ZODABWISA ZOMWE ZACHITIKA LERO KU PARLIAMENT PAMENE MA MP ANAMUITANISA CHAKWERA KUKAYANKHA MAFUNSO

  Рет қаралды 46,100

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 244
@rabisonpias5131
@rabisonpias5131 Күн бұрын
I would be happy if SULEMAIN is a Leader of opposition not CHAPONDA
@bobkatas1974
@bobkatas1974 Күн бұрын
100% correct
@MelusiMwali
@MelusiMwali Күн бұрын
Chaponda fears handcuffs
@fredkachale8297
@fredkachale8297 Күн бұрын
ndipo live
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Күн бұрын
Better
@rabisonpias5131
@rabisonpias5131 Күн бұрын
@@MelusiMwali komaso Satha kuyankhula akura Adha aja.
@JosephMakatha
@JosephMakatha Күн бұрын
Khope yachikangawayo 😂😂😂😂
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 Күн бұрын
APM is more educated and intelligent than chakwera. Kukongola sikanthu Koma nzeru
@SabinaNkhoma-o1h
@SabinaNkhoma-o1h Күн бұрын
Uyu siowoneka bwno hundsome ndi uja tidaundirayu
@BillyBentryMunthali
@BillyBentryMunthali Күн бұрын
Pitala kuphwafuka ku kamwa kuja, kukongola kuli pati? Hahahahaha 😂😂😂😂😂
@henryphiri6100
@henryphiri6100 Күн бұрын
not more but well educated than this nyau thing
@FranksonKennethChipande
@FranksonKennethChipande Күн бұрын
True 90yrs old Norman Chisale akudikira kuzatenga upresident kkkkkk
@QueenElizabethVunga
@QueenElizabethVunga Күн бұрын
Ndipo zoona​@@SabinaNkhoma-o1h
@BlessingsKadzombe
@BlessingsKadzombe Күн бұрын
🎉mbuzi ya mtsogolsli
@EmmanuelNasolo-o4c
@EmmanuelNasolo-o4c Күн бұрын
Amene akuti boma ndilomweri amadyetsedwa sadziwa kusaka.
@IanChitsulo
@IanChitsulo Күн бұрын
Zoona
@FranksonKennethChipande
@FranksonKennethChipande Күн бұрын
@@EmmanuelNasolo-o4c mukunama Akulu kungoti Inuyo simuziwa kusaka
@ShaidaJackson
@ShaidaJackson Күн бұрын
I wish if Suleman being a leader of parliament not Chaponda is very smat guy. You can see now mcp Is gaining every corners shame on opposition.
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya Күн бұрын
Koma Lazaro anawukisidwa kwa akufa uja akanakhala ngati uyu I don't think Yesu akanamuwukisa😢😢😢😢
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya Күн бұрын
Zitsilu zimangowombela mmanja asakumvando English yomwe
@AdamJames-x7x
@AdamJames-x7x Күн бұрын
wakupha wafika Ku parliament kkkkkkk
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Күн бұрын
Chakwela anapha SKC munthu yemwe anamuika pamphando, it's sad kuti Chilima ankati tivotele MCP azamange mbava mu DPP koma unfortunately akaimbidwa milandu yakatangale ndichilima komanso ndikumuphaso pompo.
@henryphiri6100
@henryphiri6100 Күн бұрын
Ndiye Malawi Congress Party imene timkaidziwa mma 1980s and late 90s ankatimanga nyakula, mkukatisambitsa madzi onunkha ochoka kubathroom.
@StarfordKAMOTO
@StarfordKAMOTO Күн бұрын
Ndipo tingaziwe kuti chipani choipa OLO titasitha msongoleri chimakhalambe choipa basi
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda Күн бұрын
Ndipo zoonad
@Yanjanani
@Yanjanani Күн бұрын
mpaka muli bwana; Bwana wa mnsikizi kapena chan?
@YoungMwacho
@YoungMwacho Күн бұрын
Chakwela answering questions ngati mwana, very useless leader, can speak unprofessional and stupid MPs busy clapping hands. No question is answered professionally. A waste of time to call Chakwela to parliament to answer questions. I wished Bingu was there to answer such economical questions. Mbuzi osanenapo za procurement ku butchery and farmacy. He can only answer pre answered questions, chitsilu cha munthu.
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda Күн бұрын
Suleman akhale leader of opposition ,ndiyekhayo yemwe ali munthu osaopa osafooka, Suleman its only our hope in parliament
@bysongeorge3243
@bysongeorge3243 Күн бұрын
Probably our next president soon...
