ZAZIWIKASO ZA MMENE AMAIMBILANA MA PHONE MU NDEGE MUJA ~ NDE MWATI NDANI ANAWAOPSEZA PA PHONE UJA?

  Рет қаралды 18,617

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 82
@FelixMaulana-i9s
@FelixMaulana-i9s 20 сағат бұрын
Mukamaulusa zopusa zanuzi muzisamalila thawi
@AdamJames-x7x
@AdamJames-x7x 4 күн бұрын
Useless inquiry, my friend your Just preaching, we know already what happened,
@DannyKalumbaWaBanda-q7o
@DannyKalumbaWaBanda-q7o 4 күн бұрын
Kodi uthengawu ukupita kwa a zungu?
@SiceloNgiba
@SiceloNgiba 4 күн бұрын
Kodi mesa uthengau ukupita Kwa a Malawi bwanji zizunguzi ufiti kwambili inu mulungu azatiuza zoona next year September
@SleepyCalicoCat-rx6wb
@SleepyCalicoCat-rx6wb Күн бұрын
Kod awawa chichewa kunalibe
@MikeMsamalaphiri
@MikeMsamalaphiri 3 күн бұрын
Za ziiiii. It will just finish our data
@esterechamba9343
@esterechamba9343 3 күн бұрын
Where is the black box???????😭😭😭😭😭😭
@catherinekadwala3839
@catherinekadwala3839 4 күн бұрын
Zaziii nkhope zokubazo musatinyase chilingamo mwasunga but one day is one day
@ZexChimwaza
@ZexChimwaza 4 күн бұрын
God must forgiven you my brother (shame on you)
@HappyBigWaterfall-xt1mn
@HappyBigWaterfall-xt1mn 4 күн бұрын
Kodi analiazungu anakwela ndegeyo?a kan at azikamba chichewa kuti tonse tiziva mabozawo
@blessinglinHand-f9c
@blessinglinHand-f9c 4 күн бұрын
Ndipo mwazi wa ánthu awa ukafunsidwa pa mitu yanu, Mulungu ndiye Commissioner Inquiry yomaliza,tikakomana kumwamba.
@DeJocrown2685
@DeJocrown2685 20 сағат бұрын
Kodi lilongwe air space imathera pati ndege ikamapita ku mzuzu
@JohnMalikebu-v7z
@JohnMalikebu-v7z 4 күн бұрын
Yankhulani chichewa chonde ndinembuli,
@chimwemwebanda9939
@chimwemwebanda9939 49 секунд бұрын
Those who allowed the plane to flying at this day their responsibile
@HildaMbizi
@HildaMbizi Күн бұрын
Umhuuu chiuta ndiyo wakumanya vyose imwe bwebwetani
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya Күн бұрын
Mukungotaya nthawi yanu tikudikira nthawi yoikika Mulungu adzakuikani poyera musayese mwachenjera zidyani ndalama za Amalawizo
@MadalitsoPkunthani-q3e
@MadalitsoPkunthani-q3e 4 күн бұрын
Amanena kuti kufufuza kwawo kukhala kwa live nde live iyo ili kuti
@MemorieMwasinga
@MemorieMwasinga 4 күн бұрын
Fuso labwinotu
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Күн бұрын
Awa mabodza CHABE dzelu za mcp idzi
@FatimaEnest
@FatimaEnest 4 күн бұрын
Zisiru zeni zeni
@francogibsonkananji9975
@francogibsonkananji9975 4 күн бұрын
palibe chazeru ndatolapo maganizo anga
@AshimayeGama
@AshimayeGama 4 күн бұрын
Agalu inu machendanu bodza dzinakambidwa kale idzi
@JohnKamwaza
@JohnKamwaza 2 күн бұрын
Za zi bwanji usatiuza mu chilankhulo chathu
@RichardHetekere
@RichardHetekere 4 күн бұрын
Koma ku malawi 😢😢😢
@vincentlamanmathebulamwana5697
@vincentlamanmathebulamwana5697 Күн бұрын
Kukamwa Ngati kumaliseche Kwa mkazi wachekwera mxiiii
@WomThocco
@WomThocco 4 күн бұрын
Let me sleep ndiumbuli wangawu, English paliponse 😢😢😢
@ChimwemweJuwao
@ChimwemweJuwao 4 күн бұрын
Awa si mazibusa athuwa ndioyipa mtima guys zioneni nkhope zaozo
@EvansEgra
@EvansEgra 4 күн бұрын
Mungowononga ndalama za ziiiiiiiii, Malo momagulira chimanga anthu akufa ndi njala, anthu wopusa inu, Apa mukubwera ndizizungu zopusa apa.
