MICHAEL USI WAYANKHULA IZI LERO ATAFIKA KU IMMIGRATION YA KU BLANTYRE

  Рет қаралды 5,634

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 31
@AlexanderYovatiKhumalo
@AlexanderYovatiKhumalo 2 ай бұрын
Weldone V/ P you are doing what the VP should do keepon serving the Malawians.
@kumbukanikafwafwa
@kumbukanikafwafwa 2 ай бұрын
Ndale izizi. Challenge ndiyaku even Muthu atakhala akupanga zithu zokomela dziko, but ngat Ena ake zikuwaphinja bas zimasanduka ndale. Umakwana manganya.ngat zikuwanyasa akasume🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@rashirdbanda8204
@rashirdbanda8204 2 ай бұрын
Awaa atikwana bwanjii
2 ай бұрын
Kamba za ma passport iwe munthu... sizikugwirizana ndi za mankhwala apa
@Jerry-vm6mo
@Jerry-vm6mo 2 ай бұрын
Awa awo ndi ma drama osati ndale. Nanga pamenepa walankhula zichiani..
@OsmanNgwali
@OsmanNgwali 2 ай бұрын
Hiyaa nothing can change coz zinalo ndale zithuzi
@OsmanNgwali
@OsmanNgwali 2 ай бұрын
Akufuna ma allowance amenei
@LeoYokonia
@LeoYokonia 2 ай бұрын
Why you didn't ask about corruption
@petertaulo8014
@petertaulo8014 2 ай бұрын
Ngati watumidwa ndi Chakwera's family! Kuti uzachite push their family business here wauponda.
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado 2 ай бұрын
Akuoneka kuti samayembekeza kuti angakhale vp alangizi ake please mulangizeni asamangozigwira gwira ayi oooo ndaona akusowa mtendere wa mumtima
@CathrineBizza
@CathrineBizza 2 ай бұрын
Ukulimbana mdi zikhale ohoooo kkkk
@AREFRIEDNELSON
@AREFRIEDNELSON 2 ай бұрын
Koma yudasi uyuuuuuu😅😅😅😅😅😅 kumpereka yesu
@LonjezoAkacharlie-r2q
@LonjezoAkacharlie-r2q 2 ай бұрын
Guys kodi mukuyamikira zichani pamenepa. Palibe chamzeru chimene wayankhulatu uyu
@HamiltonRaphael-q2d
@HamiltonRaphael-q2d 2 ай бұрын
we get tired of useles govt
@petertaulo8014
@petertaulo8014 2 ай бұрын
If he was clever enough he should start this in Central Region! Opusa Michael Usi. When did you spoke to PS 😂😂😂😂😂 Manganya!
@itubiz1501
@itubiz1501 2 ай бұрын
inuyo ochenjera? a Malawi muthu achite chabwino mumuloza zala apange zoipa ndiye worse...tonse stingayendese dziko man even amene mungafune inuyo eyendeseo papezekabe ena osawakonda. muona koma kuti mutaani
@henryphiri6100
@henryphiri6100 2 ай бұрын
Malawi immigration office ndi dimba la nick chakwera ndi zikhale ng"oma motsogozedwa ndi Lazarus. Yankhulani chichewa akulu palibe nzungu amene akukuvetsa nyasi ya chizungu chimenecho.yankhulirani munthu wakudzi ave.
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 2 ай бұрын
Amalawi 😅😅
@petroszgambo9949
@petroszgambo9949 2 ай бұрын
Judas weni weni, at akufuna kuti tiziwe kuti akulankhula .. nonsense! Politician fool.
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 2 ай бұрын
@@petroszgambo9949 bwino nthawi yatha iyi yesu akubwera muchimwa nazo zambili muziwone ndi maso a uzimu zikutsegulani maso kuti yes chofunika kukonza mtimawu siziyenda momwe tikufunila kaya ndi economy,njala,matenda,nkhondo ma floods,ananena kuti zidzachitika mu nthawi yakumapeto zikomo kumbukilani sodomu ndi gomola ndi momwemu angakhale mu nthawi ya nowa
@Chilinga_P
@Chilinga_P 2 ай бұрын
Akungolongolola ..phokoso basi....system ya ku immigration yakupeta and he likens it to medical / treatment system
@patiencechangole9825
@patiencechangole9825 2 ай бұрын
Apite ku capital hill akayankhule kumeneko ngati ali serious
@JamesKhengemussa-t1d
@JamesKhengemussa-t1d 2 ай бұрын
Kuno nku Malawi basi tizidikila tsiku lakufa
@AbunthiMtambo
@AbunthiMtambo 2 ай бұрын
Zaziiiiiii 😂
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 ай бұрын
I wish I can speak to him in person asatiyese ife opusa ndale iziii
@MakupeWekha
@MakupeWekha 2 ай бұрын
Waste of time and resources
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 ай бұрын
Za ziiiiiiiiiiiiiii musatipepeletse ife mukudziwa zomwe mukupanga anyani Inu munalonjeza kuti ma passport mwayamba kupanga lero kuli ziii zili zabodza amalawi mmationa ngati opepela eti agalu Inu Ali ndi #ya Micheal manganyayo andipatse ndimuimbile pompano mxieeee
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 2 ай бұрын
Nenani ndinu zennizeni anthu abwino amzanu a nyani good for you
@kumbukanikafwafwa
@kumbukanikafwafwa 2 ай бұрын
@@VictorKachulu-y3n kkkkk palibe wabwino padziko lapansi. The guy is trying hard. Akulubwawa ndi ana oti sakuona chabwino pa chilichonse. Zimaoneka bwino Muthu uja akachokapo. See the Presidency trend bwana. Komaso iweyo moti sukuona zomwe akupanga. I support usi. Other wise enawo nde Ali trush
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 2 ай бұрын
@@kumbukanikafwafwa good I support usi also
@ThomChanza
@ThomChanza 2 ай бұрын
Nsonda mukufuna pofera
VAMPIRE DESTROYED GIRL???? 😱
00:56
INO
Рет қаралды 8 МЛН
Mom had to stand up for the whole family!❤️😍😁
00:39
НАШЛА ДЕНЬГИ🙀@VERONIKAborsch
00:38
МишАня
Рет қаралды 2,9 МЛН
MICHAEL USI WAYANKHA ZOMWE ANANENA A FELIX NJAWALA KU MZUZU.
8:04
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 27 М.
VAMPIRE DESTROYED GIRL???? 😱
00:56
INO
Рет қаралды 8 МЛН