The Court (Zam'banja)

  Рет қаралды 56,194

Jimmy Chimera

Jimmy Chimera

Күн бұрын

subscribe, comment, like & share

Пікірлер: 75
@SamuelChauluka
@SamuelChauluka Ай бұрын
Ndawala ndiwe dolo,best actor
@ShazidaAlfred
@ShazidaAlfred Ай бұрын
Koma amuna ena ndiopanda manyazi ai iwo zaka zitatu zachepa mmmmm🙌🙌🙌
@masautoMalunga
@masautoMalunga Ай бұрын
Thawi zinaso amuna ambili sitiganidzayi mkadzi yemwe wamubelekela mwana sibwino kumamupanga nkhadza mkulakwa pamaso pa mulungu
@berhakalulu6303
@berhakalulu6303 2 жыл бұрын
ndayikunda program iyi. bambowa ndiwopanda nzelu kwambili ndiwozitamandila ndi ndlama wosawelenga za moyo wa mzawo
@AngellaNtambalika
@AngellaNtambalika Ай бұрын
Ndikuseka ngati zabwino 😂😂😂😂 koma mamuna uyu ndioyankha dunyu
@ChristinaMitepa
@ChristinaMitepa Ай бұрын
Uyu akuyeneraso kumangidwa
@mpozatv
@mpozatv 18 күн бұрын
Komaso mkaziyo amugawire Kwa mavendor a limbe Depot
@ThokoKalambo
@ThokoKalambo Жыл бұрын
I like the guy, he is always serious when acting 😊
@SaintstN-0424
@SaintstN-0424 Ай бұрын
😂😂😂
@OxdationGennah
@OxdationGennah Ай бұрын
Acting😂😂😂
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu Ай бұрын
Chigamulo chabwino kwambiri mamuna woyelekedwa mkadzi okongola ngati uyo ena amutola sachedwa
@JeffreympungoseJeffrey
@JeffreympungoseJeffrey Ай бұрын
Pamapeto azonse ovutika ndimwana maka paufulu wokhala ndimakolo onse chuma sikanthu anthuni
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 Ай бұрын
Koma mkazi yo ali bhooh heavy
@SaintstN-0424
@SaintstN-0424 Ай бұрын
Eti,zoona doloyo akuzunza nkazi wabho ngati ameneyo😂😂😂
@JeanMwandira
@JeanMwandira Ай бұрын
Ndipo sakukhalanaso ndi mkaziyo mu Mkaziyo ndiwa bho hvy
@VictorDailesi
@VictorDailesi 4 күн бұрын
Koma Bambo uyu ngati chili chamba
@mziyabenjasinga876
@mziyabenjasinga876 Жыл бұрын
Mkazi uyu ndipaseni nambala yake ENAFE tizamusamslire bambo wa chabe
@abdulhameed7808
@abdulhameed7808 Ай бұрын
Nkhani yake basi kumangokhala zachuma....
@DaveSitolo-e4o
@DaveSitolo-e4o 7 ай бұрын
Eish Bora ndinkhare osakwatila Chuma kuvutikira ndenkha hure angobwera uko azangotora zopusa
@JimmyMajamanda
@JimmyMajamanda Ай бұрын
Ndipo zoberana
@masautoMalunga
@masautoMalunga Ай бұрын
Mamuna opanda zelu vuto kudzimva Kuti Ali ndindalama ndiye basi ikhale nkhadza zomudzudza mkadziwako mkadzi ndimunthu ofunika kupasa ulemu siwose akadzi Ali olakwa ena alipo abwino Koma amakwatiwaso ndimamuna opanda chikondi
@MALIYAMULUWICHE
@MALIYAMULUWICHE Ай бұрын
Bambo ankhanza awa kaye kuda
@JosophineKaonga
@JosophineKaonga 24 күн бұрын
Bambo awa ndi obowa ndipo ngopanda nzelu
@AlidaKamlindeni
@AlidaKamlindeni Ай бұрын
Plog yabwino kwambiri ambiri sitimadziwa malamulo
@MerryWayson
@MerryWayson Ай бұрын