@TiagoAfonso-y9m
@TiagoAfonso-y9m 3 күн бұрын
Tikungofuna kudziwa amene anamuuza in president kuti ndege inafika ku in nzuzu ndikuibweza ku Kia ndi ndani? Basi zinazo ndi zanu
@MjombaMoosa
@MjombaMoosa 4 күн бұрын
Inu anthu a MCP muzatipombonetse pamene tikulongosola za ma id a kukanengo mubweleza nkhani Ina pamene timalongosola za zikwanje munabweleza nkhani za a chikangawa muzatitole mutelo
@MarryMartin-z6u
@MarryMartin-z6u 4 күн бұрын
Kodi ndi report or maloto? Mukuyakhula zomwe sizinachitike bwanji?
@GiftLanjesi
@GiftLanjesi 4 күн бұрын
Ife ndi amalawi chomanenela chizungu ndi Chan, chakwela anat inakafika Ku zuzu awa akut sinafikeko ati chani atinyasepo apa akagwele
@JumahAlie-r8p
@JumahAlie-r8p 4 күн бұрын
Kodi bwanji sakuyankhula common language yakwatu kuno kuti tose tive nawo ife ndamalawitu chatu ndichichewa kuno
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 4 күн бұрын
Ndipo. Za ziiiii basi
@FatsanNyanda
@FatsanNyanda 4 күн бұрын
Bora latulukali sizimene zimafunika
@DeJocrown2685
@DeJocrown2685 20 сағат бұрын
Ndoye zoti ndege inakafika mu mzuzu anazitenga kuti?
@CLIFORDZAKARIA
@CLIFORDZAKARIA Күн бұрын
This very Unprofessional enquiry, very useless
@M.shukriAdams
@M.shukriAdams 4 күн бұрын
Imfa ya chilima enanu mwalemera nayo Koma chuma Cha magadzi chimasatira mwini
@ElickBanda
@ElickBanda 4 күн бұрын
Tinvane akila itimasulila chizungucho😊
@LufingoMulungu-z7u
@LufingoMulungu-z7u 3 күн бұрын
Tiuzeni mu chichewa bhohbo amadise
@EvanceWame-v7v
@EvanceWame-v7v 4 күн бұрын
The Malawian citizen they are taken like fools by the government, this is nonsense
@MacdonaldMasamba-e2x
@MacdonaldMasamba-e2x 3 күн бұрын
Black box ili kuti??
@MikeMbewe-mb9it
@MikeMbewe-mb9it 4 күн бұрын
Ndekut akutiuza kut kukakhala phepo ndivula nde kut ndege zose zimagwa kapena phepoyo inaona urendo wa a chilima omwewo
@MikeChisale-g9k
@MikeChisale-g9k 4 күн бұрын
Enanu munangokha anthu otsutsa paja mumanyoza chilichose.ngat simukuvapo fusan kwanzanu akuzan
@DhlaminiBudex
@DhlaminiBudex 5 сағат бұрын
Anthuwa akunama fukwa nthawi imene inachitika Ngozi Ife enafe timapita Ku Mzuzu Koma pa nthawiyo tisanafike Ku Mene kunapangika Ngozi kunalibe Mvula komanso panjira Pana yimilira anthu achilendo awiri Koma anayang'ana kumene kunachitikira Ngozi mumanja mwawo anagwira ma laptop ndekumanamiza anthu kunali Mvula kutiko
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 4 күн бұрын
Waiting for 3rd commission of enquiry into the aircraft accident
@JohnSailes
@JohnSailes 4 күн бұрын
Wakuba samazigwila ekha sizingatheke tizaziwa chenchen mukazachoka boma lelo ndinu dolo koma muzakumana nazo kunali azanu lelo alikuti
@josephykwendah2210
@josephykwendah2210 3 күн бұрын
Muziyankhula chichewa kuti agogo kumudzi azinza nawo
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 3 күн бұрын
Apa akuwuza aku Israel
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 4 күн бұрын
This rhetoric about the weather seems to want to reinforce a narrative. If it was so bad why did the seasoned pilots fly the plane?
