Always lam leaning something from chef William, not just in the comedy only but also in reality zoone He is a chef
@AronLuka-ue5hl9 ай бұрын
Amfumu mumakwana mfumu yodekha bwino Kwambiri yaulemu wake ndipo mazimfumu midzimu adakakhala ngati amfumu William zikanakhala bwino komaso Atonde wadula pitiliza ndimasewero anu abwino choncho watching from South African
@rosemarymponda2749 ай бұрын
gaga asowe Kikikiki. Tonde more fire
@MalizinaCodo9 ай бұрын
Kkkkkkkk nadzombe ndi mbuzi yamunthu sakudziwa CHIMWE akufuna haaaaaaa ifesotu timamufuna m zione uja ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ Koma kuli mahule okhaokha uku muthindaso ndiwinaso hule nazombeso hule koma nazombe wekhawe zione uja ndimamudziwa sakulolaso
@ClementWanja-l2l9 ай бұрын
27:37 gaga
@HassanTwaibu-c6h3 күн бұрын
yes guys nice verrywell
@inessmsiyambiri85179 ай бұрын
Gaga iiiiiii🙌
@Matabwah56 ай бұрын
Nazombe is ungrateful guy The man behind mfumu is a guru...keep shinning
@Maria-x4x5l9 ай бұрын
Mukumandinvetsa kukoma zedi from south Africa
@HawaMamo-q2v9 ай бұрын
Agaga kuzolowela kuba paka mukufuna mube ndi umfumu omwe 🗣🗣🗣agaga
@AndrewHamiton-er8wn9 ай бұрын
Gaga u senior wako utenge bwino ukhala nawo mmavuto be careful 🤣🤣🤣🤣 Inuso a Davie, zione kukunkhululukirani ma blunder mbweee Mutaya omwetamwetatu a Davie kumuluza zione Proud of you guys Tipatseni number tivote basi You make my day gud
@MathewsCharles-mh8yg9 ай бұрын
Kma ziveka icho chifuna iwe sichikidziwika kkkkk aaaa.... Muleke mwana Nd WA tonde Agaga zinthu zavuta muziona kkkkk
@GOEMENGONDWE9 ай бұрын
Mude wangwilasobyenkha mamama 🎉🎉🎉🎉 snkhan iyi ikupita kwa boh guys waiting kuti xintha bwanj. Guys changu chonde
@CharlesKanyenda-m1u9 ай бұрын
Mmativetsa kukoma
@shupikayintuwaluwa-58999 ай бұрын
Kkkk zimveka aaaa ai mu2 sugwra bas nanu che davie tagwran pamoz kkkkkk
@mwanawevhudangwe77729 ай бұрын
Kubeleka mwana ndikosavhuta koma kulela- Zimveka special
@giftblack76909 ай бұрын
😂😂😂😂😂 Davie zamuvuta wabudula memo wake mapanga awili avumbwitsa ine ndikudikila gaga kuti kutsegoloku zizamuthrla bwanji
Davie kujijilika taonani izi Amfumu vuto lawo ndi chani
@khumbophiri90069 ай бұрын
Gaga saundila kkkkkkk😂😢
@WillySitambuli9 ай бұрын
Manganizo anga ali pa gaga n kuti kodi zimuthela bwanji
@bayanimponda87469 ай бұрын
Tiyeni tiwavotere anthuwa
@DennisKweza9 ай бұрын
Nazombe yamulakwila bas😂😂😂😂
@EsterLusale9 ай бұрын
I love make dola
@UmarDysen9 ай бұрын
coming back tonde wadula 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 afuna aziwalelela azawo Iwo kwawo ndikuswaa bas akakula avumbuluke Kuti ndiwake 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 koma anthu inuyo
@justinenambazo68559 ай бұрын
Big up guys
@YalediGondwe9 ай бұрын
Hiiii koma ziwone❤
@bayanimponda87469 ай бұрын
Koma a William ndi fumu yodekha. Zimveka Ali mu madzi
@ThomasSalijeni-s7i9 ай бұрын
Best comedy tonde wadura
@amosgoliat44729 ай бұрын
More fire
@simplexkanyinji9 ай бұрын
NICE
@kelvinkhudze62419 ай бұрын
Nazombe😂😂😂😂😂😂😂
@IbrahTime9 ай бұрын
Koma afumu pagaga pokhapa mupangepo kanthu nditu
@sharrifgwape71699 ай бұрын
Avide zawavuta basi chagwa kwa dolo
@MisheckAselo9 ай бұрын
Yonse 👍
@IbrahTime9 ай бұрын
Nyamata wa Joni Ali pamavuto nditu
@MaliyaDaiton9 ай бұрын
Amfumu mukuichedwesa khani mukatheni gaga
@ronaldgowelo38659 ай бұрын
Kkkk Inde zione wamchita bwino kkkk
@EsterLusale9 ай бұрын
Koma madola ndi azimveka amakhalana amadola akhuluruke basi
@CharityMafuta-y1g9 ай бұрын
Am here for ndaziona
@patricksoko13089 ай бұрын
Now Tonde is the best ❤
@HalimTalim9 ай бұрын
Well done my people 💯
@JoãoChirwa9 ай бұрын
Koma guys ine nganga amamdiwaza kwambili❤❤❤❤
@CharityMafuta-y1g9 ай бұрын
Welcome Mumde missing
@MusahMrsweet-oz1xh5 ай бұрын
makhadzi
@PromiseKhenzo9 ай бұрын
KOMA ZIMVEKA NDI MACHINE 😂😊😅😮
@YusufMaganga-rn3ju9 ай бұрын
😂😂Koma nazombe . bas2 mkaz uja 🤣🤣 Ine ndiye ndafisira 😂 wandilolaso .ati chathapo bc
@GracianMphula-e3l9 ай бұрын
Big up🎉🎉🎉🎉
@EvanceJailos9 ай бұрын
Nazombe's history is very difficult, but for a person who does not understand these things, you start to judge her as a prostitute, but He is not. I'm in the Nazombe season again, I've been rained on a lot and now I'm having a hard time.