@louisgolden
@louisgolden Күн бұрын
Galu uyu palibe aziwa iye kuba basi😊
@HolinessThindwa-pz5hw
@HolinessThindwa-pz5hw Күн бұрын
Koma zimene mkuchita Malawi kutukwana kunyoza mdzidziwa kuti mawa mzakolora zipatso zoyipa.
@ThoccoChimbali-h6g
@ThoccoChimbali-h6g Күн бұрын
Iyi nde ndi mbuzi ya ma president onse pa dziko la pansi
@EliasKawuwa
@EliasKawuwa Күн бұрын
Kuyankhula molakwika ngati ,munakutenga kuti, onyoza fumu ya dziko
@FranksonKennethChipande
@FranksonKennethChipande Күн бұрын
Awa kwao kumakhala kunyoza koma tikukhalisani pansi pompano tikalembesa kale tiyeni tivote January 2025 tione amene awine
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
Ku yoza mfumu amalawi ambiri tilibe . mfumu wasatanic okupha ononga okuba mfumu opamda nzeru ongoyenda Ngati wafya matako agalu American Koma osadziwa chomwe akupanga
@monicagondwe228
@monicagondwe228 Күн бұрын
Cry my beloved country 😢
@Godwin-xy9rg
@Godwin-xy9rg Күн бұрын
😂zot iyi ndi mbuzi ya munthu sakudziwa ndani?? Chikangawa si munthu
@HildaMbizi
@HildaMbizi Күн бұрын
Forest ya chingangawa yafika ku nyumba ya malamulo
@FaithKalonga-xm3pc
@FaithKalonga-xm3pc Күн бұрын
A MCP musamakhale ngat nyumbayo ndiyànu yokha mukupangiranj phokoso pomwe anzanu akuyankhula
@IanChitsulo
@IanChitsulo Күн бұрын
Akulitengatu bomali ngati tonse ndife a mcp
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc Күн бұрын
Berezebulo wafika Ku parliament achina Suleman panikizeni ndi mafuso ameneyo😑
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
Hassan chikangawa
@Janaphiri
@Janaphiri Күн бұрын
Ndipo Mzimu woyera akumenyabe nkhondo ndipo mupambana ❤❤❤❤❤ pitizani kutukula Malawi enawa aamaadziwa kuononga.😂😂😂Boma ndilomweli
@gomezganii
@gomezganii Күн бұрын
Either you live outside this country or mumadya nawo zokububa this is the worst government and president since independence
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy Күн бұрын
Iwe ndiiwe galu kwabasi
@MadalitsoRobert-s5k
@MadalitsoRobert-s5k 4 сағат бұрын
Kuteroko mumavala kang'wing'wi
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Күн бұрын
Chikangawa Silimangeni Razaro 😅😅😅😂😂😂😂
@SiyasiyaManda
@SiyasiyaManda Күн бұрын
😂😂😂😂
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
😅😅😅😅😅😅😅😅
@FrankKamundi-l1s
@FrankKamundi-l1s Күн бұрын
Chaka chamawa chidzasanduka chimunthu wamba ufumu utatha chimfiti ichi chinapha nzake 2025 akuti chiyimeso koma mulungu sadzaloransotu zopusazi
@MzadziWanga
@MzadziWanga Күн бұрын
Mbuli iweso nawe nde olo atapita yekha chomwe chitapindulire amalawi ndichani?? Katundu atsika mtengo? Fertilizer apezeka?? Chimanga mma admac chipezeka?? Asiya kuba ndalama zamisonkho?? Zamkutu basi😅
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
Mbuli ndi iweyo nanga akunapha kt Hassan chikangawa. Ndi okupha wasatanic
@GiftNorton
@GiftNorton Күн бұрын
Bwana ameneyo ndiwakunyumba kwanu osati ndife tomwe
@BatsonKadzuwa-tl3rp
@BatsonKadzuwa-tl3rp Күн бұрын
Chigawenga Cha Dziko
@ManjeUphl
@ManjeUphl Күн бұрын
Kuonera likasa apule😂 Kupanda nzeru kulephera kuyendesa dziko
@ClementMinyanga
@ClementMinyanga Күн бұрын
Mbuzi yamunthu iwe anthu akumvutika chifukwa chaiwe bwampini
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r Күн бұрын
Bwana chakwera mumve mumtimamo kuti munabwerera kazasiya amalawi pa mabvuto mulibe chisoni ngakhale pang, ono ndiinu munthu oipa kwambili ambuye akuoneni
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
Ngati akukwanitsa kupompa magazi awanthu angakhale ndi chisoni ameneyo
@RudeyIce
@RudeyIce Күн бұрын
Useless president uyu sangathithandize
@LomossiSichiimbauavivafrelimo
@LomossiSichiimbauavivafrelimo Күн бұрын
Kumalawi anthu ovetsa chisoni odalila zolandila😅😅😅😅😅😅😅😅
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu Күн бұрын
Ndpo zonadi nde ali nd khalidwe lomat yemwe ndadya ndalama yake ndiyemwe tapase vote akuiwala kt akugawa ndalama colinga cot akawina ataye kuvutikaso zaka zambiri sakuganiza mot akhale kuthekera kosakayekha kom ai
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 Күн бұрын
Kkkkk shame on you Mr.President.