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 3 күн бұрын
Fiti zokhazokha zili umu
@nelsonnkhambule6292
@nelsonnkhambule6292 4 күн бұрын
Westing time for nothing athu akuziwa kale kut pama udindo amaphana mnaphana mngodikila yanu nanuso siku
@MrsMtira-f2u
@MrsMtira-f2u Күн бұрын
Kd kumalawi timayankhura chizungu? tonse timamva Chichewa yankhulani chichewa kt tonse timve osati zomwe mukuchitazo ayi
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 4 күн бұрын
Zimenezi kodi mukumulongosolera ndani?,oti eni wake okhuxidwawo anapempha kafukufuku wa live,anthu opanda mizimu ngati inu
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 4 күн бұрын
Ndinu zitsilu kwambiri 😢😢😢😢akaporo olemela mwachinyengo indeed moto ukudikila inu.... Mulape ...
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo 4 күн бұрын
Black box...black box...black box...black box...........??...???...????...????
@AngelineDumha-ec5le
@AngelineDumha-ec5le 4 күн бұрын
Vuto anthu mukufuna report linene zomwe inu mukuganiza kuti mupite mukawauze anthu ofufuza umboni umene mulinawo mukulephera
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 4 күн бұрын
Mkunena zoona vuto ndilomweli aliyetse akufuna zomwe aganizila bonzore zeni zeni
@MikeChisale-g9k
@MikeChisale-g9k 4 күн бұрын
Eya sukunama anthu aDpp akufuna kt ofufuza anene zabodza ngat momwe iwowo akunamizila anthu ndipo ndizimenezotu zakutsutsan ndimomwe mumaganizila
@LottiAffati
@LottiAffati 4 күн бұрын
afiti inu tamayankhulani chichewa inu bwanji kodi cholinga chanu nchan kodi aaaa inetu zimandiwawa pa imfa imeneija
@gracemaluwa4674
@gracemaluwa4674 4 күн бұрын
Chichewa bwanji,
@StuartMkandawile
@StuartMkandawile 4 күн бұрын
Inquiry iyo ndiyawo a mcp
@ASAMOHGvN
@ASAMOHGvN 4 күн бұрын
Why amalawi mumakakamila English koma report ikupita kwamalawi aaaa fire stupid report
@EmmanuelStanzio
@EmmanuelStanzio 4 күн бұрын
Athu awa ayi ndi afisi okha okha, ife athu aku, chiladzulu tanyasidwa ndipo chakwela asazafikeso ku cz ,azaona mene tizapangile.
@MikeChisale-g9k
@MikeChisale-g9k 4 күн бұрын
Mfisi oyamba ndiwe mesa umafuna kt anene zofuna zaiweyo wachita manyaz
@AbdulMalik-o7n1q
@AbdulMalik-o7n1q 4 күн бұрын
Chizungu kufuna anthu osaphuzila omwe amavota asavenao kuti aziwakhulupililabe za ufiti
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 4 күн бұрын
Ndichomcho kumene...koma akunamatu
@AsaniFelix
@AsaniFelix 4 күн бұрын
R u telling the Queen family as ur colonial power or telling malawians?
@ChikkaLemani-qw6fn
@ChikkaLemani-qw6fn 4 күн бұрын
Are you serious? 😭😭😭
@kidaMarion-g5v
@kidaMarion-g5v 3 күн бұрын
😮
@Fkaymw1Kadango-by5mu
@Fkaymw1Kadango-by5mu 4 күн бұрын
Ubwino wake Mulungu a naona, zonse
@PhiriVictor-e9l
@PhiriVictor-e9l 4 күн бұрын
Bola mwapeza ZANU ndalama chilima.sangabwelenso azaweluza yekha yawe
@rabsonswathera738
@rabsonswathera738 2 күн бұрын
That's all useless report
@moffatmuhome3155
@moffatmuhome3155 4 күн бұрын
This is ABSOLUTE HOGWASH, Shame on you.
@AsaniFelix
@AsaniFelix 4 күн бұрын
Y malawian civil servant don't respect their own language nd culture? They Upgrade nd give more attention to the colonial powers by using English as their own language? R the malawi government ofinicial coconuts? White inside nd black outside? R u still colonize?
@StuartMkandawile
@StuartMkandawile 4 күн бұрын
Black box yilikuti maboza basi mulungu anaona kale zonse amenya nkhondoyi
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i Күн бұрын
All this is rubbish
Beat Ronaldo, Win $1,000,000
22:45
MrBeast
Рет қаралды 158 МЛН
Europe's Missing Trillions
10:01
Bloomberg Originals
Рет қаралды 621 М.
Rusland na de Sovjet-Unie: waarom is het zo misgegaan? | Peter Demant | HOVO Amsterdam
14:30
HOVO Amsterdam, Vrije Universiteit
Рет қаралды 6 М.
USAUVER S10E07 - RECEPTION
26:30
Piksy TV
Рет қаралды 52 М.