala owooo yamika mulungu ngati zako zilibwino koma tayesa kuyenda m,mizimu owone momwe athu akufela ndi njala m,zipatala athu akufa chifukwa makhwala mudzipatala mulibe chifukwa Cha mau Ako okhao mulungu akuyendele mwapadela ndithu
@StiphanoEmmanuel
@StiphanoEmmanuel Ай бұрын
Limpopo ndi radio yomwe imakamba chilungamo timayifira koopsa moto kuto buuuuuu!!!!
@user-tm3zh5zk4t
@user-tm3zh5zk4t Ай бұрын
kodi yinuyo a Dpp kuti akulande nanuso muli nivuto koma mudziwe kuti simungamayime pachulu kumayankhula zamisala zakozo ife tikupita chitsogolo choka ukununkha chipapasi pano mukukhala ngatì anthu azelu koma muzidziwa kuti akita samafa
@FortunePhiri-kl7oe
@FortunePhiri-kl7oe Ай бұрын
Ndiwe kape khala chete Seka chímbuzi chako kagwele uko
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Ай бұрын
Mkamwa monunkhamo ngati wachita chimbudzi pa guru.
Bota rangu rokamburwa Zvisina Order!!!! Dare raChief Mutasa
55:21
Karanganda Tv (Waiyepo ere ?)
Рет қаралды 26 М.
UK riots: 400 arrested amid far-right violence and clashes with police
42:28
Bony Just Wants To Take A Shower #animation
00:10
GREEN MAX
Рет қаралды 7 МЛН
WILL IT BURST?
00:31
Natan por Aí
Рет қаралды 18 МЛН
Whoa
01:00
Justin Flom
Рет қаралды 22 МЛН
BON KALINDO LERO PA 27 AUGUST 2024 |
17:02
DZIWE TV
Рет қаралды 7 М.
Mufundisi  pa Lodge Nemukadzi wemunhu Dare Rachief Mutasa
57:49
TICHKACH MTV
Рет қаралды 41 М.
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Malawi News Update
Рет қаралды 191 М.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Zodiak Malawi
Рет қаралды 81 М.
BON KALINDO 27 AUGUST 2024 KUNG’ALURA PA TUESDAY
15:37
Malawi Trends TV
Рет қаралды 986