NSOKHANO WA DPP LERO 28 APRIL 2024

  Рет қаралды 21,671

HOT 265

HOT 265

17 күн бұрын

Пікірлер: 125
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 күн бұрын
APM ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@amazingmkhungo-qt9se
@amazingmkhungo-qt9se 12 күн бұрын
Ttyl bas but bbytt4tttt TT CV7f 1:29 1:29 o HTH v call to NYU 1:58 free 1:58 hi fyi free g great t Fred ext 2:41 two years n he 5 by5by 2:00 DD😮 2:01 😅😅😅😮😅 2:07 in hi h or gh5 2:10 ut BB 1:31 FYI
@amazingmkhungo-qt9se
@amazingmkhungo-qt9se 12 күн бұрын
Ttyl bas but bbytt4tttt TT CV7f 1:29 1:29 o HTH v call to NYU 1:58 free 1:58 hi fyi free g great t Fred ext 2:41 two years n he 5 by5by 2:00 DD😮 2:01 😅😅😅😮😅 2:07 in hi h or gh5 2:10 ut BB 1:31 FYI
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 15 күн бұрын
APM my vote
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 13 күн бұрын
Dpp🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤ .... MCP vayaaa booo
@user-xu5nn2gx6e
@user-xu5nn2gx6e 15 күн бұрын
DDP woyeeeeee🎉🎉🎉.All the way from America mwana wa kumneno.
@user-fp3dt1sz8j
@user-fp3dt1sz8j 15 күн бұрын
DPP ❤❤❤❤
@StanziaElias
@StanziaElias 15 күн бұрын
Dpp 2025 boma ❤❤❤❤❤
@EdwinMabviko
@EdwinMabviko 14 күн бұрын
Team ya Anthu wodwala wokhawokha,akuveka munthu mmodzi!!!
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 15 күн бұрын
Apm vote❤❤
@user-bq5ev7de1l
@user-bq5ev7de1l 15 күн бұрын
Apm my vote ✊
@ThabisileKanyoza-sr4fz
@ThabisileKanyoza-sr4fz 15 күн бұрын
APM my vooooote
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 күн бұрын
DPP bomaaaaaa mbambande zedi ili❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 15 күн бұрын
DPP Woyeeeee ❤❤❤
@spargomw
@spargomw 15 күн бұрын
Tikufunaso feteleza uja wa 5pin. Chakwera adalephera Ubusa nde angayendetse dziko? 100% Peter akuliphula dziko mu mng'anjo ya moto 2025.
@user-mx3rw2dt4z
@user-mx3rw2dt4z 15 күн бұрын
Apm is my vote 🗳 galu busa iweyo usamale chifukwa palibe chako chakwera
@petermsamariamapira8933
@petermsamariamapira8933 15 күн бұрын
Chachikulu bola mupange chilungamo, chonde, anthu akuvutika
@user-fm5fk1zt1l
@user-fm5fk1zt1l 13 күн бұрын
Ankanena adadi nyekhwe mukuinenai mudzaione ndinu lelo ndiizi ndimafuna ndisakavote kma apa ndikavota adadi woyeeee
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 15 күн бұрын
APM 2025 Boma❤❤❤❤❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 күн бұрын
Chakwera achokeeeeee
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 15 күн бұрын
Choka iweyo
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 15 күн бұрын
Cakwera akucokadi 2025
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
@@user-hm9nc7lz6e Ndikukuuza zedi ameneyi kwake kwatha Joy
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
@@ziyamporoma377 Chikuchoka chokuba chakochibe uwona soon
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 15 күн бұрын
❤❤Dpp my vote
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 15 күн бұрын
Apm my vote ndinari konko lero MBAMBANDE Dpp ikulowaso mmboma
@casilasjawadu1586
@casilasjawadu1586 15 күн бұрын
Kkkkkkkkk awa ndiye ai bolani mcp😂😂😂
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 15 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥
@jahlakechinsewu993
@jahlakechinsewu993 15 күн бұрын
Chakwera BOMA
@user-nk5mj5ws8v
@user-nk5mj5ws8v 15 күн бұрын
tikudikila siku la voti
@AfickRobeni
@AfickRobeni 15 күн бұрын
M'busa sangalamule dziko ndikuyenda bwino
@sungananigondwe2807
@sungananigondwe2807 15 күн бұрын
Galu akumana 🔥🔥
@maxwellmajawa6091
@maxwellmajawa6091 15 күн бұрын
My Voye
@user-xw6rr9gm1z
@user-xw6rr9gm1z 15 күн бұрын
❤❤❤Adad
@user-rd2td7bg4c
@user-rd2td7bg4c 15 күн бұрын
K❤❤❤😂😂😂 kuli wa mcp ko akhoza kuzikozelatu
@spargomw
@spargomw 15 күн бұрын
Adad tikuvutika kwambiri. Chitsime chimaonekad kuphwa madzi akaphwa. Ambuye akhale nanu Adad.
