Zeni Zeni zake Zokhuza Chakwera

  Рет қаралды 19,429

Jay Kawere TV

Jay Kawere TV

Күн бұрын

Пікірлер: 151
@SaudhaKatete
@SaudhaKatete 26 минут бұрын
Mr Ntanyiwa I salute u man
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 3 сағат бұрын
Uyu chimwendo mnmm he is full of himself. May God punish him
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Сағат бұрын
Ok
@HenryKeyala
@HenryKeyala 16 минут бұрын
Ngati wafa nde zilibwino bwanj❤
@cmsanyama200
@cmsanyama200 2 сағат бұрын
Honourable Mtanyiwa you really have shown maturity here as a journalist,bravo to you!
@OwamThoko
@OwamThoko 2 сағат бұрын
Tipephelele kuti asafe chakwela pls,ali ndi ma answer oti atiyankhe pa nkhani ya imfa ya olemekezeka late Dr saulos chilima.bcz ngati angafe ameneyo onse onkhuzidwa pa nkhani imeneyi azangoti ndi a chakwela anatiuza.popeza iyeyo wapita Mapeto ake pazakhala opanda omboni.
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 2 сағат бұрын
Kuti asowe kkkkk
@RuthMkandawire-l8d
@RuthMkandawire-l8d 2 сағат бұрын
Iweso zachani nawe
@RashidPiano
@RashidPiano 2 сағат бұрын
Wafa bs Or Abise km Timukwilila Bs Uku Tikusekelela Ndipo Malilo Amene ndi olila Anthu Okha Okha Akubanjia Osati ife😂😂
@RahimLuemba
@RahimLuemba Сағат бұрын
Bravo comrade u real deserves
@TimeAbilu
@TimeAbilu 2 сағат бұрын
M'mati yimilira comrade mtanyiwa Allah bless you all the time, to fighting freedom
@SusanaMakanga
@SusanaMakanga Сағат бұрын
Mmmm Malawi Basi kumangoganizirana zoipa basi Mulungu Akadalitsa wadalitsa 🔥 All the best Mr President
@PhahlaniMugaba-e8r
@PhahlaniMugaba-e8r 27 минут бұрын
Justice delayed is justice denied
@SilenceChepiano
@SilenceChepiano 2 сағат бұрын
Ngati alimoyo akanaveka mawu
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 3 сағат бұрын
Comrade Ntanyiwa umatimilira,, viva comrade viva
@ElizabethFatch-o3w
@ElizabethFatch-o3w 39 минут бұрын
Zikomo Mr ntanyiwa timakukondani Mr ndipo mumakonda mtundu wa mfuko lanu ambuye adzikudalitsani chikufa kwa amene akanatha kufa imfa yosalakwa kathu koma Ili ndi chenjenzo lanu
@shavickmzulamzula7012
@shavickmzulamzula7012 20 минут бұрын
Mulungu si Muthu achira😢
@melnisachagwamnjira6082
@melnisachagwamnjira6082 2 сағат бұрын
Kulibe kumwalira ataaa boma ndilomweli mpaka 2030
@MadalitsochristopherMagalasi
@MadalitsochristopherMagalasi 2 сағат бұрын
😂😂😂😂
@RUNBWOY
@RUNBWOY Сағат бұрын
😢
@RhodaJere-f7o
@RhodaJere-f7o 2 сағат бұрын
Zikomo kutiyimilira zose tivera Kwa mthanyiwa
@StanleyChamasowa
@StanleyChamasowa 2 сағат бұрын
Ndipo akamwalila chinwendo kunkuyu ndi team nyamazikukuzikulu akonzekele
@SaidMkonongo
@SaidMkonongo 2 сағат бұрын
