Kkkkk kufatsa sikupusa ndaonera chemuthinda makwale ndi zakhwima atsala pang'ono kukalowa mu chitolokosi cha police. I love tondewadula.pitilizani kutichotsa nkhawa
@mickarison7488 Жыл бұрын
From south Africa 🇿🇦 big up guys gaga apondedwe wawonjeza kuba komaso mabodza 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@mollymasangano473 Жыл бұрын
Kikikiikiki Bank yangwa pasi,GAGA koma Makwale ndi Zankwima kuba too much kikikiikiki mdzidzukulu dza GAGA kuba. Your doing agreat job 👏 🙌 🙄 👌 😒.
@siskanyirenda Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 gaga akuti wagwetsa bank kkkk
@jumawasi9038 Жыл бұрын
Watching from 🇮🇪 ili bhoo heavy
@chikondiyossefe Жыл бұрын
Zakhwima ndimakwale akuba kwaafumu😅😅😅😅🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿 koma abale zinazi kkkk
@GiftNapaula Жыл бұрын
Kkkkkkk.... Koma GAGA anakonza....Gaga uzapha munthu ndi phwete iwe...
@Mpungwe123 Жыл бұрын
Koma gaga ndikatundu😂
@danielkhinguirossejuliasse6106 Жыл бұрын
From Mozambique timakunhadirani
@nicholasnamadwala Жыл бұрын
Watching from Kasungu West inuyo ndi one
@Charity-dg3eb Жыл бұрын
Kkkkkkkk agaga akumana nazo mpaka kumenena kuti agwesa bank 😂😂😂😂😂😂😂
@modesternyoni711 Жыл бұрын
Akut kaya zinazo zichani ..akut ma 100 sangankhale nthumba mwake koma GaGa anakoza kkkkkkkkk
@KimChisola-gm7yw Жыл бұрын
Kkkkk Gaga waziona kkkkk
@sayidimisessa Жыл бұрын
From johannesburg south Africa 🇿🇦 ndimakusatirani
@menaldchunda8499 Жыл бұрын
🎉🎉🎉🎉moto zakhwima....amalengeza church nkhani yake yanji😂😂😂
@chikondiperseusgeorge2533 Жыл бұрын
Nice 1guys watching from kuvukiland
@Mpungwe123 Жыл бұрын
Koma ka main sign tune kanuka mhuu one day tizakonetsa nkokoma kwabasi😂
@AgnesMasangano-uj8il Жыл бұрын
From South Africa mumakwanira guys gaga wakumana nazo kkkkk