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi Күн бұрын
Fundo less president
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Күн бұрын
Ndege inafika ku mzuzu- Wafika ku parliament.
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya Күн бұрын
Mcp ❤❤❤❤ kt buuuu
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 Күн бұрын
Poor president Malawi ever hv in history eeich zimu wachilima use mumtendere
@omarmussa8282
@omarmussa8282 Күн бұрын
Chaponda tulo too much... Kodi sizingatheke opposition reader kusintha?... Atakhala Suleman nde deal
@AleCloset
@AleCloset Күн бұрын
Ku parliament kwazaza agulo a madzi mmitu... Suleman u r the man.
@VincentKamwendo-e9t
@VincentKamwendo-e9t Күн бұрын
Background ridm disturbing
@AdamMwamadi-p2j
@AdamMwamadi-p2j Күн бұрын
Bwana wake uti
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
Eti wasatanic yu
@ProspaDMitummba
@ProspaDMitummba Күн бұрын
Our useless president Mr cikangawa😂😂😂😂😂
@EdwinZiwa-x2g
@EdwinZiwa-x2g Күн бұрын
Uyu ndi president wa mcp not wa malawi ayi saziwa kanthu uyo
@TriciaMalikebu
@TriciaMalikebu Күн бұрын
Kenakotu nyengo idzayankhula, kukana, zinazi ayi fisi adakanadi mtsatsi. For once take responsibility achimwene
@KhwimaPhiri-r3w
@KhwimaPhiri-r3w Күн бұрын
Awatu wkungokakamizika ndianthu awo muwone pano anasiya kutulusa mawu
@EnerstManess
@EnerstManess Күн бұрын
Munthu oyipa uyu
@zayeddawood4673
@zayeddawood4673 Күн бұрын
Uchose ka nyimbo kakumveka pansika zimene zikuyakhulidwa sizikumveka ife cholinga chanthu ndi khani zimene zikunenedwa osati nyimbo so just remove that
@ShazidaAlfred
@ShazidaAlfred 3 сағат бұрын
Kodi mabatani amamasuka akamaima kapena anatenthedwa😂😂😂😂
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Ngati APM Ali more educated bwanji sanapite ku parliament kukayankha mafuso
@edwinearlkachiwala3070
@edwinearlkachiwala3070 Күн бұрын
Mmmmm what?
@MagieJames
@MagieJames Күн бұрын
Nanuso kukongola kwake kuli kt handsome nd kabambe
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe Күн бұрын
AmangodIwa kuyankhula cchizungu ngati mzungu wa ku Britain koma mmutumo muli thelere lokhalokha
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
Ndi americani
@MagdaraneChidamula
@MagdaraneChidamula Күн бұрын
Ii abale mwaonjeza tiyeni tizingopemphera apa ndikumapanga manyowa kaya nkozo nkumakathira kumaminda mvula yagwayi mwina kupuma kudya chitedze😢😢
@MustapherLino
@MustapherLino Күн бұрын
Chikangawa party wakupha iwe chakwera
@JamesAlifu-v8j
@JamesAlifu-v8j Күн бұрын
si doctor so ameneyo ayi koma machende chakwela amalawi amakhala ngati anabadwa ndi nkolo limodzi kupusa akuwona ine ndikadankala ndili kumalawiko ndikulumbila kamachende uyu tawombera kalekale sakifunikaso kunkala wamo ayi kungo koka machendewe basi malawi yose kukanika kupha ameneyu malawi ndi mbuzi za anthu ndimene inafe timaganizila sitingamasunge muzi yimene yikutimpela anthu ofunika ayi ameneyu kungo mukoka machendewo basi
@VinciusmajiduMchepaanaffi
@VinciusmajiduMchepaanaffi Күн бұрын
Mizimu ya anthu 9 ibwere paiwe nd banja lako 😢😢 uli nditsoka
@CharityKampanje-wz4wu
@CharityKampanje-wz4wu Күн бұрын
Ukunama presdent ndi amweyi deeper mr presdent braval
@gracemnenula2518
@gracemnenula2518 20 сағат бұрын
Kodi ankamusankha chaponda ndani coz panali Mai Navintcha ndipo amayankhula bwino kwambiri Adpp muganiza bwanji kusankha chaponda Bambo wa ziiii yu aaaa
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 Күн бұрын
Chikangawa
@BillyBentryMunthali
@BillyBentryMunthali Күн бұрын
Osati anayitanitsa president koma anachita kukonza yekha nkupita ku parliament pemene ena mmbuyo umo ankakanika kupita
