Mulibe mfundo..nthawi ya Bingu mafuta anasowa inde Koma nthawi tichepe osati Mene zilili Pano nde zimene kulankhula APA zopanda nzeru..chakwera walephera kulamula ndipo anthu alankhula pa 16th sep
@jamestembo6724Күн бұрын
Amufinya Ben longwe ku mcp akufuna kubwera ku dpp mumukane ndichisiru Chaben longwe
Iwe ndiwe wa bodza ,za ngokukanika kuti unene zoti wamutembenukilaso chakwela wakoyo.Misewu ukunenayo mu town ya Lilongwe si process ya chakwelayo ayi.Iwe unali ku SA ufunse onse tidali kuno ayi.