The court

  Рет қаралды 46,382

Jimmy Chimera

Jimmy Chimera

Күн бұрын

subscribe, comment, like & share

Пікірлер: 55
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo Ай бұрын
Ndizaboza izi muonesese khani iyi komaso anthunomwe Ali munkhani iyi muoneseseso khani inayo anthu ake ndiofanana mmmm maboza basi
@alomuddin8801
@alomuddin8801 Жыл бұрын
Khothi lakondera azimayiwa anamunenadi mzawoyu 😮😮😮 pezani wanu mwamuna mukhalira yomweyo😮😮😮😮😮
@jtpi8362
@jtpi8362 4 күн бұрын
Amene akuyankha kachiwiriyo ndi wa mu mdyangu comedy 😅😂😂
@wabitha9769
@wabitha9769 Жыл бұрын
Za chison mmene dziko lathu lilili mkumakhalaso bzy ndi mabodza mmalo mopemphera eshhhh Malawi dziwa yesu nthawi yatha😮
@LishaMandah
@LishaMandah 17 күн бұрын
Mwakondela
@ishmaelamadu6425
@ishmaelamadu6425 Жыл бұрын
Azimai awawa akumupangila jelasi nzaoyo osati akuzimva ayi azimai awiliwa achepetse kumujeda nzaoyo azipemphela kuti apeze mamuna wabwino chifukwa avomeleza okha Kuti ananena chifukwa nzaoyo akudzimva komaso sanatchule dzina ayi sizoona azimai ameneo apole Moto amusiye nzaoyo azisangalala ndi banja lake asamuipitsile mbiri apange zao
@faruq10phiri26
@faruq10phiri26 Ай бұрын
Mahule osowa amuna . Komaso akondela akuti.kasamale banja mama asiye mahuleoo
@FatimaJuma-k3k
@FatimaJuma-k3k Ай бұрын
Kodi ayankha koyambawo si aja anabweranso mu khothi momwemo pankhani yokaniza mkazi nzao kugawaba chuma aja? Akuoneka ndi mzimayi oyambanitsa ndiamabodza
@AraujoDomingos-wy6jm
@AraujoDomingos-wy6jm Ай бұрын
Ineso ndikumuona ngat ndiyemwey
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 2 жыл бұрын
Amzimai nsanje mpaka kkk ,pezani anu amuna olemera muziyendanso ndi abusa kkkkkk
@Felista-m4q
@Felista-m4q Ай бұрын
Mmmm adzimayi nsanje ndi nzanu bwanj mumafuna adzivutika kumtima kwanu kuyera
@RejoiceKamanga
@RejoiceKamanga Ай бұрын
I have been seen people who are found in this Court. I don't understand if this is serious case cuz All of them have brought different cases to the same Court. I think this is just a comedy. You teach people.
@LizzieSaikonde
@LizzieSaikonde Күн бұрын
I think its acting chabe.Amayi akudandaulawo ndawonela milandu yawo yokwana itatu yosiyana.
@TumpaleMsukwa-l4i
@TumpaleMsukwa-l4i Ай бұрын
Kma inu mwati nkhanizi ndzoona kapena akupanga act ?akupezeka uku ndiuku bwanji
@esnathmatias7617
@esnathmatias7617 Жыл бұрын
Ndipo nkhani iyi oweluza anakondela mukhalila yomweyo azimayi pezani mabanja
@RobertCosmas-bo1uo
@RobertCosmas-bo1uo Ай бұрын
Wodandaula zamgovuta kt satha kulankhula akadawina
@Walu-b9v
@Walu-b9v Ай бұрын
Ali ndi sanje apeze awo nanga zawo akanyadira kuti usilu bas ndalama zake zikuwawa poti zawo alindi ndalama angosilira nanga bwanji iwowa zikuwa pweteka awauza chilungamo alindi ana opanda azibambo
@esteryndau8546
@esteryndau8546 2 жыл бұрын
Uyu anazolowera ma boza akwa mdyango comedy
@dalitsokaelama360
@dalitsokaelama360 Жыл бұрын
Oweruza I think mwalephera
@RobsonChilongo
@RobsonChilongo 6 күн бұрын
Wemon can not think what to say.
@HenryGulani-fq5js
@HenryGulani-fq5js 4 ай бұрын
Kuipitsilana mbili ndikuchitilana tsanje mulandile chilango batsi ndinu mxm oputsa ine ndili Joz mupange dzanu mahule
@isaacmussa2942
@isaacmussa2942 Жыл бұрын
😂😂😂😂koma Azimayi phuzirani kupanga zanu kkkkkkkk
@AlfredNazombe-jy9fi
@AlfredNazombe-jy9fi 9 ай бұрын
Uyu saziwa kuweluza kod xool yake ndiyakut yakwachaa chani kkkk kom majaji enawa iiii zikom Kom mahule awa azikangogagadisa kubakidad bs
@blessingskapalasa907
@blessingskapalasa907 Жыл бұрын
Olo kuno ku South Africa masosi amaziwa kuti azimayi athu ndi amiseche simthani chonde
@Eliwarning
@Eliwarning Ай бұрын