@ChikumbutsoMaloya-zj2jq
@ChikumbutsoMaloya-zj2jq 15 күн бұрын
Uzilimbikila pa zomwe ukupanga usamaloze chala munthu chifukwa chakulephela kwa ko
@spargomw
@spargomw 15 күн бұрын
@@ChikumbutsoMaloya-zj2jq choka iwe, Dpp boma 2025 iwe nd mbuzi yakoyo, paulendi
@user-ot8gm7nu5b
@user-ot8gm7nu5b 15 күн бұрын
My vote
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev 15 күн бұрын
Ndakayika simungadutse
@brianwalawala
@brianwalawala 15 күн бұрын
mfumuyo ngati ili ya manja lende aziyembekeza kuti chakudya chichokera kuti?
@user-wv5hz8ce3i
@user-wv5hz8ce3i 15 күн бұрын
Adad❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 күн бұрын
DPP woyeeeeeeee ❤❤❤❤ boma iloooooooo🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 15 күн бұрын
Boma limakhala kunja aise? Makweratu yokuphwa
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 15 күн бұрын
​@@ziyamporoma377ukhale maso aise udabwa
@EsnartBester
@EsnartBester 15 күн бұрын
❤❤❤❤ dpp
@user-uu9pv6jd4v
@user-uu9pv6jd4v 15 күн бұрын
Moti pali funds apa kkkkkk
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 15 күн бұрын
Matapwisi eni eni mukunamatu…MCP ikusesani 2025 mulira
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 15 күн бұрын
NO PAIN NO GAIN GO BACK 2 SCHOOL SMLL BOY
@IdrisssJabu
@IdrisssJabu 15 күн бұрын
Wa manyi mutu iweyo eti
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 15 күн бұрын
Wapwisa ndi iweyo
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 15 күн бұрын
Chakwera bomaaa akusesani sakunama 2025 mukunya mukadetsenso sanjika zautsiru
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 15 күн бұрын
Chakwera boma 🔥🔥🔥🔥🔥🤣
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 15 күн бұрын
Ndipo adad mukalowa m,boma mupange zositha zithu achite manyazi satana
@ChikumbutsoMaloya-zj2jq
@ChikumbutsoMaloya-zj2jq 15 күн бұрын
Mbuzi za anthu nonse munalikuti mu nthawi yanu ndie ngati munkapanga za nzeru munachotsedwelanju
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 15 күн бұрын
Iweso mutu wako suumagwira mene akuyendela malawi pano unganyose dpp
@moyorobert9801
@moyorobert9801 15 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤
@user-uu9pv6jd4v
@user-uu9pv6jd4v 15 күн бұрын
Mbuli zasonkhana apa kkkkkkkkkkk kunamizana aaaaaa boma la mangochi
@user-eo2ol3ww8h
@user-eo2ol3ww8h 15 күн бұрын
Mbavazikuluzikulu za DPP sangawine sleeping on duty
@MikeMalinga-xx8ys
@MikeMalinga-xx8ys 15 күн бұрын
Ha ha ha!!!! From TANZANIA..,. ZINA LANGA leni leni ndi CHIFUNDO..... A MCP... Tikumana kuseliku DPP WOYEEEEE!!!!!!
@ChikumbutsoMaloya-zj2jq
@ChikumbutsoMaloya-zj2jq 15 күн бұрын
Mukugawa za kudya lelo mukazawalengezesa pa gulu pali cha nzeru 😢😢😢
@user-pl6it7zc7c
@user-pl6it7zc7c 15 күн бұрын
awa alibe mfundo aaaa
@UseniMailosi
@UseniMailosi 15 күн бұрын
DPP ❤❤❤❤❤❤
@user-hk1lp2ho9w
@user-hk1lp2ho9w 15 күн бұрын
Moto kuti buuùu 🎉🎉🎉🎉🎉
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 15 күн бұрын
Moto wamapesi
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 15 күн бұрын
Zaziiiii pitala mungamulalikire kuti ndiwabwino mtima
@DerlinNyirenda
@DerlinNyirenda 15 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkk I hope we will fast up September 16 3025
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 15 күн бұрын
My party
@LuteSynos
@LuteSynos 15 күн бұрын
Vote for dpp
@brianwalawala
@brianwalawala 15 күн бұрын
Kkkk mudyereni ameneyo mungawinise chipani inu??