@KingstonPhiri-g5h
@KingstonPhiri-g5h Күн бұрын
Ndewe galu kwabasi👌
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Nothing is shame this is the president we want in Malawi shame on Muthalika agogo
@Andule-v4n
@Andule-v4n Күн бұрын
Chitipa east just wants a ministerial position
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
Osaiwalannso kumwa magazi ndi namapompa
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 19 сағат бұрын
Kodi mwamuona amene anatapa nyemba ya mkazi wa dan lu 😂😂mimba
@GeorgeSathula
@GeorgeSathula Күн бұрын
Koma chikangawa mawu ngati chinapha ........... Zaziiiiiu
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Bola Mr chikangawa kusiyana ndi Mr albino
@andrewkachule5049
@andrewkachule5049 Күн бұрын
I must confess the so called opposition dpp is gone this leader of opposition is nothing but a mere grany
@DerlinNyirenda
@DerlinNyirenda 20 сағат бұрын
Mtundu woziwa kutukwana ndi kunama. Itsatira ake nayo ndi anthu odziwa zomwezo
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda Күн бұрын
Chisiru chamunthu chakwera kukamwa ngati msapato
@AaronMasina
@AaronMasina Күн бұрын
Uyu ndi katundu.... wa DPP sadapiteko uku.... Komano it's a must to increase the salaries with 60% ... Kutengera kukwera kwa zinthu pa ground,Eg; k1,000 per kg Chimanga
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Chakwera sanaphe chilima koma the muthalika's anapha chasowa athu 21 ku mzuzu ma albino osawelengeka
@MMK-p3y
@MMK-p3y Күн бұрын
Nthawi zambiri nkamawanvera olemekezeka a president a dziko lino, ndikumanva chisoni kwambiri. Akufunika athandizidwe bwino kwambiri. Sizikuyenda. Sizikuyenda. Kwa amene timadziwa za economics and government state eish, akufunika kuthandizidwa olemekezekawa.
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Forest ya chikangawa ili momwe ilili afiika ku parliament ndi machine opangila machine azawo
@MatthewKaliyati
@MatthewKaliyati Күн бұрын
Kodi ndinu anthu openga munakhala bwanji, yemwe asalibwanayo ndiye ndani popeza inenso ndine bwana also wina aliyense mwayinu akudyanawo misonkho yathu kumeneko
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Ngati ali wakupha DPP ndiyakuphaso imakatani ku parliament kukavetsela wakupha
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 6 сағат бұрын
Chakwera ndichitsilu kwambiri mudziko muli njala anthu akudya chitenze matumba achimanga oti agulitse agule feteleza achitenga kutiko ngt anthu akugona ndijala
@KhwimaPhiri-r3w
@KhwimaPhiri-r3w Күн бұрын
Kod amasiyilanji kukhosomoleleanthu
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Chakwera sangavetse chisoni zake zili pabwino ma supporters ake tilipo ngabwi ngabwi akuvetsa chisoni ndi Muthalika with old age
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Sulemani akunama big yafika akatundu omanga ndimawaya
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 19 сағат бұрын
Chigawe chomwa mikozo malovu ndi magazi chafika chakwera ndiwe chilombo
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Ine ndikuti boma ndilomweli koma ndimasaka ndekha zikuthekaso kwambili
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Ngati ali mbuzi aphungu onse a DPP ndi mbuzi coz anali Koko kuvetsela
@InnocentHassan-m3r
@InnocentHassan-m3r Күн бұрын
Iweyoso ndi mbuzi
@MagdaraneChidamula
@MagdaraneChidamula Күн бұрын
Abale muzilankhulako chichewa becoz amalawi ambirivngosaphunzira.
@DanielKamwathendo
@DanielKamwathendo 16 сағат бұрын
Kulibe opposition ku malawi a chaponda kugona too much zomwe zikupangitsa kuti MCP izitansa komanso isatuluke m'boma ndipo 2025 ikuwinanso.
