Mmalawii mulibe asirikari, I wonder kutabwera nkhondo kaya zingakhale bwanjji
@FidelisKumwendaКүн бұрын
This just shows it is all a lie. People have just chosen to victimise the innocent people of Nsundwe. Try to visit Nsundwe and see how warm the people are. If you speak from far, you will always believe lies. Lies will not take our country anywhere. Some political parties are specialising in propagating lies, which are poisoning the way their followers think. Malawi is one beautiful country, and let us not confuse our brains by creating and encouraging hate and anger, when we should be having love and hope. Malawi is beautiful.
@FelixBoss-yn9peКүн бұрын
Amwene mwayankhula zoona
@stevenmwamadi30357 күн бұрын
More fire comrade osaopa osatopa osafooka Kumuuza basi chakwera yo ndi muthu oyipa ngati idya amin Koma thawi yake yasara pang'ono pang'ono kutha wasaukisa Malawi kwambili crocodile ature pansi udindo basi chakwera ndi team yake yonse zarephera kuyendesa dziko zamagazi mmanja mwao crocodile team chikangawa team imeneyo ma carward onse a mcp
Wayankhula zamzeru mot madona akufuna ulamuliro uwu uchoke ndpo zthekad
@alfredomatola32044 күн бұрын
Kulankhula mwanzelu
@richardbandah1824Күн бұрын
Walankhula mwa nZeru mchimwene
@LoydMcheleka-uq3ix7 күн бұрын
Tikamati Malawi 🇲🇼 which we means the one doesn’t matter ndiwe muchewa waku Lilongwe, ukamati kuteteza Lilongwe ukuthandauza chani chifukwa muzindawo si wa achewa ndi mzinda mu Malawi alise we all contribute to build that Lilongwe
Dziko lino cikangawa waliwononga ndipo ndikanakonda maiko asatipatse kobili za cisankho cifukwa 2025 si cisankho koma cibwana bigy mwanena cilungamo posatengela kuti mukucokela ku LLngwe tikugwilizana nanu 100% boma ili la mcp icoke palibe ca mzeru tikuciona akungonyenga mu 49, kupha ndi kuba nde zicita mcp mmalawi muno mulibe presdent cikangawa samva za munthu umenewo nde u satanikiwo.
@AlihIbrahim-s7v7 күн бұрын
Inetu ndimanena kuti tisamasapotele mtundu koma tizilikonda dziko lathu,,andalewa siyanthu owafelayi akatibela basi amatisiya ife tikuvutika,,,enafeso ndife a central region koma zimandikhudza ndikawona anthu ena akuyimbila m'manja Bomali pomwe zomwe adatilonjeza sangazilozeyi pano almost 5 year's tikuvutika dzikolose posayang'anaso central region,,,tiyeni tisapoteni munthu yekhawo wakwanilitsa zomwe adatilonjeza sizoseyi angakwanilitse komabe at list 50% tisayang'ane kuti akuchokela kuti,,,,chabwino ndiwadela lako koma udziwe kuti si m'bale wakoyi oti ukavutika Feteleza akakugulila ayi,,,tikondeni dziko lathu
@jameschidafumbwa10397 күн бұрын
When I see that surname, it's a die hard wa MCP, but why akudabwa madzi muli mwake? I thought this guy is manyaka but mmm he is good think,
@FidelisKumwendaКүн бұрын
And by his surname, will he have to be proving all the time that he is not 'manyaka'? If I come across him and have not read his post, am I justified to call him 'manyaka'? Maybe it is the guilt that some people see in his name and tribe that has compelled him to say what he has said. I don't think this is the Malawi that we want.
@Lizzie-h1k7 күн бұрын
Lero wayankhula zanzeru ndayamikira!
@user-qq6xs5tm7z3 күн бұрын
Munthu akamafa mumayamva ndi mkhutu kugontha.Awa mungotaya nawo nthawi.Sangamve malangizo.Mutu udayima pakuti amamva molakwika Kwa alangizi awo.What a shame!!!!!!?
@user-qq6xs5tm7z3 күн бұрын
Samva amamva nkhwangwa iri m.mutu.
@CarolineLiabunya-j8k3 күн бұрын
Ineyonso ndi mchewa ndithu kwathu ku Mbununu uko school taphunzira pa kang'oma cdss koma ngati zinthu sizili bwino kumanena chilungamo tisamanamizane!
@FidelisKumwendaКүн бұрын
Zoti ndinu Mchewa zisakupangeni kuti mudzidandaula. A President anabwerekedwa kuchoka Ku mtundu wanu, panopa ndi a tonse. Ngati akulakwitsa, zisakukhuzeni ngati Mchewa. Komabe, anthu a kwa Nsundwe mukuwalakwira powayika ngati anthu ovuta. Sizikugwirizana olo pang'ono ndi za anthu a bizinesi amene akuteteza katundu wao. A bizinesi amachokera madera onse a dziko lino, ndipo ambiri za ndale sizikuwakhuza. Koma mukayambana Ku ndale kwanuko, mumafuna kuononga katundu was anthu a phee. Munthu amakhala kuti anavutikira kupeza chuma, koma pa zifukwa zosamukhuza, mumafuna mukamuonongere. Izi, a kwa Nsundwe sizikuwakhuza, chifukwa ambiri ndi osauka ngati wina aliyense. Sangachoke kwa Nsundwe kudzateteza katundu woti si wao. Koma kudana ndi Nsundwe ndi chiyambi chabe chofuna kuti mtundu wonse wa Achewa uzichita manyazi ndi kusiya kusapota MCP. That is unfair. Inu ngati Mchewa, don't feel guilty, sizikukukhuzani ngati Mchewa. Chakwera belongs to us all. If he is wrong, we are all wrong. If he is right, we are all right. He now belongs to the nation, from the time he swore to lead the country without fear or favour. He will revert to be a Chewa when his time is over. He will have that right then. Right now he is above and beyond these petty tribal issues. Don't believe in lies.
