Vice President Michael Usi Kuzungulira Mu Msika Wa Mzuzu komanso kudya Nsima pa Restaurant

  Рет қаралды 6,353

AM TV MALAWI

AM TV MALAWI

Күн бұрын

Vice President Michael Usi Kuzungulira Mu Msika Wa Mzuzu

Пікірлер: 14
@LawrenceMsango
@LawrenceMsango 2 ай бұрын
Usi zeru mulibe ndikumanga musika kumeneko ndichitokuko chimenecho choyendayenda. Mungowapusisa anthu sindikuonapo zazerulu kusowa zochita zikutengelani kuti zemenezi mudziona zisazo madziko azanu mumene akuonekela.mangani chinachake tizikukumbukilani osati zombanda zeru ngati mukupanga masanje a
@LawrenceMsango
@LawrenceMsango 2 ай бұрын
Kudzionesa uphewe wanu ndi uphewe wazeru we are very poor in our mind
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 2 ай бұрын
Koma apa chot amalawi athandizika sindikuchiona .athu athandizeni njira yothesa njala komanso fertilizer osika mtengo osati zongozungulira mumsika .kodi phindu lake ndichani .
@PiusChawinga
@PiusChawinga 2 ай бұрын
Sanadye komatu anangopeleka ndalama
@AlexNthenda
@AlexNthenda 2 ай бұрын
Nde mtingo mnaikwezatu
@thokozanisukah6448
@thokozanisukah6448 2 ай бұрын
Kodi phindu lomwe apeze mzika ndilotani pa trip yi
@aggreymdunga8841
@aggreymdunga8841 2 ай бұрын
Funso labwino kwambiri
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 ай бұрын
Mukazazindikira kut zimene akupanga Usi iye akulemera ndipo inu mukusauka simuzaomberanso m'manja.
@SlyviaPhiri-bd9uu
@SlyviaPhiri-bd9uu 2 ай бұрын
Zosangalasa ndinthu ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
@TadalaKabira-f4x
@TadalaKabira-f4x 2 ай бұрын
Awatu koma akupazi anthu azaapanga chipogwe akanadekha ndizabwino koma pena sizabwino
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 ай бұрын
Usi best vice president no different ndi chilima.you two my favorite Vice president in malawi
@MaryJuwa
@MaryJuwa 2 ай бұрын
I see hope on you Mr Michael Usi
@LovelyDumplings-yf7pd
@LovelyDumplings-yf7pd 2 ай бұрын
Umeneu ndiye timati tsogoler ofunika dziko ndakunyadira avp
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 ай бұрын
Uzungulire macity onse uwone zomwe anthu akusowa . Ngwirani ntchito kopanda wina kukuopsezani vice president. Pitirizani mafuno a chilima
This dad wins Halloween! 🎃💀
01:00
Justin Flom
Рет қаралды 32 МЛН
When mom gets home, but you're in rollerblades.
00:40
Daniel LaBelle
Рет қаралды 82 МЛН
小蚂蚁会选到什么呢!#火影忍者 #佐助 #家庭
00:47
火影忍者一家
Рет қаралды 124 МЛН
龟兔赛跑:好可爱的小乌龟#short #angel #clown
01:00
Super Beauty team
Рет қаралды 81 МЛН
MICHAEL USI WAYANKHA ZOMWE ANANENA A FELIX NJAWALA KU MZUZU.
8:04
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 27 М.
Senzo Meyiwa Murder Trial | 28 October 2024
Newslive SA
Рет қаралды 290
TIKUFERANJI 01 MARCH 2006
31:41
Edson Gunsalu
Рет қаралды 302 М.
The JAAKEV SHOW with GWAMBA
1:22:11
Madness Entertainment
Рет қаралды 40 М.
Behind Bars: Wicklove anotsangura mhosva yekuuraya yaakapara
32:29
Tilder LIVE ZIM
Рет қаралды 404 М.
This dad wins Halloween! 🎃💀
01:00
Justin Flom
Рет қаралды 32 МЛН