PAlibe kumupepherera azipita kumanda basi misonzi ya mary chilima iyankhidwe basi
@MakabaBauleni-c2i
@MakabaBauleni-c2i Сағат бұрын
Ambuye ikani zanja lanu la machilitso kwa mtsogoleri wathu L M Chakwela 🙏🙏
@LoleniShabani-mt7nz
@LoleniShabani-mt7nz Сағат бұрын
Let him go
@VeraBeab
@VeraBeab 38 минут бұрын
Nyapako iwe apite ameneyu
@FeliaNgunga
@FeliaNgunga 2 сағат бұрын
Bisani matenda maliro atipeza pasanathe week, wapita wapita, no wat wat bon voyage 😂
@MikeLodzi
@MikeLodzi 2 сағат бұрын
pa inu amtanyiwa timadekhatu
@UthmanKapungu
@UthmanKapungu Сағат бұрын
Anthu ndi masooooo kuchokera Ku hospital kufikira Ku golf
@AnaphWanja
@AnaphWanja Сағат бұрын
Km mukuti zowonadi za chakwera
@JerieWytonTengani
@JerieWytonTengani Сағат бұрын
A Michael Utsi osawanamiza anthu tinned kuti character ichi chikubwelachi Chakera akusiilani kuti mukhahle pa upresident poti panali mgwirizano popeza a chilima anaphedwa? Inu Muima? Osamawanamiza anthu a UTM bwelelani mmbuyo Mathieu asanathe .Chakwera Singapore ndi pang"ono pomwe, ndiye waupodatu bwanawe.
@BatumeyoChikopa
@BatumeyoChikopa Сағат бұрын
Mhsrip Mr chilima and 8 others😢😢😢
@VeraBeab
@VeraBeab 39 минут бұрын
😢
@NikiweKavalo
@NikiweKavalo Сағат бұрын
Healing mercies 🙏🙏
@CameronVisser-k7i
@CameronVisser-k7i 2 сағат бұрын
Asathawe milandu
@NumeriChibowa
@NumeriChibowa 2 сағат бұрын
Ada amenewa atamawalira zikhala kuti Mulungu wamenya nkhondo yekha chifukwa bodza analonjeza Amalawi yodya katatu, Malawi okomera aliyense ntchito 1miliyon koma osakwanilitsa ndipo ena kumamufunabe zingoziwikilatu kut ku dziko kuno kuli asatana ambiri Panopa anthu akudya zitedze kumadya zofana ndi chinangwa kumamwalira zinthu zikungokwera daily kwacha anayimaliza kale kuigwetsa ndipo ndalama yathu yasanduka yopanda ntchito umoyo ukulimba kwambri Ambuye atichitre chifundo ife Amalawi
@SusanaMakanga
@SusanaMakanga Сағат бұрын
Kkkkkk Alomwe Inu chaka chilichose njara imakuvutani or nthawi ya peter Munkafaso😂
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 3 сағат бұрын
Amwalilebasi watikwana😂😂😂
@duncainjimmy
@duncainjimmy 2 сағат бұрын
Ame, MULUNGU NDIE MWINI KUWERUZA MUNKHANI NGATI ZIMENEZI. Chisoni channga chilipoti why Dr Chakwera kusiya Mulungu wanu ndikumatannda satana amene munyengo zowawazi amakuthawani
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 2 сағат бұрын
AKANGOPANDA KUFA CHAKWELA NDIKHUMUDWA KWAMBIRI MWAMVAAA???
@noelchilimira
@noelchilimira 2 сағат бұрын
don't wish people to die ....iwe ukuyankhulawe bwanji ukufuna kukhala ndi moyo
@PeterChipwaila
@PeterChipwaila 2 сағат бұрын
Wakhumudwa kale
@Daniel-cf4tu
@Daniel-cf4tu 38 минут бұрын
😂😂😂 msogoleli waziko emweyi mwatiuza kuti wamwalilayu?