@mightyisaac23764 күн бұрын
mawu koma awa
@chimzymhashieroo41807 күн бұрын
Dolo katatu
@AchinaKellz7 күн бұрын
Apo sukukamba za ndale koma chilungamo tonse ndife amalawi godya ya zonse ndikutukura dziko
Ndi mbuli za chabe-chabe za kwa msundwe zo. Kuvutika ndi chimodzi-modzi ali mbuuuuuuu kutuwa akangopasidwa tindalamato basitu za ziiii
@FidelisKumwendaКүн бұрын
@@VeronicaChirwa-ct4os Why the hate? And why believe lies. The devil is the master lier, and if our decisions are made from the influence of liers, we will never get things right. What do you know about Nsundwe, and which lier told you those lies?
@FidelisKumwendaКүн бұрын
You seem to believe what you are saying. Whoever told you about Nsundwe, you trust him or her too much. The best thing I would advise people when they get that emotional as saying: 'kugawana uchitsiru', is to go to the place and meet the people, have a chat, have a beer etc. You will then have a true picture of what a people really are. I have been to many places in Malawi and can confirm that people are not as bad as haters portray them to be. Visit Nsundwe and make your independent opinion. I rest my case.
@MaryChavula-jz3di7 күн бұрын
Lilongwe ndi nzinda wa amalawi si wa akwansundwe kuti wina adzi akuuteteza ayi aliyense amauteteza zikwanje zija sikuteteza ayi kufuna kudzatha anthu
@FidelisKumwendaКүн бұрын
Mukupeka nkhani kuti a kwa Nsundwe anabwera ndi zikwanje. Kenaka mukuyikhulupirira nkhani yoti mwapeka nokha. Pa mapeto pake, mukuyidzidzulanso. Ndiye muli busy. Kupeka bodza, kulikhulupirira, kenaka kulidzudzula
@noahkalima52943 күн бұрын
Paja suchedwa kuliratu ,,ukatelo ukufuna uzilita
@IyshaBakali7 күн бұрын
Kaya watani uyu kulakhula zomwe achewa anzake sakondwa akamva
@HalisonSolomon7 күн бұрын
INE NDIRI NDI FUNSO KODI KWA NSUNDWE BARRACKS INAKHAZIKITSIDWA LITILO ? IWEYO KOMA NDIMUNTHU ZIUZE ZITSIRU ZA KWANSUNDWEZO MBUZI ZA ANTHU ZOPANDA NZERU ANTHU OPANDA TSOGOLO
@hesbaluku72814 күн бұрын
😂😂 lelo wabwera sunalile
@BENSONRANGWANI7 күн бұрын
Achakwela munaphelanji chilima soka ndi thembelelo likhale pamutu panu
@FidesChandama7 күн бұрын
Kwa lero wayankhula bwino 100% mcp ili ndi mbiri yoipa
@AubreyBeniMbewe-bt1qgКүн бұрын
I'm still blaming the Inspector General and Army Commander. They are politicizing their position. Akadzamera mapiko awa mudzakumbukira mawu angawa.
@FelixBoss-yn9peКүн бұрын
Penatu achitsiru inu mmayankhulako zanzeru
@JoelMkusa3 күн бұрын
Chitsilu iwe wakhuta nandolo paja udakwatila kummwela
@InnocentTwalick-ok1vq7 күн бұрын
Muli mabalakis angati
@patriciajangaza6757 күн бұрын
Tilibe asilikali dziko muno Koma Kaya Ali kuti aaaaa Koma
@tagonjetsachiwaya94954 күн бұрын
Nanga inu ndizoona kuti mpaka kagulu ka anthu kumazitcha barracks. Asilikali kumangoonerera
@MolesBrown3 күн бұрын
Siwe nchewa iwe kapolo wadpp
@AubreyBeniMbewe-bt1qgКүн бұрын
🎉
@MoyendaChileka4 күн бұрын
Bola panotu
@Smithmame7 күн бұрын
Galu iwe
@HolmanDazah4 күн бұрын
Tiyeni tipewe kudzipaka manyi a MCP.
@ThomasJohn-j8x3 күн бұрын
Kulankhula momveka bwino kwambiri
@DalitsoMatope5 күн бұрын
Akuphatu aise chi leg ndi chi Jacket
@StephanohMoses4 күн бұрын
Bola zisakhale ndale sindimukhulupilila ameneyo muone ma videos ambuyo omwe wakhala akupanga
@MelusiMwali3 күн бұрын
Assad
@dinchisale3 күн бұрын
Wow! bravo
@FidelisKumwendaКүн бұрын
You are confused. Nsundwe has nothing to do with people protecting their businesses in Lilongwe. Why do you always link everything to Nsundwe? People of Nsundwe are just as peaceful as any other Malawian. Protecting one's business is an individual decision, done by any businessperson regardless of where they come from. Investing in business is demanding, and nobody can just allow people a businessman hasn't wronged to just come and destroy his or her empire. Nsundwe is out of the equation, unless you just hate them for your own personal or political reasons.
@MaryChavula-jz3di7 күн бұрын
Lilongwe ndi nzinda wa amalawi si wa akwansundwe kuti wina adzi akuuteteza ayi aliyense amauteteza zikwanje zija sikuteteza ayi kufuna kudzatha anthu