@LameckNgwira-t6s
@LameckNgwira-t6s Күн бұрын
Where is AIP Mr president????
@LuciusKwenje
@LuciusKwenje Күн бұрын
Dpp singawine mudzi umodzi kukhara candidate president atatu so shame kwambiri ku Mcp kulibe zolimbana pa undindo wa president
@ibrahimbamusi109
@ibrahimbamusi109 Күн бұрын
Ndiye zikungoonesela tu kut mukamati wa nzeru ku mcp ndi chakwer basi big up chika
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy Күн бұрын
Zaziiiiii
@MartinKapito
@MartinKapito Күн бұрын
A Thu sangafune udindo Ku mcp akuopa kufa Ku.wedwa magazi Ngati anamalidza. Magazi awanthu 9 kanthawi kochepa bwanji amakhala mmodzi adya ndi mafupa omwe
@InacioCement-t7n
@InacioCement-t7n Күн бұрын
Kodi nkulu ameneyu sakufunika pemphero akuoneka mwa chiwanda ndiye mfiti zikuombera manja ana anjoka
@Yusuf-j6c
@Yusuf-j6c Күн бұрын
Awa amangozwa kuyankhula chizungu bas no actions mbuzi yeniyen
@patesnkajenda4258
@patesnkajenda4258 Күн бұрын
Chizungu apule a malawi akufuna chakudya ndi feteleza kozani zimenezo anthu akuvutika
@WalesSadick
@WalesSadick Күн бұрын
Sound musamaike zikumavuta kuva
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Күн бұрын
Parliament ya kwathu ku Malawi zochitika za ma MP kuyambira a OPPOSITION NDI A Boma umbuli okha okha
@BusaGaniza
@BusaGaniza Күн бұрын
Chakwela is akiller
@CharityChirwa-v8v
@CharityChirwa-v8v 17 сағат бұрын
Nkhoswe wankulu palibe chomwe akuziwa maganizoake akulota kuchipiku konyamula sugar 😂😂😂😂😂mbuzu yapachingwe
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Muthalika ngakhale likasalo angawelenge Malo momaliza nkonono
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Chakwera wayakha bwino mafuso agogo aja anakanika kupita ku debate 2019 kuzikonda basi
@JamesYusufu-l6d
@JamesYusufu-l6d 13 сағат бұрын
anthuinu. ndisili zokhazokha. ndichakwela wanuyo. anthu onenepa misonkho yamalawin agalu iwe chakwela uziona kapeni akayambika. mbuzi
@ShakiraIdrissah-o8w
@ShakiraIdrissah-o8w Күн бұрын
Savage president
@SostenPiyo
@SostenPiyo Күн бұрын
Koma apapa pali cha mnzeru chanji,sindikumvapo cha mnzeru, tiyeni ngati a Malawi tipemphere kwambiri chiwanda chikulamulira Malawi ndithu
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Күн бұрын
Bwana ameneyu ndi wakunyumba kwanthu kumene mesa inu bwana wanu ndiwakupha ma albino ujan
@ChisDammah
@ChisDammah Күн бұрын
😂😂😂Palibe fundo yomwe ndanva pamafuso omwe wapasidwa
@GiftMuyungu
@GiftMuyungu Күн бұрын
Ichichi ndichitsilu pazitsiluzonse zomwezili padziko lapasi pano
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya Күн бұрын
Uvotelela pa social media pa ? Anthu omvetsa chisoni inu ndipo muzingotukwana km boma simudzaliwinas ai
@BeatŕiceMfundenji
@BeatŕiceMfundenji Күн бұрын
Amene akuti boma ndilomweli Mulungu amukhululukire
@Sofi-p1v
@Sofi-p1v Күн бұрын
Chizereze cha pulesident Waononga malawi uyu achoke
How to treat Acne💉
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 108 МЛН
How Strong Is Tape?
00:24
Stokes Twins
Рет қаралды 96 МЛН
SOFTWARE that can Send You a Fake POP | Calvin Rafadi
2:36:48
King David Studio
Рет қаралды 85 М.
Война, Сирия, цены: как прошла прямая линия Путина
33:29
BBC News - Русская служба
Рет қаралды 33 М.
My life began in prison | Solly Mankga
3:34:48
King David Studio
Рет қаралды 570 М.
Wits School of Governance Election Series with Mr Julius Malema, President of the EFF
2:35:53
The Wits School of Governance
Рет қаралды 254 М.