@dankunseyo6127
@dankunseyo6127 15 күн бұрын
Nkhani yabwino
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 15 күн бұрын
Animation adhadhi, koma music musithe chinyengo
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 15 күн бұрын
Tikufuna ankaka or akabambe agogo akapume
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 15 күн бұрын
Munthu kudana ndi Amalalawi azake. Galu yinu nonse... DPP sazawina ngati woyimila galu wanuyo chitsiru
@StanelyPhiri-kg1ix
@StanelyPhiri-kg1ix 15 күн бұрын
Chakwera boom!
@JamesKamgwira
@JamesKamgwira 15 күн бұрын
DPP Boma 2025
@RABSONSIKELO
@RABSONSIKELO 15 күн бұрын
Inu simmaonjezera ma wages kwa ma civil servant inu....
@afrozwayson7482
@afrozwayson7482 15 күн бұрын
Apm or asanamenye kampeni akuwina basi chofunika inu azisogireri maso pasogolo sitikufuna kuti ena azabere ma vote
@user-ul6gf4xb5l
@user-ul6gf4xb5l 15 күн бұрын
Mbavazokhazokha izi
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 15 күн бұрын
Mbava number one ndi cakwera mbusa wakumidima satana okumwa mwagazi
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 15 күн бұрын
Kodi akaluza ndiye zinthu zitha bwanji???? All reputation that he has ever had will evaporate . Kusakhutitsidwa anthu greed
@brianwalawala
@brianwalawala 15 күн бұрын
Munali momwemo kukuvotelani inu nchimodzimodzi galu kudya masanzo ake.
@KaipaEmanuel
@KaipaEmanuel 15 күн бұрын
Mcp my vote
@FRADRICKMTANDE
@FRADRICKMTANDE 13 күн бұрын
Kkkkk chipani ichi mamvuto alipo
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 15 күн бұрын
Ayinso adhadhi
@DivinePhiri-se3xc
@DivinePhiri-se3xc 15 күн бұрын
Apm woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 15 күн бұрын
Kukapempha
@MorrisMapiri
@MorrisMapiri 15 күн бұрын
The guy sounds like Muluzi
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 15 күн бұрын
Peter muthalika galu ndi azako wonse ali kumbiyo
@user-rd2td7bg4c
@user-rd2td7bg4c 15 күн бұрын
Pakunya pamako
@user-yb2zl1nh9z
@user-yb2zl1nh9z 15 күн бұрын
chilikwanzako dpp inkapanga zomwezi koma
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 15 күн бұрын
Mwanvatu a Chakwera! Kkkkmmmm😂 udzaona nyekekwe 2025.
@giftzayawemaononga-zi8ci
@giftzayawemaononga-zi8ci 15 күн бұрын
Hahahhaha Maloto a chumba
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t 15 күн бұрын
Koma ziliko
@chizandaesau4611
@chizandaesau4611 15 күн бұрын
Amalawi mavuto tikadalinawo umphawi ukutivuta tikadavotelabe chakudya chatsiku limodzi
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 15 күн бұрын
Adad omweo kuti Wawa wawa❤❤❤
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 15 күн бұрын
Banja likatha Latha bas zilimbitsanani mtimawo muleka Chaka chamawa
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 15 күн бұрын
Eti 😂 zitsiruzi
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 15 күн бұрын
Nonse agalu following galu Peter muthalika... Racist nyani pusi nkhwele
@user-zm4vy5rs4v
@user-zm4vy5rs4v 15 күн бұрын
Osaganiza kuti Dpp idzatsitsa mitengo yazinthu ndibodza zinthu zikukwera molina ndi mmene zinthu zikuyensera padziko lose lapasi magnanimous amendable ndi umbuli chabe
@user-zm4vy5rs4v
@user-zm4vy5rs4v 15 күн бұрын
Kodi mwiwara zovuta zapitara chifukwa cha njara? Njala sabweretsa ndi president koma nyengo 2001 kunali njara kodi adabwertsa ndi president?
