MANGANYA VS AKWENI - KWAPHULIKASO INA KU UTM

  Рет қаралды 52,673

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 157
@AgnesLeonard-e2j
@AgnesLeonard-e2j 2 ай бұрын
More 🔥 kweni ndimakunyadirani simusekelera zopepera ,aweee
@BentryChavinda
@BentryChavinda 2 ай бұрын
Koma a VP ,you cannot settle the dust within UTM on public meetings but through dialogue.
@Clement-vh5pf
@Clement-vh5pf 2 ай бұрын
The name of SKC is used now yet the same government did not honour him while alive and all his manifesto were not implemented.VP should ask himself why Chakwera was not listening to Chilima for 4 years yet had powerful suggestions that would develop Malawi.
@Okalekale
@Okalekale 2 ай бұрын
Corruption implication ija bwanji Chilima uja?,analidi serious zotukula dziko?.Andale ndi ma crooks,ndi mwa mwayi kuti anthu apeze munthu ngati Bingu. Amai Kaliati ndi ena azipani zinali mu tonse ndi anthu oyipa,akufuna ma political scores kuchokela pangozi ija kumati Chakwera anapha anthu aja (ngakhake akudziwa kuti alibe umboni kafukufuku sanachitike)ndipo Michael Usi is a sellout popitiliza kugwira ntchito m'boma.Patricia Kaliati ndi opportunist opanda manyazi komanso opanda chisoni pofuna kutenga uPresident wa UTM.In other words she's happy that Chilima died and Michael Usi remains in govt. with the alleged killers whom the electorate isn't happy with,so that she catapult herself to the presidency of UTM Andale ndi mbanda,hypocrites,Poona kuti anthu aja afa anaonelatu gap,gap yake ndi yoti,aMalawi akhuluilira kuti Chakwera or MCP yapha anthu aja chifukwa cha history ya Kamuzu,sinanga aMalawi ambiri school alibe, ndiye Chihana ndi aKaliatiwa akugwiritsa ntchito infa ya anthu aja kupezela support kuti mwina ndi m'gwirizano wawo or paokha paokha angadzawine.Ndiye amaiwa akumukankha VP mudzina la u sellout ndicholinga chofuna uPresident wa UTM,satan wa m'mai. Kutuluka m'boma sichifukwa cha imfa ya a Chilima ayi,anthuwa amakanika kuba m'boma chifukwa kunasintha,taonani Chilima weni weniyo anapezeka ndi mlandu waziphuphu.VP Usi ndi munthu was serious pa ntchito komanso okonda dziko lake,sali m'boma kukayang'ana mitaji yokuba koma kuyesa kusintha miyoyo ya aMalawi ndichifukwa sanachoke kukapanga ndale zombwambwana pamene aMalawi akudikila zitukuko ku madera awo.M'mayi uyu ndikale anayamba kusakasaka uPresident ndichifukwa amasinthasintha zipani kwambiri.Chihana ndi m'mai uyu ndi andale oyipa pa Malawi sangatithandize or pang'ono awonetselatu pano,koma ndale oyipa kwambiri. Mbuli komanso mfiti za a ndale zigwiritsa ntchito imfa ya anthu aja m'ma campaign kuti m'malawinso osazindikila adzawavotele.Malawi ak 13:37 upita kuphompho.
@nishanchiwaya4561
@nishanchiwaya4561 2 ай бұрын
Amanganya ndiwe chitsiru kwambiri
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 2 ай бұрын
Koma Malawi sazatheka , zi anthu zamitu ngat nguli pasipasi zili zoona bwana 😂😂
@ChristianMtambalika
@ChristianMtambalika 2 ай бұрын
Umene akupanga manganya zibwana ndipo alibe dzeru zomwe akupangq chakwera zikusangalqsa
@ArnoldThomson-d6v
@ArnoldThomson-d6v 2 ай бұрын
Pobela makobidi pa manganya wawona kuti alowele popatsa anthu ngongole kuti naye adzichotsapo Kod amalawi munakhala bwanji inu kumangopusitsidwa, Ndalamazo osakapeleka kuma company bwanji akutsitsileni katundu
@AgnesLeonard-e2j
@AgnesLeonard-e2j 2 ай бұрын
More 🔥kweni,susekelera zopusa,awe kaliyati
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 ай бұрын
Adzimai tsakusangalala povina sangavine ndi misozi mmaso yaku chikangawa,ine koma manganya tidzikutchula 🤸🤸🤸🤸
@andrewmazunda3846
@andrewmazunda3846 2 ай бұрын
Rest well SKC. Your legacy will live forever 🙏
@PaulPoyah
@PaulPoyah 2 ай бұрын
Manganya wabalalika
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju 2 ай бұрын
Becareful usi u will regret on day ....and you need to think before you do things...Ahlomwe respect always
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 ай бұрын
Mai number one kaliyati❤
@emmaculatemenzeiwa
@emmaculatemenzeiwa 2 ай бұрын
Mangamanya's deliberate move to destroy the party
@emmammatsa1284
@emmammatsa1284 2 ай бұрын
Nanga tikawaona wodya zake alibe mlandu ndi abalenso amenewo?