@isaaczuze
@isaaczuze Сағат бұрын
Chakwera akuyenela kufa basi ....galu iwe unapha chilima iweyo suzafa ....chisilu cha munthu iwe
@HopesonBuledi
@HopesonBuledi 2 сағат бұрын
Mwachidule tingoti amalawi akufuna Chikangawa atafa basi
@RabeccaMwikho-f9h
@RabeccaMwikho-f9h 2 сағат бұрын
Ndipo osakaika kkkkkk
@RaffickAllie
@RaffickAllie 2 сағат бұрын
Manyi saphimba.pangatalike chirungamo tizachidziwa
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 40 минут бұрын
Inutu musamatinamize nokha mukuti afa nokha akupita ku golf timve ziti
@KhaliluGiftMasala
@KhaliluGiftMasala Сағат бұрын
Mulungu ndiye adziwa zonse ukamapanga zoipa uziyembekezera kumwalira imfa yowawa chilungamo chake bwana chakwela amwalira
@MaxwellChaminju
@MaxwellChaminju 2 сағат бұрын
Ameneyo Afe bas sitikumufuna ife Ndi galu
@naomikumwenda7150
@naomikumwenda7150 Сағат бұрын
Kwabasi
@WickRossKaliraniKalirani-z4c
@WickRossKaliraniKalirani-z4c 2 сағат бұрын
Mwati bwanji pamenepo bisani matenda koma chaaaa.......😂
@BairdThomas-c2k
@BairdThomas-c2k Сағат бұрын
ngt alimoyo ine ndiye zindinyasa chifukwa zisangaralo tinayambapo pa c z pa m and m pano amtanyi tafufuzani kachikena mutiuze zoti wafa tipitilize kukondwela
@FatimaAtibu
@FatimaAtibu Сағат бұрын
Malawi will change, imagine chakwera waduwa then 😂😂
@StevenKamtsokwe-zn4vr
@StevenKamtsokwe-zn4vr 2 сағат бұрын
Tiapemphere kut asafe ingakayambe kubukatu ndeu kumwambako Nd chilima at wafa
@PaulKapichi
@PaulKapichi 2 сағат бұрын
Antanyiwa apo mwanama
@RabeccaMwikho-f9h
@RabeccaMwikho-f9h 2 сағат бұрын
Nde tiuzen inuyo zilungamo
@SusanaMakanga
@SusanaMakanga Сағат бұрын
Ndie atafa lero Agaru inu Mungalamulire dziko?Ndichifukwa chake Njara ikumakunyenyani Tamadyani zitedzezo boma Sitikusintha
@IsraelWanyemba-l7u
@IsraelWanyemba-l7u 3 сағат бұрын
Abale ambuye ndi wakumva sakhala chete pa ana akee Yoh mkulu uyuu wazuza Malawi ngati si dziko lake
@VeraBeab
@VeraBeab 39 минут бұрын
Apite uyu tatopa naye uyu
@TameeraInglis
@TameeraInglis Сағат бұрын
Kkkkkkkk tsono Golf akasewela bwanji? Ayi ife athu. Ndimaso mawa kapena saturday bisani matendawo Maliro tidzamva
@McshonWilliam
@McshonWilliam 2 сағат бұрын
Kodi chimwendo amazitenga ngat malawi ndi wake eti
@jumawoposi4016
@jumawoposi4016 3 сағат бұрын
Yes biggy
@MillieMalakam
@MillieMalakam Сағат бұрын
Kod guy's wabakili sapulise kod
@MaxwellKapalamula
@MaxwellKapalamula 2 сағат бұрын
Abale ndatopa ndza chakwera
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e Сағат бұрын
Kodi Ku MCP kuli chimwendo yekha ?chifukwatu fiti imeneyi tatopanawo
@RabeccaMwikho-f9h
@RabeccaMwikho-f9h 2 сағат бұрын
Munaziyamba dala kupanga chiwembu game changer kkkkkkk inu mumati muta mufa muthothoka
@NhlemahJacob
@NhlemahJacob 2 сағат бұрын
😢😢😢😢 no life bas
@MathewsChitsulo
@MathewsChitsulo 2 сағат бұрын
Sitingamufunile zabwino chifukwa iye sianafunile zabwino Chilima ndi anthu ena 8 amene afela mphepete mwa Mudzi iye akumwa fanta ku state house
@JerieWytonTengani
@JerieWytonTengani Сағат бұрын
Ine iyeyo asachile manganese.