Drama they are having some practicles ndi school yawo imeneyo now they are on practicles from their lessons
@ThomasMchonchoma
@ThomasMchonchoma Ай бұрын
Anthuwa ndi mabodza awa nthawi zonse akumabwela ndi milandu ndi anthu ake omwewa dramer iyi asamatipusitse
@aaronmagombo9805
@aaronmagombo9805 Ай бұрын
Munenadi zoona ine ndimadabwa
@YvonneSopera
@YvonneSopera 18 күн бұрын
Mtopola
@MercyJohnsonkanchure
@MercyJohnsonkanchure Ай бұрын
Bwanji wosangopempera mama
@PrudenceBanda-gh5oo
@PrudenceBanda-gh5oo 11 ай бұрын
the problem is that , the Judge has failed to analyze what the defendants said therefore dismissal of the case is not the good solution. This is because the defendants pointed out that the plaintiff is in relationship with the reverend of which is not true, what if people started to mock against the plaintif isn't that a defamation?
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo Ай бұрын
Ndie zazimayi zimenezo
@CekuzytskSkipar
@CekuzytskSkipar Ай бұрын
Futu ndilakuti sanacule zina lake
@AlfredNazombe-jy9fi
@AlfredNazombe-jy9fi 9 ай бұрын
Mahule awiliwa mahuled iiiii kom yah
@LuwisKaigwaze-gr6cg
@LuwisKaigwaze-gr6cg Ай бұрын
Kodi kupalamulako amangopalamula amodzimodzi kapena ndi ma sewero?
@earnestmkoma1729
@earnestmkoma1729 Ай бұрын
Zoonad pa programyi anthu Onse amakhala okhaokhawo
@Walu-b9v
@Walu-b9v Ай бұрын
Ogamla nawo sangawone mumene akuyankhulira mo zochita kuwonekerathu kuti amamujeda zawo
@Fwetho138
@Fwetho138 Жыл бұрын
Mlandu sunayende bwino.
@HawaAndrew-ub4hi
@HawaAndrew-ub4hi Жыл бұрын
Apulisika atengela ma boza akwa mdyangu
@samsonrasiyon1030
@samsonrasiyon1030 Жыл бұрын
Km ineyo naphudzilapo kwambili km zinthu Ngati izi zokuyipitsila mbili pachifukwa chazomwe ulinazo ambili tikukumana nazo km Kuti titsate njila Ngati iyi zimativuta chifukwa Choti tilibe kolowela Km chilungamo mwachitsata kwambili
@FlorenceDouglas-x5c
@FlorenceDouglas-x5c Ай бұрын
Kod ndi drammar???!
@promise3693
@promise3693 2 жыл бұрын
My country 🇲🇼
@TumpaleMsukwa-l4i
@TumpaleMsukwa-l4i Ай бұрын
Kma ama
@Watson-q4d
@Watson-q4d Ай бұрын
Nkhaniyi sinagamulidwe bwino kunena chilungamo
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 Ай бұрын
Sono nkhani ndi nsanje eti.?
@mussachitambi
@mussachitambi Жыл бұрын
Azimay polano moto
@HappyMphande
@HappyMphande Жыл бұрын
kudzipachika okhatu
@gomezmso9745
@gomezmso9745 Ай бұрын
Staged court but still good
@samuelben9607
@samuelben9607 Ай бұрын
nsanje azimayi
@simeonmkwembe3940
@simeonmkwembe3940 2 жыл бұрын
Kd masiya kuonetsa kwagwanji
@phillipstamaley7901
@phillipstamaley7901 2 жыл бұрын
Kwagwanji a kutuluka ku times not mbc
@scitechx8789
@scitechx8789 2 жыл бұрын
😂😂😂😂
@promise3693
@promise3693 2 жыл бұрын
Azimai ukanyembete sian osamamumaipisira mbiri mzanu
@mziyabenjasinga876
@mziyabenjasinga876 Жыл бұрын
Oweluza akondela
@RitchardiSipulirgi
@RitchardiSipulirgi Ай бұрын
Zauhule nde mabadza bas
@ElliottBelon
@ElliottBelon Ай бұрын
Priscar bwnj
The Court (Zam'banja)
23:35
Jimmy Chimera
Рет қаралды 56 М.
The Court Of Malawi
24:32
Jimmy Chimera
Рет қаралды 54 М.
Girl, dig gently, or it will leak out soon.#funny #cute #comedy
00:17
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 42 МЛН
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Malawi News Update
Рет қаралды 236 М.
THE COURT (Malawi)
24:46
Malawi News Update
Рет қаралды 62 М.
THE  COURT (Malawi)
24:40
Malawi News Update
Рет қаралды 56 М.
TIKU 9 JULY 2016
27:20
Edson Gunsalu
Рет қаралды 136 М.
The Justice Court EP 114 || DNA TEST REVEALED A SHOCKING FIVE-YEAR SECRET
31:53
HE DOES NOT LOVE ME ANYMORE || Justice Court EP 136
27:11
Justice CourtTV
Рет қаралды 408 М.