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 2 ай бұрын
Hule uyu Manganya wagonana ndi ma Sikono mpaka mkazi uja banja lake linazasokonekera chifukwa cha ameneyi ndi makumbukiranso uyu Gradys ankamufuna mpaka zinathera ma penalty adamukana Usi simunthu ai
@StanleyChinsewu
@StanleyChinsewu 2 ай бұрын
Akweni ndi VP onse asiye ndale onse akubisala kumbuyo kwa chilima
@pacharokoloviko1694
@pacharokoloviko1694 2 ай бұрын
Ingoyambisani chipani chanu bwana mupange mgwirizano ndi MCP cz palibe supporter wa UTM weniweni akukondwa nawo mgwirizano ndi MCP
@BigeeMsuthu
@BigeeMsuthu 2 ай бұрын
Kkkkkk gyx zoikana chisaka zidatha chifukwa Chan ngongole mukufuna kugawa chifukwa chot ma vote awandikira, cholinga mufuna mwakope mtingongoletu bas, mudari kut nthaw Yoseyi???
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
Nkhani ndiyakuti anthu anakonda chilima osati chipani mwini wake wamwalila mwayamba manyaka okhakha 3 stop
@TanazioUziyele
@TanazioUziyele 2 ай бұрын
Vp ankaufuna ndi kaliyati zaonetselatu
@AyebhoMfumu
@AyebhoMfumu 2 ай бұрын
Manganya you went to school komano ulibe mzeru 😅 zamanyazi😢
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 2 ай бұрын
Amufunse Mkaka with that arrogance, what has happened now??
@IyshaBakali
@IyshaBakali 2 ай бұрын
Usi kuyesetsa kuthetsa chipani cha utm Koma team chikangawa mmmmmmm mupala
@MphatsoIshmaeladam
@MphatsoIshmaeladam 2 ай бұрын
Ife tidaionera patali usi ndi wa MCP ndipo UTM mukachedwa kuchosa usi muononga chipani
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o 2 ай бұрын
Zandalezi zikundidwalitsa mitu😮😮
@Lee-lee-w1r
@Lee-lee-w1r 2 ай бұрын
Koma ndipo inu!! Andalewa ndizitsilu za anthu kwabasi. Mmalo moti azingokambilana amafuna kutipweteketsa mutu ndi za ziii
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 ай бұрын
Amalawi ena ndinu dzitsiru usavage kusaphunzira nkugona komwe mumadana nchiru ngamo, Ndipo Utsi ndichitsiru chamunthu Yudasi Mai kaliyati Ndi wa mzeru Ndi amene akumva kuwawa pophedwa Chilima pamodzi Ndi mamembala ena Chifukwa mzimai Ndi amene ama bereka manganya akulondola kudya Kwa Nkhumba imzakeyo Chakwerayo Kuma lawi kwanukooooo
@MonijaKataika
@MonijaKataika 2 ай бұрын
Awatu alibetu mfundo sakufanana ijatu ajawa🙈. Zokamba mbwewe osatolapo kanthu...APM my vote
@DENSONZULU
@DENSONZULU 2 ай бұрын
Akweni 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@PricillaMatewele
@PricillaMatewele 2 ай бұрын
Respect Akweni
@AnusaSowan
@AnusaSowan 2 ай бұрын
Manganya lipoti la imfa ya skc likamazatuluka uzakhala pa nambala 2, ka predator iwe
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 2 ай бұрын
Magalasi akula gulani asaizi yanu a Usi kkkk. Ngati president mukanaitana anzanuwo osati kuima pamenepo kuuza dziko
@JosephEmmanuel-nv5td
@JosephEmmanuel-nv5td 2 ай бұрын
Manganya ndi kape kwabasi iyaa asatinyasepo
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 ай бұрын
Ku utm kulibe mpungwepungwe as you say koma usi yoo nde si wa utm
@spargomw
@spargomw 2 ай бұрын
Manganya ndiwa ma drama😂😂😂 u vice wangogweramo
@EffordKapichi
@EffordKapichi 2 ай бұрын
Manganya is a truelly dramatist he has just found himself in vp presidency flookly .