Program iyitu ndaikonda Bambo alephera kuyankha beanji kkkk mesa mamuna wayankhula kut mkadzi waketo ndi Hule kkkk wakanika bwanji kuyankha funso lot Pa zaka zisanu amakhala limodzi mpaka Mwana, nde uhulewo amapangamo ndiiyeyotu kkkkkkk mzibambo opanda zeru
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic Ай бұрын
Amaseweletsa mitima ya azizake ameneyo
@KettieKalembera-e7q
@KettieKalembera-e7q 22 күн бұрын
Court
@patrickmasa7145
@patrickmasa7145 Жыл бұрын
Muthu opanda zelu uyu
@sulaimanamiduh5633
@sulaimanamiduh5633 Жыл бұрын
Abambo awa alibe udindo ngati mamuna
@GiftBanda-c6e
@GiftBanda-c6e 16 күн бұрын
Azimai zolira tichedwa nazo,tidzilimba mtima kumazidalira tokha
@allanbanda4388
@allanbanda4388 Жыл бұрын
Kod ili ndisewelo kapena za serious ndithu
@austinmbereka3376
@austinmbereka3376 Жыл бұрын
Sewwlo
@SamsonNambene
@SamsonNambene Ай бұрын
Seriously Kodi ndi sewero
@SaviourNyimbiri-qk1qh
@SaviourNyimbiri-qk1qh 23 күн бұрын
Nyathi ndiwe dolo
@AbuZubeir-x4c
@AbuZubeir-x4c Ай бұрын
Mamuna yu nde analibe fundo or imodzi
@SaintstN-0424
@SaintstN-0424 Ай бұрын
Eti eti, kungonyozetsa azimuna basi,tizikanika kukwatila chifukwa azimayi aziyesa ngati amuna onse ndiotelo
@YohaneGift-pf1lu
@YohaneGift-pf1lu Жыл бұрын
Mamuna opusa kwambli
@CHAPITASINGINI
@CHAPITASINGINI Ай бұрын
Ndinalibe 4n nthawi imeneyo km bambo iweyo ndi galu machende ako wamva Ky ndichamba uzawona polekela mesa nkhoswe ndi mwanayo ukuyakhula mopusa uzafa ifa yowawa pasete pako galu iwe mesa uhule wo amapanga ndiweyo pachiphwisi pako
@abdulhameed7808
@abdulhameed7808 Ай бұрын
Kkkkkk ndisewero chabetu bossman.
@samsonphiri5349
@samsonphiri5349 2 жыл бұрын
Program yabwino
@ShadreckHassibu
@ShadreckHassibu Ай бұрын
Akachite kunena kuti ali ndi ufulu opanga chibwezi nde mpaka kutengera wachibwezi mu nyumba moti muli mkazi wina just poti alindindalama ?kumakhala ndi khalidwe labwino osamadzinva undalama simudziwa kut mawa libalanji popeza mukuberekabe
@MonesiMadengu
@MonesiMadengu Ай бұрын
Mumatha acting keep it up
@friendnyirenda6392
@friendnyirenda6392 Ай бұрын
Kkkkk ndaseka uhulewo mesa amapanga ndnuyo
@osamabinraden9391
@osamabinraden9391 2 жыл бұрын
Nice one bra . l Watching with cup of coffee
@BrightWafanematola-x5y
@BrightWafanematola-x5y 22 күн бұрын
Kkkkkkkkkkk kd ndmilandu kapena drama?
@ChimwemweWanga
@ChimwemweWanga Ай бұрын
Mbuzi ya mamuna 😞
@user-lx5ux9rp2h
@user-lx5ux9rp2h Ай бұрын
Mamunawe ndichisiru opanda dzeru
@peterbanda5425
@peterbanda5425 2 жыл бұрын
Plglm yabwino kwambili
@SydneyDrinkson-h8k
@SydneyDrinkson-h8k Жыл бұрын
Mamuna,ndiololedwa ,kukhara,ndiakaziawiri ,motsatiramalamuro
@Felista-m4q
@Felista-m4q Ай бұрын
Mwamuna opusa
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 Жыл бұрын