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o Сағат бұрын
Alomwe ndinu zisilu kwabasi ndipo mulibe nzelu zaumunthu
@MarthaPhiri-q8m
@MarthaPhiri-q8m Сағат бұрын
Panyapako wava
@ReginaMulipa
@ReginaMulipa 28 минут бұрын
Unya uona alikuno uyu ku South Africa kulibe moyo kuno ndangoyandikana nayeso chipatara chake 😂😂😂 akupitaso kwa america apa akapangidwe Zina ndi Zina kkkk
@xinalungu9616
@xinalungu9616 Сағат бұрын
Koma mabodza amalawi tidzawasiya liti?
@AlfredsencoSeleman
@AlfredsencoSeleman 3 сағат бұрын
Akasewela bwanji golf ndidzanja limodzi??
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 сағат бұрын
Mposo inu
@ivymakiyi
@ivymakiyi 3 сағат бұрын
Cry cry until you cry no more
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 3 сағат бұрын
Inu achakwera kulibe wapita kukapangidwa embum komwe anali kuja kwa America tsegulan Alhazeera mumvere
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 3 сағат бұрын
Mmmmmh serious
@giftsululu4274
@giftsululu4274 3 сағат бұрын
Maganizo asatana
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 3 сағат бұрын
Serious
@OssmanAbubaker-m5u
@OssmanAbubaker-m5u 2 сағат бұрын
Bola akanafa chakwera yo watikwana kwambiri Satana kumupha mzake iyesoafe
@RusselleStanley
@RusselleStanley 2 сағат бұрын
2030 woooo!
@AbrahamManyenga-v1g
@AbrahamManyenga-v1g Сағат бұрын
The sole reason I don't follow your stories, full of speculations based on fiction
@McshonWilliam
@McshonWilliam 2 сағат бұрын
No scrate under the sun 🤣🤣🤣🤣dj song done by chimangeni
@BensonGama
@BensonGama 2 сағат бұрын
Kodi zonse zikukambidwazi mneneri wakunyumba ya boma kapena nduna yofalisa nkhani sakuzimva bwanji osatengapo gawo kt anthu asiye kubwata
@KondwaniSamson-py9kq
@KondwaniSamson-py9kq Сағат бұрын
Mwadya zambiritu inu za DPP or atapanda upitako Pali vuto
@PatumaCassim
@PatumaCassim 2 сағат бұрын
Kkkk😂😂😂mukuziwapo Kathu inu hiyaaaàaaa😂
@MasterJailos-kv5sd
@MasterJailos-kv5sd Сағат бұрын
Akuyenera kusatira chilima
@BrightSoliumFalcon-cw4nx
@BrightSoliumFalcon-cw4nx Сағат бұрын
Koma guys kwayaka iiiiish
@CHRISMWAMS
@CHRISMWAMS 2 сағат бұрын
Nkhan ibwele apule 😢
@YatoRoy-kt4lh
@YatoRoy-kt4lh Сағат бұрын
A Decoy will be around
@RuthTimothyChirwa
@RuthTimothyChirwa 2 сағат бұрын
2030 woooo ❤😂😂😂
@FelixDuli
@FelixDuli 55 минут бұрын
Awuse muntendele
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem 3 сағат бұрын
awuze anzakowo kuti big man ili moyo😂
@giftsululu4274
@giftsululu4274 3 сағат бұрын
Amuize Cadet mzake kut abwana zakudya pizza pano
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Сағат бұрын
@@giftsululu4274 mpake 2030 tiki naye naye
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 3 сағат бұрын
Mmmmm..unamiiiiiiiiii
@JuliaKalinga-t2x
@JuliaKalinga-t2x 2 сағат бұрын
Tieni tingozisia manja mwamulungu bas
@MathewsJanuary
@MathewsJanuary 2 сағат бұрын
Atamupephelelere ndi apabanja ake osakhala ife amalawi.