@EffordKapichi
@EffordKapichi 2 ай бұрын
Vera and manganya are not devoted to utm. They are after money .let them vacate .
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga 2 ай бұрын
Manganya ndi mthira kuwiri yudas sikalioti adampereka mzake chilima lero akupereka salute kwa madam Mary chilima fokofu usi tinakuzindikira kale kuti ndiwe wa MCP khala ndi Dr Chikangawa wakoyo .akweni kaliati samasekerera zopusa uyo ndiye mwadyiwanatu ngati sukuziwa uyo ndimwamuna mzako ndala anaymaba kalekale makona ose andale akuwaziwa .kape iwe usi magalasi nawoso si asayizi ako
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Kaliyati akuwonga chipani msabakile nthawi yimene abingu atamwalila kaliyati anapangaso chomozi mozi ndipo mwakaliyati mlibe usogoleli yake ndi nsanje basi koma nanga malamulo achipani akuti chani kaliyati uli ndi vuto
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 2 ай бұрын
Koma kumenekoo!!!!🙇🙇🙇
@FastCement-c7n
@FastCement-c7n 2 ай бұрын
Malawi sazakonzekaso
@MuyaoComedies
@MuyaoComedies 2 ай бұрын
I'm following Salam alaikum
@InnocentAssan-st3hb
@InnocentAssan-st3hb 2 ай бұрын
Waleko m'musalamu
@ganizanimsowoya9843
@ganizanimsowoya9843 2 ай бұрын
Ndale zaku Malawi 🇲🇼 zosekesa
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 2 ай бұрын
Akweni for President ❤❤❤a Micheal Usi sanawoneste khalidwe panthawi ya zabvuta ya chillima,mau awo oti vice amaeyenda ndi president,nanga SCK amaeyenda ndi a president???he was happy kutdziwa kuti atwnga mpando
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 2 ай бұрын
Manganya ndi wa MCP asakupusitseni
@PortiaMhlambi-y4g
@PortiaMhlambi-y4g 2 ай бұрын
Zoona akweni osaopa osafooka,
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 2 ай бұрын
Manganyayi mzeru mulibe guys, coz these are sensitive issues that needs contact dialoque not in public life this, he was supposed to called Mrs kaliyat n others to sit down n discuss
@shapilchaponda9906
@shapilchaponda9906 2 ай бұрын
I feel like he didn't show leadership after the accident. If he did , zonsezi kulibe .
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 ай бұрын
Ndiye unapanga zoti achilima azipita iwe unkhalepo pa pando gulu iwe kwambili
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 ай бұрын
Usi ndi wa MCP
@zionekansinde2817
@zionekansinde2817 2 ай бұрын
How can a whole VP settle issues like these on a public podium? Pls guys be matured and act as matured people. How then can we trust you. Be matured!!!