Matama chifukwa muli ndi ka ndlama mudzi ya munthu wamamuna
@BlessingsNamilonje
@BlessingsNamilonje Ай бұрын
Kkkkkkk koma zandikhuza 6:03
@Lameckbwanali-l3v
@Lameckbwanali-l3v 8 ай бұрын
Please program tikuifuna iyi
@wittinessnkhokwe
@wittinessnkhokwe Ай бұрын
Maso twanitwani kusatira ndalama zanga
@EusébioLucianoGaiondo
@EusébioLucianoGaiondo Ай бұрын
Kkk
@ConfusedBassetHound-zf8zs
@ConfusedBassetHound-zf8zs Ай бұрын
Koma ngat kuli mbuli pa dziko lonse lapasi ndi mwamuna uyu mmm😢
@andrewkawungamanyirenda9507
@andrewkawungamanyirenda9507 2 жыл бұрын
Why the noise behind
@AaronMisiyasi
@AaronMisiyasi Ай бұрын
Ndizambodza
@AlinafeMoses
@AlinafeMoses 28 күн бұрын
Mumatiphuzisamo zambili
@AlbertNkhoma-xk1er
@AlbertNkhoma-xk1er Ай бұрын
𝐌𝐚𝐦𝐮𝐧𝐚 𝐧𝐝𝐢𝐰𝐚𝐭𝐨𝐩𝐨𝐫𝐚 𝐮𝐲𝐮 𝐤𝐮𝐲𝐚𝐤𝐡𝐚𝐧𝐚𝐤𝐨
@mphatsochikaonda4456
@mphatsochikaonda4456 2 жыл бұрын
ili nyatwa vidio yi
@markhamdaddy
@markhamdaddy Жыл бұрын
Wakhaza.bamboyi
@markhamdaddy
@markhamdaddy Жыл бұрын
🤣
@LapilanMasauko
@LapilanMasauko Ай бұрын
@OxdationGennah
@OxdationGennah Ай бұрын
Mamuna fundo 0, tigayilen # ya nkaziyo azasambile mu nyanja ya chikondi😂
@GraceTembo-l3n
@GraceTembo-l3n Ай бұрын
bambo wopusa
@patrickgrey6984
@patrickgrey6984 2 жыл бұрын
Eeeeeeekoma
@bwenguking3894
@bwenguking3894 3 ай бұрын
I support the court decision
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 6 ай бұрын
😱😱😱
@FunnyGanuel
@FunnyGanuel 25 күн бұрын
Ngati ndipange tag galu winawake 😂😂😂
@LapilanMasauko
@LapilanMasauko Ай бұрын
Nizon
@TrinityBonjesi
@TrinityBonjesi Ай бұрын
Mamuna oputsa kwambil
@user-on6pk2tz1y
@user-on6pk2tz1y 9 ай бұрын
Kod program iyi inatha???
@nourathameedahabdullah9574
@nourathameedahabdullah9574 Жыл бұрын
😢
@GraceTembo-l3n
@GraceTembo-l3n Ай бұрын
chitsiru cha munthu. shameful man
The court
25:02
Jimmy Chimera
Рет қаралды 46 М.
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Malawi News Update
Рет қаралды 236 М.
Teaching a Toddler Household Habits: Diaper Disposal & Potty Training #shorts
00:16
Ku court
9:20
Chikoko Comedy
Рет қаралды 6 М.
DOTITO: Handibvise Pfuma Chataiita Chihure Chete Chete
38:56
ZimNews Beat Tv
Рет қаралды 25 М.
Moot Court Finals 2022
17:49
The Catholic University of Malawi
Рет қаралды 1,9 М.
Hon Ssemujju awadde bannauganda amagezi!!!!!!!
21:29
CBSFM UG OFFICIAL CHANNEL
Рет қаралды 553
IZINKABI VS POLICE OFFICERS
44:42
TRANSFORMATION LIVE
Рет қаралды 431 М.
CRUISE 5 with: TED KWELEPETA
1:16:29
Jimmy Chimera
Рет қаралды 2,5 М.
Behind Bars: Wicklove anotsangura mhosva yekuuraya yaakapara
32:29
Tilder LIVE ZIM
Рет қаралды 375 М.
CYCLONE FREDDY FUNDRAISING DRAMA #malawi
1:31:45
Kanema Online
Рет қаралды 481 М.
GWEDEGWEDE
32:56
Jimmy Chimera
Рет қаралды 389