@IshumaeliIburahimu
@IshumaeliIburahimu 2 сағат бұрын
Akatipelekele malonje😂 kumene kukupitako
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 2 сағат бұрын
RIP chakwera
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 3 сағат бұрын
Sindingataye nrhawi kumamupwmphwrera chakwela alibe phindu,imfa yachitsilu mulungu amakondwela nayo
@S-rr1eu
@S-rr1eu 2 сағат бұрын
😂 amwalire ,,,,, mizimu ya MALAWI imukhobole afe
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 2 сағат бұрын
Boma lomweri 2030 wooooooo
@MosesChazima
@MosesChazima 2 сағат бұрын
Zikut atha uza alimoyo kod aaaaa
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 сағат бұрын
State to the point comrade
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 2 сағат бұрын
Koma mtanyiwa😅😅😅achirenso?ameneyo apite basi
@LevisonMzava
@LevisonMzava 3 сағат бұрын
Tiuzeni zambiri
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 3 сағат бұрын
Mdima ukakula kunja kuli pafupi kucha mulungu atimenyela nkhondo.
@SusanaMakanga
@SusanaMakanga Сағат бұрын
Chilimayo Anali yesu kuti asafe?Zankutuuu
@Desmond-q7r
@Desmond-q7r 52 минут бұрын
Ndiwe mbuzidi
@LymanKafwala
@LymanKafwala Сағат бұрын
Apite bas
@OsmanMsusa
@OsmanMsusa 3 сағат бұрын
Tanyiwa akuti chotsemba chindakumana ndichokwawa
@ChapwetekaChauluka
@ChapwetekaChauluka 57 минут бұрын
Comrade palibe zomupemphelera apaa!
@RuthLongwe-c3y
@RuthLongwe-c3y 2 сағат бұрын
Antanyiwa pemphero la pre mupemphera nokha pokhapo
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 Сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 сағат бұрын
All de best
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 3 сағат бұрын
Popano tanyiwa atiwuza zosatira zonse
@MosesChazima
@MosesChazima 3 сағат бұрын
Tiuze zowina tanyiwa kt tiysmbe kuimba yokoma
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 сағат бұрын
Wasala Chimwendo nayenso amwalire ndithu
@MichengaPeterIbrahim
@MichengaPeterIbrahim Сағат бұрын
Zabwino zonse ayende bwino kkkkkkkk
@RaffickAllie
@RaffickAllie 3 сағат бұрын
Changu please.palibe kupereka za sposers comrade
@IbrahimMatola-h4i
@IbrahimMatola-h4i 2 сағат бұрын
Zenzen ndizoti wamwalira
@EffitaKandiwo
@EffitaKandiwo 2 сағат бұрын
Muli ndi umboni?
@IjilanMwalija
@IjilanMwalija Сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂eash
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 Сағат бұрын
Aaaaaah😂😂😂😂😂😂
Nkhani ya Chakwera mene zili inu mukuti bwanji?  Chakwera
5:58
Jay Kawere TV
Рет қаралды 73 М.
She's very CREATIVE💡💦 #camping #survival #bushcraft #outdoors #lifehack
00:26
Кәсіпқой бокс | Жәнібек Әлімханұлы - Андрей Михайлович
48:57
🍉😋 #shorts
00:24
Денис Кукояка
Рет қаралды 4 МЛН
🕊️Valera🕊️
00:34
DO$HIK
Рет қаралды 1,1 МЛН
Chikuchitika ndichani Amalawi 🤔
2:21
Malawian Cameras
Рет қаралды 28 М.
TIKUDZIWENI - 25 FEBRUARY 2019
33:12
Times 360 Malawi
Рет қаралды 109 М.
MUIMBI HOSIAH CHIPANGA MUDARE RAMAMBO MUTASA VS LEON MATESVA  KARANGANDA TV KUTORWA KWEMUNDA
18:01
Kodi nkhani iyi mwaiva zoti Chakwera.
4:05
Jay Kawere TV
Рет қаралды 47 М.
KHASU-Malawian movie_PART 1[Akila films official 2024.]
1:06:28
Akila Entertainment
Рет қаралды 211 М.
She's very CREATIVE💡💦 #camping #survival #bushcraft #outdoors #lifehack
00:26