@MaggieToneki
@MaggieToneki 2 ай бұрын
Ine makolo anga akugona ndinjala izizi za Anthu okhuta izi forseck zitafunanani
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 2 ай бұрын
Koma akweni pakamwa pawo popasula amafuna u VP Kaliati
@FWhite-w3l
@FWhite-w3l 2 ай бұрын
Ulemu upereke lero kwa madam chilima cause walanda udindo Mmmm yudasi
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 2 ай бұрын
Palibe a UTM apa Propaganda UTM yeni yeni ili ndi Kaliati
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 2 ай бұрын
This is true Akweni ndie magazi a UTM
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 2 ай бұрын
@@fredgabrielnyangulu very good
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 2 ай бұрын
Koma kwen kwa ine sandiwaza kwenkwen, ndi mmai owopsya kwambili sayankhula bwino some times, ndi mai ovuta kumfikila moti ndimakhulupilira kt even atolankhani ena amantha kwambili anasiya kumufusa mafuso kuli kuopa ishiii ai Mai asamakhale choncho chifukwa amapeleka picture yoyipa kuti ozindikila ndie kuposa onse and chilima anaziwa kuti apa si kuti tiendele 50 50 kuti vice akhale nkazi mayazi anaziwa kuti umu mwa kaliati muli moto wa lawilawi
@ArnoldKhandeya
@ArnoldKhandeya 2 ай бұрын
big mwayamkhura tava kma pangan zawumunthu , ndidziko ili, kunjakuno kuli mulungu
@AyamiClement
@AyamiClement 2 ай бұрын
Iwe manganya wallah uli nzeru ndkuwonani kkkkkk
@RonaldChirwa-e8n
@RonaldChirwa-e8n Ай бұрын
Zimatha izi ndi nkhani yosavuta munthu akafuna kukhala mtsogoleri akhale kapolo wa omwe ufuna kuwasogolera
@alexmkolongo3089
@alexmkolongo3089 2 ай бұрын
Usi ndikazitape Musamale naye chilima sakanafa2 koma zimene amakambilana uku amakamuuza chakwela
@prettytambala5687
@prettytambala5687 2 ай бұрын
Ati akakumana kuti komwe azikafusana mafuso ndi bwanawo😅
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 2 ай бұрын
Ausi inuso dyela too much, aaah iwe usi ndi galu kwabasi ukunama MCP si abale amenewa asaukisa ziko amenewa moti ukumenya kampeni ya MCP aaah iwe enafe si ana kusekelera zofooila zakozo.
@Yungjoe786
@Yungjoe786 2 ай бұрын
This guy 💯% belongs to MCP n I guess even those supporters they're from the same crocodile party angobvala ma uniforms a UTM shame
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 ай бұрын
Boza usi ndi wa MCP Galu usi❤
@loveshabani8834
@loveshabani8834 2 ай бұрын
Manganya adali NDI cholimgadi chothetsa UTM koma akunama ameneyo atha ndi iyeyo
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 2 ай бұрын
Chitsiru iweyo tulukamo amene sia UTM uyu ndiye ulikuti iweyo ndiwe wa MCP uli ku chikangawa
@MARKODSOLOMON
@MARKODSOLOMON 2 ай бұрын
If u really deserve to be a leader why not conduct top official meeting than coming on the platform and intimidating your own team.
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 ай бұрын
Nkhani ikuwawa Ndi yoti Amcp apha Chilima,koma Wanthu afuna aziwe chilungamo Ndiye uku lepheresa ndiwe Chitsiruu manganya mbuzi ya Munthu,chitsiru Ndi MCP yakoyo Ndi Galu mzako chakwerayo nkhope ngati kuphazi Kwa Njobvu
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 ай бұрын
Manganya aise ichi chakoma ichi chakoma 🙊🙉anagwa chagada ,iweyo khara ku mcp konko wayambaliti dzimenedzo,dza ma verse komaso dzotsatsa anthu kutenga ngongole
@SuzenBokola
@SuzenBokola 2 ай бұрын
Zopusa manganya kutoso basi ndiwe Wa MCP iwe
@PatrickDzanjalimodzi
@PatrickDzanjalimodzi 2 ай бұрын
Usi sakunama apa SKC anali boma pamodzi ndi Usi yemweyo ndipo Usiyo anati bwato satsitsilana pakati panyanja akatathauza chiyani apa
@Itemsworld
@Itemsworld 2 ай бұрын
He can't fire the secretary of utm, he don't know where he belong and who is with him
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 2 ай бұрын
Chipani Cha MCP ngati chimapezeka pa second pama general election nanga pano chili m'boma Ife a UTM tisamale 50+1 patokha without late SKC chathu palibe
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 ай бұрын
Upusa wekha manga ya,,sionse Amati ambuye ambuye amene akalowe kumwamba ,,usatipusise ,,iwe siwathu
