The man is so loved and needed by Malawians, his old age is a sign of wisdom. Those that claim to be young are doing nothing to the common Malawians.
@DONNEXKhama-bk1gy10 ай бұрын
We really need our president peter muthalika❤
@ErustusPhiri10 ай бұрын
Leadership is not the old age, but the reposibility.
@joelkabambe10 ай бұрын
Zoti okalamba sangalamule dziko nzabodza. Maiko ena akuchitabwino pa ulamulilo wa anthu okalamba kuposanso muthalika. Anthu akulankhula chonchiwa ndiongotumidwa ndi MCP cholinga anthu agwe mphwayi pa za Peter muthalika.
@Doreen-r3w9 ай бұрын
Inuyo mukulankhura chabe kod anyamawao apanga chan akagwere uko chakwera ndi chilima ife tifuna adad amuthalika
@BisalomuChimphako5 ай бұрын
Inuso bodza limenero bweretsani chitsanzo cha maiko omwe akulamulidwa ndi nkhalamba
@ShakirahCassim5 ай бұрын
Palibeso apa piter muthalika yemweyo
@YoungScott-p7e10 ай бұрын
We need him back kaya mulankhula bwanji koma just know kuti we are going to vote for him,amene akuti anyamatawo apanga chani pa unyamata waowo? Peter my vote
@JosephMwambe-rz2oy10 ай бұрын
Yes nomata kut ndinkhalamba
@RiteRoderick10 ай бұрын
Chikuni chachikulu kusunga moto❤❤❤❤❤❤
@OdreckNdemanje10 ай бұрын
Peter Mutharika has a vision,,not that omuzungulira akumukakamiza,,but the masses want him.
@AntonSimony5 ай бұрын
amen mukuti peter sazawina vote yanu nd banja ranu muzapange zotheka koma ife adad oyee
@RiteRoderick10 ай бұрын
Peter Munthalika he's really educated guy who can improve our country as hr did before, president sikuti azilimayi nkhani ndi nzeru zamunthu basi. APM my vote ❤❤❤❤❤❤
@RiteRoderick10 ай бұрын
@ThomasMaulidi Ndipo brother Thom, anyamatawo zikuwakanika kaaaah uwone katundu wakwelera ndipo anakwelera APM atangochoka kumeneko 2020, mmmmmm thumba la cement linali pa 6 pin nthawi ya APM. Chakwera kungolowa kukaika pa 29 pin. Thumba la fertilizer APM linali 17 pin mwamavendor ndipo Chakwera kungotenga 110 pin. Ndie chomakakamira Kuti Nyamata Nyamata Ndi chain????? Muone mmene Chakwera yo panopa Malawi wamuonongera mmmm
@ShabanIssa-il6nc9 ай бұрын
Alamule bas Apeter
@KenedyJolamu-rs9xx10 ай бұрын
Koditu omwe akuyakhula zimenezowo sikuti azika vota ndi iwowo ayi Ovota ndi ife nde APM my vote💙💙💙🔥🔥🔥
💙💙💙APM adzasitha zinthu. Afiti a MCPigs mukufuna mupitirire kupha anthu.
@chrisschikozera727110 ай бұрын
We still love ❤️ him
@RiteRoderick10 ай бұрын
DPP pachiongolero wina afune asafune❤❤❤❤❤
@mphatsomonjeza437110 ай бұрын
As amalawian Peter Muthalika he has lights to be a president again if he tied on the way he will give the one he trust that his not going to disappoint Malawians we need peter back
@EdwardZuze-r7w6 ай бұрын
We need him back as soon as possible, we really love him so much ♥♥
@Allieukacha10 ай бұрын
Ife tikufuna Peter Mutharika ayimeso.bas
@PreciousLesani-c2x6 ай бұрын
Akuyenera kuzaima osat omuzugulira ayi
@rashidlamos340310 ай бұрын
Ife tikufuna utsogoleri wabwino osat president wachinyamata koma mbuli dziko likungoonongeka lopanda president
@MoosahPonda6 ай бұрын
❤iyimeso
@GiftSalijeni10 ай бұрын
APM bas....akuluakulu andaleo bwanji apite ku mcp ndi ukuluukulu wawoi azikaba limoz....
@NifuDagas6 ай бұрын
Ameneyo waboza wamutumayo akunama ine ndimuvotela
@ChrisLessie10 ай бұрын
Abwerereso Peter ❤
@MathewsMANDUTU-lh6oo10 ай бұрын
If God says yes who can say no,,, we want change, we need APM
Pieter Atha kuwinaso Anthu akumu3ra heavy mukanena zakukula osadanda pazakhala Achinyamata othandizira A pita Ali phe pa mpando wa ndarema 2025 DPP Boma 💪💪💪
@SahilluYusuf-sk7es5 ай бұрын
We need our own responsible president petert arthur muthalika
Amusiye Peter mutalika ayimile amalawi akasankha sogoli yemwe akufuna yene ndi sa voter Peter mutalika
@TsalaniponDan9 ай бұрын
From 2014 to 2020 anatan kusitha zinthu
@jameskachulu814110 ай бұрын
Ayime
@rashiedmanjombe225510 ай бұрын
Ayimanso basi
@SofieRafik5 ай бұрын
We need him no matter his age but his love
@FrankGafferCHILEMBWE9 ай бұрын
Great
@McdonaldChimwala-w9z10 ай бұрын
Asiye anthu azavote okha
@andsenJeke10 ай бұрын
APM woyee 2025 akudusa
@MagdaraneChidamula10 ай бұрын
Kukalamba kwa chani anyamatawo akuchitapo chani mumangoganiza mutalankhula eti osamatero aliyense Ali ndiufulu musiyeni ndiufulu wake Mesa anyamata amati azasintha zinthu pano zasintha anthutu sakudana ndi chakwera koma ulamuliro wao anthu tikuzunzika or ulamuliro wa amutarika fertilizer anafikapo 100000 iwowatu ankati ndi anzeru lerobwa abale ukakhala pa kariyalaa umati driver satha kuyendetsa koma yendetsatu goo
Mulekeni munthu ndi ufulu wake kudzaima . Ngati anthu sakumufuna idzaweruze ndi vote. Inu dzavotereni munthu wakukhosi kwanu. Ife amene tikumva kuwawa ndi BOMA la tonse, tizavotera peter muntharika.
@SahilKagwa10 ай бұрын
Akumuopa Peter Muntharika yo kkkkkkkk ndiufulu wake kuyimanso
@ChristopherNdalama6 ай бұрын
APM MY VOTE🎉🎉🎉
@SteveChapola6 ай бұрын
Ife tikufuna adad taime ndipo azawina
@SteveChapola6 ай бұрын
Anime osawakhomerera
@SteveChapola6 ай бұрын
Ayime
@SteveChapola6 ай бұрын
Adadiayimebasi
@malawigeneralguide164610 ай бұрын
Agogo wo akapume ....kodi kulibe anthu ena ku dpp?