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 15 күн бұрын
Ndipo azayelekeze kubera mavoti anthu tizavuta osawelengaso kuti awa asilikari kufakufa bs boma ili latikwana ife mmmm anthu afa ndinjala zinthu kukwera mmmm mudzi iyi ya president sinayionepo ine
@user-yk9lx7xd1i
@user-yk9lx7xd1i 14 күн бұрын
Nkhalamba nthawi yawo yatha asiyeni azanu zawi zipitabe chitsogolo zipusitsani anthu osowa zochita zaulere zatitopetsa kutipusitsa ayi mulore ife tizigwira ntchito kuti banja lathu lizipeza zosowa zanu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 күн бұрын
APM woyeeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-mj3ms4jt3b
@user-mj3ms4jt3b 15 күн бұрын
DPP ikungotaya nthawi siizalowaso m'boma. Inatizuza kwa zaka 6 popanda chochita. Awuzeni amaliseche akumwera anene zomwe anachita kwa zaka 6 zomwe analamulira dziko lino zomwe zikupidulilaso amalawi.
@frankbanda7333
@frankbanda7333 15 күн бұрын
Iwe ndiwe uzungulira mutu eti kkkk
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 15 күн бұрын
Misala yamupweteka ameneyu
@user-mj3ms4jt3b
@user-mj3ms4jt3b 15 күн бұрын
Vutotu ndiloti amaliseche amwera tinawaona kale kuti ndiolephera. Chimene aziwa ndikutenga ndalama mu budget yaboma ngati akukapangira chitukuko iwo mkukangoika miyala. Mbombela university kuchokera 2014 mpaka 2020 akhala akungotenga ndalama koma mbombela university kulibe. Sizokhazo ndizambiri komaso tsankho, kumpha alubino , kupondereza, kuondera anthu akumwera okha, katangale, ziphuphu, kuba, kuikira mbamva zigawenga kumbuyo ndikusalabadila zokhumba aza amalawi. Inetu sindikungonena, pitani mukawafise kumangochiko amaliseche akumwera akakuuzani zaine kuti ndimkawauza ndipo ndimawauza mpaka pano kuti zonyasa ndizoipa zomwe munachita zotsatila zake munachoka mum'boma mukufuna. Komaso pano akukupopaniwo akungofuna apidule kuchokera mwainu koma simungawine chisankho loko Chair person wa MEC atakhala mwana wawo
@IsmailNdemanga
@IsmailNdemanga 15 күн бұрын
​@@user-mj3ms4jt3b yomweyo gule iwee 👿👹👺
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 15 күн бұрын
Inu munamanga kut madzi anayamba Inu musanabwele m'boma
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 15 күн бұрын
Racist president in Malawi, chigalu chigalu chimbwe, machende ake peter ndi omwe akumutsatira
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 15 күн бұрын
Galu zitsilu Peter muthalika. Racist president of Malawi.... Chinkhalamba chopanda nzeru peter muthalika
@MikeWyson-cf9os
@MikeWyson-cf9os 15 күн бұрын
Zikomo chehe ulaliki wanu tauva moti tikausatila tikapulumuka Ku moto wa jahanam
@PeterChikoja
@PeterChikoja 15 күн бұрын
Mukuchedwa ndi agogo
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 15 күн бұрын
Ukungovutika kuti cakwera angawine ukunama sangawine mbusa okupha oononga Santana wakumidima
@muyabasamson
@muyabasamson 15 күн бұрын
Chakwera nigalu bora adada omwewo
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 15 күн бұрын
Apm boma or wina asafune
@gladsonritche7641
@gladsonritche7641 15 күн бұрын
Useless speech
@ChrisEnos-to5uv
@ChrisEnos-to5uv 15 күн бұрын
APM my vote
@user-gh6qm5ze3b
@user-gh6qm5ze3b 15 күн бұрын
Nkharamba oyee mbombora yirikuti zaziii
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 15 күн бұрын
Adad Mosgozedwa ndi Mulungu imani nafe atifinya
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 15 күн бұрын
Ndipo kwambiri
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh 15 күн бұрын
APM my vote
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 14 М.
ОДИН ДОМА #shorts
00:34
Паша Осадчий
Рет қаралды 5 МЛН
Зу-зу Күлпәш. Көрінбейтін адам. (4-бөлім)
54:41
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 13 М.
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
一半狂热,一半冷感?14-5-2024@ahchungtalkshow8911
12:42
阿聪吹水堂 Ah Chung Talkshow
Рет қаралды 71 М.
SKC NDI MFULUUU!!MULANDU WAKE WATHETSEDWA. CHILIMA ALIBENSO MULUNDU..
36:30
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 48 М.
A NOSSA HORA |EDIÇÃO DE TERÇA-FEIRA |14|05|2024
TV Sucessomoz
Рет қаралды 11
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
Zambia's President-Elect Hakainde Hichilema Addresses the Nation
30:46
News Central TV
Рет қаралды 89 М.
INE NDI BON KALINDO MWANA OWOPYA KWAMBIRI/13 May 2024
14:14