@JosephyprosperMkandawire
@JosephyprosperMkandawire 2 ай бұрын
manganya akupha samala MCP ndi boma loyipa
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 2 ай бұрын
Ulemu wanu Mrs kaliat
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 2 ай бұрын
Ubwino wake ananena kale kuti oyamba kukapsa moto waukulu ndi iwowo ndi anzawo
@ErickTym-u2m
@ErickTym-u2m 2 ай бұрын
Manganya mapazi ako ndithu
@praisechikuni8200
@praisechikuni8200 2 ай бұрын
Anthunu muoange zanu, chilima anapanga zake anapita nazo ,kambani nfundo zanu siyani za chilima mnzimu wake uuse muntendere
@mkupabanda-nd2vb
@mkupabanda-nd2vb 2 ай бұрын
Manganya ndi kappy
@JamesEuginio
@JamesEuginio 2 ай бұрын
Manganya anapanga pa interview yake ndi joab chakhaza anati ngongole saitanira Lero watembenuka akuitanira ngongole wasavuka uyu waphwanya chipangano
@MorganLucious-ny8nl
@MorganLucious-ny8nl 2 ай бұрын
Ulibenso mfundo manganya dipo wabalalika kubalalikira2
@TrizaTalandira
@TrizaTalandira 2 ай бұрын
Uyu manganya asapusise anthu ndi wamcp kuchokera kale uyu
@PaulPoyah
@PaulPoyah 2 ай бұрын
Manganya ndi galu kwabas ...fisi ndi chakwera wakoyo
@meditationmusic293
@meditationmusic293 2 ай бұрын
A manganya sangazikwanise zomwe akupangazi
@RuthMandawala
@RuthMandawala 2 ай бұрын
Likupitakwaod😢
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 ай бұрын
Manganya pamtumbo pako ndi Chakwera wakoyo munapha Chilima kuthako kwako ndithu siwe wa UTM mbolo yako wakhala ukuchinda ma Sikono mpaka banja lawo linatha galu iwe kunyinikwako
@williamhara1866
@williamhara1866 2 ай бұрын
Moto ukazima pamatsala utsi. If you know, you know!!
@JamesChaponda-em7op
@JamesChaponda-em7op 2 ай бұрын
Bwana vp fire the secretary General please
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 2 ай бұрын
Unapa chilima kufuna udindo
@ForestElf-z1h
@ForestElf-z1h 2 ай бұрын
Please choose one position and follow hart ❤ which you are behaviors thanks,,,,
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 2 ай бұрын
Yudasi wachabe chabe uyu,drama yaku Tikuferanji yeni yeni
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 2 ай бұрын
Ndie guys utm-yi izatha ngati makatani anthu ake si achina kaliati-wa ndiwa ntima kwambili ngati si mai ndale zinamulowa ndi mmafupa momwe kwa ine kulibe chilimbikiso koma za ausi izi ndimachita kuonekelatu kuti ndi wa MCP
@SueWahna
@SueWahna 2 ай бұрын
Akwenitu sapempeza mafano mwavalazo mwayamba lit kapena mavala pogona 😂😂😂
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 2 ай бұрын
Chilima anali dolo,akweni ingotengani position ya chilima coz inuyo ndiye mukulimba mtima
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
Awusi ndani sakuziwa Kuti munali limodzi ndi achikangawa popanga ma pulani wopha chilima
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 2 ай бұрын
Tiye uko unagulitsa chilima ndiweyo unkafuna kampandoko ka uvice dyani nawo ka last muli paulendo 2025
@HaliJana
@HaliJana 2 ай бұрын
IWE USI UMUUZE CHAKWERA KUTI NDI MBUSA KOMA AKUPHA WANTHU BWANJI NDI MKHILISTU MWINA AI
@StoneckJali
@StoneckJali 2 ай бұрын
Akanamuchotsa ndi a malemu osati inu
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no 2 ай бұрын
Avice musadandaule onse onyoza , adzalandira mphoto yonyoza
@WizeyManyozo
@WizeyManyozo 2 ай бұрын
Km manganya 😂😂😂 fundo mulibe
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 ай бұрын
Manganya ndi amene akubweletsa zosakhala bwino chifukwa iyeyo ali.ndi chipani chake ndiye akufuna chani ku UTM moti iyeyo anachoka kale kale lero ali.ku MCP
@SithembilePhiri
@SithembilePhiri 2 ай бұрын
manganya ulibe chilungamo iwe
Human vs Jet Engine
00:19
MrBeast
Рет қаралды 74 МЛН
She's very CREATIVE💡💦 #camping #survival #bushcraft #outdoors #lifehack
00:26
acts of prophet miracle paul
17:23
MiracleGod1
Рет қаралды 23 М.
TIKU 30 JUNE 2018 B
27:20
Edson Gunsalu
Рет қаралды 222 М.
MICHAEL USI WAYANKHA ZOMWE ANANENA A FELIX NJAWALA KU MZUZU.
8:04
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 26 М.